SENDERA SISTERS - DPP CAMPAIGN THEME SONGS 2024/25

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024
  • Sendeza sisters campaign theme songs

КОМЕНТАРІ • 81

  • @SostinMatchado-z2o
    @SostinMatchado-z2o 3 дні тому +1

    I like this 🎶 song beautiful color wow big up to you

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 7 днів тому +2

    Your excellence.tikufuna muzaibwezeletse kwacha idzakhale ndi mpavu osati ikupitaku.ife tikupepherelani mpaka zitatheka.mukungu ndiwachifundo.ndalama ya malawi ikafika paja inafika ya zimbabwe paja.ambiki tikakhala ma lefujizi kwa eni

  • @daviskamonde4882
    @daviskamonde4882 13 днів тому +8

    I like these women and their art.
    Well organised and great melody.

  • @GeorgeBanda-x6l
    @GeorgeBanda-x6l 13 днів тому +8

    chipani chafuko mmm kuchita kunva kukoma ngati ndilikomko eee zosangalatsa ndithu ❤❤❤ APM my vote ❤❤

  • @berlz12k
    @berlz12k 6 днів тому +2

    Kunena chilungamo kulianthu osamba uku..mtendere okhaokha..ndine we utm komaso waganyu wa dpp😅 DPP + UTM bomaaa iloooo🥳🥳🥳💕💕💕

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 12 днів тому +3

    Km chipan ichi chokondeledwa ndpo kwambiri ndikuchedwera pati ndizipita kumalawi ndikavote nane bpp boma ilooooooo❤❤❤❤

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 12 днів тому +10

    Kumaona chidzindikilo chachipani abale ukayike tambala wokuda kuthandauza chani chimanga ndiye mtendele wathu amalawi moto kuti buuu dpp

  • @EuritaDeric-fz3ds
    @EuritaDeric-fz3ds 12 днів тому +6

    Ndikumva kukoma ndithu nyimbo yabwino 🎉🎉

  • @SostinMatchado-z2o
    @SostinMatchado-z2o 3 дні тому +2

    For the first time convention iyiyi munakonzekeradi kwambili mumakwana azimayi

  • @thulanimpphiri6873
    @thulanimpphiri6873 13 днів тому +5

    Kkkkkkk nkhata bay pawengi nadi suzgo kuti awini Peter. Chilima ndimweniyo akubaya wanguwawinisa 2020 sonu pamu pawengu suzgo kanthukooooooo❤❤❤❤

  • @ClementkapelulaNkhoma
    @ClementkapelulaNkhoma 12 днів тому +4

    Chiyembekezo Cha Malawi dpp boma 2025 dpp woyeeeee🔥🔥🔥🔥🔥buuuuu

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 12 днів тому +6

    Guys nyimbozi za ma audio ndingazipeze bwanji Pls guys, Peter he's our father ndimamukonda Ndipo kwathu konse ndiife a DPP

  • @user-ok8sk2uh6h
    @user-ok8sk2uh6h 12 днів тому +5

    Nduchita kunva ngati bingu is somewhere smiling for the mighty Dpp

  • @CHIWSABINYAMBOSE
    @CHIWSABINYAMBOSE 3 дні тому +1

    Woow i like the song as mtumbuka

  • @lingsonmitunda293
    @lingsonmitunda293 13 днів тому +3

    So beautiful sweet melodies, giving good hope to troubled Malawi.

  • @FelixTsabolaNamaya
    @FelixTsabolaNamaya 11 днів тому +3

    Very veryGood song, Well composed.

  • @chifunirokachingwe3700
    @chifunirokachingwe3700 7 днів тому +1

    These women know how to compose nyimbo mwee

  • @PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ou
    @PatrequeFanuelKaussiwa-nq9ou 8 днів тому +2

    Chipani chokoma ichi❤

  • @lingsonmitunda293
    @lingsonmitunda293 13 днів тому +2

    Tinyimbo tofewa, kupereka uthenga wa chiyembekezo chabwino ku dziko lathu la Malawi pamene anthu akudutsa munyengo zowawa kwambiri pa ulamuliro wa Chakwera.
    Mulungu atithandize ndithu

  • @user-ww9rj2wx8d
    @user-ww9rj2wx8d 13 днів тому +3

    Nice song and so ❤d with more people

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 13 днів тому +4

    Chipani chafuko ichiiiiii ❤❤❤❤❤❤ I can't wait kuchiponyera vote ❤❤

  • @mabvutomunyenyembe1344
    @mabvutomunyenyembe1344 3 дні тому

    I love the tune

  • @DoreenLivata
    @DoreenLivata 8 днів тому

    Ulemu wanu azimai ndikuchita kumva kukoma dpp mbambande

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 12 днів тому +3

    Azimai amavina awa ❤❤❤

  • @JeremiahMlotha
    @JeremiahMlotha 6 днів тому

    I like it🎉🎉🎉❤❤

  • @samuelsergio5343
    @samuelsergio5343 7 днів тому

    Zikufunikila kuganiza bwino poka vota apiter akawina adzasitha zithu zochuluka.

  • @MiddieChavula
    @MiddieChavula 10 днів тому +1

    Azimayi awa amaimba bwino ndth.... Mighty Dpp🫶🫶💙

  • @RiddleQuizGame
    @RiddleQuizGame 8 днів тому

    So powerful a song honestly. Atolankhani amabungwe amipingo ndi azipani kodi mukudziwa kuti nditapita ku NRB ndapeza National ID yanga akuti was issued pomwe ini sindinapatsidwe? Kodi ziphasozi zikumapita kuti? Motero pakanali pano sindine wokhutitsidwa kuti chaunzika chidzagwiritsidwe ntchito povota. Lamuloli likufunika likasinthidwe mwachangu ku Parliament.

