DR JOYCE BANDA KUYANKHULA KOYAMBA MU CHAKA CHINO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 10 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 269

  • @user-ee6be5kl5o
    @user-ee6be5kl5o 5 місяців тому +14

    Ife sitikufuna zaulere ayi ife tikufuna kumazidyetsa tokha tikamalima amalawi ndi anthu olimbikila panonso sitikufuna mbusa ayi takanana abusa onse avunda basi ife sitizawakhulupililanso ayi abusa mwatipusitsa iweyo Joyce Banda usamathe zamkwamwa palibe angakuvotere iweyo ayi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 5 місяців тому +10

    Inu mai banda mukuthandiza anthu because ndalama zimene munabera amalawi. Ndalama za cash get munagulisa ndege imene bingu anagula ndalama zili kuti musakhale ochenjera apa

    • @user-jn2oc3cn3q
      @user-jn2oc3cn3q 5 місяців тому +1

      Zoonadi akuona ngati tinaiwara mbava yachikazi

  • @jamessingini-fh1bz
    @jamessingini-fh1bz 5 місяців тому +8

    Boooooooon kalindo🔥🔥🔥activist mmodzi yekha

  • @khumburanimukhupa4792
    @khumburanimukhupa4792 5 місяців тому +2

    Please pamene pafika malawipaaa, sizomazichemereraaa ndizithu Zaulele. Help these people to be independent not tizizichemerera ndikupereka zithu zaulele. Mai Joyce Banda you are contributing to the poverty of this country. Help these people to be independent like you not this Nonse of building nyumba. Let’s give malawi good future, don’t take advantage of these people. 😢

  • @user-vd6gu7tv5u
    @user-vd6gu7tv5u 5 місяців тому +14

    Mayi ngati mukufuna ulemu musankhe kukhala chete.

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 5 місяців тому +7

    Ine ngati zika ya Malawi Joyce banda Chakwera chilima asakhaleso atsogoleri amalawi moyo wawo wose ngati mukufuna Malawi akhale wabwino.

    • @edohjere4
      @edohjere4 5 місяців тому

      Chilungamo and aliyese kuyipa kwawo akuphuzila kupheleza kuwonesa mwano

    • @josiahgarley3824
      @josiahgarley3824 5 місяців тому +1

      Mwaiwala mmodzi, pitala asakhalenso president

    • @user-le9su3mt7r
      @user-le9su3mt7r 5 місяців тому

      Chilima ndio wati pulumusa kubagamoyo

    • @user-le9su3mt7r
      @user-le9su3mt7r 5 місяців тому

      Chilima watani chilima wati pulumusa ku bagamoyo not chakwela mbuzii

    • @IsmailNdemanga
      @IsmailNdemanga 5 місяців тому

      Eya sazalamulaso anthu amenewa ineso ndikugwilizana nazo

  • @RobertLuka-wy9cl
    @RobertLuka-wy9cl 5 місяців тому +7

    Iwe ndi hule chitsilu wayamba kapeni iwe wagwa nayo my vote is peter

  • @EvansKachere
    @EvansKachere 5 місяців тому +1

    Bon kalindo wachita chani pa Malawi pano ziko lino likufuna anthu ozlimbikira okha osati zolandilira Malawi azakhala osauka nthawi zonse zhifukwa chodalira zaulere. Amai mwalasa mfundo ndiwebe President wa mason mphenya bravo amai

  • @saisonmwenda1275
    @saisonmwenda1275 5 місяців тому +1

    I like the massage osalola kulolodwa kuti ndiwe osauka powerful massage

  • @user-gj4li2gc8o
    @user-gj4li2gc8o 5 місяців тому +2

    Best speech our beloved former president osat chopotoka mikono chija ayi

    • @user-vd6gu7tv5u
      @user-vd6gu7tv5u 5 місяців тому +1

      Lunga lunga mkubadwa chilema chidza usana, bola mzako wangopotoka koma wako azangowudula zamawa sidziziwika.

