CRUISE 5 WITH MAI NAYERE JEKETE - 11 APRIL 2021

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 13 кві 2021
  • Mai Nayere Najere ndi mai otchuka kwambiri chifukwa kupatula kukhala mzamba, ndi katswiri othandiza anthu pamavuto awo okhudzana ndi kugonana komanso kubeleka.
    Mai Nayere adayamba ntchito yauzamba mzaka zamma 1980 kutsatila kumwalira kwa mai wao amene amachitanso ntchito yomweyi. Iwo akuti mai awo atamwalira adawaonekela kumaloto komwe adawaululira mankhwala onse.
    Kuyambila pomwepo adayamba kuthandiza amai ndi abambo amene siatha kubeleka, kuthandiza amai kuchila, kuunika mavuto okhudza kubeleka a amai.
    Mai Nayere amakanitsitsa kuti si sing'anga koma dokotala. Akuti iwo saombeza ndipo sapeleka zizimba.
    Pa zina zodabwitsa zomwe maiwa amachita, amatha kuunika mmimba munthu pogwilitsa ntchito galasi ngati logwilitsa ntchito popesa.
    Mai Nayere amapezake ku Lilongwe mmudzi mwa Chipalamnjira, TA Chadza pafupi ndi Nanjiri.
  • Розваги

КОМЕНТАРІ • 88

  • @user-ux2pj6sd3z
    @user-ux2pj6sd3z 19 днів тому +3

    Joab wakumana nazo koma unabwera kuzagwila ntchito big up

  • @aly-xchagwanumbi5675
    @aly-xchagwanumbi5675 2 роки тому +2

    Chakhaza,you are great investigator umafunsa mafunsa omwe aliyense amakhala nawo ndipo ndilibe nacho chokuthokozera 👍

  • @steveBilly-yo7fr
    @steveBilly-yo7fr 24 дні тому +1

    Mesa ananena kale zopempherazo awa kukonda kubwelezesa muthu mafutso aaaa😊

  • @user-ux2pj6sd3z
    @user-ux2pj6sd3z 19 днів тому +1

    Joab panga zoti ukhale ndi mayi ako

  • @kellylottie7776
    @kellylottie7776 2 роки тому

    So amazing, mulungu achulukitse masiku amoyo wanu mai

  • @mkupabanda-nd2vb
    @mkupabanda-nd2vb 14 днів тому +1

    Ada awa amandiwaza koma😂

  • @upiletambala1991
    @upiletambala1991 2 роки тому

    Ayendatu amayiwa. A Nayere this is great

  • @moseskavalo3304
    @moseskavalo3304 8 місяців тому +4

    We need more people like these traditionalists..long live mayi Nayere

  • @robertkamanga6043
    @robertkamanga6043 16 днів тому

    She's been doing a great job. She's been well supported. She just needs to be integrated with scientific midwifery personel and resources on her facility because her expertise are rare and may deminish soon after her inactivity. She's personally a genius and might not pass some of her skills to the next generations

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 3 роки тому +4

    We need more people like mayi nayele💞💞💞💞💞👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍👍💞👍💖💖💖💖💖💖💖💖💖💖💖💖

  • @rosesimango7107
    @rosesimango7107 3 роки тому +3

    Ntchito yabwino mayi Nayere

  • @rafickanusa3525
    @rafickanusa3525 3 роки тому +3

    Ati ka cup kothimbilira pezan kena komaaaa😂😂😂😂😂😂

  • @edisoniadini4522
    @edisoniadini4522 3 роки тому +1

    Good job mr 🥰

  • @steveBilly-yo7fr
    @steveBilly-yo7fr 24 дні тому

    Ati chiofuofu kma mai nayele❤❤❤❤

  • @Chikomukomu
    @Chikomukomu 3 роки тому +4

    Wow, this is amazing..She is doing a wonderful job

  • @calistoh7083
    @calistoh7083 2 роки тому +4

    Chakhaza ndiwe dolo

  • @geraldkomakomama1016
    @geraldkomakomama1016 3 роки тому +5

    koma chakhaza nchito mukuyigwira zikomo

  • @junaidiwen3422
    @junaidiwen3422 2 роки тому +4

    Koma Joab ndiwe dolo shaaaa .... kkkkkkk

  • @truthtellerlastonk.m.p4985
    @truthtellerlastonk.m.p4985 13 днів тому

    Mayiwa akufunika kuwayendera mwapadela 😂😂😂

  • @tendymakmusic3155
    @tendymakmusic3155 Рік тому

    koma ku Malawku guys...dzikoli likanakhala lolemera heavy..koma kupondelezana..mayiwa amayenera kulemera heavy..

  • @fancylipipa7034
    @fancylipipa7034 Рік тому

    Mai nayere yehova akuze malire amoyo wanu mama

  • @steveBilly-yo7fr
    @steveBilly-yo7fr 24 дні тому

    2000 kwancha ndalama yochepa,, zimayenera atawapasa galimoto yowatandizira

  • @user-hs7yu9pq3y
    @user-hs7yu9pq3y 12 днів тому

    Recieve your flowers Joab

  • @edisoniadini4522
    @edisoniadini4522 3 роки тому +3

    May almighty lord bless you mama 🇲🇼 🙏

  • @frankjuma2359
    @frankjuma2359 11 днів тому

    Chakhaza tipaseni number ya gogo nayele nanjele

  • @giulliannafokoloni
    @giulliannafokoloni 2 роки тому

    she is a blessing mayi Nayere . Very gifted

  • @melodybashiriahmad914
    @melodybashiriahmad914 10 місяців тому

    good work gogo

  • @driver1142
    @driver1142 3 роки тому +2

    🤣🤣 A Chakhaza Anayele akudikira cup kkk

  • @ibrahdickson145
    @ibrahdickson145 2 роки тому

    good work

  • @highcallingglobalministries
    @highcallingglobalministries 12 днів тому

    ndingawapeze bwanji mai amenewa? i need direction or her contact

  • @Calycious_Loves
    @Calycious_Loves 3 роки тому +3

    mayi Najere got jokes... koma Joab your giggles ine kundisekesa

  • @mikewilzmphundi4927
    @mikewilzmphundi4927 2 роки тому

    Wow.

