Nkhanga zaona. Chakwera lero Ali busy kuti Born Kalindo aphedwe.

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 22 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 218

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому +19

    If you want to see people your house today just do that this🎉day you gonna be last day for you mr chikangawa I tell you

    • @AngolanChinga
      @AngolanChinga 2 місяці тому

      Ndiponso live he's gonna also we can't care about chakwela he's full of no nonsense don't try that mapwala ako chakwela

    • @zimmekapachika6784
      @zimmekapachika6784 2 місяці тому

      Ndipo chitsilu mr Chikangawa galu okupha ​@@AngolanChinga

    • @Lingstone-r3z
      @Lingstone-r3z 2 місяці тому

      That's no sece people, guys don't play bad games please we are one

    • @AlgentChilanga
      @AlgentChilanga 2 місяці тому

      ​@@AngolanChingathat's true ngati atamupha kalindo ulendo uno Dr Chikangawa awona sitizamusekerera mpang'ono pomwe.mnthu watizuzayu kokwana

    • @BlakRedGrin
      @BlakRedGrin 2 місяці тому +1

      Ndipo sindikutha kudziwa ngati kuli dziko lina limene limapanga ndale zaumbuli ngati Malawi, ka dziko kakang'ono koma mabodza thooo! And the gullibles believe everything they hear on social media. Those guys cooking these lies are just taking advantage of umbuli wanu omakhulupilira zilizonse izi. Manyazi akugwileni koma

  • @GeorgeTembo-v6i
    @GeorgeTembo-v6i 2 місяці тому +9

    Bon kalindo sangaphedwe olo zitafuta motani God bless kalindo

  • @GiftMakowa-k9f
    @GiftMakowa-k9f 2 місяці тому +1

    God keep mr kalindo continue what you doing don't stop 💥💥💥💥

  • @ChisomoBisani
    @ChisomoBisani 2 місяці тому +1

    Muyelekeze muone.kodi Mr chikangawa mwayamba kuzimva mphanvu kuposa mulungu?? Mukufunq kuuyese mkwiyo wamulungu kapena? Muzafaa imfa yowawa

  • @chisalebeston
    @chisalebeston 2 місяці тому +1

    There is no super man in the world, anafa queen ndiye CHIKANGAWA mkachani

  • @PatriciaSame-j2v
    @PatriciaSame-j2v 2 місяці тому +12

    Sopano chakwera akufuna akhale eka zikoli😢😢😢

  • @BrownMainje-sh7hj
    @BrownMainje-sh7hj 2 місяці тому +5

    Ngati angamuphe bon Kalindo , ifenso timupga iyeyo amene watuma zoti bon Kalindo afeyo . Timupha magazi ake ndidzamwa ineyo

    • @AlgentChilanga
      @AlgentChilanga 2 місяці тому

      Pamenepo ndiye aziwe kuti amalawi ndiwokwiya komaso atopa naye Dr Chikangawayu

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 2 місяці тому

    Comrade Ntanyiwa,Kalindo & o malawianz we r in this 2gethr A.P.M it's our vote

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 2 місяці тому +5

    Ndipo akunama awa chaka chake ndi chino ayelekeze mawali asaliwone namanyi ameneyo mr chikangawa kalindo alipo ndipo azafa nthawi yake ikazakwana ndi mulungu

  • @PaulKalambo
    @PaulKalambo 2 місяці тому +1

    The DC sangaphedwe i swear.... Something will happen in this country. We will not fear whether the president or what

  • @DamaliceWamalanguluko
    @DamaliceWamalanguluko 2 місяці тому +2

    Anthu oipa kwambili ndi akazi monica chakwera mkazi wa usi mkazi wa kunkuyu akukhala ngati kuleba sanafikeko kodi pobereka mwana zikukhala bwanji pamakhala zowawa kwambiri pls pls osapha anthu

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 2 місяці тому +2

    Ndipo Malawi ayaka moto ayensere kumpha Kalindoooo more fire 🔥

  • @GRACIOUSKENAN
    @GRACIOUSKENAN 2 місяці тому +2

    Inuuu atelo ndan kod tandiuzen ndiziweee,chakwera kod??? Aaaaaaa panyapacheeee ndthu.......

