Prophet Austin Liabunya: Chimene Chinapha a Chilima Cheni Cheni - Malawi Latest Prophecy (part 1)

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 26 чер 2024
  • Izi ndi zomwe anayankhula #ProphetAustinLiabunya:
    -Chimene Chinapha Dr Chilima
    -Explaining My Journey With Dr Chilima
    -Mulungu Akuti Chani Pa Tsogolo La Malawi
    -Zimene Mulungu Akufuna Dr Laz Achite Kuti Atengenso Boma Mu 2025
    -Umboni Wanga Pa Mphekesera Za Kumangidwa.
    -Ndi Nkhani Zina Zambiri..

КОМЕНТАРІ • 40

  • @MaryMlongoti
    @MaryMlongoti 4 дні тому +1

    Chilima sanaphedwe thaw unamukwanila

  • @BenNkhoma
    @BenNkhoma 9 днів тому +2

    PALI NGOZI YAIKULU, KUSIYA ZA YESU KUYAMBA KUTUMIKILA ZA NDALE,

  • @RUSTOYOTA-k3d
    @RUSTOYOTA-k3d 8 днів тому +1

    Only God knows,may the souls of our beloved ones rest in peace

  • @GiftShugah
    @GiftShugah 7 днів тому +2

    Mulungu akukhululukireni Man

  • @user-rk3jx3kg8i
    @user-rk3jx3kg8i 6 днів тому +1

    Mbuzi ya munthu, mulungu wasala pangono kt akutopele,

  • @Sheillamponda
    @Sheillamponda 25 днів тому

    Ok prophert of God

  • @user-eu5wo5kt9u
    @user-eu5wo5kt9u 7 днів тому +1

    Mulungu adzachilangaichi

  • @LonjezoAkacharlie-r2q
    @LonjezoAkacharlie-r2q 4 дні тому

    Tayankhula zomveka iwe ukuti chani kwenikweni

  • @Jeremiahchalombanthu
    @Jeremiahchalombanthu 7 днів тому +1

    Kod mulungu wake ndi wa major 1 kod panopa mulungu amangonena zandale

  • @BrunoChakukuma
    @BrunoChakukuma 4 дні тому

    Koma zoti chilima wachita kuphedwa ndi chakwera simukunena bwanji

  • @lulukunkeyanih8271
    @lulukunkeyanih8271 2 дні тому

    Komatu iwe

  • @michealmzumara8471
    @michealmzumara8471 6 днів тому

    Ndiopenga akufunika mankwala

  • @PeopleOfYah
    @PeopleOfYah 3 дні тому

    Milungu ndi yambiri. Ina imamuwuzadi munthu zimene akunenazi. Pajatu satana ndi mulungunso wa dziko lino.
    Mulungu wathu satenga mbali mu ufumu uwu wa kumapazi kapene kuti ufumu wa chilombo chopanda dzina

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 16 днів тому +1

    Koma ngati ndizedidi zimene mukuka.bazo kt mudapanga prophesy kt atuluke Avice president mu tose alliance ndiye kt mudolosera chifukwatu adadfa imfa yowawako.aso yosaiwalika

  • @EmmanuelGasiten-fo5dr
    @EmmanuelGasiten-fo5dr 6 днів тому

    Tizikasaka ma Post amiyezi imeneyo, koma tigwira ntchito?

  • @EliasApofu
    @EliasApofu 5 днів тому

    😮

  • @ABMWALEBorder
    @ABMWALEBorder 29 днів тому

    Komano ineyo zomwe mukufuna kunena, sindikuvetsa kuti mufuna kunena kuti chani.

  • @innocentmanyamba5042
    @innocentmanyamba5042 7 днів тому

    Kape uyu osauka akuona ngati atola chikwama oputsa uyu

  • @GiftChitsulo
    @GiftChitsulo 8 днів тому

    Iwe ASE usamasewele ndimulungu mulungu si abambo ako chonde chonde usamana ize anthu kuzela kwamulungu musiyeni mulungu akhale mulungu ,,,,tchito zaboma zimafanana ndindale ngati wasata zaziko wasephana ndimulungu man musatichimwise,,Kodi mulungu akuuze iwe ndindani iwe baibulo lake liti

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 9 днів тому

    Chilima penapake anali wamwano born kalindo wakhala akunena

  • @CharlesKalua
    @CharlesKalua 6 днів тому

    I saw your prophecy they is no that condition pliz and you say it with confidence that chilima Will be a president,,chonde venselani kwa mulungu osalankhala za mumaganizo anu

  • @PaulNtonya
    @PaulNtonya 8 днів тому

    Ndikufuseni mukutumikila utitiuti Mulungu wake 🤔

  • @peterkampira7613
    @peterkampira7613 4 дні тому

    Your are operating under the power of money

  • @user-ye7fv4yo9f
    @user-ye7fv4yo9f 5 днів тому

    Aaaaaa

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 9 днів тому

    🙄

  • @masautoMalunga
    @masautoMalunga 9 днів тому

    Is good to look something to do not to lies to the people that your poster Kodi ubusa wanji ongokamba zandale

  • @ClifordBwwanali
    @ClifordBwwanali 12 днів тому +1

    Now you stop preaching jesus .everyday stories we arw tired

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q 4 дні тому

    Achibale a munthu uyu chonde mutengereni ku mental hospital.
    Am crc.

  • @johnmsona8845
    @johnmsona8845 5 днів тому

    Kodi satana uyu. Ndindani siyeni chilima mzimu wake uuse muntendele

  • @GabNice-rp8mt
    @GabNice-rp8mt 8 днів тому

    Vomelezani kuti mwaphonya prophecy,false prophet exposed in false prophecy.

  • @rabisonpias5131
    @rabisonpias5131 6 днів тому

    It seems like this MAN don’t know what he is saying. “Everything is I think “

    • @philemontitusnkhoma7740
      @philemontitusnkhoma7740 6 днів тому

      Yea, I also noted that. U know the reason? Here, the repeated use of 'I think' is due to his reluctance in mid speach to divulge what he realy knows. So he is trying to remain calm, careful, and at the same time, inoffensive.

  • @user-nl5nk2wx1q
    @user-nl5nk2wx1q 4 дні тому +1

    YOU DON'T KNOW WHAT YOU PREACHING.
    DZIKOMO MULUNGU MWANDIONESA ANENELI ONYENGA.

  • @user-jm8kw9gw2d
    @user-jm8kw9gw2d 11 днів тому

    Sir you don't know how to communicate or deliver, God is not using you because we can't get you at any point

  • @masautoMalunga
    @masautoMalunga 9 днів тому

    Most of poster they busy to lies

  • @scoltenroma6240
    @scoltenroma6240 5 днів тому

    False Prophet in the last days,repent & turn to God.Kufuna kutchuka eti,tisiyeni tikulira maliro ife.SKC RIP😭

  • @GreyKwenje-td2uy
    @GreyKwenje-td2uy 9 днів тому

    He is not a man of God manof chakwera

  • @madalitsokalima8533
    @madalitsokalima8533 19 днів тому

    Musakambe ngati Mulungu ndi brother wanu, that accident was very painful to everyone get something to get famous with, what you are saying is just nonsense remember this CHILIKWANZAKO CHIGWIRE NYANGA you will remember this proverb , Mark my words. Musagwiritse ntchito dzina la Mulungu pachabe.

    • @jamesjanuary5423
      @jamesjanuary5423 10 днів тому

      Aaaa kaya mwina enanu mukumva ine ndepalibe nditolaine