Kwabasi and ndimadabwa kuti anthu aku Malawi sanadzegukebe mmaso why, bushiri ndi wa satanic ndiopa heavy, Chakwera, Joyce Banda ndi asatana awa, anthu amati Bushiri alindi ndalama koma sungaloze church yoti anamanga ayi
Ana Amma 2000 mumangosatira zili zonse. Makolo ankanena Kuti MCP ndi yoipa munkachita makani. Koma dziwani Kuti makolo athu anazunzidwa ndi chipani chimenechi.
@@EdwardDixies Makolo kumene amanena Kuti ma card anali okakamiza mayi oyembekedzera amatha kuchilira pa njira kukanizidwa kudutsa kamba alibe a ndalama can you emergin ufiti ndeno ndi izi
Ana ama 2000 musamangiwanamizira ,ndi angat anakavotera MCP 2020,, your failure to confront the current problems its not as a result of a certain group that you see so fragile to attack,,kakonzenitu inuyo ama 80s n 90s pomwe analakwisa ama 2000po
Grace Chinga . May your soul continue resting in peace. U said it, but people ignore that, and Joyce Banda and Bushiri indeed are included as you said earlier,,.. Where do Malawi going to,, we need to Pray hard against this satanism political party,,. Kulibe kanthu konse komwe yehova adzabisire Ana ake
Ndipo olo ena akamati bola dzikoli akadalamulira ngt president Bushiri ine ndimangotseka a Malawi kutengeka ndikusamudziwa zintchito zake Pali mau amati: Kusadziwanso ndi kufa komwe. Osadabwa munthu opanda chisoni chifundo eeeeh kungoti zoopsa km
respect the MAN OF GOD bushiri. i know a prophet is not respected by his own city or family but remember he brought millions to Christ and saved thousands of souls. if he is a Satanist then what are you? Satanism is done in secrecy so what were you doing to notice his satanism? on behalf of millions of his followers, we are not moved not even a single inche.
Kulakwa osamusokonezera mbiri mfana Bushiri chitsiru cha munthu ichi its true Anthu sitikufunadi mcp koma osamanamiza Anthu osaona patali Mbuzi ya munthu ikulakhulai
Nkhomdo iyi sitilimbana ndi kuthupi koma ma ulamuliro adziko lino ndi mphamvu za kumidima Kubwela kwa bushiri zinthu zidaipa choncho tiyeni tipemphele molimba
Zaugalu mukapangana kuti mupeleke mangadzi ndiye chifukwa kumalawi kuli mavuto ambili zingodzi tikuziwonazi musokhane nose mupeleke ana anu nosenu mbiri yabushiri mukuyiziwa mukusithanisa ndi magazi anthu moto wamulungu ukufikileni nonsenu nema of jesus fair
Ndipo apa ndipang'ono zikubwera Zina zoposa apa coz kumene aliko ndiye akutenga mphamvu zochuluka Malawi tikapanda kugwada pasi kupephera zolimba titha ndithu komaso chomwe mungaziwe tili mu thawi yakumapeto Yesu akubwera posachedwa
Yah thus true akukatenga mphamvu zina
@@PeterMPWWailes Zoona coz Apapa nde tili pamoto ndipo tilira mpaka Yesuyo afika
Coz step watenga pano kukhala ngat wabalalika Koma chomwe akuchita akuchidziwa
"Malawi tipemphere bas Kwa Mulungu kt chikho ichi chitipitilte"
Amen
Ambuye chikho ichi chitipitilire😢😢😢😢
I don't believe this is true
Continue exposing each other... Malawians we need to stand in prayers against spirit of accident.Holy spirit will take control in Jesus Christ name.
Ameeen mulungu atithangata tonse Malawi, ameeen
Amen
Amen
Mwati amkaka nawonso analipo pa meeting? Ndichifukwa ankati ndale zawo amapanga usiku eti yooooh 😭😭😭 Shalom Malawi shalom
😂😂😂😂
Finally yafika pambalambanda audio
I got it December 2023😅
Groly to almighty God
Heeeeeee mulungu ndiwamphamvu 🙏🙏🙏🙏 tamvako zisinsi yoooooo 🙆🙆🙆🙆🙆
History is the best teacher,kwa amene muri mburi pa tsogolo la dziko ndiomwe mukuwononga dziko. Afiti
Best teacher bwino 😂😂😂😂
Is true bushiri akutha anthu Ku Malawi Kuno ndipo wokonda iyeyu ndi mfitiso
Eti esh
Koma😢
Exactly eshiii 😢😢😢
Kwabasi
Kwabasi and ndimadabwa kuti anthu aku Malawi sanadzegukebe mmaso why, bushiri ndi wa satanic ndiopa heavy, Chakwera, Joyce Banda ndi asatana awa, anthu amati Bushiri alindi ndalama koma sungaloze church yoti anamanga ayi
I remember Grace chinga zimene Anafotkoza asanamwalire
Ana Amma 2000 mumangosatira zili zonse. Makolo ankanena Kuti MCP ndi yoipa munkachita makani. Koma dziwani Kuti makolo athu anazunzidwa ndi chipani chimenechi.
