Nooo nooo nooo even you Brian you know what exactly is on the report and what Mr chikangawa said to Malawian on his first bliefing is exactly parallel to this carrent report and the second thing is Mr chikangawa azaziwikabe
Amene adalakwitsa ndi amene adamulola(adamuwuza)munthu kuti akwere ndege yosakwanira zipangizo ameneyo ndi amene adalakwitsa.Anthu amene damwalira pamalopa ndi anthu amene amathandiza pachitukuko cha dziko lino.
@@ShemieMavuto If you are Malawian make sure and don't miss to 👂👂🦻🦻 Limpopo FM, Bakili Muluzi tv and The DC Bon Kalindo.Anthu andale kodi simumakhala ndi chifundo pa anthu anu aumphawi,osowa,ovutika ndi amasiye?
This accident will be talked from one generation to the other till the end of the universe.... whether chikangawa is out of leadership or not... people will never stop talking about it
Even the president himself knows that Malawi has many parties and their signs ,so why moving out frags of the other parties to me this must stop just let the president to address the people at any time he wish even at aplace where flags of other parties hungedup
The camera 📸 man has to do better next time please. & Also when watching from this channel most of the time the videos jam, 😊 you need to improve on that.
no one has the right to stop people from crying. let the mourners cry unt they finish. And these leaders must know that they lead different people of different like/choices. In order to be good leader u must reespect different choices
Koma pa zonse mukumbukile kuti a President ananena kuti ndege anayibweza ku Mzuzu (Pamenepo) Funso: 1-Kodi ku Mzuzu anayibweza ndindani?. 2- Anamuwuza President ndindani?. 3-Why they decide to lie to Malawian?. Ndege kusowa 10am akufufuza kuyamba usiku 5pm?. Still mare question coming.
Wondar Mskiska please if you don't want to talk about the pain death of Chilima which was caused by jealousy people, do not bother yourself in defence of these killers
Za ndege kungoyiwalako,,,akapanda kalindo kupachika moyo wake kuti achititse mademo..mkuyembekezera chani 😢😢😢ndiye akuti final report 10-12months 😢😢😢 obvious azatulusa after ma voti 😅😅😅😅
Brain, Brain your question about why the president, chimwendo and Nancy spoke is very unfortunate.. You know very well a bout the serious allegations, So my question is" do you want or expect MCP just to remain silent on these serious allegations ??????
Unbelievable politicians they have no shame no integrity no conscious they don't think of others apart from their own. Imagine after all sorts of insults Jefu Wa Jefu said to Chakwera and mcp today she can stand and say kwacha kwacha!!!! For real??? U think u can fool us??? Fine and good chiona ndi chipande poomola
A Brian mukuchita kuwonekelatu kuti muli ndi khwinthi pa a mcp. Anthu akhala akunena misonkhano you have never gone against them. Muzikhalako ndi manyazi komaso umunthu. Shame on you. You are trying to bend the story but your friends they're trying to point you the right direction but still opposing them.
Ndale za ku Malawi nzautsilu or ikanakhala mcp bwenzi pano akuchita zomwezo. Kodi a Chakwera sankaonetsa kuti iwo sadzaba pano akutani??? Ankati katangale atha pano bwanji??? Kudzakhala ma mega farms ali kuti??? Pano anthu a kudya chitedze why a Malawi simumatha kulankhula chilungamo. We are tired of the leadership of Malawi. 😭😭😭😭😭😭😭 Amayoooo God where are You??? A blood shade country. No love in our nation. Sagrigation, cruel leaders. We need God's intervention
It’s all political, ena azibale awo amwalira last week yomweyi apanga move on koma akuti akulira chilima, ndani apa asakugona kukhalira kulira kuti chilima anamwalira. Andale onse akugwiritsa ntchito chisoni cha anthu kuti apite patali kugwiritsa ntchito imfa ya chilima. It’s all politics, vama candle ivi, how many people lost a close family member after chilima that are lighting candles for their loved ones. Even his own family has accepted and we are not letting them move on. The way MCP was ready to betray chilima while he was alive we can say they killed him twice, but politicians should not fool us that chilima was their hero because he’s dead.