    • @DokotalaPhungu-lk4kn
      @DokotalaPhungu-lk4kn 5 місяців тому

      Auze

  • @JonesMajiya
    @JonesMajiya 5 місяців тому +1

    Well spoken i do proud of you always mama

  • @user-oq5rg5mz7q
    @user-oq5rg5mz7q 5 місяців тому +2

    Good speech i like how you Tok my best Mom, onyasidwa anyasidwe

  • @JONAHMWALUGHALI
    @JONAHMWALUGHALI 5 місяців тому +1

    awonetsedi ntchito zawo nawo a JOYCE BANDA adzaonetsa zawo

  • @JohnPoul-lk5yq
    @JohnPoul-lk5yq 5 місяців тому +3

    Allomwe kwao ndi kutukwana nanga si sukulu inavuta

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 5 місяців тому +4

    Nkhani ndiya straight iyi peter mutharika anthu amadana awa kwacha mayi atisokosere uyu anapumatu😂😂😂

  • @AishaChipande
    @AishaChipande 5 місяців тому +2

    Mungozitukwanisa inu aaaaa daily salu pa phwewa grace chinga akukudikilani ku mwamba mukayakhe

    • @isaacchirwa9518
      @isaacchirwa9518 5 місяців тому

      Anachita naye chani Grace chinga tiuzenkoni

  • @user-ul6gf4xb5l
    @user-ul6gf4xb5l 5 місяців тому +1

    Mama mumakwana

  • @McphersonMsulira-zx2lj
    @McphersonMsulira-zx2lj 5 місяців тому +4

    Ife zogawazo tatopanazo tikufuna tizipanga zanthu zolandilazo ndiye zausiruzo zimenezo

  • @IbrahimWezely-qd4vj
    @IbrahimWezely-qd4vj 5 місяців тому +1

    Bravo JB

  • @marshacee8315
    @marshacee8315 5 місяців тому +2

    Nthano zakalekale pa nsonkhano aah zopoila nthawi yanu inatha Mai ife tikufuna munthu okhwima nzeru atichose mukapolowu anthu oipa inu Okuba ndege

    • @user-hd7wq2yc6m
      @user-hd7wq2yc6m 5 місяців тому

      Munthu wothandiza sazichemerela mu bible muli mau onena kuti dzanja la ku manja likamathandiza lakumanzeli lisawone tsopano kuthandiza kumene mukuthandiza inuyo ndikosathandiza olo even yesukritu amachiza anthu matenda osiyanasiyana koma samakhala pa platform kumazicherela mayi Inu thandizo lanulo ndilosavomerezeka pamaso pa mulungu mwinaso ndindala zomwe munkatibela ndi cashgate yanu yija ndege yathu ija munagulisa ndalama zake sizinawoneke munaba mayi wochenjere moyipa mwautsiru

  • @LeoC-in6um
    @LeoC-in6um 5 місяців тому +2

    APM the best leader

  • @PeterThawi-jc7zl
    @PeterThawi-jc7zl 5 місяців тому

    Joyce Banda is a wise president....I love her

  • @giftjamali8204
    @giftjamali8204 5 місяців тому

    APM my vote koma kalindo ekhayo akusambwanzani mayiii

  • @user-yj5xv4cy8x
    @user-yj5xv4cy8x 5 місяців тому

    Kumeneko ndiye kuyankhula

  • @NgomaRaheem
    @NgomaRaheem 5 місяців тому +3

    Mfiti yaikadzi kulimba mtima shup it kamzimayi koononga azakuvotera azibale ako omwewo

