Munthu ngati Lucius is not a good person to a Government spokesperson,,, udindo umene uja umafunika anthu abodza ngati Gospel Kazako...Lucius is too straight, and honest
Koma munthu amene anganyonze Lucius Banda ndi munthu otembeleredwa. Lucius ndi Paul ndi anthu ofunika kwambiri mu mbiri ya dziko la Malawi kumbali ya music yomwe ndi gawo la chikhalidwe chathu. Adayamba kutukula nyimbo ku Malawi ndi baba amenewa. Munyengo imeneyi tikuyenera kuwapemphelera kwambiri kuwaonetsera chikondi.
I pity the situation Lucius and his family are going through, but by saying the current government is better placed to helping Malawians is a fallacy. Things have worsened when we were promised Canaan. Start fighting for the poor as you used to and if being part of the government is making you fail to do so, then quit so that you maintain your legacy. Otherwise, wishing you full recovery .
Mau anzeru Lucius: As citizens, we need to reflect on ourselves to deal with our individual weaknesses rather than always pointing fingers at political leaders. My addition to his point is this: If you don't do something to improve your own living standard, no one else will.
Pankhani yabwatoyi pamenepo Brian Banda wasimikiza kuti ochimwenewa he is very clever like ok onsewa ndi adabanda amaziwana wonse ndi amodzi apapa Brian anakumaniza ndithu 😂😂😂.RIP solder L.Banda great wise from you
Lucius is talking from experience he knows what he's talking about exposing people whose stilling doesn't mean you helping people of malawi anthu sakufuna kumva zakumangidwa kwa anthu pomwe anthu akulephela kugula feteleza komanso chakudya DPP imaba UDF imaba koma sizinali chonchi ndipo anthu anali busy kulongosola zawo osati zamboma koma panopa anthu daily kumangkamba zokazokazo chakwela ndamene ali pasogolo pa anthu akuba Lucius akudya ndi chakwera sangakambe zachabe za chakera mr Lucius thank you for failing malawians keep eating the money and enjoy with your family but one day you will need them thank you
Lucius Banda ndizowonadi anthu ena anali m'boma angasangalala ndiye yeyo pano ali m'boma ayenela asangalale koma sangapange nawo katangale kulankhula kwabwino kwambiri
This was nice interview. I grow up listening to Lucius Banda's music & I like almost them all.
Am Zambian, but I have fallen in love with your program.❤❤❤❤
Umuthu wachibadwidwe umakhala opindulila aliyese ngakhale mulungu amakondwela nazo well done Mr banda God bless you
I think Lucius is better posotioned to be government spokes person than ajawo ndithu.
Munthu ngati Lucius is not a good person to a Government spokesperson,,, udindo umene uja umafunika anthu abodza ngati Gospel Kazako...Lucius is too straight, and honest
Koma munthu amene anganyonze Lucius Banda ndi munthu otembeleredwa. Lucius ndi Paul ndi anthu ofunika kwambiri mu mbiri ya dziko la Malawi kumbali ya music yomwe ndi gawo la chikhalidwe chathu. Adayamba kutukula nyimbo ku Malawi ndi baba amenewa. Munyengo imeneyi tikuyenera kuwapemphelera kwambiri kuwaonetsera chikondi.
The Legend, well spoken sir. May God give you more grace and Good health
Pp
Mr Lucius Ur so intelligent keep the 🔥 burning.
Brian Banda ndi lucius Banda Agogo awo ndiamozi😂😂😂😂😂
Legends met and well composed questions were been answered constructively.
I like this guy Banda from Times tv for asking good questions
Interview koma imeneyi akanakhala ena mukanamva akuyankha za a president..... Under the dynamic leadership of fwe fwe fwe.... Lost the big brain
Lucious Banda....Get healed in Jesus name.personally I love you sir
Lucius has convinced me
Apatu Soldier unagonjetsa Brian kkk pankhan yabwatoyii
I like the way he was answering the questions,he is very brilliant
Koma Brian!!!!!! Iwe ndiwe munthu ofunika kwambiri
Ndithu
Nice guys God bless you lucia's
I pity the situation Lucius and his family are going through, but by saying the current government is better placed to helping Malawians is a fallacy. Things have worsened when we were promised Canaan. Start fighting for the poor as you used to and if being part of the government is making you fail to do so, then quit so that you maintain your legacy. Otherwise, wishing you full recovery .
Mau anzeru Lucius: As citizens, we need to reflect on ourselves to deal with our individual weaknesses rather than always pointing fingers at political leaders. My addition to his point is this: If you don't do something to improve your own living standard, no one else will.
Pankhani yabwatoyi pamenepo Brian Banda wasimikiza kuti ochimwenewa he is very clever like ok onsewa ndi adabanda amaziwana wonse ndi amodzi apapa Brian anakumaniza ndithu 😂😂😂.RIP solder L.Banda great wise from you
I don’t like the Interviewer
Ku balakako kuli anthu odziwa kulankhula osati mabwatabwata uh
Mmmmmmmm
lucious was a wise..rip😢
Wishing the legend well
Get well soon and u are really a fighter
Powerful points by Lucius and massive questions from Brian Banda, God bless you all.