  • @LegendaryMatafale
    @LegendaryMatafale 2 місяці тому +1

    Awatu afika popepera nawo udindo akusakira pofera ohoo😢

  • @CassimMbalaka
    @CassimMbalaka 2 місяці тому +11

    Mulungu achita chotheka pa kalindo

  • @MaryBanda-n3h
    @MaryBanda-n3h 2 місяці тому +2

    Kuchoka 2020 kufika lero zitukuko zitatu zochoka ku mcp kumpha anthu kugwesa ndege komanso kugwesa ndalama ulendo Uno muziona sitikusiyani

  • @ChikumbutsoJohn-rs4tt
    @ChikumbutsoJohn-rs4tt 2 місяці тому +14

    Do you know God of Shadreck, misheck and Abidnego? You never kill Kalindo, Kalindo is son of God ndipo sizichitika believe me

  • @gracephiri4440
    @gracephiri4440 2 місяці тому +2

    May God protect bon kalindo

  • @YasmeenYalabi-b2c
    @YasmeenYalabi-b2c 2 місяці тому +2

    Aitu Allah yemwe ndimmodzi yekha amene timamupembeza ife salola kut aborn kalindo aphedwe Allah akuona zomwe akuchita chikangawa ndi team yake

  • @WarriorKB-u3k
    @WarriorKB-u3k 2 місяці тому

    Yes Mr chikangawa we know u planz try u will see what's gonna happen if u wnt peace free bon kalindo

  • @yazah22
    @yazah22 2 місяці тому

    Akalindo pita ku school, osama tchukili zinthu za ziii. We Malawi we are busy following stupid things rather than concetrating on things that can develop our country. A kalindo ndi anthu anu mukusokoneza dziko la mbuli kale ili.

  • @fundosakala633
    @fundosakala633 2 місяці тому

    We are still crying about chilima now if happening this you will see Malawi 🇲🇼

  • @AnnieKwisanja
    @AnnieKwisanja 2 місяці тому +2

    In the name of Jesus bon kalindo saphedwa ambuye timenyereni nkhondo timadalira inu 🙏

  • @Lazarus-qo1sl
    @Lazarus-qo1sl 2 місяці тому +2

    Sizingatheke kumupha born kalindo zachibwana

  • @TwalikiWisiki
    @TwalikiWisiki 2 місяці тому

    A Chakwera muyaluka chaka chake ndi Chino,, God is watching you,,😂 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 olo utapha amalawi onse utsale wekha,koma Mulungu adandiuza kuti akuyalutsa 💯

  • @FaheemChipojola
    @FaheemChipojola 2 місяці тому +11

    Boni kalindo kungophedwa malawi ayaka moto komaso dziko malawi likhala manja mwa nsilikali

    • @EdwardRichman-zs5pl
      @EdwardRichman-zs5pl 2 місяці тому

      iweyo ndindani ukuyakha zomwe s ukudziwa

    • @EdwardRichman-zs5pl
      @EdwardRichman-zs5pl 2 місяці тому

      A Malawi ndiiwe bwelani poyela tikuoneni

    • @ClementinaViola
      @ClementinaViola 2 місяці тому

      Inu ndinu a chani bwana?​@@EdwardRichman-zs5pl

    • @InspirationalOffroadCar-km5xm
      @InspirationalOffroadCar-km5xm 2 місяці тому

      ​@@EdwardRichman-zs5plndie muziopseza anthu? Mukunamatu man

    • @InspirationalOffroadCar-km5xm
      @InspirationalOffroadCar-km5xm 2 місяці тому

      Ndipo siku likubwera ndipo dziko ndi anthu amalawi omwe mukuwanenawo muzawaona ngati oipa ndipo dziko lizakukulirani siku limenelo ndipo muzalakalaka nthaka itang'ambika kt mulowe pansi koma sizizatheka bet me​@@EdwardRichman-zs5pl

  • @kangungufoundation2020
    @kangungufoundation2020 2 місяці тому +2

    Zilibe umboni izi osazitengera palibe amene akufuna kupha Bon kalindo a malawi siyani nkhani zokamba za imfa you will reap what you sow