@@EdwardDixies Makolo kumene amanena Kuti ma card anali okakamiza mayi oyembekedzera amatha kuchilira pa njira kukanizidwa kudutsa kamba alibe a ndalama can you emergin ufiti ndeno ndi izi
Ana ama 2000 musamangiwanamizira ,ndi angat anakavotera MCP 2020,, your failure to confront the current problems its not as a result of a certain group that you see so fragile to attack,,kakonzenitu inuyo ama 80s n 90s pomwe analakwisa ama 2000po
Ndpo nkhan imneyi yandikumbusa muthalika akumukana kt bushir azagawe chimanga ndpo boma la dpp linkaziwa kt bushir ndi wa magaz eish 😢😢
Yaap
Eyetu Peter amamudziwa bwino Bushiri koma timkamutukwana lero tazindikika kuti anthu adyelawa amkangowona za mpando wa u president lero ndi izi
Anakanadi
Koma yaa
It's only believers who understand the current situation.The end is near musawasokoneze anthu kaganizidwe ayi
Grace Chinga . May your soul continue resting in peace. U said it, but people ignore that, and Joyce Banda and Bushiri indeed are included as you said earlier,,.. Where do Malawi going to,, we need to Pray hard against this satanism political party,,. Kulibe kanthu konse komwe yehova adzabisire Ana ake
Amalawi ndizimenezotu azabweza magazi
Amalawa vuto boza nde nde timalikhulupila heavy
Man Khan iyi njowona for some reason
Eeeee inu ameneyooo?????
Muzasalatu inu
All
Allah make Easy this difficult things for us we can't do nothing it's only your
Power chosani zoyipa zonse
Koma Mulungu inuyo ndiokongola 🙏🔥
❤❤❤
Kkk ndowokongoladi tugwirizana
Ndipo ndiowaladi MULUNGU
Allah atimenyera khozo kuti zonsezi zithe
Mulungu mulikodi kumwamba izizi zikuonetsa kuti mcp ikuthela pompa, chonde amalawi tisazavoteleso mcp izi simoyo koma malilo okhaokha 😢😢
Mulungu siwamasewera, zakumidima zayamba kuululika, ndalirira Malawi wanga
Big Amen
Koma DPP singawineso zosatheka
No wonder ngoz zkuchtikaz ....God protect us
Hmmmm zoophya kwambiri
Tipephere amalawi timugwetse bushili afe ndithu, Allah tithandinzeni rabi rabi rabi 🤲🤲🤲🤲
Mmmmm musamapemphere chonchi mulungu simunthu
Basi mungotenga magazi a chakwerayooo ,,,kusiyana mkutenga magazi aanthu osalakwa,,
Koma ndiye zoopsya zomwe zikuchitika ku Malawi
Ndipo olo ena akamati bola dzikoli akadalamulira ngt president Bushiri ine ndimangotseka a Malawi kutengeka ndikusamudziwa zintchito zake
Pali mau amati:
Kusadziwanso ndi kufa komwe.
