Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

Chipani cha UTM chalengeza kuti chatuluka mu mgwirizano wa Tonse Alliance

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 11 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 247

  • @spargomw
    @spargomw Місяць тому +25

    Ng'ona zizidyana zokhazokha tsopana😂😂😂😂😂😂 Ngat ali Chauta yemwe wakuuzan kut mutuluke, tingoti Alemekezeke Yehova coz ku Tonse mukadatha Psitiiiiiiiii. Atsaleko Manga yekha ku Tonse'ko😂😂😂😂😂

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 Місяць тому +24

    Zakhala bwino kutuluka mumgwirizano, congrants utm and dpp my votes

  • @kelvinchola739
    @kelvinchola739 Місяць тому +4

    Mmmm a Malawi chonde tengani Maiwa ngati mtsogoleli wa dziko la Malawi, ali ndi mphatso yaikulu Kambili. Kuchokela ku Zambia 🇿🇲

  • @user-ml4bl2ll2g
    @user-ml4bl2ll2g Місяць тому +15

    Mwachita zimene mwini wake wa chipani SKC akadachita akanakhala kuti alipobe Ambuye akudalitseni utm senior leaders

  • @FazackKambwiri-he8xe
    @FazackKambwiri-he8xe Місяць тому +11

    A UTM mwachita bwino kutuluka alliance yanu mmmm inali yakupha

  • @MorganBanda-oc2jx
    @MorganBanda-oc2jx Місяць тому +2

    mwachedwa nazo zinthu anthu inu. munawonerera muvi kuti ukuloweni m'maso ndipo lero ndizi chipani ichi sogolo kweni kweni silikuoneka

  • @alexgweje8610
    @alexgweje8610 Місяць тому +1

    Mwachedwa inu mukadapanga izi nthawi imene Chilima adakali ndi moyo anthu amkakuuzani kuti mutuluke Alliance koma kusamva inu bwelerani ku Dpp basi

  • @Dean-De-Matrex1
    @Dean-De-Matrex1 Місяць тому +13

    Zikomo UTM pothetha mgwilidzano umeneo ndi anthu akuphawa

  • @SothinieKanjuchi
    @SothinieKanjuchi Місяць тому +13

    UTM for life ❤

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Місяць тому +3

    Job well done 😅😅😅😂😂😂😂atsaleko adzidyana okha okha yomweyo mr Chikangawa 😅😅😅😂😂😂

  • @willardkajalika-m8g
    @willardkajalika-m8g Місяць тому +4

    I'm just saying all the best mwachita bwino ndithu akhaleko okha akanganyawo

  • @JamesKadango-qs3ej
    @JamesKadango-qs3ej Місяць тому +4

    Congratulations faz for SKC

  • @DonexMajiga-su9yv
    @DonexMajiga-su9yv Місяць тому +8

    Dpp my vote😂😂

  • @EagerChicken-qj6xu
    @EagerChicken-qj6xu Місяць тому +3

    Komabe ndikukhulupilira kuti mwini wake sakadakhalanso ndi maganizo obwelelanso ku chipani cha dpp. Kuli aford udf konso ndi zipani zina. Think twice .f,

    • @user-qp8kh2hj9o
      @user-qp8kh2hj9o Місяць тому

      Zoona nkhani ikumveka bwino ndithu palibe chifukwa chibwelera ku DPP

  • @CharlesChipwere
    @CharlesChipwere Місяць тому +3

    Mai kaliyati mwachita bwino kutuluka allance ndizomwe ndimadilira zikomo ndamva bwino kuchoka Kwa mavaphire sianthu away taonani mmene ikungwera kwacha sangakwanitse kuyendetsa boma

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Місяць тому +2

    Ken msonda azalowera kuti ngati MCP yaluza 2025?

  • @GertrudeMakumba
    @GertrudeMakumba Місяць тому +4

    Zosangalatsa kwambiri changa chikunkhala chisoni mmmmm imfa imandiwawa

  • @BlessingsmadalitsoShumba
    @BlessingsmadalitsoShumba Місяць тому +1

    Perfect breaking news 🎉🎉 i love it keep up ❤ utm

  • @InnocentBanda-u8y
    @InnocentBanda-u8y Місяць тому +4

    Nde ndiwe mtsogoleli nkumawopa kukumana ndi anthu omwe ukuwasogolera pali zabwino pamenepa ndiyankheniko