    • @Nelson-yp7ln
      @Nelson-yp7ln 5 місяців тому

      Palibe angavotere pp uli mu mcp

  • @mabvutobanda9168
    @mabvutobanda9168 5 місяців тому

    Bon kalindo the DC simukugona naye tulo eti 🤣🤣

  • @user-ki8hm1xp4p
    @user-ki8hm1xp4p 5 місяців тому

    Apm my vote

  • @MosesBanda-ef6fj
    @MosesBanda-ef6fj 5 місяців тому

    Kuyankhula moputsa kumeneko mai Joyce Banda nde mukufuna kuti tiguletse ufulu wathu ndi thumba la chimanga mmene likuyendela boma la dzitsiru ili tingagulitse voti yathu ndi chimanga tsiku ndi tsiku kwach kugwa takhalani serious bagamoyo chakwela walephera

  • @user-dd4mn3yk4f
    @user-dd4mn3yk4f 5 місяців тому

    APM MY VOTE

  • @PetersKondana-g6o
    @PetersKondana-g6o 5 місяців тому +3

    Mutilakwitsa mayi, zipatseni ulemu nokha

    • @KondananiNjakwa
      @KondananiNjakwa 5 місяців тому

      Mudzilakwitsa nokha koma Peter sadzapeza chonena, munthu oyipa

  • @user-wm5tv7on2u
    @user-wm5tv7on2u 5 місяців тому +1

    Good job❤

  • @user-qm3tw3vs1x
    @user-qm3tw3vs1x 5 місяців тому

    Help Malawi akhale NDI zochita osati zongogawa iyaaaaaa
    Phunzitsani anthu kupeza zochota osati mwagawa zingati aaaaah Kaya ndale zakwathu izi

  • @PeterThawi-jc7zl
    @PeterThawi-jc7zl 5 місяців тому

    Truth is anapeza bingu akuliyendetsa kale bwino dziko li....but all the same ..she tried during her tenure

  • @clintonhodda9830
    @clintonhodda9830 5 місяців тому +1

    Awa atumidwa ndi Chakwera kudzasokoneza APM koma akunamatu

  • @khanilapozo-fj5tq
    @khanilapozo-fj5tq 5 місяців тому +3

    Akufuna azimenyera kampeni Bushiri watch the space

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i 5 місяців тому

    Akhalechete chifufa musiyeni alankhule ndindaletu zimenezi

  • @user-oj5do1sd4j
    @user-oj5do1sd4j 5 місяців тому

    Yes

  • @AbdirashidMohamedIbrahim-ib9uy
    @AbdirashidMohamedIbrahim-ib9uy Місяць тому

    💯👏👏👏👏

  • @Lizzie-h1k
    @Lizzie-h1k 5 місяців тому +1

    Aaaa...mai mwayamba bodza zisiyeni....mudzakomoka nthawi yatsala pang'ono.... simungawauze anthu zochita akudziwa kale..inu mungopangitsa convention mudzisiye😂😂😂😂😂....mfundo zatha

  • @SimonMisomali-jw3vk
    @SimonMisomali-jw3vk 5 місяців тому +1

    Zomvetsa chisoni. Four years of unnecessary noise

  • @Omwale
    @Omwale 5 місяців тому

    ma speech anu ngolimbikitsa ulesi basi, umanja lende.. kutereku oimba ng'omawo sagwira ntchito yotukula miyoyo yawo azidikira kuti muwamangire nyumbazo...
    kafuseni Dr Dzombe kudowa...
    muzipeleka sustainable plans, kuti inu mutati mwachoka, umoyo waanthu udzakhala otani.. osati azingolandira.
    FWETSEKE!!!

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i 5 місяців тому

    Panopa sitikubwelelaso mbuyo ayi udf inapita dpp inapita pp inapita dpp yapitaso komaso mcp ikupita pompano

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 5 місяців тому

    A malawi ndi osauka, ndipo chakwera anakhalapo chairman wa maiko osaukitsitsa, Inuyo a Joyce Banda munalekeranji kumuza kut asalore ife ndi olemera

  • @JonesChingaya-yf4gg
    @JonesChingaya-yf4gg 5 місяців тому

    Inuyo a Joyce Banda ndiamene mwabweresa njala ili m'dziko muno ndi Tonse alliance.fetereza otsika mtengo simunatipase, cholinga tikanike kulima mudzizatipasa chimanga ife tizikuomberani m'manja koma mfiti za anthu muli inu nomwe.

