SILVESTER NAMIWA MPAKA LERO KUYANKHURA IZI?KODI IYEYU SAMAOPA? TAMVANI ZOKHUNZA IMFA YA CHILIMA ZIJA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 112

  • @MonijaKataika
    @MonijaKataika 8 днів тому +7

    Namiwa may God protect you. U are blessing to us.

  • @Ada-u6g
    @Ada-u6g 8 днів тому +15

    Namiwa ndiiwe munthu wakoru malamuro umaziwa chonde bungwe ya cded itimenyere nkhondo ❤

  • @dalitsonambazo
    @dalitsonambazo 8 днів тому +4

    Zabwino zonse Mr namiwa potimilila mulungu akutsogoleleni pachimenechi🙏💪

  • @JosephCompan
    @JosephCompan 8 днів тому +3

    no one is like namiwa in this country bigg up

  • @JohnKapyola
    @JohnKapyola 4 дні тому

    Powerful papa 🎉🎉 God bless you

  • @rectormasanjala
    @rectormasanjala 8 днів тому +3

    Koma skc anafa imfa yowawa Kwambiri mmmmmm Ambuye akuwona zonsesi Ndipo akunva 🙏

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 13 годин тому

    I like this guy continue fighting for Malawians.

  • @JeremiahKapundu-j1p
    @JeremiahKapundu-j1p 8 днів тому +1

    Namiwa God bless you

  • @cydrickchikuse2563
    @cydrickchikuse2563 7 днів тому

    God bless you Mr Namiwa and CIDEDI

  • @HurmlysLangwan
    @HurmlysLangwan 8 днів тому +3

    HRDC ndyimweyi CDED yi😅😅

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 8 днів тому +5

    Mwama mlomwe ameneyo alibe masewela ....chakwera ndi munthu wopusa kwambili

  • @LawrenceMalinda
    @LawrenceMalinda 8 днів тому

    Mr Namiwa this speech is well spocken

  • @LawrenceMsamira
    @LawrenceMsamira 6 днів тому

    Power da d

  • @PeterChimbalanga-k8s
    @PeterChimbalanga-k8s 7 днів тому

    ❤❤❤❤❤namiwa woooo yeeeeeee

  • @MosesYokaniah
    @MosesYokaniah 8 днів тому +4

    Ipase moto

  • @YasinMmadi
    @YasinMmadi 7 днів тому

    Mr namiwa big hand to you

  • @MchengaAssama
    @MchengaAssama 8 днів тому +4

    Kkkkkk anamwaliranso kawiri

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 7 днів тому

    Anawiwa mulungu apitiliza kukusama lilani mumatha ndi zila zazikola thu❤❤❤

  • @RebeccaToyoyo
    @RebeccaToyoyo 8 днів тому

    You are the best namiwa

  • @MwayiKalirani
    @MwayiKalirani 8 днів тому +2

    Inu ngati otiyimilira munakapilira osathawamo...

  • @SamuelAntone-mz6nq
    @SamuelAntone-mz6nq 8 днів тому

    Ndye kuyakhula kumeneko bwan auzeni zoon avetse tse 💪💪💪👉

  • @JabesiNason
    @JabesiNason 7 днів тому +2

    Mmmmmmmm Omenyera ufulu aku Malawi mbuzi zokhazokha,,, palibe zomwe angapange Namiwa uyu khwangwala wachabechabe uyu

    • @MudaMsukwa
      @MudaMsukwa 6 днів тому

      Yabaya 😂😂😂mboli yako patiii akutero JB

  • @cgdammw963
    @cgdammw963 8 днів тому

    More fire namiwa 🔥🔥🔥

  • @LonjezolistonH
    @LonjezolistonH 7 днів тому

    Namiwa kutchaya kugwetsa, Big up

  • @TiwongeChikhoza
    @TiwongeChikhoza 7 днів тому

    Bravo Namiwa

  • @ISHMAELFRIDAY-ki6ry
    @ISHMAELFRIDAY-ki6ry 8 днів тому +4

    Chakwela ziko lamupana ngt zip wapalisani kukweza zip pain,kusisa zip pain yokhayokha 😂😂😂

