Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Mavuto onsewa ndi chakwela ndi a chimwendo,Kunkuyu ndi Jesse kabwira ndi amene akupangiza izi akumayikira Achewa kumbuyo ndiye tikabweza akuti ndife oipa komaso asaganize kuti tonse tingavotele mcp akunama khalidwe lawo a mcp
Vuto ndilina ndilakuti aliyense akufuna kuntchuka, mutamvera mau a chairman wakundilande market uja! Zikuonetseratu kuti angofuna potchukira basi
Akuyambisa chakwela 😊
Kuyendela limodzi kuchitika MCP yikazachoka m'boma
Ndibwino kuvomereza zotsatira, owina amakhala m'modzi.
Vuto ndi usongoleli umene ulipo panopa
Onsewa akufuna misonkho ya Amalawi.Ndalama zopanda munuwake zamasiye zopanda signature.Zopanda Mwini Mwini.Osakhala ngati Ibrahim Traoli ku Bukina Faso.President Osadzikond,pa 2years yokha Ku Bukina Faso kusinthilatu!Or Jose mulika wa Yuligwayi!
Kkkkkk koma nzoona ndix sisunga kape kunkuyu ndikape
Muli bhoo guys continue tell them truth
Mavuto osewa akuyambitsa ndi achakwera bwanji sanakawamange azikwanje aja?
Kodi amapha ng'ombe ku Lilongwe zachitika kangati ndiye amadzudzula ? Zikachitika ku Blantyre amamanga msanga komano ku Lilongwe ayi simukuona kuti boma lolamula ndilimene likukolezera?
The don't care about people are died and suffer every day because the got everything but one day judgment play me lucius Banda chigawenga
First comment
Khaniyo ndiyona
Mavuto onsewa ndi chakwela ndi a chimwendo,Kunkuyu ndi Jesse kabwira ndi amene akupangiza izi akumayikira Achewa kumbuyo ndiye tikabweza akuti ndife oipa komaso asaganize kuti tonse tingavotele mcp akunama khalidwe lawo a mcp
Vuto ndilina ndilakuti aliyense akufuna kuntchuka, mutamvera mau a chairman wakundilande market uja! Zikuonetseratu kuti angofuna potchukira basi
Akuyambisa chakwela 😊
Kuyendela limodzi kuchitika MCP yikazachoka m'boma
Ndibwino kuvomereza zotsatira, owina amakhala m'modzi.
Vuto ndi usongoleli umene ulipo panopa
Onsewa akufuna misonkho ya Amalawi.Ndalama zopanda munuwake zamasiye zopanda signature.Zopanda Mwini Mwini.Osakhala ngati Ibrahim Traoli ku Bukina Faso.President Osadzikond,pa 2years yokha Ku Bukina Faso kusinthilatu!
Or Jose mulika wa Yuligwayi!