Palibe Anganditume Ine Kuti Ndikasake Munthu - Mike Chitenje aka Bangwe One

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 23 тра 2024
  • On Nyasa VoiceBox, Businessman Mike Chitenje aka Bangwe One refutes claims that he is one of the alleged individuals sent by government to hunt down Owner and Manager of Bakili Muluzi TV.
    Ku Nyasa Voicebox, bambo Mike Chitenje aka Bangwe One akutsutsa zoti ndi m'modzi mwa anthu omwe akuganiziridwa kuti anatumidwa ndi boma kukasaka Mwini komanso Manager wa Bakili Muluzi TV.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 83

  • @user-zk7jw9up6m
    @user-zk7jw9up6m 2 місяці тому +13

    ADPP anakhapidwa kulilongwe bwanji ngati muli madolo simukuwasaka mukulimbana ndi mfana wa bakili tv mknkuyu nkhani ya witika isakupweteke ukuziwapo kanthu

  • @alexsumani6823
    @alexsumani6823 2 місяці тому

    Thumbs up Mike for coming open and clear yourself and kuyankhula kwambiri,kuyipisilana mbiri baasi

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos 2 місяці тому +1

    Kuno ku South Africa bwerani koma sumuzabwerera bakili tv is our Chanel

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 2 місяці тому +4

    MCP ngati mumapha anthu ndikale lomwe lija not now nthawi munapha achinagama aja.
    MCP Ndichakwela emweyo pantumbo panu

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 2 місяці тому +1

    Aaaaaa akunama sangampedze bakili muluzi

  • @giftdulamkalenga7344
    @giftdulamkalenga7344 2 місяці тому +2

    Amalawi Ali ku south Africa Ali ndi mifuti yambirimbiri Koma ndi zitsiru zosagwirizana akabwera ziombelani KOMKO

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 2 місяці тому

    🔥🔥🔥🔥

  • @LeonardjSteshy
    @LeonardjSteshy 2 місяці тому

    Abwelele komwe anachoka💪💪💪

  • @QueneteCatundulo
    @QueneteCatundulo Місяць тому

    Good

  • @user-mm3es3ph7h
    @user-mm3es3ph7h Місяць тому

    Brother man Bangwe one ,mumatiyimila.

  • @successm-vt3dx
    @successm-vt3dx 2 місяці тому +2

    nyasi zanuzo kumalawi konko kuno mudzamenyedwa ndi azimayi

  • @LamieTiger
    @LamieTiger 2 місяці тому

    Koma ndizot south Africa angakudulekhos sangaziwike usayelekedze kusaka muthu abweleekha ofalitsa uthengayo

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 Місяць тому

    Wayakha bwino Brother amphawi awa asiyeni

  • @StainDandize
    @StainDandize 15 днів тому

    Ma💯👍

  • @OwenJambo
    @OwenJambo 2 місяці тому

    Auze bro akanganya amvesese bho

  • @user-zi8pj5ey4t
    @user-zi8pj5ey4t 2 місяці тому

    Atha kupita ameneo asaname ameneo

  • @mayesojameskatete
    @mayesojameskatete 2 місяці тому

    Abwele ku south Africa kuno tiwaphela konkuno manyiwo azipanga ku Malawi komweko

  • @NelsonMoses-t6t
    @NelsonMoses-t6t Місяць тому

    Kunkuyu ndiwe opusa kwambli zoona uzikhara ulimbana ndi za pa social media

  • @user-vb1iq5un5p
    @user-vb1iq5un5p 13 днів тому

    Nanga boma limasankha omgwilitsa ntchito? Mmesa amapereka chithumba?.. ndizowona ..komanso akati Ali ndi ndalama kale ,ndalama zimakwana..palibe akulimbana nanu atopwa...utsi sufuka popanda moto. Chilipo chomwe chachitika...

  • @user-qi8xe7qh1e
    @user-qi8xe7qh1e 2 місяці тому +1

    Komanso akamanena kuti akufuna awathandize kuti alowenso m'boma akuthandauza chani anatumidwadi garu ameneyu

  • @ThivadoartistDyson
    @ThivadoartistDyson Місяць тому

    Apite ku South Africa adzathela konko

  • @chimajrbhahat2334
    @chimajrbhahat2334 2 місяці тому

    Kuno ku SA zopusazo ayi ndale zaku malawi osabweletsa kuno anthu olephera. Musiyeni bakili muluzi TV limbanani ndi mbava kwanu konko anthu a MCP opanda chikondi ndi amalawi anzanu

  • @hakimbaiton
    @hakimbaiton 2 місяці тому

    Ngati mumapha nhthawi imeneyo si panopa ayi akukuyu abwele yekaha tsake yekha osamawatuma anthu kufuna kuphesa osalakwa..