  • @Thokozanikufandiko
    @Thokozanikufandiko 5 днів тому

    🔥🔥🔥

  • @augustinkapenuka6153
    @augustinkapenuka6153 8 днів тому

    Namiwa more 🔥🔥🔥🔥

  • @RightwellZumbwe
    @RightwellZumbwe 8 днів тому

    💪💪anamiwa apaneni amenewa osawataya awa mpaka anene zoona

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 8 днів тому

    ❤❤❤❤ Namiwa

  • @wilsonchimtikaphiri9496
    @wilsonchimtikaphiri9496 8 днів тому

    NamiwA ❤❤❤❤

  • @MarriamShakira
    @MarriamShakira 8 днів тому +3

    I ❤ you namiwa

  • @BenjaminMoyo-s6u
    @BenjaminMoyo-s6u 8 днів тому +2

    ❤❤

  • @serakillo8668
    @serakillo8668 8 днів тому

    Kkkk love you namiwa zoona asatitole kodi athuwo anamwalira kawiri chakwera ndi ngulu lako....dont take malawi grated pls

  • @MarkElia-i7q
    @MarkElia-i7q 7 днів тому

    Kod Black Box 🎁🎁 ilikut sadaikambe mu report ija Mmalo Mwake amayankhula ngat Zolengeza zapa Malilo 😊😊

  • @HappyAutumnTrees-cd9ye
    @HappyAutumnTrees-cd9ye 8 днів тому

    Mwaphera dala nabiyen dzikoli mutsale nayo😭😭😭😭

  • @McfastonMkhala
    @McfastonMkhala 7 днів тому

    Iwe Namiwa, Bon Kalindo ndi Wandale same Whatsapp group.kod munatani anthu akumeneko?

  • @PatrickMwizozo-ep3vg
    @PatrickMwizozo-ep3vg 8 днів тому

    To train a soldier is not a joke ..wake-up Malawian

  • @ShakiraEra-f5n
    @ShakiraEra-f5n 3 дні тому

    Mmmmm kma mulungu akhale mulungu

  • @GraceCbwanali
    @GraceCbwanali 8 днів тому

    Mr Namiza umati yimirila Mulungu azikudalitsa

  • @ThandiMatin
    @ThandiMatin 8 днів тому

    Ati boma ili akulamulira nsima mafiya😂😂😂😂 apo nde wang'aluradi

  • @RosinaPatel
    @RosinaPatel 8 днів тому +1

    Anthu anafa aja ndi anthu ndithu..tisasiyire pamenepa atiuze choona chake.. SkC anafa imfa yowawa pamodzi ndi anthu ena aja..anthu opanda chisoni nkhaza anaoanga zonyasa

    • @spargomw
      @spargomw 8 днів тому +1

      Kufa ngat chiweto, m'malo mofera ku chipatala mkukafera kuthengo😭😭😭😭😭

  • @NicolasKamunga-rv9vr
    @NicolasKamunga-rv9vr 8 днів тому

    Kkkkkkkk mpaka apulu kupanga chipidigolilo😂😂😂😂

  • @TroubleMuthala
    @TroubleMuthala 7 днів тому

    Ulemu wanu Mr namiwa

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 6 днів тому

    Next time nyimbo iyo mupeze ina

  • @MarryNyilongo-s5x
    @MarryNyilongo-s5x 8 днів тому

    VIVA AAA

  • @thomasphiri7799
    @thomasphiri7799 8 днів тому

    You are the voice of the voiceless Namiwa❤

  • @SolidrockKanyenda
    @SolidrockKanyenda 8 днів тому

    Only rast man standing NAMIWA

  • @AgnesGondwe-l3b
    @AgnesGondwe-l3b 8 днів тому +1

    Anamiwa osaopa komaso osatopa tili pambuyo panu

  • @user-jmuller
    @user-jmuller 8 днів тому

    Dolo ka 500🤞🤞🤞

  • @VincentMapira-h1f
    @VincentMapira-h1f 8 днів тому

    I want to be a member of cded. Ndipange bwanji

  • @MathewsWisick
    @MathewsWisick 8 днів тому

    🎉🎉🎉🎉

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 8 днів тому

    True Malawian

  • @GodfreChayamba
    @GodfreChayamba 8 днів тому

    Bwana namiwa mukukwanila pitilizani tili PA mbuyo panu

  • @eliasgondwe
    @eliasgondwe 8 днів тому

    Chizeleza Mamiwa, kapelekeni umboni kumakanaso ndalama, umadyazo zikupha!! Nanga zachisankho zikugwilizana chiani?

  • @NASTARANDREW
    @NASTARANDREW 2 дні тому

    umboni wonse uli mu black boxs, kod black boxs inapita kuti?