  • @user-ql8nf2vb8s
    @user-ql8nf2vb8s Місяць тому +5

    Very good very good very

  • @joejoman4541
    @joejoman4541 Місяць тому +1

    ❤nw i can able to go home n start support our country

  • @Chifundokapondodza-f6d
    @Chifundokapondodza-f6d Місяць тому +4

    Mwapanga zanthengo wapatari kwambiri

  • @user-fi7ko7bl6f
    @user-fi7ko7bl6f Місяць тому +1

    Lululuuuuuuuuiuuuuu mwachita bwino kwasiya atombolomboyo a MCP aziphana okha okha. Very soon freedom is coming tomorrow mwachita bwino kutuluka . Lero ndigona bwino iiiiii infa ya Dr Chilima aaaayosaiwalika😭😭😭😭

  • @NoxyNyika
    @NoxyNyika Місяць тому +1

    OLO MUTATULUKA ZILI NKANTHU😂😂😂
    MOTO WAMAPESI SULIMBA

  • @FrancisBanda-g9v
    @FrancisBanda-g9v Місяць тому

    Osada nkhawa ninthawi ikubwera 2025 kwakhala minyezi yocepa mai

  • @GracePendame
    @GracePendame Місяць тому +4

    Yomweyo apapa ndiye ziribwino

  • @ThomasMwandila-tn7cf
    @ThomasMwandila-tn7cf Місяць тому +5

    Mama mwayankhura nthaks

    • @SydneySibande-z6k
      @SydneySibande-z6k Місяць тому

      Very wise Leaders of UTM and all members, Leave crodiles alone to eat themselves,RIP Baba Saulos Chilima

  • @emmaculatemenzeiwa
    @emmaculatemenzeiwa Місяць тому

    It's not too late it's a united movement ❤

  • @SuzgoMunthali
    @SuzgoMunthali Місяць тому +1

    Mukatuluka 2023 bwezi chilima alipo Lero Koma Palibe yomwe amaziwazamawa only God knows

  • @SamuelAntone-mz6nq
    @SamuelAntone-mz6nq Місяць тому

    Tili momo UTM tikavotabe basi kya tikaluza kya tiwina tilimomo ife

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 Місяць тому +1

    Kaliati ndinu a experience ku ndale musalore Manganya kukupusitsani.ndiwazitsutso

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 Місяць тому +2

    Manganya ndiwa mcp,mayi Patricia kaliat congratulations for your speech

  • @user-zr7wk4oq2x
    @user-zr7wk4oq2x Місяць тому +2

    We're a little bit happy now 🙏

  • @Vaps-king
    @Vaps-king Місяць тому +1

    I can feel the pain inside her speech 😢

  • @Inayake
    @Inayake Місяць тому

    Manganya ndi wa MCP, he is not a genuine member of UTM, Hon. Kaliati I salute you!!

  • @WysonMalack
    @WysonMalack Місяць тому

    Mhuuu aaa ine nkhani ya a Chilima omandivetsa chisoni mukayankhura kungotchurapo a Chilima sindipilira Loma kututsa misozi naso manga basi ndipo ndimati adaferanjiii? Mzimu wawo uziusa mu ntendere mpaka kumuvula kohala maliseche mhuuuu Malawi mchiyani?

  • @user-qp8kh2hj9o
    @user-qp8kh2hj9o Місяць тому

    SKC forever in our hearts ❤❤❤❤❤❤

  • @misheckjanuary1696
    @misheckjanuary1696 Місяць тому +4

    Zathapo 🤗

  • @MAGIEWAJOHN
    @MAGIEWAJOHN Місяць тому

    Ai zikomo kwambiri mwachita bwino ndithu ambuye adzikutsogorerani ndithu

  • @HaroonAlibarara
    @HaroonAlibarara Місяць тому

    Zili bwino ndinthu utm oyeee🎉🎉🎉🎉

  • @user-wq9ex2sf3b
    @user-wq9ex2sf3b Місяць тому

    UTM for life from Zambia 🇿🇲

  • @MphatsoSteven-r8n
    @MphatsoSteven-r8n Місяць тому

    Mwachita bwino kutulukamo mutonse mai Patricia kaliat mwalankhula bwino kwambili🎉👏👏👏👏

  • @MonicaSembo
    @MonicaSembo 28 днів тому

    SKC made me to join politics

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj Місяць тому

    Mbbambande UTM awawa asiyeni apange zawo
    Bon kalindo uja wosadzamuphweketsa
    Ndikatundu womanga ndi mawaya

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Місяць тому

    Koma MCP afune asafune ati uze chidagwesa Ndege, ngati sati uza bwino m'malawi muno,sizizayenda bwino kufikira Chakwera tizagwira m'manja nthawi ina iriyonse tizawona kumene azakhale, Osati phera Wanthu muno,iyo Ndiye siti ngai mve,ikalakwa ilakwe,ikaza chimwa iza chimwe

  • @user-nz9ty3ih1v
    @user-nz9ty3ih1v Місяць тому +1

    kkkk kuteloko apa paseweredwa game kungoti apange gwilizano ndi DPP UDF ndi a FOD

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z Місяць тому

    Kaliati morefire mai inuyo MULUNGU adzikudalitsani ine utm my vote

  • @HassanIssaAbdulKarim
    @HassanIssaAbdulKarim Місяць тому

    Strong woman .
    Courageous.
    Fearless.
    Few we have .