  • @TrizaGeorge-q8w
    @TrizaGeorge-q8w 2 дні тому

    Powerful 💪💪❤❤

  • @thomhenry1127
    @thomhenry1127 10 днів тому +1

    Koma azimaiwa atayamba kuimba Gospel akhoza kupita patali zedi.....Ndikumva maitanidwe amwambuye

  • @RodneyMpahah
    @RodneyMpahah 2 дні тому

    Very interesting

  • @AlexMsowoya-o1t
    @AlexMsowoya-o1t 12 днів тому +1

    Dpp woyeee,chaka chamawa boma lizakhala lomwori la dpp.

  • @veronicamalisero2671
    @veronicamalisero2671 2 години тому

    boma ilooooooooooooo🔥🔥🔥🔥

  • @ChawezChinkhuntha
    @ChawezChinkhuntha 12 днів тому +1

    Beautiful women's 🔥🔥🥰

  • @ThomasJossam
    @ThomasJossam 9 днів тому

    Pa zimayi awa okha sanamphonye olo pangono keep it up

  • @vitumbikocobysinyiza-5116
    @vitumbikocobysinyiza-5116 8 днів тому

    Komamzomera ngwira wakhalako

  • @EphraimKaombe
    @EphraimKaombe 5 днів тому

    Dpp woyeee 2025 boma

  • @FelixMachika
    @FelixMachika 7 днів тому +1

    Eeeeeee, ndikumva mtendereeeeeeeee😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂❤️❤️Iwe bwa?

  • @funnynyirendafunny7888
    @funnynyirendafunny7888 2 дні тому

    Ipaseni moto

  • @TelezaManyela
    @TelezaManyela 6 днів тому

    nyimbo yabwino

  • @funnynyirendafunny7888
    @funnynyirendafunny7888 2 дні тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @NKANAMWANOGENERALDEALERS
    @NKANAMWANOGENERALDEALERS 7 днів тому

    Kma kampeni nyimbo iiyi kaya

  • @WinerdShadreck
    @WinerdShadreck 8 днів тому

    Amazing 🎉

  • @WazingwaGift
    @WazingwaGift 15 годин тому

    Kma azimay awa amatha

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 8 днів тому

    Wa Mcp chitsekula mmimba

    • @berlz12k
      @berlz12k 6 днів тому

      Zitsiru zikumva pain😂😂😂

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 9 днів тому

    Mukuimba bwino Azimai❤

  • @Crysis25
    @Crysis25 11 днів тому

    Akumveka mwa chitonga azimayi athuwa

  • @NKANAMWANOGENERALDEALERS
    @NKANAMWANOGENERALDEALERS 7 днів тому

    Kma inu mukumva bwanji mthupimo kkkkkkkk

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 8 днів тому

    Fire

  • @KembastaSll
    @KembastaSll 13 днів тому +1

    Nyimboyi iri bwino kwambiri

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 11 днів тому

    My vote ❤

  • @AnnastasiaChakwiya
    @AnnastasiaChakwiya 9 днів тому

    Zikuchita kubeba

  • @PeterJames-i8y
    @PeterJames-i8y 9 днів тому

    2025 boma❤❤❤❤

  • @AlexMsowoya-o1t
    @AlexMsowoya-o1t 12 днів тому

    Ana achepa ❤❤❤❤❤

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick 13 днів тому

    DPP Bomaaaaa iloooooooooo ❤❤❤❤

  • @Innõva88
    @Innõva88 13 днів тому +1

    Machine

  • @rhodahjere8747
    @rhodahjere8747 6 днів тому

    Boma 2025

  • @Donnexbatumeo
    @Donnexbatumeo 12 днів тому

    Kuwalatu😍😍😍😍

  • @oramachimkango9773
    @oramachimkango9773 9 днів тому

    ❤❤❤❤❤ DPP 💙✔️

  • @JoyceLiwonde
    @JoyceLiwonde 9 днів тому

    ❤❤❤❤❤ Boma ilo🎉🎉🎉🎉😂😂

  • @paulmanyamba5437
    @paulmanyamba5437 12 днів тому

    Koma chipani ichi kukoma kodi akuti mayi wina uja anapita kuchikangawa kkkk aziona

  • @PrinceBlessings-bv5bs
    @PrinceBlessings-bv5bs 13 днів тому

    Azimai awa amaimba ndithu msanje uko❤❤❤❤

  • @KhooMadex
    @KhooMadex 9 днів тому

    Jomo for me😂😂

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 13 днів тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤💃💃💃💃

  • @EliqueJoséHazuwelo
    @EliqueJoséHazuwelo 9 днів тому

    Saimoni and kendo

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo 12 днів тому

    Moto kt buu dpp basi nde yanga

  • @trynessmsowoya4187
    @trynessmsowoya4187 9 днів тому

  • @EllenNamulu
    @EllenNamulu 8 днів тому

    Apm

  • @user-lp8wj3vq4x
    @user-lp8wj3vq4x 13 днів тому

    ❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e 12 днів тому

    ❤❤

  • @PreciousMasauli-uk9hs
    @PreciousMasauli-uk9hs 8 днів тому

    Can someone type that first song for Me please 🥺

  • @RahimRashid-py3vb
    @RahimRashid-py3vb 11 днів тому

    Azimayi a DPP osamba kawawa

  • @alexjeremanuel2541
    @alexjeremanuel2541 12 днів тому +3

    Azimai amavina awa ❤❤❤