    • @BlakRedGrin
      @BlakRedGrin 2 місяці тому

      Ndipo ndizovetsa chisoni kuti ma comments ambiri apa angokhulupilira zilizonse angave, Malawi tili ndi ndale zaumbuli kwabasi

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому +1

    Basi kungowapotiladi mmanyumba mwawo anthu amenewa, akupanga zimenezi akuwopa kuti akatuluka mboma adzamangidwa nkona akukakamira mipando mind you God is watching

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 2 місяці тому

    Mmmmmm 🙌🙌🙌 ayetsele awona kut dziko ili tiotcha. Aliyense awone kolowera 😢💔💔💔💔

  • @BlessingsBanda-ol2pg
    @BlessingsBanda-ol2pg 2 місяці тому +10

    Zimenezo sizingatheke kumupha kalindo

  • @gwatandingo9502
    @gwatandingo9502 2 місяці тому +1

    Zitsilu siziphedwa kupha kalindo bora kupha mbuzi ya bele bro usamaname

  • @EllahEllah-hu7hi
    @EllahEllah-hu7hi 2 місяці тому +6

    Nde mukutukwana bwanji,, chilungamo kuwawa,,chikagawa fanz

  • @AgnesMatola
    @AgnesMatola 2 місяці тому +3

    Oipitsitsa ndi Monica Chakwera Masamuyiwale akuyendetsa nawo dziko la Malawi.......!

    • @AchinaKellz
      @AchinaKellz 2 місяці тому

      Nyanga amasunga ndi zimayi

  • @PraiseMasinga
    @PraiseMasinga 2 місяці тому +2

    Komatu pakhala mwazimwazi angoyesela kupanga zimenezo kuti atiphele bon kalindo wathu

  • @RichardMatumbo
    @RichardMatumbo 2 місяці тому +1

    Iwe Chakwera mutuwako suganiza ukumapanga mma plan ukupha kalindo ulibe nzelu

  • @DavieChisale-w1z
    @DavieChisale-w1z 2 місяці тому

    Kalindo more fire

  • @EdwardMukholi
    @EdwardMukholi 2 місяці тому

    Kkkkkkk koma mr chikangawa tayelekeza

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 2 місяці тому +1

    Live from kongo 🇨🇩

  • @emmanuelchokocha
    @emmanuelchokocha 2 місяці тому

    Koma is this true a real man of like God a chakwera mwafika apa? But why?

  • @BrianAmos-s2k
    @BrianAmos-s2k 2 місяці тому

    Lazaro wafikapo.Dziko lake lokha iye momwe amachita mademomuja alipo anamupangila chiwembu?Ndichifukwa anathawa kuubusa onyenga yo

  • @AubreymjBanda
    @AubreymjBanda 2 місяці тому

    Angoyesa kuphedwa bon kalindo chakwera one Malawi m'mene izachitikila

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 2 місяці тому +2

    Bon kalindo sangaphedwe ay ndipo sizingatheke

  • @LoydKamtedza
    @LoydKamtedza 2 місяці тому +1

    Try it, Mr chikanga chakwera u follow him to grave dust to dust u witch craft u died it too wheath u want or not try it today

  • @VeronicaYohane
    @VeronicaYohane 2 місяці тому

    Akangosowa bon kalindo anthu asasekelele ayi nawonso adzasowa siku limodzi ndwa ku mulanje mwanayo mukampha muona chomupmhela simudzamphatso wina ayi

  • @RoseMkandawire-e2g
    @RoseMkandawire-e2g 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂 chakwera akuziwa kuti chaka chamawa sazawinaayi ndipo akuziwa kare kuti amalawi sakumufunaayi ndipo akuziwa kare kuti waluza kare ndipo akazaruza akuzifusa kuti kodi nizarowera kuti uzarowereso kuubusa kwako uko kuusatanikikwakouko

  • @mablembeza4580
    @mablembeza4580 2 місяці тому

    Mulungu wathu ndiwazatheka bwanji, no weapon formed against Kalindo will prosper

  • @GanieAlidih-gu7no
    @GanieAlidih-gu7no 2 місяці тому

    🎉zodadi ifetadusa mamawa popop km palidi anyamata ochuluka kwambili brother 😢😢 atanyamula zibhonga

  • @WillianBanda
    @WillianBanda 2 місяці тому

    Izozo asayelekedze chakwerayo nanga azapha anthu angati?kodi ndi uja mmati m'busa ameneyo?