  • @BenedictChikaoneka
    @BenedictChikaoneka Місяць тому

    Akuluakulu achipani basi omwewo? Tizipani tinati koma guys

  • @Fredoh10
    @Fredoh10 Місяць тому

    Ndipo maganizo abwino amenewo ndthu, ndiye chomwe akuyenera kupanga achipan cha UTM nchoti agwire ntchito nd a DPP ndipo zinthu zizayenda bwino even awo sazakhalaso nd mphavu

  • @HopefulCoralReef-tx4vx
    @HopefulCoralReef-tx4vx Місяць тому +1

    Achita bwino ndithu potuluka chipani cha MCP or blood part

  • @HarrisonMponela
    @HarrisonMponela Місяць тому

    That's a brilliant idea

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Місяць тому +2

    Utm now can team up with DPP, afford if possible urogise Mary chilima as VP kaliaty as president

  • @HastingsMaclondonmuhoko
    @HastingsMaclondonmuhoko Місяць тому

    Good decision

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Місяць тому

    Chipani chikufunika mtsogoleri ochangamuka ngati SKC, akweni mukukwanira pa udindo upresident.

  • @FatsanTobiyas
    @FatsanTobiyas Місяць тому +1

    Ngati ifa yakwamulungu alemekezeke ngati ndiabusa chakwela mulungu adzaziona ngati falawo safelapo

  • @user-fn5pu5zw5t
    @user-fn5pu5zw5t Місяць тому

    Osabwelelanso ku DPP please

  • @user-es4jt6ds8m
    @user-es4jt6ds8m Місяць тому

    Macheal utsi asapiteso Ku UTM please guys

  • @MemoryGalaonga
    @MemoryGalaonga Місяць тому

    Chipani cha utm chachinyata

  • @YAKOBEMAGANA-oe5hd
    @YAKOBEMAGANA-oe5hd Місяць тому

    Palibe chifukwa chokakamila ku mcp

  • @BittonNgwangwa
    @BittonNgwangwa Місяць тому

    Mungotenga thomu mpinganjira asogolere chipani tizawina 2025 basi

  • @user-px6tc4in6s
    @user-px6tc4in6s 24 дні тому

    Mary wachita bwino kuzisiya, ndalama anakamudyera iya

  • @SphiweSendaluzi
    @SphiweSendaluzi Місяць тому

    UTM standing for us youths too
    Tikavote guys❤

  • @HakeemJossam
    @HakeemJossam Місяць тому +1

    look sharp 🎉

  • @FredrickKachingwe
    @FredrickKachingwe Місяць тому +3

    Utm motto ku buuuu

  • @linahmpl9709
    @linahmpl9709 Місяць тому

    Mbuzi izi bwanji simukhatuluka chilima alimoyo cause chilima amakhala akunena nde mumadikilira alowe Manda Kaye mwadya unsi

  • @user-pw1kl3vo5d
    @user-pw1kl3vo5d Місяць тому

    Inu mwachita bwino korma sindikuvetsetsa Kuti Kodi pakutuluka DPP mudapita kukaphetsa mtsogoleli wanu Kung,one za mcp

  • @yusufsadic2930
    @yusufsadic2930 Місяць тому

    Zot chilim adavomer kukhal vc kwachakwer chifukw chozichets ndizabodz adalol chifukw chakut chipan chak poele utm ndi mcp
    mcp ndiyaikul kupos utm osamakomes zinth powon kt chilimay adaf bodza silimang mudz

  • @florenceharawa519
    @florenceharawa519 Місяць тому

    UTM Moto kuti🔥🔥🔥

  • @MoosahChikwakwa
    @MoosahChikwakwa Місяць тому

    😂😂😂😂 anjawala can you read again I didn't understand nicely 😂😂😂😂😂 now they understood that manifestos are clearly not correspondence from Yahoo finance of vice president and all 😂😂😂😂😂 aaah what is meaning of this statement 😂😂😂😂😂pa group sipali bwino 😂😂😂😂 koma ayi a MCP pali bho chifukwa mifuti 400 ili chile😂😂😂😂😂 and anthu angoona ngati tizitoy toopyezera ana😂😂😂😂😂

  • @user-tw2zf7bj3e
    @user-tw2zf7bj3e Місяць тому

    Akweni zabwino zonse osaopa

  • @janealinanemthunzi2880
    @janealinanemthunzi2880 Місяць тому

    Koma osabweleraso ku dpp

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya Місяць тому

    Apa ndiye mwachita bwino, asaleko amagazi okhaokhawo, Chipani choipa chosamva madandaulo awanthu, ntchito kumanga, kupha anthu osalakwa agalu a MCP

