KWAGWANJI / U KUSANKHIDWA KWA MICHAEL USI

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 21 чер 2024

КОМЕНТАРІ • 91

  • @blessiousphiri3109
    @blessiousphiri3109 15 днів тому +5

    Kumakhala bwino ndi anthu muma office mu a Malawi chonde. Big up Banda, Chunga and Msiska

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 15 днів тому +3

    Koma mcp mene yachitira treat chilima according to agreement manganya asamale mcp ndi yakupha and dishonest

  • @KennedyChitunda
    @KennedyChitunda 15 днів тому +6

    Dziko lalowa chibwana mpaka manganya kukhala vp,,,,ur not serious

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 15 днів тому +4

    Komtu azibambo inu musamakonde kumutchula Mulungu munkhani zandale bashop usatchule dzina la Yehova Mulungu lako pachapabe bashop bashop

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 15 днів тому +3

    Zibwana zenizeni ndi dziko maliro sanathe koma asankha munthu

    • @wisdom20mkango49
      @wisdom20mkango49 14 днів тому

      😂😂😂 Boy this is the country not family thing..... There is a constitution that runs not people feelings... Show maturity before you utter nonsense

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw 15 днів тому +3

    Muzikagona azimayi a eni autsi muli ndi mbili yonyasa kwambili inu

  • @josephhchimpepa8753
    @josephhchimpepa8753 15 днів тому

    That's a good discussion! Those who have ears have heard something!

  • @AAbiner
    @AAbiner 3 дні тому

    Bwato sasisirana pakati panyanja🎉🎉🎉

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 15 днів тому +1

    Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥

  • @SahijidNgwindima-qd3dk
    @SahijidNgwindima-qd3dk 15 днів тому +3

    Koma mummuuze manganya akumbuke .mama sikono........chibwana. ......

  • @blessingkamanga1781
    @blessingkamanga1781 15 днів тому

    Very educative discussion

  • @user-xc2zm9bu1i
    @user-xc2zm9bu1i 15 днів тому +1

    We are waiting incompetent inquiry
    Poor leadership
    Not following the democratic values
    Remember next year is just around the corner
    Things are not working on the ground
    Guys we need a servant leader

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z 15 днів тому +1

    Wakupha uyu chilima adali amfanaoganiza bho .akutha Mau sakudziwa ZA mawa a usi mau awawa adzakutembenukilani soon.ife tli ku ma stand

  • @emmammatsa1284
    @emmammatsa1284 11 днів тому

    Mr Ndevu zamwai timati, ❤Mdyanyemba amaiwala koma mtaya makoko saiwala chifukwa amazaloza pomwe anataya osati Mdyamakoko chitukwa makoko a nyemba sitidya ayi

  • @blessiousphiri3109
    @blessiousphiri3109 15 днів тому

    Suziwa zamawa yes. Fact to the point ❤

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 15 днів тому +2

    Koma palakwika pangono chifukwa thawi yachepa kwambili sikale lija aikidwa malilo lija ngati panafunika kudikila kaye

  • @user-ve2ts3yr2n
    @user-ve2ts3yr2n 15 днів тому +1

    Ndipo mukhalisepo atumwi inu.....aaaa ma compassion aanthu mpaka zaka peletu ati sanasayinile.....

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 15 днів тому +3

    Kod awa atatu ndiamene ali oziwa kwambiri amangokhala pamenepa bwanji

  • @user-wx1jt5fd2j
    @user-wx1jt5fd2j 15 днів тому +1

    Ndi andale ochepa amavomereza kuti chiweluzo chiliko ndi chifukwa chake samasamala za anthu Ena ngakhale akubvutika bora iwo zawo zikuyenda koma mulungu ndi oweluza olungama

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 15 днів тому +2

    They think that this TTV it's belong to them kom kumakhala bwn ndi anzanu zatsogolo lamunth amaziwa ndi Mulungu

  • @ClementJacob-sd8lf
    @ClementJacob-sd8lf 13 днів тому

    Malawians group of discussion without solutions doy you think you will change Malawi for the situations just wait and see

  • @MustafaAbdullah-pb5zv
    @MustafaAbdullah-pb5zv 14 днів тому

    Powerful message

  • @corretabanda7685
    @corretabanda7685 15 днів тому +1

    Ine sanandipeze speech yawo nsaname

  • @user-vu4cz1mt4f
    @user-vu4cz1mt4f 15 днів тому +1

    Tili nchisoni chanji,anagawana zovala zanga yesu anatero

  • @ClementJacob-sd8lf
    @ClementJacob-sd8lf 13 днів тому

    Sugar k200 Lifeboy soap k50 nthochi 20 t, zibwelele kwa d.r banda ngati sizitelo nde kutinamizako ife sitifuna ndale

