pano atumiza aku Embassy mu ma churches kuno ku South Africa kuti aliyese alembetse amene anabwela kuno ndi pasport.....date line pa 7 September....aliyese akhale atalembetsa ....Johannesburg,cape Town, Petersburg ,petermalisburg...
Kuno big " Mr don't trust " pa Durban pali mushe yipondeni fadah ndikumvani 😂😂 more!! fire 🔥 mungondiwuzilako a " MCP " tili ku excile tikumana 2025 buuuu!!!
Mukamati mbuzi including your parents? Chifukwa nawonso ndi amalawi bro kumayankhula bwino you don't call peoples kuti ni mbuzi tizasiya kukupanga follow
Bingu anali katundu or Apm my vote
More fire dont trust😢😢😢😢😢
Ku Kempton park mwatiimima Mr don't trust we love u mwaaaaaa Limpopo fm radio more fireee
Big up brother mr don't trust ❤❤
Ine pheee kumvera Limpopooooo
Welcome Mr Don't trust
Koma apolice chimene akumapangira matama sichikuwoneka pothamanga kukamanga munthu woti akumenyera ufulu wa iwowo
Long live Mr Dont Trust God's protection should be upon you
Tili limozi limpompo mpaka 2025
Mtanyiwa ndi 1
Wooooza woza akamuna big up
More 🔥 Limpopo mumatiimilira
Following..... freedom fighter 💪
Ineyo ndikupempha Limpopo andigaile wailesiyo imandewaza
Lipopo more fire fire
Muli bwanji mr don't trust
More fire
Limpopo yomweyo kuti wawawa kkkkk❤
Kkkk waza don't trust Mr pangoline wapa Limpopo fm
😂😂😂 pomwepo live from chikangawa
Boma loyendesedwa ndiafiti
Yaaaa awuzeeni arimpopo agalu amenewa atisiiyatu pausiwaa away atiphatutonseee kumalawikuno chimunthutu choyiipa ichi
Dj don't trust iwedi ndipangolini😂😂😂😂😂😂 l,m proud of you
Boma lamamafiya wokhawokha iyi
Ndipo live mr don't trust ❤❤❤❤
amwene mundipepheleko kwa vice president kt andipaseko chisot ndi make ndizipanga masewelo
More Liiiiiiiiiiiiimpopo
Don't trust please timakunyadirani koma pankhani yanyimbo mzitiyikira zabwino zomwe amakonda kubwera nazo ntanyiwa .ineyo Limpopo FM imandiwaza akandiyikira nyimbo ya Kain Kodi achilima alikuti?😂😂😂
Port Erazabeth in kostern we are good Peter Thomas sauth Africa
Hamayo ine tamia uja
Wooo zaaa kkkk ukunvek
Km Adah awawa amandiwaza kwambilit 😂😂 ukali wawo km
Mbuzizo ndi mmene ife amalawi tikuchitira mkana akuti amalawi tili ngati mbuzi sitichedwa kuiwala
Kkkkkk koma Don't Trust...Mayi wa mitala ya Azimbambo. Vera Kamtukule kkkkk
pano atumiza aku Embassy mu ma churches kuno ku South Africa kuti aliyese alembetse amene anabwela kuno ndi pasport.....date line pa 7 September....aliyese akhale atalembetsa ....Johannesburg,cape Town, Petersburg ,petermalisburg...
Kuno big " Mr don't trust " pa Durban pali mushe yipondeni fadah ndikumvani 😂😂 more!! fire 🔥 mungondiwuzilako a " MCP " tili ku excile tikumana 2025 buuuu!!!
Nyatwa
Zafika pokuti akugotapa nthumba lomwe wandikana nalo ndipo sakuwelega kuti kodimawa limati chani
Katundu don't trust umakwana
Bingu was great
Ndipo inu eeee dziko ili ayi chakwela akutizuza
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
Tang'alula iwe
Bingu anari mashin opangira mashin azake
Kuwina mcp ndizachoka ku malawi
Ulemu wanu limpopo fm
Komadi malawi ndi prison pa yokha
Don't trust more fire
😅😅😅😅😂😂😂mpaka dzaka 25😅😅😅😅😂😂😂
Mukamati mbuzi including your parents? Chifukwa nawonso ndi amalawi bro kumayankhula bwino you don't call peoples kuti ni mbuzi tizasiya kukupanga follow
boma la zigawenga ili mbava zitsiru zokha zokha izi
Umatha Aise
boma la zigawenga ili
MBAMBANDE
Akamuna bambo
Atamia 😅😅😅😅
Tili pa following
Kkkkk umakwana
Udzigwira ntchito pa weka osamadalira boma pachili chonse
All the way from Chikangawa party
Koma adawa amaziwa tchito serious
Zomvesa chisoni kwambiri mmm
Ndipo kwambiri
Big up Limpopo