- 243
- 727 764
Malawi Exclusive
Приєднався 25 сер 2024
Welcome to Malawi Exclusive Limited. Our ultimate goal is to inform, educate, and entertain Malawi by providing insightful content on the latest trends in Malawi. Through engaging videos, the channel seeks to foster a deeper understanding of cultural, social, and technological developments, ensuring that viewers stay updated and entertained.
APM AND USI TO LEAD ALLIANCE 2025, APM WAGAWA CHAKUDYA KU MACHINGA, TONSE ALLIANCE ZAMBIA LAUNCHED
DAILY UPDATES FROM MALAWI EXCLUSIVE
Переглядів: 113
Відео
APM AZAWINA NGATI TRUMP, AMALAWI AKUFUNA MPANDO WA VICE PRESIDENT UTHE, MTALIMANJA ATULEPANSI UDINDO
Переглядів 2649 годин тому
MALAWI EXCLUSIVE DAILY UPDATES
PRESS CONFERENCE YA FREDOKIS INALI YACHIBWANA, NJALA YAVUTA, UTM & FAMILY KULIMBILANA CHUMA CHA SKC
Переглядів 5532 години тому
MALAWI EXCLUSIVE NEWS 6 NOVEMBER 2024 (Watch the press conferences on @ZodiakMalawitv & @times360malawi
KU EQUATORIAL GUINEA AMAKATANI, MCP IKUDZIWAPO CHANI ZA MWANA WA TEMBO, CHILIZA CHA GWANDA CHAKWAMBA
Переглядів 1,7 тис.4 години тому
NKHANI PA MALAWI EXCLUSIVE
CHAKWERA TO BE IMPEACHED, KAMBALA NOMINATION, GUINEA SEX SCANDAL | NKHANI MADZURO
Переглядів 2,1 тис.7 годин тому
EVENING NEWS WITH MALAWI EXCLUSIVE ON 4TH NOVEMBER
KABAMBE VS MTUMBUKA, DAUSI ABWERASO, @nyasabigbullets IN THE FINALS, @luluandmathumelaband NEW SONG
Переглядів 2,1 тис.9 годин тому
NEWS UPDATES FROM THE MALAWI EXCLUSIVE
FELIX NJAWALA ATI A MICHAEL USI AKUNAMA ZOMWE ANAYANKHULA PA @ZodiakMalawitv EXCLUSIVE INTERVIEW
Переглядів 6619 годин тому
A FELIX NJAWALA ATSUTSA ZOMWE A MICHAEL USI AMAYANKHULA PA ZODIAK EXCLUSIVE INTERVIEW KUTI KU UTM SAMAWALEMEKEDZA NGATI MTSOGOLERI, IWO ANENA IZI PA MIJ ONLINE. @dancehallvidz@ZodiakMalawitv @times360malawi
NGONGOLE YA FETELEZA, SKC MEMORIAL KU NSIPE, KALATA YA MERA, A THOM MPINGANJIRA APEPESASO?