  • @ChikondiBJosaya-pr1zu
    @ChikondiBJosaya-pr1zu Місяць тому

    Apa ndiye DPP 2025 wooo

  • @TorshKadango
    @TorshKadango Місяць тому

    Ndpo zachita bwino kwambli osatopa osaopa osafooka

  • @tiyowoyechiparton2785
    @tiyowoyechiparton2785 Місяць тому

    Muphese ma lawyer pano 😂😂😂

  • @FrankSpison-o7o
    @FrankSpison-o7o Місяць тому

    Zikomo kwambili ndipo yehovah satitaya ife ayi anamalirs🎉

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge Місяць тому

    VERY GOOD KUTURUKA KUMANDAKO MMMMMMMMM🙌🙌🙌🙌🙌😢 R.I.P SKC 😭 😭😭😭😭

  • @user-je8jm5uy1q
    @user-je8jm5uy1q 29 днів тому

    Mwachita bwino manganya simunthu nsiyeni

  • @Mary-lb4ce
    @Mary-lb4ce Місяць тому

    May the soul of my president rest in eternal peace

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Місяць тому

    Yes I wish chilima had done it in July 2022

  • @andyngola3542
    @andyngola3542 Місяць тому

    Mcp ikhale yokha, all the best

  • @HopeMakoka
    @HopeMakoka Місяць тому +2

    Atsaleko ekha wazisudzoyo

  • @HussainKabila
    @HussainKabila Місяць тому +1

    💔💔💔💔🤪🤪🤪🤪😭😭zosangala mwachita bho kwambili osaopa

  • @B1Chitatata
    @B1Chitatata Місяць тому

    Salute UTM osaopa osatopa osafooka

  • @ClifordMumba-f1i
    @ClifordMumba-f1i Місяць тому

    Nice potuluka mugwirizano

  • @veronicamalisero2671
    @veronicamalisero2671 Місяць тому +1

    Zandikomela kwambiri ,Kweni ndi ma members onse a UTM mwachita bwino mwachoka m'manja mwa 🐊🐊🔥🔥🔥🔥

    • @anastanziaelia-gk3tt
      @anastanziaelia-gk3tt Місяць тому

      Uku ndiye kukhala uku osamakhala adyera ayi mitala ya chipani siyabwino ineso zandiwaza

    • @user-fi7ko7bl6f
      @user-fi7ko7bl6f Місяць тому +1

      Eeee wadyera ngati Manganya mmmm manganya my foot katyali ndamene anaphesa Chilima

  • @GeorgeLipengaphiri
    @GeorgeLipengaphiri Місяць тому +1

    Amai takulandilani inu mwabwela

  • @KeddwaBenjaminMkandawire
    @KeddwaBenjaminMkandawire Місяць тому +1

    So ndili ndifuso vp nawoso atukamo mu tose aliance 😂

  • @AufiThera
    @AufiThera Місяць тому

    Mulungu wayankha the DC 💪 alandile ulem

  • @NgongireMwakasungula
    @NgongireMwakasungula Місяць тому

    Achita bwino koma ntima wanga ukulumphalumphabe ndi ng'ona za mcp chakwera patumbo pako

  • @MadalitsoTamayenda-ez5pj
    @MadalitsoTamayenda-ez5pj Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂 skc woyee 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯💪💪💪💪

  • @NDIZOTHEKABANDA
    @NDIZOTHEKABANDA Місяць тому

    Koma mulimba?

  • @BwanaGD
    @BwanaGD Місяць тому

    Komati inu a UTM kudzinthetsa mwadzi nthetsako mutiphetsa amatitu akamawona inuyo amalimba mtima koma apa eee tikuntha bas

  • @RobertGoliat-gt2qh
    @RobertGoliat-gt2qh Місяць тому

    Bwererani komwe mudachokera congrats UTM

  • @DeveriousKowera
    @DeveriousKowera Місяць тому

    Yaaa apa zakhala bwino aphane okhaokha

  • @JimmyIsaac-xd4ef
    @JimmyIsaac-xd4ef Місяць тому

    UTM achitabwino kutuluka mu mngwirizano ndi MCP chipani chakupha

  • @julietbanda5203
    @julietbanda5203 Місяць тому

    Tikubwera kudzavotera utm 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 buuuuuuuuu

  • @ElliottBelon
    @ElliottBelon Місяць тому

    No alliance nkhan yabwino mai kaliat anthu akupha achoke Malawi siwawo

  • @user-du9qs4tb6u
    @user-du9qs4tb6u Місяць тому

    UTM you have to move manganya