  • @user-co3wr3rn4h
    @user-co3wr3rn4h 15 днів тому +1

    Manganya ndi ka yudasi kakafupi kwambili fiti kapha, zake chilima

  • @yusufbakali
    @yusufbakali 14 днів тому

    ❤ Manganya ndiyekhayo maso a malawi

  • @EsnartMartin
    @EsnartMartin 15 днів тому +1

    Ma guy inuyo simuli serious ndale zakulowani

  • @user-ty7mc9mg1f
    @user-ty7mc9mg1f 5 днів тому

    Ausi adzakhara president.

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 15 днів тому +1

    Kodi malamulo adziko amachokera kuti ndipo amapangidwa ndi anthu akuti?

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 14 днів тому

    Yaaa aghothiiii akhutukunve malo moti azitengera mphunziro pa zinzawo.

  • @ChrissySasenga
    @ChrissySasenga 14 днів тому

    Nice kma

  • @ClementJacob-sd8lf
    @ClementJacob-sd8lf 13 днів тому

    Wina president akachoka mtengo kumakwela liti zizasitha mpake tife tose zopusa

  • @user-nw6ie3xx8b
    @user-nw6ie3xx8b 15 днів тому +1

    Wishing you the best , help chakwera he is the man of God

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 15 днів тому +1

    Zomwe lankhula sizingatheke muone azangoti pasakhale owasokoneza nduna zina zidangowelamila pansi muona when it comes to action let's wait

  • @ykzt
    @ykzt 14 днів тому

    Walowa dziko litavunda kale palibe chingasithe apa😢😢

  • @user-bl6km6kx7n
    @user-bl6km6kx7n 15 днів тому

    Mabwana chonde kuyamikila tiyamikile koma kod chikalidwe chathu monga amalawi chimati chani munthu akafa plz timakukulupililani

  • @CalvinThabang
    @CalvinThabang 14 днів тому

    Tikuferanji amaLawi pomwe Manganya ali m'bwaLo??!!

  • @AllanSanena
    @AllanSanena 14 днів тому

    Zosakoma dzikoli😢😢

  • @rabeccamasebo6261
    @rabeccamasebo6261 14 днів тому

    Life is in stages

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude 15 днів тому

    Tizikhala bwino ndi anthu🤣🤣

  • @FortuneNkhoma-bc9hh
    @FortuneNkhoma-bc9hh 10 днів тому

    Kharedwe ndichuma

  • @80kiloputodaboacena9
    @80kiloputodaboacena9 15 днів тому

    Mphaka Manganya kula vice president

  • @MaggieCement
    @MaggieCement 15 днів тому

    Kwathu kosauka ine olo wagalimoto kulibe

  • @Geraldmkwewu
    @Geraldmkwewu 15 днів тому +3

    Chisiru manganya yudasi atiphera chilima ndichakwera achina nkunkuyu zikhare ngoma osatchura mulungu zautsiru zimenezo manganya Mesa amafuna udindo kuyiwara kt ose ndichakwera kt awupeze udindowo ndichilima tikulira chilima wanthu lfe 😢

  • @LovemoreTaulo-yj3pj
    @LovemoreTaulo-yj3pj 15 днів тому

    Times mcp tv mbuyomu inali times ya bwino km pano anawadyesa Baz awa

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 15 днів тому

    Mulungu mutimenyele nkhondo taluza chilima munthu yemwe anthu adamukhulupilira

  • @dymonleven7571
    @dymonleven7571 15 днів тому +1

    Abambo asikono kumeneko zalowa chibwana ndithu 😊

  • @maulanaallie6194
    @maulanaallie6194 14 днів тому

    Umbuli

  • @wonganichakakanyirenda3299
    @wonganichakakanyirenda3299 15 днів тому

    Inu inu abrayan musazafee

  • @homeremedys3748
    @homeremedys3748 15 днів тому

    Akufuna Aphe Born Kalindo then APM, chenjerani nayoni boma ili zinali kokambilana dzulo

  • @blessiousphiri3109
    @blessiousphiri3109 15 днів тому

    Mudya nyemba amayiwala, koma mudya makoko sayiwala

  • @adibwekumz3085
    @adibwekumz3085 13 днів тому

    That's illegal. Kupusa

  • @wypatrickdakankhoma9655
    @wypatrickdakankhoma9655 15 днів тому +3

    Mwakwera m c p😢

  • @polesanamakwenda6932
    @polesanamakwenda6932 15 днів тому

    Kkkkkk

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 15 днів тому

    Ausi kaya ndi usi wamutengo utiwo koma mumbari yopha chirima arimomo koma nawo apitabe basi