  • @LongiMtimabii
    @LongiMtimabii 4 місяці тому

    Apm vote yanga

  • @user-ez1kc7zp9m
    @user-ez1kc7zp9m 5 місяців тому +1

    Pantumbopako joyisi bandawe pamodzi ndi onse akukuombela m,manjawo

  • @Misiyusuf
    @Misiyusuf 5 місяців тому

    🔥

  • @hadgeyahyaa8574
    @hadgeyahyaa8574 5 місяців тому +1

    Good speech mama❤❤❤

  • @charlesmartin6990
    @charlesmartin6990 5 місяців тому +1

    Useless, tikavote chifukwa cha zaulere, "vote for solomonic wisdom "ukapereka usayembekezele kubwezeledwa',thats not kupereka koona mtima"

  • @ChrisThaulo
    @ChrisThaulo 5 місяців тому

    Akuti alikunja Kwa Boma ... Aaaaa sad😢

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he 5 місяців тому

    My president JB ,l like you very much

  • @CASSIMKAMWANA
    @CASSIMKAMWANA 5 місяців тому

    Tizavota YDF

  • @VictoriaKumwenda-k6o
    @VictoriaKumwenda-k6o 5 місяців тому +1

    Mayi banda woyeeeeeee

  • @user-zh9kb2sj2i
    @user-zh9kb2sj2i 5 місяців тому

    Mayi banda sitingawanyoze anayesesa

  • @user-rg4du4vu9r
    @user-rg4du4vu9r 5 місяців тому

    Amarawi segurani maso anu musankhe moyenera osamango ombera manja zirizonse apa kunena zowona ariyense amene ana kharapo president wanzeru ndi bingu bas

  • @CharlesTchongwe
    @CharlesTchongwe 5 місяців тому

    Ng'ombe yamkaka

  • @EmercianahKasiku-en6hl
    @EmercianahKasiku-en6hl 5 місяців тому

    Ngati Dr Chilima dadzaima pazifukwa Zina vote yathu a Malawi ndi Joice Banda Agogo opha malubino aja ife ai Agogo olephera kuyatsa magetsi aja a Malawi takana, Agogo openta tsitsi kuti axioneka ngati mnyamata ife ai,munthu osunga dzifukwa ife pa ndale ayi adzatiphera ma judge oko dedwa munthu wanji Anthu Ake aputa ndi madzi osathandizako or 1tambala munthu wanji otuma mwana wake kupha ma Somalians okwana 30 kuwakwilira mu Nkhalango ya Chikangawa,munthu wanji odana ndikupikisana naye ku convention munthu wanji osatha kuyanjanitsa Ana Ake ku Çhipani uja kwake kunatha mdala wa zaka 83 wakula azikatsegula Manda kwake kunatha and Chilima ananena kale kuti a DPP ndi mafana achepa kwambiri ali kunja Kwa BOMA lero alboma mungamake ndi Chilima yo kkkkk kudzinyenga ndi Chala kumeneko Mai Joice Banda Chilima yooooyeeeeee moto kuti 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @mozykavalo7352
    @mozykavalo7352 5 місяців тому

    Kumalawi ndife anthu opusa mkazi unamugwila ndimamuna lelo ukatiso ubwele lane naye kupusa chani peter chakwela chilima onsewa ndi mbuzi sitingamalamulilidwe ndi nkhalamba ija mufuna tionongeso ndalama ndi malilo

  • @user-xn3lq1hj1r
    @user-xn3lq1hj1r 5 місяців тому +2

    Mfiti yayikazi ndiyoopsa kwambiri. Kunamidza anthu akuba aja akugawa chani???