Discussing Nsete zokha zokha yet you know ma statement opusa adayankhula chakwela n Valentino Phiri which illustrated lies n contradictions Kaya mwapasidwa chani Kaya kuti mudzipanga zansete zanu mukupangazi
Bereavement takes time for other it takes one year and others two years even threes to give years depending upon the therapeutic sessions, but with other people's reactions they may be taken to a mental level acute for clinical depression because they have not received closure inparticular cases where the families which have lost their beloved ones via first degree murder or homicide during court proceedings where they take about years for the judge to deliver a verdict. Looking at the case of jinkid and Mellys the rapper in usa or shanquila Robinson. People have the right to mourning their beloved ones who have passed away.
Imfa ya chilima anthuwa salinayo ndi chisoni ayi,koma they are happy cz the political parties are looking to benefit out of his death .trust me anthuwa sichisoni ayi nooo!
Pali kusiyana kwa makambidwe pakati pa chikangawa kunkuyu wankulu wa nkhondo ndi kulephela kwa achitetezo were confused guys it can not be end this until when we know exactly what was happening in chikangawa to those 9 malawi who killed including our let vp
Chakwera ndi president wa dziko, ndalama zomwe amayendera ndi za a Malawi azipani zosiyanasiyana, asamapite ku malo nkumakatumbwa za chipani chake, azitha kusiyanitsa chipani ndi boma
It really pains where it hurts, we will never have another Chilima💔
Nooo nooo nooo even you Brian you know what exactly is on the report and what Mr chikangawa said to Malawian on his first bliefing is exactly parallel to this carrent report and the second thing is Mr chikangawa azaziwikabe
We are not stopping about chilima tikufuna chilungamo
We never stopped talking about Chilima and 8others Deaths
😢😢😢😢😢😢
As Malawians Dzimatiwawa
Imfa ya chilima inapweka Malawi ndipo tidakalirabe
The best program with the best journalists
Amene adalakwitsa ndi amene adamulola(adamuwuza)munthu kuti akwere ndege yosakwanira zipangizo ameneyo ndi amene adalakwitsa.Anthu amene damwalira pamalopa ndi anthu amene amathandiza pachitukuko cha dziko lino.
❤❤❤ mbambande Brian banda ndi team yonse
Mr B.Banda Ndikufuna ndifunse kuti Pali radio 📻 Ina Koma siyakumalwi ayi,ikumafotokoza list yawathu amene anakhudzidwa pa imfa ya Chilima.Kodi inuyo simunaimvere nanga iwowo akudzitenga Kuti, ngati ndizoona inuyo simukufuna kuliwuza Zoona Dziko lino.
Radio yakuti imeneyo boss??
@@ShemieMavuto If you are Malawian make sure and don't miss to 👂👂🦻🦻 Limpopo FM, Bakili Muluzi tv and The DC Bon Kalindo.Anthu andale kodi simumakhala ndi chifundo pa anthu anu aumphawi,osowa,ovutika ndi amasiye?
Inuyo ndye mumawudziradi mayeso more 🔥🔥🔥🔥 guys following from Germiston
This accident will be talked from one generation to the other till the end of the universe.... whether chikangawa is out of leadership or not... people will never stop talking about it
Nyamata inu atatu futso ndiili
1- kodi chimene chinawaziwitsa kuti Ndege yasowela ku chikangawa ndichani ngati zipangizo inalibe?
2- Nonse apo ndinu antola nkhani, mnapitako Kuja kugwela Ndege kodi ndizoona kuti kunalidi kutali ndi Mizi kuti anthu angamve kuti uku kwagwa chinthu chinachake ?
3-Kodi bwanji ngoziiyi zinakhuza atsilikali akutali than kuudza amoyale barracks kuti afunefune Ndege, pakuti iwo anali kufupi ndi komwe kunapangika ngozi?
4- kodi ndizoona kuti ndege akuyenda kopanda kena kalikose Ka emergency? eg Palachuti, black box and etc?