  • @JohnThenfordJande
    @JohnThenfordJande 2 місяці тому

    zatikwana zomwe akuchita chakwera ndipo mulungu sangamusiye choncho ambye tinthandizen

  • @wilfredkazembe676
    @wilfredkazembe676 2 місяці тому

    Kkkkk!! Chipani chanji chimenechi koma zitha zimenezi ife si akamuzu aja ayi achawera zukani pano mfuti lolo mmangochi tikungodikila pano ife takakhala tilipanfchito imeneyo pa joni ntanyiwa we are ready

  • @MaryRasmussen-mr4zo
    @MaryRasmussen-mr4zo 2 місяці тому +1

    He will not die
    May God protect him and be with him

  • @Andrew-u5i8n
    @Andrew-u5i8n 2 місяці тому

    Usanamize anthu naweiwe. Usatumizako zachisisimuso bwanawe " unaliko? Uchepa nzeru ndiwe.

  • @PhilipMatolino
    @PhilipMatolino 2 місяці тому +1

    Kod akuluakulu anthuwa phamvu zikuwachulukira et but in the name of Jesus asatanic amenewa chakachino adunsa awiri ndipamene ataziwe kut iwowo siwochuluka nzeru than mulungu

  • @mansonchinkhuzi
    @mansonchinkhuzi 2 місяці тому

    Zabodza akalindo ndindani Malawi oti Boma lingade nkhawa Malawi angapinduleko chani ndi akalindo okhawo opanda zochita angatanganidwe Malawi Azeri Ali bize kupeza njira zopezera chuma awawa asiyeni azichedwa ndizibwana

  • @HannahTulizoh
    @HannahTulizoh 2 місяці тому

    Olo kusowa okuphayo nde mpaka akaphe kalindo munthu ozerezeka ngati ameneyo?? Mulibe zochita zina kodi zokuti mutha kumabweretsa pano eti?? Wat is Kalindo pliz??

  • @EstherBonga
    @EstherBonga 2 місяці тому

    Never anamulenga siiwo ndipo BON Kalindo adakangalulabe Mulungu wathu siwakufa afe ndi iwoo

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 2 місяці тому

    Kungophedwa born kalindo,, nkhondo iyambila popho mosakaikaso ,, chifukwa pano tili lede kuyambitsa nkhondo yakufa kwa chilima anytime ikuyambika muno malawi ,, kungofika pa 30 mwezi uno popanda report kutuluka muzionaso

  • @ChristinaNyirenda-zb1if
    @ChristinaNyirenda-zb1if 2 місяці тому +5

    President waifeamalawi osauka atilekele mulungu awalange lelo lomwe mzina layesu

  • @LusunguPhiri-i2v
    @LusunguPhiri-i2v 2 місяці тому +1

    Kupha Bon Kalindo ndi mistake a Malawi azakwiya ndi okwiya kale ndi kufa kwa Chilima

  • @JamesChiphwanya-m4v
    @JamesChiphwanya-m4v 2 місяці тому

    Chakwera yesera wuone zimenezo ngati munapanga chilima akhale yemwe uja wakwana yelekezani muone

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 місяці тому

    Kodi amangodziwa kupha kokha?ndiolephera adzilenga ndikulemga otsati kupha kokha

  • @JohnConar-kq4hi
    @JohnConar-kq4hi 2 місяці тому

    The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC never did bon kalindo never did 🇲🇼🇲🇼✊️✊️✊️✊️✊️✊️✊️✊️the DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC

  • @yazah22
    @yazah22 2 місяці тому

    Limpompo mukusocheretsa anthu osalakwa... pitani kwina

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому

    Munya muwona sizitheka bon kalindo anatumidwa ndi Mulungu kuti ayimilire anthu wosauka, Mulungu akukanthani nonse, munapha Chilima inu apa nde zikuchita kuwonetseratu kuti achakwera ndinu amene munapha Chilima tikufuna report la ndege afiti inu bas kumangolimbana ndi anzanu opanda chifukwa Mulungu akukantheni nonse okupha inu

  • @MeriaMasinga
    @MeriaMasinga 2 місяці тому

    Kodi chikangawa anthu 9 aja sanakukwane?

