Mulungu wa David muchilitseni mwana wanu. Zimene mudachita pa ana a Israel pa 2mafumu 2 vs 19-23 muchitireniso mzimayi uyu ndikuti dziko lapansi likulemekezeni🙏🙏🙏
very sad but glad that her husband is still around. God will heal her, the fact that she met Rodwell it"s proof that God is clearing her healing journey.
What God can not do does not exist 🙏 ambuye onetselani Kwa mayiwa kuti palibe chokulakani, palibe chomwe mumalephera,Yehova akhudzeni mwapadela dela 🙏🙏
Yehova adzakupewetsani ku matenda aliwonse. Sadzakugwetserani matenda owopsa aja munawadziwa ku Igupto, koma adzawagwetsera pa odana nanu. Deuteronomo 7:15. Get well soon mama
Satana amabweresa zosakhara bwno pa moyo wathu kuti tizimufusa mulungu mafunso osakhara bwno, km inuyo mulungu chitanipo kanthu pa Mai awa yesu mwana wa David muchitilen chifundo mwana wanu amene akuvutika ndi matenda
Ambuye onani mayi uyu akuzum,zika kwambili ndi nthenda koma zonsezi ndikusiya m,manja mwanu amen
Mulungu wa David muchilitseni mwana wanu. Zimene mudachita pa ana a Israel pa 2mafumu 2 vs 19-23 muchitireniso mzimayi uyu ndikuti dziko lapansi likulemekezeni🙏🙏🙏
Mulungu away awayendele mwapadela I can fill the pain there going through
Our almighty God who at in heaven hear the cry of this woman lord for we know that you never fail have mercy upon thus woman lord in the name of jesus
Ambuye amene munamuchiza Hezekiah atadwara aendereni Mai awa apeze bwino mu ukuku wanu Ambuye 🙏🙏
Moyo wanga iwe,,,,ulinazo zifukwa zoyamikira Yehova
Ooooh mulungu wanga ndzakutamandani matsiku onse amoyo wanga mkhuzen mzimayiyu ndi dzanja lanu lamachilitso
may Allah almighty afewesele mayiwa kwa Allah ndikomwe timadalira
Ameen
Ameen
very sad but glad that her husband is still around. God will heal her, the fact that she met Rodwell it"s proof that God is clearing her healing journey.
Mulungu achilitseni amayiwa muntchifunilo chanu amen
What God can not do does not exist 🙏 ambuye onetselani Kwa mayiwa kuti palibe chokulakani, palibe chomwe mumalephera,Yehova akhudzeni mwapadela dela 🙏🙏
What God Cannot Do Does Not Exist #NSPPD 8AM FIRE 🔥 PRAYERS
Mulungu woziwa kuchilisa iyikepo zanja.amen
Eish ziko lapamsi
Eish 😭😭😭😭may God heal you mama....please Lord touch this woman and heal her
Eee Ambuye awachitile chifundo mu dzina la Yesu
Ambuye nchilitseni nzimai uyu mudzina layesu amen
God this is too much please touch this woman with you healing hands 👐 please God hear our prayers
Ameen!!
So touching.God Please do something what she needs is your touch
This is so touching!!! God please touch this woman
Ambuye Mulungu muyendeleni mayiyu mukhuzeni ndimachiliso anu .Palibe chimakulakani Mulungu wanga muchoseleni ululu mayiwa
Ambuye ngati munachitisa batrumeyo kuonanso choonde muoneseni mayi uyu amen
Healing Grace
Yaaaa ALLAH!! may you soften for this Lady please so she be healed!!
This is disturbing eeeeh! God please see this woman and heal her. Amen
Eeeish that's indeed Mighty God touch her with healing
Ena akuvutika pomwe ena akuba ndalama zanthu eish Allah amuthangatile dzimayiyu mapumidwe ndiovutaso eish
Ambuye ikani dzanja lanu kwa mayi uyu amen
Achita kuoneka kuti alipaululu😢😢 Ambuye achiliseni mayi wa
Ambuye muchitireni chifundo mwana wanu achiritsidwe mudzina la mwana wanu yesu khristu sikukulamulani Koma kukupemphani 🙏
May the healing river flow over your life mama😢😢
Lord have mercy😢😢😢😢 touch this woman with your healing hand
Pomwe ife nzeru zathu zathera mpomwe mumayambira Yehova wathu pakuti chifundo chanu ndi mphamvu zanu zilibe malire simuwerengera mphulupulu zathu.tikhulupilira muchita chozizwa ndithu.amen
😢
Healing mercies from above mama
Yehova adzakupewetsani ku matenda aliwonse. Sadzakugwetserani matenda owopsa aja munawadziwa ku Igupto, koma adzawagwetsera pa odana nanu.
Deuteronomo 7:15.
Get well soon mama
Please God😢😢🙏 get well soon mama... May God see u through
😢😢😢😢 so sad. God have mercy.
