Ofunika kuyamba kudzudzula zipolowe ndi Atsogoleri, chitsanzo kwa Nsundwe palibe chomwe chinadziwika pa road block yomwe inayikidwa ndi anthu osadziwika koma opanda onangidwa.
Musapange bulemu anthu ogenda koma olakwa ndi awa president chakwera ndi nduna zake. Mukulu wa polisi ndi apolisi wose . Mukulu wa silikali ndi asilikali wose ndi amene akufuna kuononga malawi. Musapite ku osusa or anthu wamba . Chilipo chimene chakwera wachitapo mukulu wa silikali mukulu wa polisi pankhani ya zikwanje?
Mtsukuluzi (Jona ) I always appreciate you when it comes to your turns cos mmayima pama facts okha okha😊 keep it up osadzaopa mayaz we always follow you bro
Unu a Hot current mulungu akusongolereni chilungamo mumachichita. Ku UTM a mai Kaliati amazitrnga ngati a wina koma amayibala kuti she doesn't qualify. She wanted to take an advantage of the death of our Chilima but we knew her very much. God help Kambambe to work and put together our beloved UTM
Vuto ndi mr chikangawa agwade achoke iyeyo ziko lamulephela. Ziko si church nyimbo ikhale ya nepman tikuweta mikango tikanali mujango. Iyeyo ndi ng'ona ndipo ationesa zilango 😢
U keep fighting Usi, he asked to resign but the greedy ppo didn't want to dirt the party name, hoping kuti mwina they will be party president. You just dont see but Usi is now campaigning for himself, you too focused on Usi
Well said komano pempho langa ndiloti chipani chomwe chili pa mpando chayenela kukhala chosogolera pokhazikisa bata cz zonsezi zikuchitika kaamba kolekelera now enawo akupanga ngati revenge, cz aboma akachita zinthu president kungokhalirapo now enewa sizikuwasangalasa nkani mkuona zipolowedzi zikuchitika solutions a chakwera ayambe atenga gawo ngati sogoleli wa dziko cz he's got all powers to do so kunako enawo will follow
The chinseu Bridge is totally destroyed and worse will be destroyed with this coming of rains this season. Businesses are destroyed annually more especially the coffins done there. Politicians have been coming promising and leaving and bit even from the CDF has money been allocated to the reconstruction of this bridge and people got weary and tired of the Politicians who now wanna use this bridge as a campaign project yet they left it to be destroyed and allegedly kumkuyu came and wanted to make more empty promises and people got angry. Politicians should learn to develop things within their term than let things lot to then use those damages as campaign cards .people are wise now
Vuto lilipo ndiloti tili ndi presdent amene ali mbuzi za ma mbuzi boma la zisilu zikungonyenga,cikangawa nuyu wapeleka mimba ku 49,mcp ndi 0% cifukwa zimene zisilu zina zikuti cikangawa delivery sizace ndi za APM akuona ngati sitidziwa. A gwape amenewa a mcp 2025 akupita smart matc sigwila tcito angotaya nthawi.
Mkutha kuona kuti mcp is avoiding mademo by making up unnecessary programs ndipo it's not first time to do so komanso zonsezi akuchita ndi presdent chakwelayo cz alibe fundo zomanga he's the one behind all zipolowedzi cz sangapange ma program ake yeti akudziwa kuti pali ma demonstration
Dzikoli kwachitika zinthu zitatu zimene president amayenera kutuluka ndi kuyankhula ku mrundu wa Amalawi. President sanatuluke kuwtipanga update pa vuto la mafuta. President sanatuluke kudzudzula zipolowe pa ndale. President sakupereka update pa vuto la njala mdziko. Pena kumazifunsa kuti kodi President sakuona, sakudziwa mavuto athu?
Is Hot Current a spokes agent UTM and other parties. The way i see you have become a partisan. Why you question USI on his actions? Like any politician you can not blame him or tell him to leave the party.
Find good microphone, musamachite kumakuwa mumatibowola makutu, plus i feel like you losing your energy raising your voices. Find good and better microphones
Bodza ili timaona maiko ambiri ngat pena pake pakuvuta amalowa pa msewu South Africa and other more achina melema timawaona akumema ndyedi zimachitika osat zomalepheletsa ma demo a president tikungoonela kwathu komweko
Dziko lathuli akuliononga ndi akuruakuru andale omwe akutengela advantage amalawi ovutika ndi njala... Kumawapatsa ndalama kuti azisokoneza
💯
Ofunika kuyamba kudzudzula zipolowe ndi Atsogoleri, chitsanzo kwa Nsundwe palibe chomwe chinadziwika pa road block yomwe inayikidwa ndi anthu osadziwika koma opanda onangidwa.
