COMRADE NTANYIWA PA LIMPOMPO FM - KALINDO AMAFUNA KUPHEDWA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 101

  • @LeyvanSamuel-pe5tc
    @LeyvanSamuel-pe5tc 2 години тому +12

    Ameneyo ndye ntanyiwa 😅 kuswakuswa bas palibe kunyengerera iweyo unabwera kuzakhala 🙌 God continue keeping you safe in Christ Jesus Name

  • @RitaKainga
    @RitaKainga Годину тому +6

    Akufuna atipusiyse nao commission of enquiry imeneyi,ndpo,more 🔥 🔥 Comrade

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he 7 хвилин тому +1

    We are following
    Koma aaaaa ayi
    Ambuye akuonaa
    Big up achalume

  • @Mavitoabdulla
    @Mavitoabdulla 32 хвилини тому +1

    Matanyiwa God bless you keep it up

  • @ShownMboma
    @ShownMboma 19 хвилин тому +2

    Ambuye azikutetezanibe ❤

  • @DoricaGoweka
    @DoricaGoweka Годину тому +3

    Ulemu wanu Comrade Ntanyiwa. Timadziwa zooonadi kuchokera kwa inu.Inu ndiye maso athu a ife amalawi osaukafe. Ambuye azikutetezani nthawi zonse.Anthu awa omwe asakhidwa kuti achite kafukufuku wandege ife amalawi sitikukhutitsidwa nawo akungofuna kutipusitsa ife amalawi. Antanyiwa chonde ngati muli ndikuthekera kotenga black box yandegeyo teroni ndithu.Kuti akanyimbi amenewa ayaluke

  • @MasterBlack-r2n
    @MasterBlack-r2n Годину тому +4

    mmaso mwanga ndikuona nkhondo Ku Malawi 😭😭😭😭😭
    nkhondoi akubweresa ndi a MCP
    mark my words

  • @BasheerBilalie-q6w
    @BasheerBilalie-q6w 50 хвилин тому +2

    MAY YOU MTANYIWA BE BLESSED AND PROTECTED UNTILL EVER

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 2 години тому +4

    Only radio we trust Limpopo fm

  • @blessingskhonyo
    @blessingskhonyo 22 хвилини тому +1

    Comrade ntanyiwa kuno ku mulanje bale,amfumu achikandwe aonjeza chinyengo.kodi ndizoona subsidy azigawana anthu Zina limozi?

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 5 хвилин тому

    Chilungamo sichipezeka apooo mtanyiwa ❤❤❤❤ mumatiyimilila

  • @KanyozaMatope
    @KanyozaMatope 23 хвилини тому +1

    Uhmmmmuu... Dziko lapansi.. womukhulupilira ndi Mulungu bsi... Even Limpopo akanaisankha.. bali chisintha

  • @AliceMalinki
    @AliceMalinki 8 хвилин тому +1

    Koma ndikurakwa Ife tikulirabe koma sizitheka mulungu alipo kumwamba awulura chisisi😢

  • @ConnexKhomba
    @ConnexKhomba 2 години тому +10

    Ineso namiwa akundikaikisa

  • @DanielGanizani-h8r
    @DanielGanizani-h8r Годину тому +1

    Mulungu akutetezebe bro.Ntanyiwa,koma kungoziwa kokha sikuthandiza kanthu bwanji mupange njila ya action molumikizana ndi ma activities oima pa chilungamo,,mophatikizana ndi zipani zosusa,Namiwa Mulungu akuone

  • @RitaKainga
    @RitaKainga Годину тому +2

    Aikemo Bon kalindo kut tikhulupilire,namiwa wadya Banz

  • @SylosLipenga
    @SylosLipenga 42 хвилини тому +1

    A Thawale omwe ali mu inquiry ndia mudzi umodzi ndi Avelentino Phiri,,, onse ndiakumchinji

  • @EstherTemwa-j1g
    @EstherTemwa-j1g 39 хвилин тому +1

    Thanks comrade ❤❤❤❤❤❤

  • @SamuelAntone-mz6nq
    @SamuelAntone-mz6nq Годину тому +2

    Amuchotse ameneyo akupanga zachibwana tikufuna chilungamo ife osati zoti atinamize ife ai 😮😮😮

  • @dyba-x9w
    @dyba-x9w 2 години тому +4

    is there to cover up criminals, let's hope koma ngati zili choncho tisayembekezere eligible results

  • @JosephIsaac-s1c
    @JosephIsaac-s1c 58 хвилин тому +1

    Thanks Comrade ❤❤❤❤

  • @InnocentHassan-m3r
    @InnocentHassan-m3r Годину тому +1

    We trust comrade m'ntanyiwa

  • @mbaliehaward947
    @mbaliehaward947 2 години тому +3

    Big up mtanyiwa

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he 2 хвилини тому

    Komanso
    In our culture
    We need to
    Consult a kumbumba then awoo pambuyo
    Komanso aku mbumba a
    Vomeleze
    Then we can say we are agreed

