Ndiye mumpezawina jecket ilibi lisilo mukolalamu avekele mulungu Kulibe ati mwiniwakeyo anachita kuva kuchokela kwazungu.pomwe man of history is here and akushula dzila lamulungu molilemekeza komatso mosimikiza kusonyezazoti iyeyu ndimunthu oti amakhulupilira kuti kudzikokuno mulungu alipo.kmatsotu inuyo abakili muluzi mutati muyambe ubusa ziwanizoti church chanucho chikhoza kumazaza heavy
Watching from Israel kumunda
Kkkkkkk mulipaufulu yeti kkkkkk
I love this my brother, I ask Allah to give you more life
Ameen
Just a small point at the beginning. Scientists use telescope not microscope to look at distant objects in the sky.
Just a slip of a tongue
Big man u always discover undiscoverable u r the great of the greatest much love from Lusaka Zambia 🇿🇲 🇿🇲 🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲🇿🇲
I see you brother
I love you too much bakili muluzi tv
Brother ineyo kumalawi kuno sindikumuonanso munthu wa sayasi ngati inuyo anthu amene akuba ndalama zabomawa ndikumakweza zinthu pansika sikulina mulungu azawaonesera china chake ndpo azadadwa zonsezi azazisanza ndthu zonsezi mulungu akumuona watching from Mozambique never give up bg brother timakunyadirani kwambir potiwululira zisisi zobisikazi zambavazi
Watching from Krugersdorp south Africa malawi from ntcheu Austin village am jafali
This channel is the best ever 🎉🎉
I respect you brother man!! Keep it up!
IWE KOMA UMATHA...... USAZAFE UZANGOSOWA 😂🎉😅🎉😂
Love you so much some times I just repeat watching your vedios as part of contribution . May God keep you safe
Ine olo ku school ndinapita koma kunena za bakili TV history ndi #1💪
Thank you Sir.
Well spoken 👏
Inuyo ndi mphuzisi wa history
Bakili muluz TV the great news
Eeeeeee chiyambicho 😂😂😂🔥🔥🔥🔥
Kkkkk
😂😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂😂
😂😂😂
😂😂😂😂
Zaphamvu keep it up brother
Best tv ❤❤❤🙏🙏🙏
Powerful keep it up
Watching from Venezuela in Caracas ❤❤❤
Thanks boss you are a great analytics on national affairs
Listening you from vubwi district Zambia eastern province
Ipondeni fadah
I like this Chanel guys lnuyo mumatsa kufukura mozama brother. Ulemu wanu.
Listening from Johnsburg love you much brother 4:27
salute to this man, i can verify that most of the information he has highlightened here is well read from scholastic books.......
Bravo brother we do hear sensitive issues from u, keep up the good work
From lusaka❤
Chiyambicho😆😆😆😆😆😆koma abale
😂😂😂😂
😢😢😢😢😢😢
Watching from RSA DN
Your great person sure
Following from Antananarivo, Madagascar🎉
Watching form Vaal University we proud of you Boss
Our big brother our hope we love you boss
Big up brother always with you ❤❤❤❤
Thanks brother for news
This is great I like it brother
Watching from Eastern Cape Port Elizabeth
Watching from Phalombe
Iweyo umatha kulongosola momveka bwno I like dat..enjoying from Russia.
❤❤ I like forever mulungu apitilize kukudalisana mukhale anthanz ❤🤝🤝
Great job🔥
Zodabwisa timavela kwayinu big man mulungu akupaseni luso lopambana ❤❤❤❤❤❤❤
You are the great man
I love you bro all the time and my allah guide and protectyou all the time🇲🇼
Ada a BMtv amandiwaza,kumapetoko mwaimaliza bwino heavy
You're best bro God bless you
❤❤❤Bro keep it up
I love you so much bakili muluzi tv
All the best🎉
Keep on moonlight Nyasaland mr man
Best journalist ever!
my brother keep it up and kulibenso wina kumalawi angamake kufotokoza zinthu
Inuyo ndi one ndpo mulungu akuze malire amoyo wanu ine Doreen kuno krugersdrop kumalawi kwathu kumwanza❤❤❤❤
Peleka nambalayo tiuzane zina ndizina iwe Doreen kkkkkkk
Ur the best
Watching from Johannesburg
History ndinamenya koma iwe ndi dhilu keep it up biggy
Keep going brother
Ndipo live from cape Town pa boma much love
Powerful massage
Timakunyadila man kwambiri ❤❤ ❤
Long live brother🎉🎉🎉
So educative
Mbambande brother
Adawa amandivesa kukoma saname ❤❤❤
Mumakwana big💥💥🔥🔥
We love you bro
History ndimamenyad koma inuyo ndi akatumdu,zikomo kwambiri Bakili mukuz tv wanu from Zambia
Thanks bg MN potipasila nkhaniyi yasala
Big up
Best tv ever ❤❤❤❤
Tsiku lina uzangoika ka tone kokhako tizavineko😂😂
Nice boss
Inuyo boss ndi Mfumu mumatha zedi Malawi yonse mulibeyi size yanu boss❤❤
Kkkkkkkkkkk kmatu funolesi anthu osauka kudziwa mbalume nde iweyo miyalayo singakuswinja
Always following sir Bktv
Watching from port Elizabeth south Africa mumakwana inuyo pitirizani kutipatsila zabwinoz
New syllabus explains new developments related to solar system. Exclusion of Pluto is one of these new developments..
Kept up
Never give up bro
BMTV ND I 1 I LOVE THIS TV FOREVER FORGOO
Good is great
Ndipo anthu andale aku malawi mulungu awafikire ndithu akuzuza anthu dziko lathu ili kuzikundikira basi
Great reason
Umakwana Man 💪
Iwe ndi dolo 🔥🔥🔥🔥
Umakwana Bakili Muluzi...❤
Bakili TV 🔥🔥💪💪
Ndiye mumpezawina jecket ilibi lisilo mukolalamu avekele mulungu Kulibe ati mwiniwakeyo anachita kuva kuchokela kwazungu.pomwe man of history is here and akushula dzila lamulungu molilemekeza komatso mosimikiza kusonyezazoti iyeyu ndimunthu oti amakhulupilira kuti kudzikokuno mulungu alipo.kmatsotu inuyo abakili muluzi mutati muyambe ubusa ziwanizoti church chanucho chikhoza kumazaza heavy
inu mumatiyimilila i love you two much
Best tv ❤❤❤
Bakili Muluzi TV, imatiimilira timaziwa zambili through this channel.
Respect bk tv
Adzasiyila ana awo
Ngati ndiliretu pomvera audio iyi, zikomo kwambri big brother.
Zikomo tadziwa nawo, geographytu iyo kulephera nkufuna.
I love u brother
Koma inuyo big mumativesa kukoma inuyo ndi number 1 palibeso winaaa
Best tv number one
Best TV ever
Kkkkkk mumakwana mkoziiiii
I like this tv