Ambuye akhunzeni mayi ndimkono wanu wamachilitso pakut paiwo okha sangathe koma adalira mphamvu yanu
Dear God....😥😭😭
Ambuye akudzeni amayi wa ndi zanja lanu lamachilitso 😢😢😢
Matenda achilendo awa eishh ambuye bwerani muzatiweluze 😭😭
May Almighty Lord heal you Mama 🙏
So touching, anyway God lives. Otherwise atolankhani zifunsani mafunso ogwirika malingana ndi condition yamunthu.
Allah knows the best
Chinena ndilibe koma Mulungu yekha akuoneni mwapadera pa ife sitingathe 😢😢
Mulungu wanga tikudziwa timakuchimwilani tsikunditsiky 😢koma please ambuye muchitileni chifundo nzimayiyu ndipo mupatseni machilitso pamoyo wawo😢😢😢
Eeiishh mzimayi ameneyu ali mu ululu owopsa mmmm Ambuye Mulungu tikukupemphan mpatsen machilitso mzimayi ameneyu chonde chonde
Eishhhh mayiwa akuvutika tisanamei
Dzanja la ambuye lamachilitso likukhudzen mama
Mmmmmmm zosayenda
Mmm somvesa chiso Mulungu awayang'anile Mayi amenewa
Apapa pakuyenera kuti mathandizo osiyanasiyana awafikire ndipo pakuonetseratu pakhomopo kuti Pali zosowa zambili ambuye atithandize kuti titengepo step tisangoyakhula or only comment ife anthu a kuntandire
Mulungu akuonetselen machilitao ake aphamvu zodaphitsa mudutsemo munyenho imeneyi mukhala bwn mu phamvu ya Yahweh
Satana amabweresa zosakhara bwno pa moyo wathu kuti tizimufusa mulungu mafunso osakhara bwno, km inuyo mulungu chitanipo kanthu pa Mai awa yesu mwana wa David muchitilen chifundo mwana wanu amene akuvutika ndi matenda
God have mecy and heal her
😭😭😭Ambuye mulungu ndinu nthandizo laliyese ambuye ayendereni amai awa
Healing mercies from above 😢😢
Mmmm very sad 😭... Koma sound musamaike mkati kati mwa interview disturbing
😂😂😂😂😂😂 zikundiwawa kwambili ndi nkhani yayikulu kunena zoona
Nde mukuseka??😢
Chusekesa ndichan abale?? Mmmm
😭😭😭🙆🏻♂️ lord please forgive this mum
😭😭😭😭 ambuye loweleranipo musakhale chete inu mulungu
Ambuye chitaniponi kanthu pa Mai awa😢😢
Allah tikupepha chitapo kathu
Rest in peace Mai Nyumwa..you fought a good fight
Pepan Mai wanga 😢😢😢😢😢😢
This life😢
Healing mercies
Ambuye inu mwini moyo mwini machilitso akhudzeni mwana wanu mayi uyu ndi dzanja lanu la machitso baba m
Almighty GOD 🙏 please do favour to this lady
Our heavenly father the creator of everything have mercy with her please
Ambuye ndinu mumadziwa kuchilitsa tikupepha kuti muwachilitse mayi anthu
Mulungu wachifundo komaso ochilisa akukhunzeni mzina la yesu
The mother is in pain😢😢
Calling for healing mercies upon her
May her soul rest in peace 😭😭😭💔💔💔💔
Ambuye akhudzen mayiwa
God have mercy
Yehova mulungu wamakamu mpaseni populumikila mwana wanu inu ndi m'busa wathu
Ndimamudziwa ine zimai uyu ankabwera kwanthu ,, ambuye anafika apa😢😢😢😢 mulungu wazifundo chitan monga mwamau anu chonde chonde
Mulungu akhudzeni amayi awaa 😢😢
God HV mercy
Healing mercies upon her..... she is in pain abale😢😢😢😢😢
Next musazaike background song, its disturbing. Get well soon mama, may God's healing hand be upon you.
Avele za iweyo
God touch her with your healing hand
Ambuye perekani machiritso kwa mayi mzathuyu kuti apitilize kusamala banja lake. Chonde chonde
Mulungu awachitire chifundo
Ambuye azikudalisaniso inu a Lodwell anthu ambiri amathandizika kuzera mwainu
Ambuye akukhudzeni Mai wanga ndipo ndukuikizani mmapemphero
Mulungu achitilen chifundo
😭😭😭😭😭😭 nooooooooo
Mulungu a hitless çhifundo
Ambuye mulowelelepo nkhudzeni mwana wanu
Ambuye awachitile chifundo
So sad 😭,
Ambuye ndiwabwino akuona nyengo zanu asisi
May God see this woman through
Mmmmm life
Pepani mai wanga
God heip our sister
Mulungu awankhunze amayiwa,mmh alipa ululu mayiwa
Ndamva chisoni😭😭
😢Mulungu mukhuzen mai uyu
God have mercy on her
Zonvesa chisoni
Ambuye atichitire chifundo Mai wathu akhale bwino
My God mmmmmmm ambuye chonde