  • @Jacksonerutu-c6i
    @Jacksonerutu-c6i 50 хвилин тому +1

    Mmakwana bro

  • @NellieKabvina
    @NellieKabvina 2 години тому +7

    ntanyiwa umakwana more fire

  • @LoyidKarebe
    @LoyidKarebe 57 хвилин тому +1

    Koma Comrade aaaa tiuzenizoona

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 57 хвилин тому +1

    Mbuzi ndi amalawi.....everybody knows which gang killed chilima....
    Commision of enquiry kungowabela amalawi taking chances for ignorant malawians.......
    After election anthu azakhapana yazikwanje live...coz mbavazi sizikulora kutuluka m'boma by fire by force

  • @Zebron-kg2qz
    @Zebron-kg2qz 2 години тому +2

    NGAKHARE MUTAGULA ANTHU WOSEWO DZIWANI KUTI A BANJA LA CHILIMA SAKUSIYANI AYI NDITHU NKHANI IYI SIYIDZATHA

  • @LoyidKarebe
    @LoyidKarebe 56 хвилин тому +1

    Kuphulitsakuphulitsa

  • @EnelesKanyerere
    @EnelesKanyerere 2 години тому +4

    Ine ndine mmodzi mwa amene sindimagwirizana ndi boma ili, koma sindimagwirizana ndizimene Ntanyiwa amakamba, inayo ndi jealous, dolo ndi BM TV

    • @MayimunaZuber
      @MayimunaZuber Годину тому

      Nkhala choncho ife tikumunkhulupilila

    • @MonalisaMongolo
      @MonalisaMongolo 16 хвилин тому

      Ndie bwanji osamangolimbana ndi BM TV yako yomweyo bwanji

  • @WonderfulPrince-b9g
    @WonderfulPrince-b9g 41 хвилина тому

    Kuyesesa bro umayesesa koma anthu ife kusamva

  • @kangungufoundation2020
    @kangungufoundation2020 2 години тому +1

    Amalawi simukudziwa mphamvu ya lilime tachuluka Onena zonyoza and yet tikuti tikufuna ntendere I don't think so tisamale kwambiri ndipo tisamalise kuti tikolore zabwino chifukwa tikuzala zonyasa kunene chilungamo, chakwera ndi woyipa koma ifeyo ma citizen ndife woyipisisa makhalidwe

  • @TressLuka
    @TressLuka 2 години тому +2

    Game on Mtanyiii

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 2 години тому +2

    Namiwa ndanena kale kuti ngati anamiwa akupitira amalawi apite kaye kwa mutumiki wa Mulungu yasini gama akamulumbirise kuti apitira chilungamo ku inquiry apo bii ngati akukana namiwayo nayeso ndi mibulu yebiyeni. Koma namiwa ngati wadya ndalama Mulungu wamoyo akutemberera moyo wako wose uzaziwa kuti kumwamba kuli Mulungu. Chakwera sakuziwa kuti minyama yose ikuchitika ku Malawi ndi mukwiyo wa Mulungu koma sakufuna kulapa

    • @RitaKainga
      @RitaKainga Годину тому +1

      Akudziwa Koma sakufuna kuvomeleza ndkugonja pamaso pa Mulungu

  • @JosephIsaac-s1c
    @JosephIsaac-s1c 50 хвилин тому

    Kupusa kwa ife a Malawi tinapeleka mphanvu zose kwa mtsogoleri ngati Mulungu ndiyetu ndizimenezi akutidoda

  • @MakawaPartrick
    @MakawaPartrick 15 секунд тому

    A Malawi tilimbe mtima mabzi ataika saoleleka palibe chimene angayankhule wapha keliyara kupotsa opalatsa njinga😂😂😂😂

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Годину тому

    Namiwa dzimachende dzako kapusise amako😢😢😢 panya pako

  • @EmmanuelNgambi-y6h
    @EmmanuelNgambi-y6h 22 хвилини тому

    Ndnkaona ngati Namiwa ndi munthu wabwino osadziwa kuti ndi satana weni weni

  • @P.Bilali
    @P.Bilali 2 години тому

    Ndipo press briefing yomwe apanga zana ija kkkkkkk aaah Ali kutali ndi chilungamo

  • @Mathewskabichi
    @Mathewskabichi Годину тому

    komano commission of inquiries amayenela awayimise ntchìto anthu onse omwe akukhuzidwa ku chikena ku police mpaka order above

  • @BeatŕiceMfundenji
    @BeatŕiceMfundenji 6 хвилин тому

    Abusa a Nyirenda zoona ndi inuyodi????