Osadabwa munthu opanda chisoni chifundo eeeeh
kungoti zoopsa km
Zoona
Ndinkhope zingati pacithuzipa zikuonesa kuti ndi nfiti, iam waiting for the list 😮
I remember he said that "I will shed blood "
"Ndikhetsa mwazi"
😭😭
Komabe Mulungu Wathu Ali maso
shalom shalom Malawi ndili ku USA inee 🙌
Kkkkk kumbukirani Grace chinga mai ake
🤞🤞
Tiphedwa bas
INU AMENE MUKUTSUTSA NKHANIYI MITUYANU SIMAGWIRAYI , MUKUONA NGATI UYUYU ANGANGOZUKA NKUMAKAMBA IZIZI? DZIWANI KUTI PALIBE CHOMWE CHINGABISALE PANSI PATHAMBO ILI KUTI SICHIDZAULULIKAYI MULUNGU AMADZERA MWA ANTHU KUTI CHINSINSI
CHIDZIWIKA NKHANIYI NDI YOONA MUKANE MUSAKANE WAYANKHULAZI NDI ZOONA VUTO A MALAWI SIMUCHEDWA KUIWALA KUTI MUKHULUPIRIRE MUKUMBUKIRE ULOSI WA MALEMU GRACE CHINGA MZIMU WAKE UUSE MUMTENDERE , MALAWI ATHA UYU TIKUPEMPHA BUSHIRI KATENGENI CHAKWERA NDI BANJA LAKE KOMANSO ABALE AKE CHIFUKWA KUMENE MUNKAPANGANA A MALAWI AKUFAO KUNALIBE MALAWI NDI OKOMA 😅😅😅😅😅
@@HalisonSolomon Ndipo inu angozifera Malawi
Mulungu awakanthe
Awaaa mesa alinawo kare kod magazi bushiri
God is watching this and he will rescure as from this,lets pray hard a malawi😢😢
Ndipo ngozi zosayamba dairly hmn 🙌
Grace Chinga,ananena kale zadzimenezi ,,,😭😭😭😭😭 GRACE.ANZTIFELA IFE A MALAWI
Shallom malawi shallom
That's why APM amamukana
Mmmmm ndi chifukwa ngozi zikuchitika daily eee ambuye atithandize ndthu'
Aaaa zabodza ixo
Amayoooo!!???
Jesus is the king ✝️🙏🙏🙏
True speach
Shalom malawi shalom 😢😢😢
Magazi mpakana afuna akapange blood juice mwati prophet bushiri osawonongerana mbiritu
Ambuye mulungu bwerani mudzakanthe ana a njaka Abuka nmalawi wiwa iyhoooo malawi wanga
Subuhanallah
respect the MAN OF GOD bushiri. i know a prophet is not respected by his own city or family but remember he brought millions to Christ and saved thousands of souls. if he is a Satanist then what are you? Satanism is done in secrecy so what were you doing to notice his satanism? on behalf of millions of his followers, we are not moved not even a single inche.
Malawi wanga uja ine mayo wamalizika
Peter anatiphera Ana athu ku mzuzu mumaona ngat tkumaywara ife
Amalawi tilindivuto munthu akankhala ndi ndalama mukuti ndi wasataniki koma bushiri akuyesesa kumbali yake
Aaaaa pezani zochita abwana
Ause,mumtendere grace onalosera zaziko lanthu,
Kulakwa osamusokonezera mbiri mfana Bushiri chitsiru cha munthu ichi its true Anthu sitikufunadi mcp koma osamanamiza Anthu osaona patali Mbuzi ya munthu ikulakhulai
Palibe cisisi pansi panthambo, Mulungu sadzasitha adzakhala iyeyo paka kale
Mmmmm uphawitu ukukupangitsani zosezi bushili chikumukhudza ndichiyani pa zandale zanuzi
Nanga bwanji amayakhula Kut Dpp isazabwere bwanji Dpp imadana ndi ufiti
Koma zikufika Malawi gozi ndi deile 😮😮😮
Dzauchisilu mukupha anthu osalakwa 😢😢😢
Grace chinga ananena kuti kuzabwera chipani cha mwazi ndi chimenechi tisadabwe ai
Grace chinga asanamwal8re ananena kuti pakubwera chipani koma chamwazi apa mpamene anthu akungofaku.
Ife tidzavotera mcp ndipo uyu amalankhulayu ndiwabodza komaso siiwe wamcp . Galu wabodza iwe. Or ngati akuwuza kuti uzinama zimenezi kadeti iwe ungodzivuta. Mcp tikuwinaso ngakhale mayi ako akudziwa zimenezi. Akuluakulu koma mcp simukugona nayo tulo eti? Simunati mpaka 2050 wooo
Magaziwo azibweza akutunthu kwawo yemweyo galuyo la 40 lakwana bs eshiii ambuye atopa nawo anthu amenewa mmnn🙆🙆🙆
Always God have macy for us
Chokani inu nditi ndinu, anthu osokoneze mabodza basi
Amumwe chakwelayo,,, coz alindimagazi abwino,
Simmene kuliri 😂😂😂
Malawi the warm heart of Africa ❤
zosayenda
Chipani cha magazi ananenakale grace tchinga
Yes eshii ananenatu mchifukwa chake anamuphaeshiii
Koma a Malawife kusamva😢
MCP inakhalako asanabadwe grace
Ndiwe wopusa kwambiri.Mulungu akukhululukire
Amalawi why kumangomvera zilizonse munthu watumiza pa social media inu ndikumakhulupirira thats why umphawi sanje, kaduka sizidzachoka kumalawi. Anthu inu opeka nkhani mukutiwonongera dziko lathu Ambuye akutengeni mwachangu ndinu anthu osafunikira mdziko muno.