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 15 днів тому

    Iya mapazi anu

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 15 днів тому

    Chilima anali munthu osunga nthawi ndipo tidzamusowa

  • @ZungeniBanet
    @ZungeniBanet 15 днів тому +1

    Inu chupiti

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 15 днів тому

    Agalu atatuwaso atinyasa machende anu

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos 15 днів тому

    I disappointed MCP

  • @RABSONSIKELO
    @RABSONSIKELO 15 днів тому

    Moyodi ndi pelete

  • @PaulChaleka-lb4vx
    @PaulChaleka-lb4vx 15 днів тому

    Koma mcp tikuchotsa 2025 yatililitsa koopsa

  • @ykzt
    @ykzt 14 днів тому

    Kod pali chodyadira pamenepo anthu inu

  • @Yungjoe786
    @Yungjoe786 15 днів тому

    Pachoka nzako palidi Malo...

  • @ChrissySasenga
    @ChrissySasenga 14 днів тому

    Chilima anali dolo simukunama

  • @AlfredNazombe-me2ly
    @AlfredNazombe-me2ly 15 днів тому

    I hate nyana these guys bcoz even they isolate Jona Pankuku every program they put Jona at last sit why and they use to cat him word on the mouth when ever he is speaking just wash 5 kwagwanji and hot current u will agree with me

  • @user-nj5vu8cd5l
    @user-nj5vu8cd5l 15 днів тому

    Vote for USI ❤❤❤

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 15 днів тому

    Dziko latha

  • @IssaJohn-cb8vn
    @IssaJohn-cb8vn 15 днів тому

    This stupid radio this days we must stop listening and trust

  • @user-mv4us2yx1o
    @user-mv4us2yx1o 15 днів тому +1

    Zopusa zeni- zeni,manganya mzomwe amafuna amamuyenda mmapazi chilima,mmmmmm ,dziko lamalawi larowa chibwana ,mpana Usi?mzimu wachilima komwe uliko ukunva chisoni

  • @MAYGOSPELALBUMSChawawa
    @MAYGOSPELALBUMSChawawa 15 днів тому

    Don't take malawian as stupid because the president has got powers to make decisions like on this situation to change the decision because you can see when did we did the barial for Chilima and today you're busy enjoying with the post of vice president shamm on you mr. President and your vice president

  • @AlexAlick-bx9by
    @AlexAlick-bx9by 15 днів тому +2

    Times it's mcp TV

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani 15 днів тому +1

    MCP yamagazi yanuyo ngakhale itachita zabwino komabe mbiri yake ndiyamagazi basi

    • @SaidiMbawa-st6bj
      @SaidiMbawa-st6bj 15 днів тому +1

      Dpp so ndi yamagazi ndiye musathe mawu boma ndi Boma

    • @tasmania527
      @tasmania527 15 днів тому +2

      Ndipo DPP yinathiphela abale athu 20 ku Mzuzu mu 2011. Yinapha Chasowa, Njaunju, ndi ma membala a UTM ku Lilongwe; kodi amenewo si magazi a anthu? Kodi anthu onsewa ophedwa ndi DPP anali nkhumba? Nde musamalankhule kuti MCP yamagazi ngati muli ndi umboni- DPP umboni ulipo.

    • @MaryNyirenda-nq3mh
      @MaryNyirenda-nq3mh 15 днів тому

      Kod anthu mulimbalibe ya MCP yomweyo uhuuuu bola zipani zina osat MCP yakupha

    • @tasmania527
      @tasmania527 15 днів тому

      Za zii. I would rather support MCP than family parties of killers like DPP or UDF

    • @kingsleyhopematchaya5184
      @kingsleyhopematchaya5184 15 днів тому

      Nanga popeza yakhala mcp yokha chipani cha phavu nanga muthu wa zaka 92 angaganize zulu zinatha tiyenazoni bola mukavote katatu aliyese koma kamodzi aaa mcp ikudutsa

  • @JafaliAkimu-ll1bf
    @JafaliAkimu-ll1bf 15 днів тому +1

    boma lolamula ndi chigawenga

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 15 днів тому

    Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 15 днів тому

    Palibe ndipo ine ndiye ndakodwa kwambili ausi vice 🔥🔥