  • @FortuneGwadiyo
    @FortuneGwadiyo 2 місяці тому

    Kalindo kungophedwa chakwera naye afa basi ndipo angaphedwe ndimanja

  • @MrThomas-j9d
    @MrThomas-j9d 2 місяці тому

    Chakwera akuzuza Malawi kwambili

  • @ElizahMadi
    @ElizahMadi 2 місяці тому +1

    Ndale Za Ku Malawi ,kumangokamba zokupha basi , come to South Africa muwone ndale Za anzanu , Mwana uyu Jullius Malema ,ngakhale alankhule BWANJI boma silipanga ma plan wopha anthu ayi , AAA Malawi fokofu

    • @EdwardZuze-r7w
      @EdwardZuze-r7w 2 місяці тому

      Ndale za ku Malawi ndi zoputsa kwambiri, Kuno sangapange zoputsazo ayi

    • @BlakRedGrin
      @BlakRedGrin 2 місяці тому

      And according to you wakhulupila zomwe zikukambidwa apa kuti ndizoona? These liars are just taking advantage of you guys pomakhulupilira zilizonse mungave pa social media. Pamene alili Kalindo anthu oti angamuphe mu nthawi in ndi a opposition kuti apeze ma political scores, MCP yoti akudziwilatu zoti munthuyo akulimbana ndi iwo kumupha sindiye kuti azipalamula dala moto. Kumaganiza a Malawi pena

  • @isaacchiwaula731
    @isaacchiwaula731 2 місяці тому

    Mumangonvera nkhani zamabodza ngat zimenezi amalawi chifukwa chani? Zoona mumganvere bodza la ntheretu ngat ili? Aaa koma anthu mumasowa zopanda comment mwanva.!! Zoti born kalindo anayamba kalekale kumangoti akufuna kumupha moti simudziwa? Zaziiii muzitukwana dala boma muli ndimantha kut tsiku lina zizakutembenukirani nkumaopa then nkummadzi pherera pomatumiza mauthenga oti akufuna kukuphani😂😂😂😂😂 muziona!! Ngat timakutumani kut muzinyoza alamulira ife

  • @JosephHill-fy1bb
    @JosephHill-fy1bb 2 місяці тому

    Kalindo adzamwalira panthawi yake, ndipo enanu mudzayambilaso ndinu kufaaa...
    I curse you all team Chikangawa

  • @ActiveMghogho
    @ActiveMghogho 2 місяці тому +1

    Bonikalindo can not be killed God be with him sory to someone who make plans to kill bonkalindo

  • @RhodaPhiri-d6q
    @RhodaPhiri-d6q 2 місяці тому

    Mmmm mumakamba zomwe zimangogawa dziko muli ndi chiwanda choipa palibe choona chomwe chinabwera choona bolaninso mtambo pali iweyo ndi uja wa muvi wachilungamo palibe chomwe mumanena zaphindu

  • @THOCCOChimbali
    @THOCCOChimbali 2 місяці тому

    Chakwela wakulira ku mudzi mu umphawi

  • @DickinsonLikhoma
    @DickinsonLikhoma 2 місяці тому

    Koma chikangawa ukagoyelekeza kupha kalindo uziwaso🛠️🛠️🛠️🛠️🛠️🛠️🛠️🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹🏹

  • @GanizaniKamvazaana
    @GanizaniKamvazaana 2 місяці тому +1

    Sangaphedwe sizingatheke ndipo sizingatheke komatu akaphedwa ADC NDE KUMWAMBA KURIBE MLUNGU

  • @MaggieToneki
    @MaggieToneki 2 місяці тому

    Sizithekatu ndipo sizitheka iwo akudana ndi ma damo? Zaziiiii😢

  • @ChristinaMitepa
    @ChristinaMitepa 2 місяці тому

    A ndale jahena salinayo patali, cz amakgala anthu a bodza komaso olimba mtima

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 місяці тому

    Once born kalindo kuphedwa kumalawi kuzakhala Moto ndi mkhondo yosatha chikangawa ntchito zawo kupha basi agalu amenewa

  • @VictorKachulu-y3n
    @VictorKachulu-y3n 2 місяці тому

    Wachita bwino apheso ndi iwe yemwe zikomo kwambili popeka nkhani yabwinoyi mudzakolola zomwezo ndipo mudzaweruzidwa

  • @GnessBanda
    @GnessBanda 2 місяці тому

    Kodi iwowo pansi pano anabwera kudzakhazikika?