Ine anthu awa ayamba kundidabwisa adya masikono agalu awa
Yes best program ever ❤❤❤❤
Ngati simaiwalika kukamba zachina Gadama what more the fresh one singasiyidwe kukambidwa guys chalowa mumtima nchovuta kiwala nawonso amve kuwawa ngati momwe tumvera kuwawa osiyidwa💔💔💔💔
One of the best programs in Malawi
Watching from Limpopo
Point wonder anuthuwa akupepuza IFA ya malemu chilima
Even the president himself knows that Malawi has many parties and their signs ,so why moving out frags of the other parties to me this must stop just let the president to address the people at any time he wish even at aplace where flags of other parties hungedup
Umudi mmatenthadi ndipo mmasukuluzadi atsogoleri keep it up gyz
It's really painful to us but one thing pipo are asking for credible commission of enquiry but government is so silent to this n why?
😭😭SKC was a real soldier like Ibrahim T from Bkukina faso
Itangochitika ngozi adanena kuti chifunga koma lipotili sidakambepo akuti mudalibe zipangizo zili za bodza anapha basi azivomereza
Sanamulakwire kumugenda Chakwera inenso nkadakhalako nkadagenda nawo
Imfa iyi imatiwawa heavy....ndipo sitizayiwa Anthu munawatani even ma phoni awo osapezeka inali ngozi kapena kumphedwa.....💔😭😭😭😭Anthuwa eeeeish munatilakwila
The camera 📸 man has to do better next time please. & Also when watching from this channel most of the time the videos jam, 😊 you need to improve on that.
Mr Ndevu zamwayi anthu akumakamba za group ya Gadama ndi Matenje mene anafera kalekale nanga inuyo mukufuna anthu aleke kulakhula fresh news.Mukunama Chilungamo tikuchiva inu khalani chocho,Koma Dziwani maso tilinawo Bmtv Komaso Limpopo FM samatibisira dzithu.
Gentlemen That's a Straight Forward Matter,Live All In God's Hands Eagles Eye
Wonder ndi wa nzeru
Sitingasiye kulira Chilima Chilima ndi anthu ena 9 aja anafa imfa yowawa ma photo kuchita kukha pidwa chonchija ngati akupha chinyama tidziganiza kuti zomwe zinachitikazi atakhala mbale wawo angambve bwanji?
Non politicians and politicians are the ones to cry more than you want the cry to be OKEY!
Proud of you guys ❤❤❤
no one has the right to stop people from crying. let the mourners cry unt they finish. And these leaders must know that they lead different people of different like/choices. In order to be good leader u must reespect different choices
Imfa iyi ndimalephela kumvetsa ine😭😭😭😭😭
One day is one day chikangawa party muzayaluka
Chikangawa the place to remember
Koma pa zonse mukumbukile kuti a President ananena kuti ndege anayibweza ku Mzuzu (Pamenepo) Funso: 1-Kodi ku Mzuzu anayibweza ndindani?. 2- Anamuwuza President ndindani?. 3-Why they decide to lie to Malawian?. Ndege kusowa 10am akufufuza kuyamba usiku 5pm?. Still mare question coming.
APM was the best and we have a hope in APM 2025
Lilian Patel is a very good example, chiyambireni cha UDF sanachokepo mu Chipani,anthu atengerepo phunziro
Ayaluka a mcp chilima tikumulilabe❤❤
Yes ndigwilizane ndi Mr msisya cz uyu wa MCP ndyemwe anazusa mkwiyo mmitima yanthu ena pokazula mbendela zazipani zina sikhalidwe labwino
More fire guys chilungamo❤❤❤
Wondar Mskiska please if you don't want to talk about the pain death of Chilima which was caused by jealousy people, do not bother yourself in defence of these killers
We never get true atill we change government only
Makosana you have to improve guys nthawi inailiyonse ukamaonera koma kujama nde sinkhani pena munthu umaboweka ukamaonera this channel
Za ndege kungoyiwalako,,,akapanda kalindo kupachika moyo wake kuti achititse mademo..mkuyembekezera chani 😢😢😢ndiye akuti final report 10-12months 😢😢😢 obvious azatulusa after ma voti 😅😅😅😅
Koma ma guys awa anabwera,alibe mbali
Malawi toooonse Tili ndi vuto ,ma demo wochotsa Chakwera amafunika ,sure sure
Koma akulu akulu mumadziwa kuphika nkhani, ulemu wanu ndithu.