Переглядів 20312 годин тому
MALAWI EXCLUSIVE NEWS
NKHANI MSABATAYI | UTM CONVENTION, FUEL SHORTAGE, SYLVESTER NAMIWA, NGEYI KANYONGOLO, FLAMES COACH
Переглядів 67112 годин тому
ZOMWE ZACHITIKA MSABATAYI KU MALAWI
AWASO NDE ACHOKERA KUTI? ATUMIDWA NDINDANI? AKUTI CSO YAWO IKULIMBANA NDI DPP! KOMA ZILIKOTU ZILIKO
Переглядів 20314 годин тому
AKUTI DPP IKUFUNA KUBERA CHISANKHO
MAI JOYCE BANDA WAUZA A CHAKWERA KUTI VUTO LA MAFUTA SANGALITHE CHIFUKWA ALIBE MA CONNECTION
Переглядів 6 тис.16 годин тому
JOYCE BANDA KUPHUNZITSA CHAKWERA ZOYENERA KUCHITA
GEORGE KATSAKULA AKUTI A NAMIWA AKUTUMIDWA NDI APM KOMANSO DPP KUTI ASOKONEZE COMMISSION OF ENQUIRY
Переглядів 16916 годин тому
GEORGE KATSAKULA KUTOKOTERA A SILVESTER NAMIWA
VUTO LA MAFUTA LIPITILIRABE | ONERANI ZOMWE AYANKHULA A HENRY KACHAJE
Переглядів 7416 годин тому
VUTO LA MAFUTA LIPITILIRABE | ONERANI ZOMWE AYANKHULA A HENRY KACHAJE
DR MATHEWS CHINOMBA MTUMBUKA KUKUMANA NDI MA DELEGATES KUMVA NKHAWA ZAWO PRIOR TO THE CONVENTION
Переглядів 19419 годин тому
DR MATHEWS CHINOMBA MTUMBUKA KUKUMANA NDI MA DELEGATES KUMVA NKHAWA ZAWO PRIOR TO THE CONVENTION
COMISSION OF ENQUIRY SILIBWINO, AKUFUNA AZIPANGA KAFUKUFUKU MOBISA | NAMIWA WAZITULUKA
Переглядів 30219 годин тому
COMISSION OF ENQUIRY SILIBWINO, AKUFUNA AZIPANGA KAFUKUFUKU MOBISA | NAMIWA WAZITULUKA
KULONGOSOLA NKHANI YA GOD PAPA, PATRICIA KALIYATI & SAULOS KLAUS CHILIMA | CHOONA NCHITI?
Переглядів 10 тис.21 годину тому
KULONGOSOLA NKHANI YA GOD PAPA, PATRICIA KALIYATI & SAULOS KLAUS CHILIMA | CHOONA NCHITI?
FUEL CRISIS KODI ZILIPATI KU MALAWI?
Переглядів 25421 годину тому
FUEL CRISIS KODI ZILIPATI KU MALAWI?
SYLVESTER NAMIWA NDI ANZKE ONSE OMWE ALI MU COMMISSION OF INQUIRY ALUMBILISIDWA KUTI AYAMBE NTCHITO
Переглядів 491День тому
SYLVESTER NAMIWA NDI ANZKE ONSE OMWE ALI MU COMMISSION OF INQUIRY ALUMBILISIDWA KUTI AYAMBE NTCHITO
ZOMWE ANAYANKHULA KWENI PATRICIA KALIYATI ATAWATULUSA PA BAIL PA MLANDU WOFUNA KUPHA CHAKWERA
Переглядів 263День тому
ZOMWE ANAYANKHULA KWENI PATRICIA KALIYATI ATAWATULUSA PA BAIL PA MLANDU WOFUNA KUPHA CHAKWERA
BINGU ZA DEVALUATION AMAKANA, NGONGOLE YA IMF & WORLD BANK AMAKANA, IYE KOMA FOOD SECURITY BASI !
Переглядів 223День тому
BINGU ZA DEVALUATION AMAKANA, NGONGOLE YA IMF & WORLD BANK AMAKANA, IYE KOMA FOOD SECURITY BASI !
A CHAKWERA ANKAYANKHULA NGATI AMADZIWA KUYENDETSA DZIKO KOMA LERO NDI IZI!
Переглядів 955День тому
A CHAKWERA ANKAYANKHULA NGATI AMADZIWA KUYENDETSA DZIKO KOMA LERO NDI IZI!