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 Годину тому

    In poli-tricks they say that everyone has a price

  • @MandressMbebe.kundwe
    @MandressMbebe.kundwe Годину тому

    Koma limpopo FM ndiya DPP.TSONO mukwanitsa kodi?

  • @YammsyZebron
    @YammsyZebron Годину тому

    Mtsnyiwa💥

  • @SamuelNandolo-s5w
    @SamuelNandolo-s5w 31 хвилина тому

    Namiwa mmmmmm

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 12 хвилин тому

    Ndizoona palibe chophindula olo chimodzi olo akuti pusisa kwambili

  • @SostenCDzimeza
    @SostenCDzimeza Годину тому

    Auze comrade

  • @BeatŕiceMfundenji
    @BeatŕiceMfundenji 3 хвилини тому

    Abusa a Nyirenda zoona ndi inuyodi??????

  • @Xolani-jd7fo
    @Xolani-jd7fo Годину тому

    Boma Ia mcp ayi zikomo 😢😢😢😢

  • @dankopland-dp3vx
    @dankopland-dp3vx 2 години тому +1

    Tipemphe president WA seventh day Adventist church asalowe NAWO ntchito yobisa mwazi okhetsedwa CHOONDE Yehova akwiya nanu

  • @RuthChaola
    @RuthChaola 3 хвилини тому

    Chimfine chavutanso atanyiwa

  • @lungsTug
    @lungsTug Годину тому

    Ponyani messages koma kutethatu 😂😂😂 zovutatu.....

  • @TakondwaSulani
    @TakondwaSulani 2 години тому +1

    Iyetu kufuna kubisa chilungamo

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza Годину тому

    Asiyeni adzikalumbira Mulungu yekha ndamene akudziwa zonse, pangatalike zidzawululika

  • @StaffordNgalande
    @StaffordNgalande 34 хвилини тому

    Ikwayale imeneyo ilepheleke chifukwa athuo ndi osokoneza okhaokha

  • @DadTshepo
    @DadTshepo Годину тому

    Ntanyiwa ndiiiwe Kape nawe umangozfuna ndalamazo at first ndinkakukhulupilira kma ndiiwe Zoba Shasha ndi Bakili Muluzi TV Inu ndiyopanda kalikonse mapwala anunso

  • @BeatŕiceMfundenji
    @BeatŕiceMfundenji 9 хвилин тому

    Abusa a Nyirenda zoona inuyoo?????

  • @OnexAliMwale
    @OnexAliMwale 32 хвилини тому

    Tsiku lomwe Ntanyiwa azapatsidwe ntchito ndi Boma anthu azanenanso kuti wadya ndalama...analipo achina mavuto Bamusi, Ben longwe pano mukuti namiwa wadya ndalama chifukwa sanakusankheni...Amalawi ndiovetsa chisoni coz amankhulupilira anthu omwe amawapusitsa...

  • @StaffordNgalande
    @StaffordNgalande 27 хвилин тому

    athela kuwili ose samachedwa kufaa

  • @NtchindiChirwa-l8o
    @NtchindiChirwa-l8o Годину тому

    Bola namiwa timamuona ndi maso koma iwe umangokamba koma osaoneka

  • @MandressMbebe.kundwe
    @MandressMbebe.kundwe Годину тому

    Tsono nanga mukufuna chani amalawi.mesa munkati mukufuna achakwera akhazikitse commission of inquiry?tsono chalakwika ndichani kodi anthu inu.mukufuna chani?mukufuna moyo wa Achakwera kapena.

  • @ItaiKafunse
    @ItaiKafunse Годину тому

    Ndipotu izizi ndiye zoona zokhazokha ndi ntanyiwa timupase ulemu

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 2 години тому

    Ndimaona ngati tidikile Kaye ndicholinga choti tizaone zimene angazatulutse after kafuku fuku wa comission of inquiry yasankhidwai ,
    Ndicholinga choti mafunso omwe tilinawo ngati amalawi azayankhidwa mu lipoti lomwe azatulutselo .
    Ngati m'malawi wina aliyense akuzafuna kudziwa yemwe anamuletsa Richard chimwendo banda kuti asakwele ndege ponenakuti inadzadza , pomwe ndegeyo inali yokwela anthu 18 , koma panthawiyo inali itanyamula anthu 9 okha ,
    Komanso tikufuna kudziwa chifukwa chomwe Chakwela analetsela anthu kuti asapitilize kufufuza ndege pachifukwa choti kunada itasowa ??
    Komanso amalawi akufuna kidziwa chifukwa chomwe anampasila Chilima kuti akwele ndege yomwe inali yosakwanila zipangizo ngati black box ??
    Komanso kayalidwe kankhani kakusiyana ponenakuti ndege inafika ku mzuzu ndikubwezedwa , pomwe wina akuti ndegeyo siinafike ku mzuzu , ndiye tikufuna chilungamo chiyende ngati madzi .