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 місяці тому

    Zomupha bon kalindo ndizonama ,
    Ngati zilizoona tidikilile 3 days from today

  • @AlfredMacdonald-g2n
    @AlfredMacdonald-g2n 2 місяці тому

    sizingatheke ,,,, tili komweko

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 місяці тому

    Old state lodge stlye basi yapafupi ndi moyale basi

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 2 місяці тому

    Mulungu amugolere born kalindo,,,, tipita kwa chakwela komweko anthu onyasa a mcp oyendela mamina akhosa

  • @jomochirwa
    @jomochirwa 2 місяці тому

    Uyu sindimumvela amachulukitsa mabodza,chanel ndi bakili muluzi kawawa wosati izi ayi ,uziwuza wanthu amisala .

  • @KhumboChirwa-z2u
    @KhumboChirwa-z2u 2 місяці тому

    Nyasi zokha zokha, zikunenedwa apazi. Why a malawi mkukhala ngati mkusuta ganja zo ganiza zanu, kweni kweni mkufuna chani a Ntanyiwa Nzeru ndizo mlibi let him. Kuganiza ngati khoswe.

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 місяці тому

    Chikangawa chakwera nyama za anthu 9 aja ukalibe ukhuta

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 2 місяці тому

    God is great Mr DC kalindo he will last long

  • @MulatuBekele-j7w
    @MulatuBekele-j7w 2 місяці тому

    Bon kalindo ambuye akhale kumbali yake

  • @FrynessMoyo-to2du
    @FrynessMoyo-to2du 2 місяці тому

    Munasiya mtalika munthu wamulungu kukasankha wa satanic 😢😢

  • @MsondaBanda
    @MsondaBanda 2 місяці тому

    Vyaboza namwe, vyose vya mbembe pela, kalindo luta ku parliament ndiko ukapangenge ivyo

  • @BraghtYohane
    @BraghtYohane 2 місяці тому

    MULUNGU mukuloleranji izi kod kut dziko rathu tizidandaura muthu modzi pangani chotheka tikufuna mphamvu yanu ioneke pa maso pa amalawi tikuvutika ndimuthu modzi chonde mulungu tikufuna inuyo ife talemphera

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 2 місяці тому

    Koma ichiso ndichaboza ichi zinthu ngati zakuvuta basi tangosiya ukuwona mulungu wakukana kulankhura kuchikamwa kwakoko lilongwe yake iti itapange mademo mawa zaziiii muzipanga kwanuko iweso ndiwe mbuli yophunzira ntanyiwa

  • @EvasonThupilifana
    @EvasonThupilifana 2 місяці тому

    Kom amalawi nkhaniyi titaiva mukuti nayo bwanji kod chakwela palibe plan imene anthu angapange

  • @HedgensChisale-n4b
    @HedgensChisale-n4b 2 місяці тому

    Chikangawa usamale munthu amaluzatu akulamula ose amaluza aja amakhala akulamula

  • @BennettNjedza
    @BennettNjedza 2 місяці тому

    My God protect all freedom fitters

  • @Lhanow
    @Lhanow 2 місяці тому

    Kodi dzikoli palibe china choti tingamachite koma kuphanaaa

  • @WillardMasika-yf3dw
    @WillardMasika-yf3dw 2 місяці тому

    Dziko lomvetsa chisoni 😢😢😢

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms 2 місяці тому

    Ndipomwe muzawawone amalawi moyo wawo

  • @CeciliaBamusi-fn8io
    @CeciliaBamusi-fn8io 2 місяці тому

    Ndipo agalu aMenewa a mcp akundinyasa kwambili