you are matured man and you spoke that leadership type of malawian we need bravo Dr Bakili muluzi THAT IS WHY I HAVE BEEN VOTED FOR YOU IN YOUR ALL TERMS WE ARE ONE MALAWINA AND ONE NATION NOT AWA ASABWERE THAT KUGANIZA MOPEREWERA MU UBONGO
Malawians, the chair still looks charismatic and Speaks with a sense of humor. Let’s keep watching at the depth of his speech. We may not see the reasoning behind his sense of humour now but rather things will unfold for the better Malawi or not. My hope is that all is well and there is no sinister move
A chair ulemu wanu apule wodzichepetsa, wanthabwala, woseka ndi anthu osati dzina tikudziwona lelori manyaka eni eni mukhale ndi moyo wautali apule anthu opuma❤❤❤
Well said mr president former deserved even your voice shows that you were chosen to be our leader words of unity may Allah keep you alive may you live longer insha Allah
I will never trust politicians Kuteroku muitenge bwino speach ya atcheya,then take kamphekesera kanamveka kaja kut udf ndi mcp ali limodzi,mupeza mayankho onena kut this people ali limodzi.ndipo tizavote mwanzeru,apo ayi tivotera magazi njala ndithu.
Abakili muluzi adamangidwa ndi DPP komaso kuberedwa boma ndi DPP, nde MCP ndi DPP wankhaza ndani? Akhara kuthandiza banja lamunthalika koma osawayamika ,agaru lero akufuna awathandizeso awuponda
Inde big koma atupele akufuna asewelese anthu kuwatenga ngati zisilu zoona UDF kugwilizana ndi mcp chipan chakupha bwanji kuwasiila achewa chipani chomwe akuti ndi chawo
Very comforting speech a Chair , may the Lord God continue to bless you Sir!
Wow! Ndawakumbukila a chair,, anabwera pa school yakwathu awa ,, President wozichepetsa,, voice yokhayo yaaaa
Wow that's amazing
Adala asyeene ulumu wawo❤❤❤
😅😊😊
Bakili Muluzi is a true STATES MAN
Live live
so nice, a speech worthy praising.......a man among men indeed
you are matured man and you spoke that leadership type of malawian we need bravo Dr Bakili muluzi THAT IS WHY I HAVE BEEN VOTED FOR YOU IN YOUR ALL TERMS WE ARE ONE MALAWINA AND ONE NATION NOT AWA ASABWERE THAT KUGANIZA MOPEREWERA MU UBONGO
Adha awawa muli voice💯💯
We will never have a people president like him, may u live Long a chair athu..
Good speech from Dr bakili muluzi
So powerful speech from a chair Dr Bakili muluzi ,the former president of Malawi ❤❤
Boma ndilomweloli basi❤
I love Udf I love Bakili muluzi
Kuyankhula kwa true Democratic man kumeneko. A chair long live!!!
Every lmppressive Dr Bakili Muluz❤️🩹
I love UDF since i was young❤❤❤
Your respect chair Bakili Muluzi
Kulakhula kwabwino .....kwambili A chair......makwana inuyo ndinu munthu wamkuludi.... respect mr Chair❤🔥
Ulemu wanu a Chair, tinakusowani ndipo tidzakusowani masiku onse. Mukamayankhula, uyo anali ndi nkhawa zimachoka, matenda amachira, maudani amabalalika. Akulu ndi mdambo mozimira moto. Adzikusungani Mulungu. ❤❤❤❤🎉🎉🎉
Nyc speach Dr muluzi we like you
I just like this man. His charisma 🎉
My vote Dpp
Ndimakukondani a chair. Free exercise book ndi ma pen ❤
Acheya woyeeee ❤❤❤❤
Ulemu wanu ❤❤❤❤❤❤❤ komaso mcp yachita bwino osabwera kumeneko
A chair akunoneka kt Ali mbali ya MCP bas Dpp limban mtima zativuta
More fire 🔥 big man ayini ndale mu malawi 🇲🇼, osati ndale za chakwela zophaa azanuzo kumuphaa chilima chifukwa chaudindo galu iwe chikangawa
He was deserved to be president indeed mr chair we really appreciating you together with your administration ❤❤
Chair born to be a leader keep on
Democratic leadership
Kd anthu munangozolowera kutukwana? DPP ndi UTM yalakwa chan pamenepa mukamaika macoment opusa?? Zankutu,osaitchura MCp Bwanji akungogawa ndrama kwaoimba anthu akufa ndi njalao
Akutukana DPP ndi UTM zisilu za anthu
Sakupuma nayo bwino DPP awa alekeni akutayitsani nthawi @@SliviaJosephy
Ndizitsilu zimakhala kuti zalandila bundle ya Mcp kuti izitikwana dpp munya muona ndipo simunati zitukwanani ndi bundle ya magaziyo mbuziii
Malawians, the chair still looks charismatic and
Speaks with a sense of humor. Let’s keep watching at the depth of his speech.