  • @Razarusmbavachakwera
    @Razarusmbavachakwera 5 місяців тому

    Ngati zulizimenezo bushiri ndamene akuthandiza

  • @charlesmbewe4001
    @charlesmbewe4001 5 місяців тому

    Awa anathapo kale ataludza 2014 anazigulira Malo Kwa Bushiri ku south Africa 4yrs lero anganene chiyaninso akagwere uko kwa chakwera

  • @user-rk3gq7gd8f
    @user-rk3gq7gd8f 5 місяців тому +1

    Kodi amalawi akuvutika chifukwa chamuthu ameneyu chilima Lazaro zaugalu basi anaba ndalama boma ndani sakuziwa

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 5 місяців тому

    Ulibe manyanzi iwe kodi ndala unaba zija unazimaliza ukufuna kuzatibelanso kawili Malawi sazalamulilidwanso ndi nkazi aliyense

  • @BraveShugah-xm5dt
    @BraveShugah-xm5dt 5 місяців тому

    Aaaahhh koma Joyce😂😂😂😂😂

  • @user-uk8sj2vd2v
    @user-uk8sj2vd2v 5 місяців тому

    My vote peter

  • @carlossadimba595
    @carlossadimba595 5 місяців тому

    Kkkkkkk koma JB molalo ngati wa chair .......

  • @patricgama4788
    @patricgama4788 5 місяців тому

    Iwe dzaka dziwili una gwetsa kwa iwe unayi pedza li pa 500 wayigwetsa yafika pa 2000 galu unali osauka pano uli pa top 10 ya anthu olemela kunokumalawi mu ulamulilo wa zaka dziwili dzokha ndiye uku funa ubetso nyiniyako

  • @user-qq3ip1od6i
    @user-qq3ip1od6i 5 місяців тому +1

    Mai oipa uyu

  • @imranhabibu1743
    @imranhabibu1743 5 місяців тому

    Inu ndi wakuba Chakweraso ndi wakuba ndiye mwakumana chifukwa mukubakilana

  • @imranhabibu1743
    @imranhabibu1743 5 місяців тому

    Mayi mutukwanidwa nazo izi chabe,zisiyeni

  • @DOMINICSELETA
    @DOMINICSELETA 5 місяців тому

    Zoonadi mayi

  • @user-rc3ze2oi7u
    @user-rc3ze2oi7u 5 місяців тому

    MULIBE MFUNDO AMAI NDIPO MULUNGU AKUKHULULUKIRENI PA ZIMENE MUKUGANIZARA 🎉🎉🎉🎉🎉

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he 5 місяців тому

    JB mmakwana , anthu wenawa kutukwana ndiye kudya kwao

  • @FefieTenisha-du7ge
    @FefieTenisha-du7ge 5 місяців тому +1

    This speech is so empty...
    I wonder whether she really sat down to prepare for it....
    What will she benifit by attacking political activists like Bon Kalindo who are just trying to enlighten Malawians so that they can make informed decisions regarding their country's political fate...
    Is she trying to mean that if you have no money then you have nothing for Malawians...???
    Knowledge is power , don't underrate what genuine political activists are contributing to the polical stage of this nation by providing the most necessary tool ie knowledge to the already low thinking population base...
    Timaona ngati muyankhula zanzerutu... nonsense...
    With this deluded kind of thinking by our leaders Malawi can never develop!

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 5 місяців тому

      Ali chete ku tonse olo kudzudzula Corruption ili kumeneko Mayi wa bodza uyu🙌🙌

  • @user-vn6di8hc1v
    @user-vn6di8hc1v 5 місяців тому

    Mfundoless...chairman of poor nations chakwela

  • @user-is5dl7np9g
    @user-is5dl7np9g 5 місяців тому

    Uyu ndiye akununkha cashgate akagwere APM my vote 2025

  • @AmusedDimSum-hd5yp
    @AmusedDimSum-hd5yp 5 місяців тому

    madam cash gate

  • @yasitafuphiri-nw2he
    @yasitafuphiri-nw2he 5 місяців тому

    Amalawi ambiri ndife ozizira mmitu 😢

  • @JosephMwenyali
    @JosephMwenyali 5 місяців тому

    Amayi opusa awa,Joice wayiwala kuti unayankhu ku njamba kuti coronavirus kulibe ,muthalika akuopa chisankho