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule 8 днів тому

    Music kumbuyoko imandichosapo apa

  • @HurmlysLangwan
    @HurmlysLangwan 8 днів тому +1

    Katundu

  • @HenryEdwinKapindu
    @HenryEdwinKapindu 8 днів тому

    Fire them,,,, ife zikudibowa zomwe akuchita agalu amenewa

  • @JohnBandawe
    @JohnBandawe 8 днів тому

    Tien naon mademo tipange commission of enquiry yathu osat nyasi izi RIP SKC

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 6 днів тому

    Inu maina ali mu cump iyo asakupusisen plzzz oho aliyese amaziwa komwe amachokera

  • @JordanSuliwa
    @JordanSuliwa 8 днів тому

    Mulungu asogolele Malawi. Mr Namiwa tisatope mpaka chenicheni chidziwike.

  • @PeterMLiwaya
    @PeterMLiwaya 7 днів тому

    Mukamationa tikunyoza chilungamo mwayankhulacho musadabwe tili mgulu lokondwera ndi imfa ya skc cozakanatilanda upulezident 26:50

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 8 днів тому

    Koma Namiwa mulungu azikudalitsani pa ntchito yabwino imene mukugwira

  • @KelvinBandah-o5v
    @KelvinBandah-o5v 8 днів тому

    Rip saulos chilima tiva zambiri

  • @CharlesBanda-v8k
    @CharlesBanda-v8k 8 днів тому

    Chilima anali mwana pandale sakanayenera kupanga nawo alliance ndi mikangoyi

  • @TamUs-u2h
    @TamUs-u2h 8 днів тому +1

    Kuchikamwa ngati wadya manyi iwe Namiwa wa DPP

    • @SiboNkundi-hm1si
      @SiboNkundi-hm1si 8 днів тому

      Mwapusa bwanji? Apa akukamba za DPP or akuyankhula za amalawi? Ngakhale ukuyankhula kupusa choncho chonsecho ukuvutikila limodzi ndi ukuwachemelelawo akusangalala okha

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 8 днів тому

    Following Namiwa , yes for those who are satisfied with that nosense report then just be quite ,,,,,,we want to hear and know the truth about the death of SKC & 8 others

  • @EmmanuelWhite-d2f
    @EmmanuelWhite-d2f 8 днів тому

    Koma namiwa akuyesetsa koma amalawife tili ziii

  • @SteveZimba-e8s
    @SteveZimba-e8s 8 днів тому

    Namiwa Mulungu azikusogolera ndikukudalitsa chifukwa umaima pa chilungamo osagulika Ngati enawa timakudalira kwambiri aliuze zoona dziko la Malawi Kuti zidakhala bwanji pangozi ya ndege tikufuna chilungamo basi.

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 8 днів тому +1

    Namiwa umakwana kobasi

  • @Homeofpeace321
    @Homeofpeace321 8 днів тому

    Chakwela analakwitsa kupha Chilima, ana achilima amafunaso adakamaona bambo awo

  • @BenjaminMoyo-s6u
    @BenjaminMoyo-s6u 8 днів тому +1

    Akutitola kwambiri abomawa

  • @BarakiChriss
    @BarakiChriss 8 днів тому

    Za chikape wa DPP ndiwe munthu akuyimilira amalawi Ife iwe ndiwakut ulibe umunthu

  • @AtupereSadiki
    @AtupereSadiki 7 днів тому

    Ndizoona akunena Namiwazo ndi report yopanda pake bolanso anakangisiya zausilu basi

  • @ChikumbutsoChiphaka
    @ChikumbutsoChiphaka 8 днів тому

    Apite kulikonse namiwa, ngozi I dachitika bax

  • @MussahChidothi-y5k
    @MussahChidothi-y5k 7 днів тому

    There no secret under the earth and evil begets evil choti mudziwe amalawi fiti siyiziwulula yokha zimene yimapanga Koma yikakumana ndizokhoma ndipamene yimawulula

  • @ChikumbutsoChiphaka
    @ChikumbutsoChiphaka 8 днів тому

    Mmmmm, kodi namiwa amadziva kudziwa zinthu kwambiri?, chifukwa chani adatulukamo mu commission mmalo moti akapeleke ma umboni wakewo, iyeyo ngati ndi dolo apange yake inquiry, and akayambe kupanga inquiry anthu amene adamwalira kumudzi kwao

    • @wilsonchimtikaphiri9496
      @wilsonchimtikaphiri9496 8 днів тому

      Akadamusowetsanso

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 8 днів тому

      Awa ndi achitsiru ngati sanavese linawengedwa ndi amene amapanga kafukufuku koma kuti anthu akhale ndi ma copy a report azapeleka president akaliwona ndiye timavesa akulu wa