KUMANGIDWA KWA A KALIYATI KWABWELESA MGWIRIZANO KOMANSO CHIMVANO KUMBALI YOTSUTSA BOMA
Переглядів 1,2 тис.День тому
KUMANGIDWA KWA A KALIYATI KWABWELESA MGWIRIZANO KOMANSO CHIMVANO KUMBALI YOTSUTSA BOMA
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH JESSY KABWIRA MCP PUBLICITY SECRETARY
Переглядів 605День тому
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH JESSY KABWIRA MCP PUBLICITY SECRETARY
DPP MGONA RALLY RESTREAM BY PUBLIC DEMAND | UKU KUNACHEMA OSATI MASEWERA
Переглядів 246День тому
DPP MGONA RALLY RESTREAM BY PUBLIC DEMAND | UKU KUNACHEMA OSATI MASEWERA
KANDIMVERERE NDI CHAWEZI BANDA & DEUS SANDRAM | ANGONAMIZA ANTHU BASI AWA
Переглядів 11914 днів тому
KANDIMVERERE NDI CHAWEZI BANDA & DEUS SANDRAM | ANGONAMIZA ANTHU BASI AWA
UPDATE YA NKHANI ZA KUMANGIDWA KWA A PATRICIA KALIYATI. ZILIPATI SO FAR
Переглядів 44314 днів тому
UPDATE YA NKHANI ZA KUMANGIDWA KWA A PATRICIA KALIYATI. ZILIPATI SO FAR
TRENDING! A PATRICIA KALIYATI AMANGIDWA | ZAKHALA BWANJI??
Переглядів 27414 днів тому
TRENDING! A PATRICIA KALIYATI AMANGIDWA | ZAKHALA BWANJI??
JOE GWALADI NDI KATUNDU PA NKHANI ZA MAIMBIDWE KOMANSO PA STAGE
Переглядів 36714 днів тому
JOE GWALADI NDI KATUNDU PA NKHANI ZA MAIMBIDWE KOMANSO PA STAGE
KULONGOSOLA MAVUTO OMWE ALI KU CHIPANI CHA UTM, KODI WOLAKWA NDANI PAMENEPA
Переглядів 77514 днів тому
KULONGOSOLA MAVUTO OMWE ALI KU CHIPANI CHA UTM, KODI WOLAKWA NDANI PAMENEPA
BOMA LIMAGULA MAFUTA PA NGONGOLE NDIPO NGONGOLEYO INAKULA MPAKA SUPPLIER ANAKANIZA MAFUTA AKE
Переглядів 11714 днів тому
BOMA LIMAGULA MAFUTA PA NGONGOLE NDIPO NGONGOLEYO INAKULA MPAKA SUPPLIER ANAKANIZA MAFUTA AKE
Sizoona..manganya ndi wa mcp
andalewa amatipepelesa kwambiri
Zamabodza izi angofiuna mubisa a m c p pa nkhani ya imfa ya chilima
Abale anthuwo mkanawapatsa ma uniform pls akuyimba bwino kwambiri
Zabodza
Network sabwerekana❤❤❤big up Dr joyce Banda
Amibawa inuyo ndi one
Munthu ameneyo anakuuzani amalawi kuti saziwa kanthu ayi iyeyo amagwira nchito kuchipiku ndiye mati angayendese dziko nduna zake zonse dzamamina even nchito yeniyeni imene anamusakhira kuti akhale nduna samaiziwa munthu achokele kudambwe watopa kuvina gule nkumuuza kuti iwe ukhara nduna yadzachitetezo chikhalileni munthuyo anali driver ndiyogwira imeneyo amalawi anamachende amenewa achoke basi mboli zamawo
Kod mayi amenewo akusitenga ngati ndani mayj jozifer akusitenga ngati mziko lamalawi ndieawo coty ichaja nanga ndawi ya dadi zisiteke kumuchosa jon asaajawo achoke amenewo mwana jontembo
Mutengereni Anjella Ku Khoti ngati akunama?
Ngati lili bodza za God papa ,tamutengereni Anjella Ku Khoti mimbulu inu yachabe chabe inu. Nthawi yinoyo ndi ya god papa.