Anthu mkuvutika panopa kumbuyoku kunali ziiii koma ndale eeee kufuna kuwina mpakana kumapangisa anthu ena ngati siabwino and zimenezoso muluza nazo chifukwa mulungu akuwona zose
Open your eyes,pray hard fear God brother
Remember kalata ya grace chinga
Ndipo grace chinga amkanena zoona
Asiyeni amene akukanirawa azavomereza Ali kati mwa poto akupsa, tiyeni tipephere molimba dziko laipa ili
Zikamugwera pabanja lake ndipamene azaziwe kuya kwa chisime
Joyce,bushiri ndi chikangawa tamuoneni chimutu gwape iwe okumwa magazi inu dzisilu inu
Nanga ngozi zochitika mmaiko ena? Ndiyemweyonso bushiri?
Chakwera mutu sukugwira angoyenda ngati zisiru ena ndi awa angodya nsima mma restrant ngati munthu wamba mwazi wa Chilima muyaluka agalu inu
Dramatic vice president 😊
Nkhomdo iyi sitilimbana ndi kuthupi koma ma ulamuliro adziko lino ndi mphamvu za kumidima
Kubwela kwa bushiri zinthu zidaipa choncho tiyeni tipemphele molimba
Vuto la sosho midiya wina amangokhuta mowa wache nkuyamba kuyankhula, kwachuluka masewero kwambiri
Ngati boma likugwilisa ntchito njila zakumidima nanga anthu wamba apanga chani nkhani zolesa asing'anga asamagwila nyanga za anthu pemene ukuziwa kuti ufiti uli ndiwe galu wachabechabe
Rest in peace Grace chinga, ur always in our heart
Komatu mukuchedwa ndikulankhula bola mukasake ndalama mugule chakudya mudyese family yanu
Wakhuta nsima ameneyu
Ndikumbuka yesu anati ndalama iyi ndiyandani yakayesara paseni mwini wake zamumulungu ndiye zanthu amalawi lero kayesara akufuna zake😂😂😂😂
A Malawi Inu simudziwa kuti masiku omaliza kudzakhala zovuta zambiri. ngozi mukunenazo zikuchitika mayiko onse.
Zaugalu mukapangana kuti mupeleke mangadzi ndiye chifukwa kumalawi kuli mavuto ambili zingodzi tikuziwonazi musokhane nose mupeleke ana anu nosenu mbiri yabushiri mukuyiziwa mukusithanisa ndi magazi anthu moto wamulungu ukufikileni nonsenu nema of jesus fair
Nkhani yoopsa iiih koma😢
Guys musamawapepeletse anthu pano pa social media, izi ndzabodza mwangokonza ka Audio
Ndimadabwatu nkhaza chikangawa
Kodi anthu inu mukamanama mumapindula Po chani? Audio ya 2016 iyi
Ichi nchabodza kwabasi, akuti kuyankhula ngati chikunena zowona, ichi mchitsiru kwabasi
Malawi yafika pochitiza manyazi ndipo lero ndikuneneza kuti dziko lamalawi kungowina Mcp zindizabwelera pakana imfa yanga
Ukunamatu kadet bushir ndi mcp zikugwirizana chyani galu iwe mabodza akowo siya
Pangani bwino kampeni inu osanamiza ife ngati ndife ana ai pitani uko ndi maboza anu
Ukunama galu iwe bushiri sizikumukhuza
Aaaaaah mkulu uyu wabodza bwanji?
Tsono ngati nkhani ndi imeneyo magaziwo akuwafuna lero bwanji zausiru basi
Mesa bushiri ndi satanic nde tiziwona tithilabe nsembe ya magazi
😳😳😳.. Mulungu akuyendeleni
Zukunveka mwanthabwala koma izizi munthu sangadzuke nkumayakhura izi....let's wait and see.
Uyuu ndi wa bodza akanagokamba za dale zakezooo osatii aipitse anthu ena fotseki
Mulungu ndi oopsa. Exsodus 14:14( yesaya 54:17) Hebrews 12 :29
A Malawi ambiri mwasowa zochita ndithu. Don't hate Bushiri for nothing. Mutha nonsenu, ife ndiye sitili ku Malawikoku, munya muwona
Kkkkkkkk iwe usandisekese
Malawi sadzathekaso iweyo choyamba inene kaye dzinalako usangoyambila pakati wusayipitse dzina la bushiri ndiwegalu wamunthu
Yehova akumenyaso nkhondo yake
Kodi bushiri osakamupereka ku South frica bwanji chibwerereni bushiri ngozi ndye za ocheza kwambir miyoyo ya anthu ikutha bwanji?