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 8 днів тому

      Anamiwa ngati muli ndi mayakho tangowawuzani a Malawi munthu wina aliyese Ali ndi nthawi yofera we have to accept that all of us we are going to die which malawian did not eat food for what reason

    • @WelingsLongwe
      @WelingsLongwe 8 днів тому

      Ngakhale munthu atakhala wopanda nzeru sangasakhe commission of inquiry ngozi itangochitika kumene anamiwa taziyakhulani munthu mtsogoleri

    • @JabesiNason
      @JabesiNason 7 днів тому

      Eti iyeyo osangopanga yake inquiry bwanji?? Kudzimva kuzindikira ili mbuzi yeniyeni

  • @festonselemani4491
    @festonselemani4491 8 днів тому

    Ku Malawi kuli anthu ena ena wolimba mtima

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 8 днів тому

    Boma loyendesedwa ndi zigawenga komanso mbava ....chakwera uzaziona nthawi ikazakwana

  • @MatiusChinawa
    @MatiusChinawa 8 днів тому

    Kkkkk guys skc analakwa chan.

  • @ChikondiBannet
    @ChikondiBannet 8 днів тому

    Macheso wqsunga ndiwe namiwa

  • @BandahLemos
    @BandahLemos 8 днів тому

    Munachita bwino kutulukamo kut inu mubwerese chilungamo

  • @SiboNkundi-hm1si
    @SiboNkundi-hm1si 8 днів тому

    Yeah indeed someone must pay the price, dzikoli asalitenge mopepela choncho ngati la abale awo

  • @ColiamAbineli
    @ColiamAbineli 8 днів тому

    Kodi inu mudali mmodzi mwa osankhidwa kukhala mwa ofufuza nawa ndipo tidaakudalilani kuti tidziwa zambiri kuti zidakhala bwanji kuti miyoyo ya osalakwa iluzike inu mkutuluka, tizikhulupilire bwanji zomwe mukulankhula ku mtundu wa amalawi bwana?

    • @McfastonMkhala
      @McfastonMkhala 7 днів тому

      Palibe wina aliyense wanzeru amee angatsatire iwe chitsilu Cha DPP ndani samakudziwa. Imalifuna report lachani munthu unakana kuuza amalawi zoona. Usayankhuleso kanthu panjhaiyi

  • @MaulanaIriyasa
    @MaulanaIriyasa 8 днів тому

    Kukwela ndege mpaka kuwuma magazi koma zilikoliko

  • @HellenNdalama
    @HellenNdalama 2 дні тому

    Kod report limenelija amapangira mtundu wa aMalawi mwina amapangira kuza banja lawo momwe agawira chuma chawo akazamwalira?,koma anthu amene aja ndi olengedwadi ndimulungu akapange report ngat akuulusa nkhani pa tv or wailesi, stupid enquiry

  • @JamesYusufu-l6d
    @JamesYusufu-l6d 8 днів тому +1

    eeeeee koma chakwela. ndigalu. weniweni. lopoti limenero akamuwuze monika. kaziwake. zopusazo. ai

  • @ChristopherChakometsa
    @ChristopherChakometsa 8 днів тому

    Go go namiwa tuliuzeni zoona

  • @williempinda505
    @williempinda505 8 днів тому

    The 😂

  • @WarriorKB-l3i
    @WarriorKB-l3i 8 днів тому

    Kkkk apo nde mwalasadi bigy aliense amene ali boma atimva di kuyabwa coz akuzolowela.Ma actionz a kuenela atengedwe mosacedwa cifukwa zimene anamiwa akulankhulazi ndizomwe a malawife tikulankhula ndizoona kuti lipotili angotitayisadi nthawi ndi kobili zathu zisilu zimenezi Anamiwa tili pambuyo panu osadanda.

  • @JohnLyton
    @JohnLyton 8 днів тому

    Iweyo ngopusa iwe unkathawilanji

    • @DoriceMagawa
      @DoriceMagawa 8 днів тому

      Akafuna apeze nthaw yabwino yodzaona zolakwikazo and anali nd zochita zina zofunikilaso nthaw yomweyo. Apa nde tikufuna kudziwano from mcp commission

  • @ChoopsyaLloyd
    @ChoopsyaLloyd 8 днів тому

    I think namiwa akufunika ku mental

  • @PatrickKatentha-x7s
    @PatrickKatentha-x7s 8 днів тому

    In

  • @DoriceMagawa
    @DoriceMagawa 8 днів тому +1

    ❤❤❤❤