  • @LaurenChisanga-eg5hr
    @LaurenChisanga-eg5hr 18 днів тому

    How can I get in touch with this woman please.
    Watching you from Zambia

  • @JesterMadi-lv9jk
    @JesterMadi-lv9jk 5 місяців тому

    Ndimafuna nambala ya amayiwa

  • @khonjek125
    @khonjek125 2 роки тому

    She needs support

  • @LaurenChisanga-eg5hr
    @LaurenChisanga-eg5hr 18 днів тому

    How can I get in touch with this woman.
    Watching from Zambia

  • @giftmkandawire2783
    @giftmkandawire2783 3 роки тому +4

    Tikufuna nambala ya agogo nakwenda

  • @frankjuma2359
    @frankjuma2359 11 днів тому +1

    Hjy

  • @lemmymmola9228
    @lemmymmola9228 Рік тому

    nice

  • @ussimasi2458
    @ussimasi2458 2 роки тому

    Mai nayele ndiachisangalotu kkkk

  • @dominicdziko9118
    @dominicdziko9118 2 роки тому

    am so proud to see this mayi doing great job ,thanks to be to God 💗💗💗

  • @LaurenChisanga-eg5hr
    @LaurenChisanga-eg5hr 18 днів тому +1

    Joab frank chakazha am kindly asking for her contact information please

  • @saisonmwenda1275
    @saisonmwenda1275 4 місяці тому

    Kodi wakwatira çhakhaza pakana pano ndiwe single

  • @osamabinraden9391
    @osamabinraden9391 3 роки тому +2

    Cruise 5 keep up bro 💞💞💞💪💪💪💪👊💞💞👍👍👍👦

  • @MemoChakwana-oe6ok
    @MemoChakwana-oe6ok Рік тому

    Mayi awa ndiakatundu ndipo ndilinawo umbonid

  • @monteirobechane9511
    @monteirobechane9511 2 роки тому

    Iwe chakhadza bwanji sunawapephe nambala bwanji 🤗🤗 apo wandilakwila kwambiri

  • @steveBilly-yo7fr
    @steveBilly-yo7fr 24 дні тому

    Kmatso awa kufusa kumawamvuta aaa

  • @kondwanitembo4041
    @kondwanitembo4041 3 роки тому +1

    Thanks Ochakhaza

  • @BlessingsNjanji-dj7oq
    @BlessingsNjanji-dj7oq 14 днів тому

    Masiku Tcholofo

  • @issahsabitilawey2091
    @issahsabitilawey2091 3 роки тому +1

    Kkkķkkk Koma apite number mayiwo please jowabu

  • @chrisebanda5917
    @chrisebanda5917 Рік тому

    Is this gogo is still alive ?

  • @user-en8sr2vk7u
    @user-en8sr2vk7u 4 місяці тому

    Ineso ndikuyifuna number

  • @Mary-hx9fc
    @Mary-hx9fc Рік тому

    Kkkk koma nayere

  • @inessmsiyambiri8517
    @inessmsiyambiri8517 8 місяців тому

    Joab chiwofuwofu chanuimitsa mutu kkkkkkkkk

  • @anitakamwendo5349
    @anitakamwendo5349 3 роки тому +4

    Phone number bwanji. And how far from lilongwe Town.

    • @Leratopink12
      @Leratopink12 2 роки тому

      Number munayipeza?

    • @godsgirl480
      @godsgirl480 2 роки тому

      She's from nanjire nathenje she doesn't have a phone number..she's well know just go to nanjire they will direct u from there

    • @thokophiri1093
      @thokophiri1093 2 роки тому

      @@godsgirl480 inenso ndufuna numbe or yamunthu oyandikira

    • @sweetmother1521
      @sweetmother1521 2 роки тому

      Kodi amene anabeleka kare koma ana akura akufuna winanso koma sakubwera amathandiza?

  • @macdonaldmnthambwe2163
    @macdonaldmnthambwe2163 23 дні тому

    Share her contact pliz

  • @mabenastudiochannel2966
    @mabenastudiochannel2966 3 роки тому

    Kunonela kuchoka kuno ku Johannesburg cosmo city mudela la Randburg Koma kumudxi ndimachokera ku ntcheu . A chakhaza tikiyamikileni ntchito mukuigwira ma program anu ndimawatsala ndipo sindifuna kuphunya kuwonela ndikukhulupilila program imeneyi ikhala ndi part 2 coz ikuwoneka kuti yathera panjira. Koma ndikupepha ku part 2 ngati iliko mudzatingaileko phone number ya amai amenewa

  • @frankjuma2359
    @frankjuma2359 11 днів тому

    Tipaseni number ya gogoyo

  • @frankjuma2359
    @frankjuma2359 11 днів тому

    Tipaseni number please

  • @jacksonmtonga7849
    @jacksonmtonga7849 Рік тому +1

    We need her number

  • @frankjuma2359
    @frankjuma2359 11 днів тому

    Kodi number anakukanitsani

  • @LukeBanda-qu9il
    @LukeBanda-qu9il 21 день тому

    Number please

  • @marknthala4990
    @marknthala4990 Рік тому

    Chakhaza phone number pls

  • @getrudechinseu7988
    @getrudechinseu7988 Рік тому

    Phone number bwanji mayi nayere