Timalize Kaye Kafukufuku Kenako Ofalitsa Zabodza Amangidwe - The Voice

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 5 жов 2024
  • On Nyasa VoiceBox, The Voice pleads with Malawi Government to resist from arresting people before the investigation on what caused the Chikangawa crash is concluded. It would be better to first get to the bottom of what caused the crash so that if anything government will be more that justified when arresting anyone spreading fake news on the issue.
    Pa Nyasa VoiceBox, The Voice ikupempha boma la Malawi kuti lidethe pomanga anthu asanafufuze zomwe zichititsa ngozi ya ndege ku Chikangawa. Zingakhale bwino tiyambe ndifufuza zomwe zidachititsa ngoziyi kuti ngati ndikumanga aliyense amene akufalitsa nkhani zabodza pankhaniyi boma yikhale ndi umboni wamphamvu.
    #malawi

КОМЕНТАРІ • 122