  • @user-kx3en7hy5j
    @user-kx3en7hy5j 2 місяці тому

    Bwerani ku South Africa kuno tikuphulani osati masewera
    Tikudziwa kuti ena ndi a Dpp pakhope pomwe mumtima ndiwa mcp
    Ozatsaka Bakili Muluzi TV
    Kuno ndimuphula

  • @user-tb6yh1kx3o
    @user-tb6yh1kx3o Місяць тому

    Bangwe 1 kukonda ndalama ku SA akaphwedwa za u Bangwe 1 kubangwe konko

  • @JonasIdrissah
    @JonasIdrissah 2 місяці тому

    Aise tangoti pasila voice yo tiinvele, mukuchulusa zoyakhula

  • @wisemanjere6572
    @wisemanjere6572 Місяць тому

    Press fleedom. What does it mean. Please Malawians. These ministers. Democracy is what it means to be flee. If we copied this Democracy from the west. Do you follow how Americans behave. The land of flee in every aspect. Why does it pain you if one express his mind and opinion.

  • @user-xx4mt8ox8e
    @user-xx4mt8ox8e Місяць тому

    Kulavula chingamu chifukwa cha mtedza wolawa😅😅😅

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx 2 місяці тому

    Ndipo Ali busy kusaka bakili muluzi tv osasaka anthu akuba ndalama za boma koma kusaka za zii aPita ndi iyeyo ku ndende akusakila azawo ziwatsata

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 2 місяці тому

    Mwati imeneyi ndi nduna kapena mbuzi?

  • @Elvin-dr8tv
    @Elvin-dr8tv 2 місяці тому

    Sayixiwa south africa abwere ndithu azamuonesa anyamata

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika Місяць тому

    Auzeni

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 2 місяці тому +1

    Namachende ameneyo asabwele kuno athela mmanja zikutiwawa zomwe likuchita boma la agaru atonse bolo zawo

  • @LukaAron-el5qh
    @LukaAron-el5qh 2 місяці тому

    Moses bizy ndi za ziiiii osafufuza nkhani yophwedwa ka Alani witika,kumenyedwa kwa adpp kulilongwe bwanji,izi zaonesa kuti nde police basi malo moti muwasiyiile apolice ntchito manja mwawo

  • @PreciousElias-lx2pz
    @PreciousElias-lx2pz Місяць тому

    Kkkkkkkkkkkkkk km kumeneko malawi kokoma sizachoka sikuthawa ku malawi kuno kokoma ife ndi aphawi odya bwino

  • @Moses51
    @Moses51 2 місяці тому +1

    Galu ameneyo kwambili kukunyo

  • @QassimuKatsobola
    @QassimuKatsobola 2 місяці тому +1

    Moses agulu inu wakubaso ameneyo

  • @jafalikalepa
    @jafalikalepa Місяць тому

    Osusa akamusakeso ususa 😂😂 andiyankhulila bwino zikuchi kunveka kut munthudi wandalama

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому

    😂😂😂 kunkuyu mkazi uja akuti sumakoma unangoona kupha witika

  • @mphatsogondwe1836
    @mphatsogondwe1836 Місяць тому

    Ubwino wake tamva kale kuti politics your doing at night but one day is one day

  • @ExcitedCornflowers-nw9oc
    @ExcitedCornflowers-nw9oc 2 місяці тому

    Chi kumkuu mbuzi,nthawi iyi ndi ufulu chidzete kumkuyu.

  • @cynthiakananji1608
    @cynthiakananji1608 Місяць тому

    Ndalama zikugula anthu kut azigwira ntchito yausatana yosaka anthu osalakwa,sizikuyendera kut ali ndi ndalama kale.anthu ali ndi chuma chosefukira koma amafuna zambiriso.or ali a dpp atha kutumidwa ndi a mcp

  • @YohanePatrick-lc2lq
    @YohanePatrick-lc2lq 2 місяці тому +1

    Iwe galu kwabasi chendako

  • @user-xy9vz6jj4u
    @user-xy9vz6jj4u 2 місяці тому +1

    Iwe manyiiii

  • @harrymicah6140
    @harrymicah6140 Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂 umakwana chief kkkk

  • @HassanMbalaka-gb5sv
    @HassanMbalaka-gb5sv Місяць тому

    Ife timamva zowona kuchokela kutive imeneyi zopusa ayi

  • @ZainthwaSikelo
    @ZainthwaSikelo 2 місяці тому

    Uyu wa Bangwe waniyo,ndi mmodzinso amene ali mgulu lakupha the late Evison Matafale,now you want Bakili Muluzi tv,muphedwa ndi inu tsopano agalu inu

  • @gremsonswart1083
    @gremsonswart1083 2 місяці тому +2

    17 Billion ya Covid ija sitinaiwalebetu

  • @HassanJameskananjie
    @HassanJameskananjie 2 місяці тому

    Muphedwa kuno si kwa masewera zimenezo komweko

  • @kaiimbansofwa9154
    @kaiimbansofwa9154 Місяць тому

    Ba Malawi....kunyanda.