Brian alindi mbali
Brain, Brain your question about why the president, chimwendo and Nancy spoke is very unfortunate..
You know very well a bout the serious allegations, So my question is" do you want or expect MCP just to remain silent on these serious allegations ??????
Ineyo anthu awawa nde akundidabwitsadi kuonjezeraso apo pa mbc akut pali pg inayake mkumat utm bola ibwerele ku mcp zaziii
Chakwera anapha chilima and others machende Ake 😢😢😢😢
Ndiye kuchosa mbendera ndikugenda anthu kuti apangengozi anthu amwalire kupanda nzeru koseko bwanjiniwowo osakabweza kuzura mbendera ya mcp than kufuna kupha anthu zonsezo ndizaboza chilungamo ndichakuti anatumidwa ndi dpp basi
What is wrong is wrong Chilima adachita kuphedwa
Olira samutseka pakamwa komanso chakwera adati ndege adaibweza pa mzuzu airport pamene report lidati ndege siidafike kumzuzu zoona ndiziti chakwera akudziwapo kanthu adawapha ine nda gamula mulandu basi
Unbelievable politicians they have no shame no integrity no conscious they don't think of others apart from their own. Imagine after all sorts of insults Jefu Wa Jefu said to Chakwera and mcp today she can stand and say kwacha kwacha!!!! For real??? U think u can fool us??? Fine and good chiona ndi chipande poomola
Iwetu ngati wadya ndalama za mcp uyaluka ngati akukamba nkhani ya amatenje agadama anthu woti anafa kale.ndiye iweyo devu za mwayi wauze amalawi asamakambe za anthu amenewa iwe wopenga wadya ndalama
Ineyo nditsimikizeso,,,anatchayadi dzuro
Nkhaniyi ya Anthu 9 imatembenuza matumbo.
Koma chi program ichichi ndi kawAwa
Mmmmm chilima ukaganiza misozi imangotuluka hhhhmmm mulungu yenkha akudziwa zonse
Ndipo inu mmmmm
Boma lankhulani chilungamo,miyeZi itatu tsopano .boma likuchita ngati ana pa ntchenga😢😢
What if sanaphedwe. Wonder ndiwanzeru
We have unstable Politians in malawi because they don't have good visions for this country instead they are just after fast money
Ntaba chigawenga wakhala akupha ma alubino
Brian mpaka nyazi limozi kkkkk athuwa umuthu aribe komaso sakudziwa chomwe akuchita
Brian nanu mwaonjeza i think nkwiyo wanu wawukulu
Azibambo awilio anadya banzi ,mfundo zao zikuonesa mbali
Apule asamve kuwawa choonadi akuchidziwa,
A Brian mukuchita kuwonekelatu kuti muli ndi khwinthi pa a mcp. Anthu akhala akunena misonkhano you have never gone against them. Muzikhalako ndi manyazi komaso umunthu. Shame on you. You are trying to bend the story but your friends they're trying to point you the right direction but still opposing them.
Ndege ya anthu 19 inasaza bwanji ndi anthu 9?
Khani ndititi akava khani ya chilima amava kuwawa ponkhalila poti akuziwa kuti iwowo ndiamene anampha SKC masiku akutha chilingamo chiziwika
Anyamata awawa tsiku lina tidzasimba zina😄😄😄😄
Cholakwika chikachitika mumaona chayambitsacho so padakapanda kuzula mbendera anthu sakadagenda convoy .
Mwanyoza kalindo kudya kwake ma vn😂😂😂😂
Ndale za ku Malawi nzautsilu or ikanakhala mcp bwenzi pano akuchita zomwezo. Kodi a Chakwera sankaonetsa kuti iwo sadzaba pano akutani??? Ankati katangale atha pano bwanji??? Kudzakhala ma mega farms ali kuti??? Pano anthu a kudya chitedze why a Malawi simumatha kulankhula chilungamo. We are tired of the leadership of Malawi. 😭😭😭😭😭😭😭 Amayoooo God where are You??? A blood shade country. No love in our nation. Sagrigation, cruel leaders. We need God's intervention
Kodi a Ndevu zamwayi mwadyA bans eti???