We may not see the reasoning behind his sense of humour now but rather things will unfold for the better Malawi or not. My hope is that all is well and there is no sinister move
Very powerful speech we need such kind of leadership
Ife taphunzila nthawi ya a chair .ku school makope osasowa
Timalandira aulele
Zoona❤
Ndinayamba sukulu ya ulere std 4 /1994, tinkalipila K4.00 komatu kuti ipezeke eeeh anali mavuto.
Zikomo Ambuye Yesu
Zikomo a Chair
Zikomo UDF ( free primary school)
Adpp mwachitatu manyazi APA muluzi wakutsutsani Kuti anakhalilana pansi Kuti MCP aitanidwe.
Ulemuwanu baba❤❤❤❤❤❤
Koma mukumva anzathu asadziwa tanthauzo la democracy? Akati politics samatanthauza kuti ndi udani pa personal.
Kulankhula komanga mtundu wa Malawi osati zinkhanira zinazi
Mphongo zizioneka love you chair all the from machinga
Kulakhula atcheya komanga Malawi mukhale ndi moyo wa utali atcheya
A chair ulemu wanu apule wodzichepetsa, wanthabwala, woseka ndi anthu osati dzina tikudziwona lelori manyaka eni eni mukhale ndi moyo wautali apule anthu opuma❤❤❤
We proud for you
Achir sadzakulaso bas tivomereze🙏🔥
Achir sadzakulaso bas tivomereze🙏🔥
Achir sadzakulaso bas tivomereze🙏🔥
Inunso a DPP 😈 zitsiru munaba Boma ku UDF, munali ndani inu?
Ndizoona koma ubwino wake sanaphepo munthu in a mcp mwamupha chilima shame on you
Well said speach komano it abit late cz zinthu izi monga kholo la matipaty amayenera kuyankhula izi since pomwe zipanizi zinayamba kudana osati kukhala pa convention komabe zamveka ndipo ndikhulupilira kuti boma komanso osusa boma aphudzilapo
A chair 💺 🤣 😅 😂 god bless you my grandfather 👴 🙏 ❤️ we love you so much mr president Bakili muluzi ulemu wanu big president ❤️ 💙 😀
ALL THE BEST UDF WE NEED SOME CHANGES ALICK DYSON FROM JONHASBERG
Atcheya is true leader shame
Kuyakhula kwa muthu wamkulu ukuuu Mulungu apitilize kukusungani Dr Muluz
Wow nice Achar ❤❤❤❤❤❤
A chair , ulemu wanu Baba.
Ndipo ambuye akupatseni moyo wawutali chifukwa cha upangiri wanzeru gogo president a chair. Congratulations
This is a powerful message from Chair Muluzi. Agalu a DPP ndi amene akuononga democracy muno Malawi. Mwachita manyazi lero chairman wakumasulani
Awuzeni a DPP avetse chifukwa democracy samayidziwa mult party democracy
This guy pankhani ya peace he was great.koma anthu amabukuwa eish they feel like they are owning everything
azimai achipani kodi muli ndi album yanu yanu
Well said mr president former deserved even your voice shows that you were chosen to be our leader words of unity may Allah keep you alive may you live longer insha Allah
Ameen
Thanks a chair.