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 2 місяці тому

    Sufuka popanda utsi sinanga munthu ukakhala okaikitsa🙆

  • @MosesWitness
    @MosesWitness 2 місяці тому +1

    Abwele takonzeka Malo moti timuphe chakwela tipha iyeyo tili lady

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika Місяць тому

    Inuyo mukufuna muzibisa zanuzo

  • @ChikumbutsoTsalangu
    @ChikumbutsoTsalangu Місяць тому

    Kulu wa yakhula zoveka bagwe 1

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 2 місяці тому

    Napantumbo kunkuyu ukunama ndizosatheka zimenezo

  • @PempheroAlufandika
    @PempheroAlufandika Місяць тому

    Akukuyu pitani nokha koma simukabwera

  • @user-cy7gd1go6y
    @user-cy7gd1go6y 2 місяці тому +2

    Usaname galu iwe upita koma chot uziwe ndiyichi imeneyo ndi mcp mukapeleka bakili tv next ndiiweyo mcp imasinda mawamba isakutembenukila chisazo zadiki miya alikut anatotolatu pamoz ndi fayisi wake a mcp or kumalilo kwa zadiki miya sanapitu or moz zadiki miya kungopita ngat chizilu kumanda nde iwe usamale ndiganyu wako 🖕

  • @MosesSolomoni
    @MosesSolomoni Місяць тому

    Kunkuyu opusa ukufunika gahena iweyo galu iwe

  • @MbombeGogwe
    @MbombeGogwe 2 місяці тому

    Akusowa zochita awa

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet Місяць тому

    Wakukhalila baliiti khalamba ibwele ti yiske

  • @superiormoses4802
    @superiormoses4802 2 місяці тому

    Amutuma uyu tikuphulisa mutu ukabwera kuno demeti

  • @MalakamMillie
    @MalakamMillie 2 місяці тому

    Athu amisala inu

  • @ibrahmdoka7486
    @ibrahmdoka7486 2 місяці тому

    Chimanga chimalora opanda mano

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 2 місяці тому +1

    Muphedwa kuno msete zanuzo muzipangila komko shit

  • @Silverkaunda-ig5lf
    @Silverkaunda-ig5lf 2 місяці тому +1

    Kunkuyu mboli yake

  • @MemoryDesire
    @MemoryDesire 2 місяці тому +1

    😂

  • @RebeccaMaluwa
    @RebeccaMaluwa 29 днів тому

    😂😂😂😂 chilungamo

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 2 місяці тому

    Kkkkk kuyankhulatu

  • @AsherzMultimedia
    @AsherzMultimedia 2 місяці тому

    Zovuta kobasi

  • @TheresaNtodwa
    @TheresaNtodwa 2 місяці тому

    Koma ziliko???????kkkkkkkk

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p 2 місяці тому

    Dpp boma 2025

  • @kondwamlungu8384
    @kondwamlungu8384 26 днів тому

    Bangwe one asaname osakhulupilila munthu

  • @user-st4fh1vf4m
    @user-st4fh1vf4m 2 місяці тому

    Zimapanga hate iwe wekha osati enafe
    It only hates 1% of Malawians .Sanena zabodza amene uja .Chifukwa chan a court akufuna kumufufuza the so falled minister of finance?
    Kugulira mwana ma galimoto 20....So ukapanga hate ndani ...Musayerekeze kutuluka m'bomamo you will be arrested surely

  • @ThokozaniDavismlamba
    @ThokozaniDavismlamba Місяць тому

    Kd iye wabakili muluziyo alibe ufulu oyankhula chitukuko cha mcp ndikumanga anthu?

  • @user-vl5on2lj8b
    @user-vl5on2lj8b 2 місяці тому

    Koma ndiye munya kunkuyu ndi chakwera wakoyo simungampedze ameneyo

  • @kaiimbansofwa9154
    @kaiimbansofwa9154 Місяць тому

    Ba Malawi....kunyanda.

  • @kaiimbansofwa9154
    @kaiimbansofwa9154 Місяць тому

    Ba Malawi....kunyanda.