Thanks broh for your congrats
Brian went off
😢😢😢😢😢 rip
Nice interview. Yobebatu
👍👍💥
God bless you soldier your the icon
Anali ndi masomphenya😢😢
Koma brain Banda ndimakuyamika ulibe ubale
Lucius banda he talk reality 😢
Lucius is talking from experience he knows what he's talking about exposing people whose stilling doesn't mean you helping people of malawi anthu sakufuna kumva zakumangidwa kwa anthu pomwe anthu akulephela kugula feteleza komanso chakudya DPP imaba UDF imaba koma sizinali chonchi ndipo anthu anali busy kulongosola zawo osati zamboma koma panopa anthu daily kumangkamba zokazokazo chakwela ndamene ali pasogolo pa anthu akuba Lucius akudya ndi chakwera sangakambe zachabe za chakera mr Lucius thank you for failing malawians keep eating the money and enjoy with your family but one day you will need them thank you
The greatest musician who ever lived
Loved this conversation
I have enjoyed this
God bless our Legends Lucius
Honestly speaking Brian Banda ali bwino kwambili ndipo ntchito amayidziwa. 👍
Well spoken Mr Lucious Banda....
Kkkkkkk zinazo a Brian mumatisangalasa ambuye akudaliseni mafuno abwino kwa mr Lucius Banda
So genuine! Humble personality, kind heart. You are loved Angoni!!
Lucius Banda ndizowonadi anthu ena anali m'boma angasangalala ndiye yeyo pano ali m'boma ayenela asangalale koma sangapange nawo katangale kulankhula kwabwino kwambiri
Wishing the legend well.
A NEW VERSION WILL GOVERN OUR LAND SO HELP ME GOD
Kuyankhula kwanzeru lucius.
Legend
Mr lucius very good 🔥🔥🔥❤❤❤🙏
Lucius Banda umatha kuganiza, maliro akwanu musandikakamize kulira 😂😂😂😂
Mulungu azikudalitsan Mr chicco Banda
Brian you are genuine.
Mulungu ayendere family ya Banda pa zomwe akudutsamo i like the close relationship between Lucius and Paul long live our legends
♥
Chonena ndilibe soldier 😭😭 only God knows why may your soul rest in peace 😢
So there is no one to give this guy a kidney, shame on us, he deserves love, a kidney donation !!!
He has said that when they're stable will undergo surgery in India
You can be the first one
You can also donate to him
Can't you give him yours
Shame on you
Ok
Brian Banda weyo nd Dolo kwambili keep it up ❤
😂😅😂😂 Koma Brian
Onelove to the highest degree
Ambuye akanamapeleka mwai wachiwiri padziko pano mmm,mhsrp Lucius...
someone who knows how to talk in public, You impress me Angozo
Amalawi timakhulupilira kulima ndiye ngati boma likukweza zipangizo zaulimi dziko likwera bwanji?
Good point , we are to look ourselves as amalawi and solve our concerns (issues)
Kunena zoona kumapeto Kwa mawu afusa fuso labwino koma Iwo ndimunthu mozi analiwosayamika Bingu anali sogoleri wabwino kumalawi koma sanamike analowesa ndala Lucie's
May Allah Bless U Sir Soldier
Rest well soldier 💔
Kkkkk pano ndi soja wamabwana atsatinamidze Lucius Ali mugulu lakubanawo ndipo palibe chadzeru chimodzi chomwe wakamba
Thanks forr bringing Mr Lucius Banda , we had missed him. Very intelligent man, am impressed.
a Lucius akunamatu apa, yankhani bwinobwino funso loyamba ndi ili likuba ndi liti?
kd mukamat boma la New 1 mukutathauza chan ? boma lot latha 3 yrs likhala bwanj ! la New 1 ?
Our own musical legend Lucius Banda, answering questions convincingly
Yes
Makwana Banda mupangeso interview ndi nomani chisale
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk koma adha Brian ase akut Lucius akuyakhula ndie uti
Where can I get a CD in Mzuzu
Kuyankha mafuso mwazeru ndithu, zinthu zabwino zedi.
Munthu mulala kkkkk' maliro akwanu musandikakamize ine kulira
Maliro a kwanu musakakamize ena kulira... although we are moving from bad to worse
Thank you Brian and Lucius Banda. Powerful discussion
Lucius Banda is so wise
Very intelligent
The way i I love this man im crying 😪😪
NKHANI YOVEKA BWINORUSIYA BANDA TANKHUDZIDWA TOSE
Following
He is intelligent and wise
Lucius umakhwana
Brian u know how to ask .kkkkkkk
Koma Brian banda mmmmm amakakamilatu
I love cos
Legend ❤
Brain aaaaa ndiwachipongwe koma anafunsa mafunso omveka kwabasi
Rip soja
P
You ate MLAKA MALIRO's money
Mr soldier wa amphawi mumatiimila humble number.
Nice
Kulankhula moona mtima ndithu ulemu wanu big
Lucius atha kuwina ngati wayimila udf anakawina
Masaka kids
Apa timat Njobvu Zakumana
Obrigado
Brian ndiye umaseka eeee
Tililadi mosiya bwana takuvani ok