  • @Chikwawa
    @Chikwawa 2 години тому

    Zoona. Kuononga ndalama kwa anthu ogulidwa.

  • @RichardZakaliya
    @RichardZakaliya Годину тому

    Popanda Limpopo amaliwife tingakhale ntulo kwambili

  • @McDonardMapala
    @McDonardMapala 29 хвилин тому

    A a a a a chan? Oh😮😮

  • @YusufAjida-t8r
    @YusufAjida-t8r Годину тому

    Sorry abraz ife timamuvera ameneyu

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g Годину тому

    Koma chikangawa ai zicomo

  • @AlicksonMakata
    @AlicksonMakata Годину тому

    Ndiwe wopusa kwambiri chifukwa mumaumiliza kuti ichitike ndiye aipanso.

  • @paulpaseli6310
    @paulpaseli6310 2 години тому

    Anamiwa ndimapasa ulemu koma zoti angafuse zoti achakwela anauza kt ndenge anaibweza kuzuzu ndan

  • @ElizabethMaononga
    @ElizabethMaononga 36 хвилин тому

    Mwayambakotu kkkkk

  • @bridgetmajor3646
    @bridgetmajor3646 Годину тому

    Boma la Mcp ayi Zikomo😢😢😢

  • @SaudhaKatete
    @SaudhaKatete 2 години тому

    Namiwa ndi wa mcp sangatithandize muthu oyipa

  • @samanthamuller7643
    @samanthamuller7643 Годину тому

    Big up

  • @hagayichiluwe
    @hagayichiluwe Годину тому

    Uzinamiza mbuzi zizako garu iwe

  • @WysonAdamu
    @WysonAdamu 2 години тому

    Komaso inu aboma nose odzungulila Mitu inu mayi kaliyati thawi yoseyi ankhala ndimalemu chilima lelo mukwapekela Kuti akufuna kumpha chakwela Kodi inu mwadzungulila Mitu nose mukonena Kuti tikuwamanga chifukwa UTM ija mukuziwa Kuti mayi kungowuna chani palibe chadzelu mwachiona Kuti tiwanamidzile Kuti akufuna kumpha chakwela inu dzimenedzo mukuudza ana Koma samalani thawi ndikachisilu

  • @JOHNSANGWALI-n2f
    @JOHNSANGWALI-n2f Годину тому

    Pena akuluwaa amanamaaa

    • @MonalisaMongolo
      @MonalisaMongolo 15 хвилин тому

      Iwe tanena zako zoonazo chikangawa iwe

  • @TraffleInnocent
    @TraffleInnocent 32 хвилини тому

    Ndiyetitani amalawi nkothekakutiathuwakuwaimisa ndikusakilamo ena

  • @ComfortSabe
    @ComfortSabe Годину тому

    Ife pa mbuyo pa ntanyiwa basi

  • @DanielJuwawo-s5n
    @DanielJuwawo-s5n 2 години тому

    Ndipo ndizoonadi zili choncho kumene ndipo zinadziwika kt zitero

  • @JeremiahKapundu-j1p
    @JeremiahKapundu-j1p Годину тому

    Palibe chimene tingaembekezere

  • @ShashaTown-v9m
    @ShashaTown-v9m Годину тому

    Ntanyiwa ndi moto...

  • @bpssecurity-l3c
    @bpssecurity-l3c Годину тому

    Wabodza uyu musamamvele amachita kutumidwa, naye amapezelapo mchere wake don't trust enewani guys

  • @LucianoKapepuza-sy9wx
    @LucianoKapepuza-sy9wx Годину тому

    Namiwaso ndi kape

  • @stevenmwamadi3035
    @stevenmwamadi3035 2 години тому

    Zomvesa chisoni kwambili

  • @TakondwaSulani
    @TakondwaSulani 2 години тому

    Koma kulimba mtima kumalumbira osaopa Mulungu

    • @youmad9087
      @youmad9087 Годину тому

      Iweyo umaopa mulungu koma chigololo ndi ufiti sumasiya bwanji

  • @ChanceZambika
    @ChanceZambika 2 години тому +1

    Umakwanaa boss ❤❤❤❤

  • @StanleyDama
    @StanleyDama 2 години тому +2

    Chokaaaa iweee mbuli ya munthu

    • @JohnKawondo
      @JohnKawondo 2 години тому +1

      Bmuli ndiyinuyo machende ako

    • @chilembwekanjirawaya4296
      @chilembwekanjirawaya4296 2 години тому

      Kodi ukudwala matenda anji

    • @youmad9087
      @youmad9087 Годину тому

      Sukunama aise ndi mbulidi ya ku Limbuli imeneyi, udzingomva chizungu

  • @ThoccoChimbali-h6g
    @ThoccoChimbali-h6g 7 хвилин тому

    Big up ntanyiwa