Musapange bulemu anthu ogenda koma olakwa ndi awa president chakwera ndi nduna zake. Mukulu wa polisi ndi apolisi wose . Mukulu wa silikali ndi asilikali wose ndi amene akufuna kuononga malawi. Musapite ku osusa or anthu wamba . Chilipo chimene chakwera wachitapo mukulu wa silikali mukulu wa polisi pankhani ya zikwanje?
😅 kung'alula mosayang'ana nkhope
You are the ones guys fueling this chaos in the nation
Mtsukuluzi (Jona ) I always appreciate you when it comes to your turns cos mmayima pama facts okha okha😊 keep it up osadzaopa mayaz we always follow you bro
Jhona mpakoko khani ndiyoti athu akamakhazikisa chipani amakhara ndi athu awo chomwe ndingawuzeni ndarama 😮 Amalawi anakhazikika pandarama (kwambirili athu okamedwa kwambiri ndiwathu oti saziwa kudzisakira okha ndarama .thas is point
Unu a Hot current mulungu akusongolereni chilungamo mumachichita. Ku UTM a mai Kaliati amazitrnga ngati a wina koma amayibala kuti she doesn't qualify. She wanted to take an advantage of the death of our Chilima but we knew her very much. God help Kambambe to work and put together our beloved UTM
Vuto ndi mr chikangawa agwade achoke iyeyo ziko lamulephela. Ziko si church nyimbo ikhale ya nepman tikuweta mikango tikanali mujango. Iyeyo ndi ng'ona ndipo ationesa zilango 😢
Kodi akugenda usi ndi dpp ai ndi anthu omwe akudana ndi ulamuliro wa mcp not dpp sapota yomwe yagenda ai anthu akundilande okhala ku ndilande not dpp
It's good to talk openly and honestly
vuto achakwera ndinduna zawo akufuna athese democracy muno mumalawi ndichifukwa apolice akugwirisidwa ntchito mwamantha
wala dpp
Nkhani yose yangona kwa president kudzuzula woyanganila kwa sundwe
U keep fighting Usi, he asked to resign but the greedy ppo didn't want to dirt the party name, hoping kuti mwina they will be party president.
You just dont see but Usi is now campaigning for himself, you too focused on Usi
Well said komano pempho langa ndiloti chipani chomwe chili pa mpando chayenela kukhala chosogolera pokhazikisa bata cz zonsezi zikuchitika kaamba kolekelera now enawo akupanga ngati revenge, cz aboma akachita zinthu president kungokhalirapo now enewa sizikuwasangalasa nkani mkuona zipolowedzi zikuchitika solutions a chakwera ayambe atenga gawo ngati sogoleli wa dziko cz he's got all powers to do so kunako enawo will follow
Kkkkkkk eeee kupita athu akuli kupita kukwatangulaso kunkhuyu ndichisilu kwambili mafuta kulibe chakudya kulibe feterreas kulibe mcp isiyekupanga misongano arepera kare MC NRB mayi akukana kutula pasi udindo ndiye itiineyo zinkhondo imeneyo
Azimai onse otsatira a Manganya atabvala makaka a Utm ndi azimai a Kongiresi . Imeneyi ndi njira imodzi ya Kongiresi yofooketsera Utm ya a Kabambe .
Gwero la zikwanje ndi utsogoleri olekerera pomwe zinthu zikulakwika pomwe atsogogoleri olamula akulakwitsa,osakhala ndwi.
Zimenezo mumapangitsa ndinu a social media
Andevu zamwayi akuti kumowa timati bayala😂😂
You are not just inuyo A Brian
A wanda ndi a msukuluzi pamozi ndi mmedez ang'ono zng'onowaa
The chinseu Bridge is totally destroyed and worse will be destroyed with this coming of rains this season. Businesses are destroyed annually more especially the coffins done there. Politicians have been coming promising and leaving and bit even from the CDF has money been allocated to the reconstruction of this bridge and people got weary and tired of the Politicians who now wanna use this bridge as a campaign project yet they left it to be destroyed and allegedly kumkuyu came and wanted to make more empty promises and people got angry. Politicians should learn to develop things within their term than let things lot to then use those damages as campaign cards .people are wise now
Usi has a movement Odya zske slibe ml andu he will achieve his political ambition.