Nganga basi😅😅😅
Ine kuwona kwanga ndikuti MCP sayenera kuyankhulapo pa nkhani ya mkulu wachisankho chifukwa chipani cha MCP, UTM DPP AFORD UDF, ayenera kukhala gulu limodzi lonena za chisankho kuti chikhale free and fair. Ngati a MCP akuyankhulapo kuyankhulira bungwe la chisankho ndiye kuti Ali limodzi ndi MCP Payenera kusiyanitsa pakati pa nthambi za Boma ndi Chipani. Bawalekani achisankho aziyankha okha osati Boma kapena chipani cholamulira. Ndiko kuti chilipo. Kabwira ndi wonenera chipani osati bungwe la chisankho. Mwafulirwa ndi Mneneri wachisankho. Mzayankhulepo pa izi ndalembapo. Ziipani chiyenera kukhala ndi aneneri ake, Boma ndi Mneneri wake, bungwe la chisankho Mneneri wake. Osayankhulirana Chonde tanenanipo apopo
Thanks
Machender ako Dan Lu pasanapako amako akumvutika uko chisiru unalindan yiwee chipanda kukutora garu
Sitingamykhurupirile mmayi wabozayu
a Malawi chonde ..musatero plz muli ndikuphika nkhani eishhhhh
Ulemu wanu mama
Zonse MCP pathako panu
paja ku MCP aliyense amatha kuyankhula pena paliponse zikuoneka kuti sasata job description kwenikweni
padziko la pasi palibe chisinsi ,pasi pa nthambo palibe chobisa
Kaliyati ndiowopya anasowetsa anthu osawona alinduna ndibakili iiio
Zausilu basi
Zaboza
Map
Propanda always flops
Panyapano nkhondo yaku kuyukileni ili mudziko muno masende yako kunkuyu uziganizira za witika masende ako
PANYAPAKO KUNKUYU TIKUPONDA
Mbudzi ya munthu ma - +Ake chakwera
Achoke chakwerayo ,.. ife tatopanaye
Kugwetsa ndege
Kagalu
Manbodza awa! Chifukwa Bieni kulibe sangathe kuziyankhulira ndiye kumangowapaka ndowe chonchi!!!!!
Komatu nthawi Yanu mungotayila Za ziii
Cholinga tisamaganizire boma pa nkhani yophedwa kwa chilima, mbuzi za MCP
Moto kutiybuuu
mwaiwalatu akazi abusa pa list po kkkkkk koma Apolice alowelela privacy yamunthu,,,komaso azimayiwa zimawasangalasa becoz they gave their consent before filming pena ngati Mulungu angotumiza mwana wake adzaweluze dzikoli mmmmmmm
The woman if she was the first person to contact Papa, she wouldn't have disclosed this sensitive issue. Use psychology here. MCP plan.
What a lie
Where did she get the same story. This woman must be followed to a latter.
Bring God Papa here and acknowledge what you are saying
@shadreckphiri1799 Thank you simple
Improve your voice madam
Now umboni wokinza kuphedwa kwa a chakwera ngati unaliko umeneo uza tuluka
Koma nkhani yakuti a late Chilima yimfa yao ina chikela pa God papa izatengera kubvomela kwa God papa kuti ndizoona mankhwala otero anakonzedwa
@@happyluhanga3387 zaboza izi akufuna kupanga anthu confuse
Now pali nkhani ziwiri apa tiseye kukokana a mai kaliati alimoyo Umboni wa ku God papa uthakudziwika kuti zinaliko kapena ayi coz akugwiritsa ntchito zinthubza actual zoti ngati kunalibe apokice alephera A God Papa mesa aliko ku nigeriako?
Dzikomo kwambili mai apa mwalongosola mwachilungamo ngakhale mu nkhani zina mukuma onesa mbali ya DPP koma apa mwafotokoza mwa proffession ya reporting ya just
Akayambe abambo ake
Kodi impeachment si Democracy
Zowoona man jomo ya njanisani basi ndimakunyadilani
Mumakwana man jom cholembedwa palibe angakulandeni
Kkkkkk😂😂😂😂