It’s all political, ena azibale awo amwalira last week yomweyi apanga move on koma akuti akulira chilima, ndani apa asakugona kukhalira kulira kuti chilima anamwalira.
Andale onse akugwiritsa ntchito chisoni cha anthu kuti apite patali kugwiritsa ntchito imfa ya chilima. It’s all politics, vama candle ivi, how many people lost a close family member after chilima that are lighting candles for their loved ones. Even his own family has accepted and we are not letting them move on.
The way MCP was ready to betray chilima while he was alive we can say they killed him twice, but politicians should not fool us that chilima was their hero because he’s dead.
We can not stop talking about this killing which 9 lives were lost in such way, we can not keep quiet
Wonder is intelligent and wonderful ananjaikowa akuoneka kuti Ali brainwashed
Nanjaikoyutu amafusa dala akudziwa amafuna inuyo mukambe ku mbali yanu not iyeyo.
Kodi mukutanthauza kuti anapha chilima Ndichakwela?
Discussing Nsete zokha zokha yet you know ma statement opusa adayankhula chakwela n Valentino Phiri which illustrated lies n contradictions Kaya mwapasidwa chani Kaya kuti mudzipanga zansete zanu mukupangazi
Bereavement takes time for other it takes one year and others two years even threes to give years depending upon the therapeutic sessions, but with other people's reactions they may be taken to a mental level acute for clinical depression because they have not received closure inparticular cases where the families which have lost their beloved ones via first degree murder or homicide during court proceedings where they take about years for the judge to deliver a verdict. Looking at the case of jinkid and Mellys the rapper in usa or shanquila Robinson. People have the right to mourning their beloved ones who have passed away.
Program imeneyi ndiyabwino mutsuka m'mitu atsogoleri komanso ife tonse timatsukidwa m'mitu simunthu modzi ayi.
MCp ikuzigwirisa onkha Chifukwa chiyani Chimwendo sanakwere nawo ndege
Wonder wandiyakhulila bwino kuti nkhani ya infa ya chilima tisiye, fukwa nde ukumawawa ngati tsabola,eeeh tingoyisiyadi
Ikambidwa mpaka nawo amve kuwawa ngati momwe akumvera ana aomwalirawa abale azikazi awo isaiyidwe amve kuwawa kumene
Ife sitisiya kuyakhula
Zisiyeni za chilimazo brain zitayeni wa dpp iwe
A banda ndi kape coz uli mu boma bwanji sumanena zoipa za MCP
kodi apankuku munalandila ndalama ,kulira saletsana
Zowona gays inuyo mmayitha simubisila ndipo mulibenso mbali (karonga)
Imfa ya chilima anthuwa salinayo ndi chisoni ayi,koma they are happy cz the political parties are looking to benefit out of his death .trust me anthuwa sichisoni ayi nooo!
Guyz musakhare ngat ndinu ana ayi kodi Dege ya a siliki imasakha malo otera? Zachibwana ayi ngat mwakhuta tea zikasewerani mpira
Shisha anadya ndalama.akuoneka mayankhulidwe ake
Otsutsa ambiri amukondaliti chilima.Kodi fundo zakampeni alibe for example DPP Mmene imumadera muja
Mcp inapha chilima
@@Musa1828-l5d Ngati anamupha palibe vuto chifukwa anamusezera machimo ake.palibe wambeu aliyese azafa
Pali kusiyana kwa makambidwe pakati pa chikangawa kunkuyu wankulu wa nkhondo ndi kulephela kwa achitetezo were confused guys it can not be end this until when we know exactly what was happening in chikangawa to those 9 malawi who killed including our let vp
That shows chinachake chinachitika choipa
Zungoonetseratu kuti iyiyi siinali ngozi koma zokonza
@@GraceMwasendipo zoonadi inu mwava
Wopanda manyazi ndinu iwowo ndi kusankha kwawo
Chakwera ndi president wa dziko, ndalama zomwe amayendera ndi za a Malawi azipani zosiyanasiyana, asamapite ku malo nkumakatumbwa za chipani chake, azitha kusiyanitsa chipani ndi boma
Ija inali ngozi chabe
Ndege singayende ilibe zipangizo zokwanila
Chikangawa ndi chakwela ndi chimwendo