Kodi ukagenda utasiya ufa kulibe kunyumba, ukabwera umapeza nsima yitaphya? Apatseni ma loan osowa zochita awa.
Inu ndi amene mumayankhula zooona zokhazokha osa za achawezi ndi amzawo achina mvula ndi amzawo a MBC aja amangobakira mcp
Mabwana inuyo mumatiimilira kwambiri koma bvuto ndi boma lolamulirali zikwanje zakulilongwe chonde mutsindike kubomako ndi apolice adzigwira ntchito mosakondera panopa zawawa kwambiri kamba koti zachitikira abomawa zinakachitikira wotsutsawo sanakayipatsa moto choncho sibwino ayi
Chilima rest in peace Koma munayambisa nkhondo Malawi analiko bola uyu 2019
Pa timemeschimwendo zkakuuzani kuti taba pangani za past ife tikupanga za future muzifufuze
Chitetezo kulibe ku Malawi kuno anthu atipha ndithu
Chimwendo Banda ndi Zikhale Ng'oma ndi omwe amapereka ndalama kwa amphawi kuti azikakhapa anthu kumademo
Kaliati waluza angovomeleza anthu sanamvotele amanyanya kunyoza usi nde akhaula udindo amaufuna ndiwowo nde aluza angovomeleza anthu sanamvotele mpikisano amapezeka modzi owina yangokula ndi nsanje amaona ngati awine ndiiowo ndasangalala kuti aluza amadzimwa zedi usi munanyanya kumpanga chipongwe anthu oipa inu
Mabvuto awa adayamba ndi Andalucia one two amipingo mambungwe,media zodiack
Vuto lilipo ndiloti tili ndi presdent amene ali mbuzi za ma mbuzi boma la zisilu zikungonyenga,cikangawa nuyu wapeleka mimba ku 49,mcp ndi 0% cifukwa zimene zisilu zina zikuti cikangawa delivery sizace ndi za APM akuona ngati sitidziwa. A gwape amenewa a mcp 2025 akupita smart matc sigwila tcito angotaya nthawi.
Mkutha kuona kuti mcp is avoiding mademo by making up unnecessary programs ndipo it's not first time to do so komanso zonsezi akuchita ndi presdent chakwelayo cz alibe fundo zomanga he's the one behind all zipolowedzi cz sangapange ma program ake yeti akudziwa kuti pali ma demonstration
Zoonadi
Usi osadzamuphweketsa anaonera patali ku UTM panopa kulebe mgwirizano.
Andevu zamwayi mumakwana apolice asilikali pano onse ali ku mcp
Bwana vice president need to think about what he's doing
mukanadzudzula achitetezo osati achinyamata. kodi tilibe achitetezo?
Dzikoli kwachitika zinthu zitatu zimene president amayenera kutuluka ndi kuyankhula ku mrundu wa Amalawi.
President sanatuluke kuwtipanga update pa vuto la mafuta.
President sanatuluke kudzudzula zipolowe pa ndale.
President sakupereka update pa vuto la njala mdziko.
Pena kumazifunsa kuti kodi President sakuona, sakudziwa mavuto athu?
Chonde chonde Bambo Cakwera chonde chonde Bambo Muthalika bwerani poyera zuzulani chikhalidwe choyipa chomwé chikuchitikachi musafune udindo pogwiritsa ntchito nkhondo.pomwe upindula ndi inuyo,poyera zuzulani .Achinyama akaneni andale pa zinthi zopusa ngati zimenezi inuyo achinyama simusapindula nawo,samalani.
Nkhonya yobwezera koma kuwawa
Mumatiimilila guys pitilizani kuima pachilungamo
Chakwera ndi boma lake la Mcp akuziwa kuti alephereratu kuyendetsa dziko li nchifukwa chake akuopseza ndi zikwanje
Hatremwazala ndinu pa radio
Can you see what is happenning to UTM now?
Kkkkkk! Koma andebvu mumatha. KHAPALA ndiye amene akukolezera anyamata a MCP Kuti azipanga za upandu.
Akamangidwa ndinomwenu ndikukamwa kwanuko kuyamba kuyankhula mwamtudzu ndi Brian Banda wanu
ausi ndiosokoneza kodi akupanga izi chifukwa Ali ndi mphamvu za u vice president? Asaiwale kuti mphamvu zimatha ikubwela nthawi azatifuna opusafe
Usi he calculate already his future.