  • @ALEXKAUYE-it9os
    @ALEXKAUYE-it9os Місяць тому

    OK mama

  • @thomaskalima7379
    @thomaskalima7379 5 місяців тому

    Good speech former president

  • @user-ce6hy6tp7e
    @user-ce6hy6tp7e 5 місяців тому

    Iweyo zinakukanika kale chitsilu iwe joice banda ndpo pita uko ukagwere

  • @SandikondaPhiri
    @SandikondaPhiri 5 місяців тому

    Kodî ndege yija adagula bingu ndimisonkho yaamalawi yilikuti?

  • @patrickkapinga7091
    @patrickkapinga7091 5 місяців тому

    Kupanda kumupha bingu ukanaurawa u president

  • @MussaJamess
    @MussaJamess 5 місяців тому

    Palibe chabwino ku dziko la Malawi Mulungu yekha Ndi amene akudziwa😭😭😭

  • @GiftMambiya-fh7xb
    @GiftMambiya-fh7xb 5 місяців тому

    Mayi oipa iwe

  • @abangaabanga4677
    @abangaabanga4677 5 місяців тому

    Mawu amayi anga 👏

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x 5 місяців тому

    Kd pa salu asitha ayikapo purple ee dangerous colour kuli.zilipo mmm

  • @ophlexmkondowe8107
    @ophlexmkondowe8107 5 місяців тому

    Kodi nyumbazo tiyika mmbale ndi kudya?😂

  • @patricgama4788
    @patricgama4788 5 місяців тому

    Ndalama zimapedzeka tchile dzija ku capital hill galu iwe

  • @aufiJafali-uj6gg
    @aufiJafali-uj6gg 5 місяців тому

    Ine ndimawona ngat mupemba apule asitse feteeleza Kut anthu Ali tilila 😂😂🎉

  • @user-rk4ch1ly3z
    @user-rk4ch1ly3z 5 місяців тому +1

    Iweyo ndiye oyipisisa ndi adzakowo,,pano ukubaso misokho ya amalawi.

  • @user-pb1yr1jx5g
    @user-pb1yr1jx5g 5 місяців тому

    APM MY VOTE 🗳 ❤️

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 5 місяців тому

    Kkkkkkk koma ziliko eesh, osanena za Corruption ili ku tonse yi bwanji inuso apa nde mwapala Vote ndi mumtima 🔥🔥

  • @amaleeehmuzik-official
    @amaleeehmuzik-official 5 місяців тому

    This country we have start war 😢 guyz amene mwakozekha bweran ku Dm tayamba group yomwe tingayambitse force acting komaso u'll get salaries b4 kulowa nchire

  • @GersonKalongonda
    @GersonKalongonda 5 місяців тому

    Chilungamo mchopweteka. Koma kunena zowona andale adakakhala kuti amagawa zithu ngati mene amachitira pa campaign bwezi mavutowa atachepa

  • @MoreenGeorge-dn7js
    @MoreenGeorge-dn7js 5 місяців тому

    Amalawi wabwino samuziwa my vote

  • @shaibuJames-c3w
    @shaibuJames-c3w 5 місяців тому

    apeter osati tonse zazii

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 5 місяців тому

    Ndiwe chisilu iwe mu 2020 unatinamiza iwe kt voterani chakwela sakutukwanazana ndi muthu wamulungu lero alikuti Lazaro wakoya galu iwe mu 2020 unapangapo chani iwe palibe chimeni ungatinamize iwe

  • @samungwira6927
    @samungwira6927 5 місяців тому +1

    Akunama zinamukanika kale