Ena afuna ku gwiritsa chipani cha UDF kuti adane ndi MCP
Nice speech a chair we still love you
True sense, kulankhula kwabwino kwambiri kwa mtsogoleri wopuma Bakili Muluzi,.si AGALU aja achina DPP ndi UTM. Kupusa
Mwayiwala mcp
😂😂😂😂😂😂 ndipotu @@SharonNdadza
Komaditu kkkkk
A true democratic champion
Achalume kweleko😂😂😂
God bless 🙏 you gogo wathu
Shame to DPP party which is fueling division among malawian. Chair is atrue democrat
Mmm nanuso nde ziti mukukambazi tatiyeni tingosapota a chair basi sizikugwilizana ndi dpp ayi
Yes yes yes andikumbutsa zakare,koma kare likati lidzibwelera
Nice 👍 speach Boss
Kuchikwesya Allah wape umi welewu in sha Allah
I will never trust politicians
Kuteroku muitenge bwino speach ya atcheya,then take kamphekesera kanamveka kaja kut udf ndi mcp ali limodzi,mupeza mayankho onena kut this people ali limodzi.ndipo tizavote mwanzeru,apo ayi tivotera magazi njala ndithu.
I agree with you
❤ndipo mkuluyu akadangoyambaso ndale ndithu anawa satipititsa kulikose ayi
Inu ndiinu munthu wakulu palibenso ena ayi ulemu wanu
Ku Changoma, Salima, T/A Mwanza, president yekhayo amene anakapondapo, alipa helicopter.......katunduuyu
Great speech
Mwayankhula zomveka a muluzi Moti adpp atengerepo phuziro
makosana magwilagwila mpaka mwationetsa babe kkkkkkkkkkkk
Achair amandiwaza Ambuye azikupasani moyo wautali munatimenyela khondo yosaiwalika
Machine kuchitekete, katundu omanga ndi matcheni ulemu wanu
Machine
Indeed nyc speech
Long live a Chair
Abakili muluzi adamangidwa ndi DPP komaso kuberedwa boma ndi DPP, nde MCP ndi DPP wankhaza ndani? Akhara kuthandiza banja lamunthalika koma osawayamika ,agaru lero akufuna awathandizeso awuponda
Aaaa ndaledi zidapita ,kudali a chair munthu wachikoka pa graund wosati zalelozi za muthalika ndi a chakwelazi ayi .kkkkk
Kikikiki chair
Ulemu wanu a chair timakunyadilani pobweretsa Democracy Ku Malawi
A chair inuyo ndi one ndimakumbukira nthawi ineyo tinakumana nanu ku shop rite anangoti nonse muli muno tengani zomwe mukufuna koma kunali kuseza njinga ma fridge kkkkkkk ndilipira ndine achair mumativesa kukoma 😊
A dpp apange manyazi being thieves stealing government from dpp when muluzi for government duties in Mozambique
Shut up
Acheya woooye ngakhale munatinamiza sapato tikudikilabetu Ife 😂😂😂😂😂😂😂
Tikuzifunadi sitinaiwale awuzeni😂😂😂
Cheya wooyeee mcp moto buuu
Point of correction we are not segregating any party but frankly speaking nobody can be happy with what Chakwera is doing he is evil and arrogant.
za power mr patrone
Dziko la Malawi langokhala lovuta , koma achair analidi president wa Malawi
Inde big koma atupele akufuna asewelese anthu kuwatenga ngati zisilu zoona UDF kugwilizana ndi mcp chipan chakupha bwanji kuwasiila achewa chipani chomwe akuti ndi chawo
Achair munthawi yanu mudali ndi readership yoyanjanitsa amalawi,choonde phunzitsani a chakwela ndi a muthalika chifukwa zikuwonetsa kuti nzeru zochepetsa tsankho mulibe mu readership yawo atsogoleri amenewa.
Tunda kuchitekete
Kkkkkkkk acheya mumandiwaza kwambili
Hahahahahahahahahahahahahahaha🤣🤣🤣🤣🤣🤣Uyu Tcheya sadzatheka🤣🤣🤣🤣🤣
A chair 🔥🔥🔥🔥
Main democracy party
Zimene anena Bakili Muluzi ziwapatse phuzilo a times andevu za mwai ndazawo achite manyazi chifukwa akulimbikitsa tsankho mdziko muno, nanga kodi adpp pakut ndi omwe analanda boma la udf akoma lelo muzichitako manyazi a Blian Banda polankhu
Nanga po nyambita ma company adziko lino simunalankhulepotu.
President wa mzeru othaso kuyakhula
Zomwe mukunena mukhale phee Linda madzi ndipo muziti tadala mutunda ndiwautali pa Sept