Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
He is very wise Nep Man keep up osamangoulula zili zonse ayiii good boy 👍💯💪
EEh Nepman fans lets show love by liking my comment
Bro got me out here in the middle of the night laughing out loud😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
Uyuyu ndee ndi nzika🎉 yamu ndix😂
He was so happy to drink 😂
Anayamba ndi MolaloNepimani koma kumapeto wathelaka 2 akungoseka😂😂😂
Nnnakwerapo minibus ndi Nepman...good vibes and very generous...kufika mu Limbe anamuuza conductor keep change ndalama yambiri ndithu
DEFIA ndi vibes heavy ananganiza look sharp Hurd
Olo ili yobweredza tiyiwonelaso😂😂
I have watched TRUTH or DRINK koma iyi yokha 🤣🤣🤣 ipeze ma award 💪💪💪
Adha awa ndikatundu amwene😂😂😂😂😂
Watching from boksburg north SA 🇿🇦 nep watibuka heavy yooh koma amatha ❤
Truth or drink ndi more fire Nepman on the building
Been waiting for this episode
Km lero mowa wakumana nazo 😂😂😂 nep iweyo ndi shatta
Munayamba kupangira panja komaso masana kodi program iyi?
😂😂😂😂😂😂😅😊 Madala Nepman I ❤ it so much kkkkkkk
Fira defiya🔥⌛
Ichi ndi Chidakwa amwene
Nepia aseh 😂 et azikuwuza mageji kut kukhala ngat wasintha oil 😂😂😂😂😂🙌
😂😂😂😂 akuti amuna amapanga ngati chiongolero
Nepman is a gangster guys
Nepia wabweradi kudzamwa mowa uku😂😂😂😂
Reaaal Badman... He nah sell out
😂😂😂 zimene anabwelela ndizimenezo mpaseni shot 😂😂😂
Aaa ndie mwabisa zambiri especially pama game 😮😮😮
apa ndy atinamizadi Live
I miss truth or drink
Nepman umakwana Koma 😂😂😂 ati tachitani chokumwachi Fuso ndalephela ili
Much luv nep man,
Kd Mesa munaponya kare ichi?
Tipatsen wasalawo ndiwapulumtse abwanangawo 😂😂
😂😂😂 Finally Nepia loves all
Nepman umangondiwaza basi 🤣🤣🤣 zimandiwaza mmenenso umamkondera mfana KUNTA KINTE " Mtengano"
Kudya ntondo kunaphweka..ndipamene amazitenga chi self
😂😂uyuyu ndi dolo
Chinep ase akuti tathilani thilani mowa🤣🤣🤣😂😂😂😂
More edits than before
Mukupanga post kawiri bwanji,? 🤔
ÑÈP MÀÑ ✨🌟💥🔥🍺🍻🍻
Nep man ndi mundu wa.bho samazikwesatu
Again?
Komanso ka mtuuu! Ka kakubowesa bwanji 😂😂😂
Jaa kev waonjezadii😅😅😅
Ndimanyadira jah man 🎉🎉🎉🎉😂
nepman🤣🤣🤣
Kd big Truth or dirik inatha kd???????
Nepman wabwelela kuononga uyu😂😂😂😂
Ndix 😂😂 ife tiliphee
Awa ndiye angokumwerani mowa wanu! 😂
Nkhani ndiyachakumwa 😂😂😂😂
iweyo sukumwa nawo bwanji ,how can u invite a guest and watch them drink while u doing nothing ?
Eeeee akulu awa kukhosi kunapselelatu kkkkkk short imeneyi
Nep ndi vibe🤣🔥
Nepman Yu ndi Fana wAbho Samafuna zaudan
🎉😂
Amewo amayitha 😂😂😂😂😂
Adhawa amaseka eeh😂😂
Kumeneko ndiye kuthako😅😅😅😅
Udolo Balala hahaha
Awo nde saziyankha mafunsotu azingofuna mowawo bas
Nep man ndi galu ukongwa kkkkk
Eeee koma mowawu anauchaliratu boss wa
Anazolowela masese kumakutumula shot ngat mwasalila zitsenga
So you advertising Jameson for free...😱😱
Ndabwerera mashot basi😂😂😂😂
54:17 ziii😂
Interview iyiyi inakozedwa
Kachikena💰
Live from Randburg (South Africa)
Kkkkk nep atha kuphwanyisa budget ndithu🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Nepman ndi dolo koma mowa wathana nawo amamwama monthamangira nthawi
Mafuso ena koma mumafusa auchisiru mpaka ku chipinda nkhani yake ya ka mowa mwagulako ndiye Zibwana zimenezo
Ifeso ndi mr 65 65
Chikungomwa🤣🤣🤣🤣🤣🤣
Akut onseo ndimawafira kkkk
Nepia❤
Lights out😅
Koma ase ukumadula voice bwanji
😂😂😂😂Analenguka
😂😂😂😂
😂😂😂 koma ichi
Koma vuto wabisadi zambili ase aaaa usamatelo koma ukumalakwosa
Kukhotetsela pansi🤣🤣🤣
Mwachita bwino mwayipNganso upload iyi imkasowa
Tikuonera zobwereza apa
😂😂😂chitani
Kukhotetsa🤣🤣🤣
Ine mundiyitane zangomwa nawo mowa
😁😁😁 Nepman adha kkk
Uyu amatha kucheza
Ati zotapitsa🤣
Munthu wamau a original 😂
ndiye muco panga hide zina ndi zina why??
Mowa sinkaka 😂😂
Zotapitsa😂
kumeneko nde kuthako
A edit tooooo much!
Madala madala nep😂
Allan ngumuya bwaaa
Tathilaniii🤣🤣
Haha koma adha😅😅
He is very wise Nep Man keep up osamangoulula zili zonse ayiii good boy 👍💯💪
EEh Nepman fans lets show love by liking my comment
Bro got me out here in the middle of the night laughing out loud😂😂😂😂😂😂
😂😂😂😂😂
Uyuyu ndee ndi nzika🎉 yamu ndix😂
He was so happy to drink 😂
Anayamba ndi Molalo
Nepimani koma kumapeto wathelaka 2 akungoseka😂😂😂