Kodi atolankhani awa walandira ndalama?Pena amandimvekera kuti kachiphuphu kamayendamo
Nkomwenkomwe ndife AMalawi opemphera sitiyenera kumapwetekana ndi miyala tokha ai.
I think zipolowe za ku ndirande sizikukhudza chipani chilichonse.
Don't blame any party
Is Hot Current a spokes agent UTM and other parties. The way i see you have become a partisan. Why you question USI on his actions? Like any politician you can not blame him or tell him to leave the party.
Dzikolo mtsogoleri ndi ogona kwambiri zosezo o Chakwera
ndipo alakwisa akanagenda bwino ndithu chifukwa anthu ena akapangako zabwino sathamangisidwa
ku ndirande kuno sikozapangila zachibwana zanu
😂😂😂😂 amapha ngombe
Jona kkkkkkk sazatheka samawopa 😂😂😂😂😂
Find good microphone, musamachite kumakuwa mumatibowola makutu, plus i feel like you losing your energy raising your voices. Find good and better microphones
Adawachita bwino kuwagenda mkumene cz MCP ikuziyambisa okha kumaenda mzikwanje ngati kuti alindiudindo uliose m'bomamu yet police is there.
Koma guys kkkkk ya utsi yo ndie yandiwaza
Kodi mau oti nkhondo akuchuluka bwanji mu utsogoleri wa a Chakwera ,pamenepo ndi pamene Pali vuto, mtsogoleri oipa mtima
😂😂😂😂 usi afunika kumuuza ndi chimbama
Where r the soldiers to protect the protesters
A Msiska zonsezi amalawiwa ndinuyo
The guy on the middle is too emotional and animated by the issues. It’s like watching a fully handsomely payed actor. Useless opinions.
Osatheka ku kutukwanani inu mumati imilira kwambir
Times is very biased. Ndevu, Johna and Chunga
UTM is divided
Ndirande ndi likulu la dziko lino more fireeeeee 😂😂😂😂
ndalama lopephapepha
Achakwera atule pansi udindo
Vuto ndi mayi yolamu ,pemphani Mai yolama asiye zopusazo
Kumalawi kulibe sogoleli owasogolela athu ngati asowa mafuta. Angakwanise kulelesandewu
Akulu akulu mumatiimilira ufuluwu tisazaudelere adzathu akukhalira kuthawira nthengo khondo alibe mtendele
More fire ndix
@Jona Kkkkk 😂😂😂 simanyengerera
Anyotedi bas
Anayambitsa ndi mwana wa ng'oma yemwe anayambitsa zikwanje
Kodi muti chani
Kkkkkkkkkk 😅😅😂 Dambisi
Khapara😂😂😂😂😂
Umphawi siwabwno ndthu
Vuto lilipo ndilotii chipolowe sichingathe kamba ka anthu omwe pena amabwela ngati omenyera ufulu pamene anthuwa ndiongoyambisa zipolowe chifukwa mabungwe omenyera ufulu agwirisa anthu andale. Zomwe zikuyambisa kuti tikusowekera chowonadi chomwe malawi akufuna paumodzi wanthu ngati malawi izi ndizomwe tikuvutika nazo popano omenyera ufulu amamema zipani zizipanga zioneselo pamene zipani zili ndimalo othesela mavuto awo kuli kunyumba yamalamulo osati kumema zipolowe anthu omwe akuyitanisa nkhondo ndi awo akunamizila ngati amabungwe amasowekera chani kusakumana ndi aboma bwaa tiyeni tizikonda dziko lathu chonde
Bodza ili timaona maiko ambiri ngat pena pake pakuvuta amalowa pa msewu
South Africa and other more achina melema timawaona akumema ndyedi zimachitika osat zomalepheletsa ma demo a president tikungoonela kwathu komweko
Muli booo azibambo inuu
Amtsukuluzi the way you cinduct your speaches sizikuthandiza amalawi mukuika lkwiya pa malzwi ndi inuyo ndinu anthu amenr lukusikoneza amalzwi
Anyamata okondeka inu
Kkkkkkkkk😂😂😂😂😂😂khapara
Dr he is in plan from confusions in UTM.i think akudikila kabambe awayankhule then he will start from there
Chitetezo palibe
Vuto apa ndi dyela pasi