Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Uyu ndi kamuna
Khodzani Malawi bwelera we don't want anymore and do not let Malawi goes to astray just rescue Malawians from these Assasins
President uyu akanakhala wina akanatha kulamula kuti achoke
Palibe m'malawi emwe sanva chichewa,,,koma Amalawife timafuna kuti Azungu anziva zomwe timakambilana basi or Parliament yathu English yokhayokha basi or imakhala yopindika😂😂😂koma timakakamilabe
Ndife opusa a Malawi timanjenjemera anthu akunja. Sitimazidalira tokha ngati a Malawi. Koma titapeza President odziwa ntchito yake komanso okonda dziko lake. Zonsezi zidzatha ndipo anthu akunjawa atha kudzawathamangitsa.
Ma CHAINA amandibowa...