Bakili muludzi ndi team yake,i just wanna say thank you so much for saving us we are born free because of you guys,anthu amayakhula za mbiri zokhuza ulamuliro wanu koma sakuziwa zomwe mwatichitila or kukumana nazo kuti mpaka multiparty ikhazikike.
Allah akbar.... I can feel his pain. Komanso mwapadeladela joab mafunso ako umafunsa momveka bwino not like zinazi.... Ineyo i dont mis cruz 5 kamba ka joab.... Mr BYSON K.. ALLAH salakwitsa ali ndicholinga ndimoyo wanu, I'll need to mit in person wen i vist malawi
Very powerful testimony,this is Grace 🙏🙏🙏 and this is the mercy of the Almighty.Glory Glory be to God .😭😭😭 Dear heavenly,may your mercy,grace, favour and your protection be to everyone who shout and wait upon your name.May your healing mercies locate everyone Lord.Above all may love lead in every one's heart,mind and soul 😭😭in the Mighty name of Jesus'Christ
Bakili muludzi ndi team yake,i just wanna say thank you so much for saving us we are born free because of you guys,anthu amayakhula za mbiri zokhuza ulamuliro wanu koma sakuziwa zomwe mwatichitila or kukumana nazo kuti mpaka multiparty ikhazikike.
True
It's true..vutotu anthu masiku ano sadziwa nkhondo inalipoyo
From this i have learnt that kufa ndi nthawi , ngati sinakwane umapulumukabe
moni kuchokera kuno ku Zambia
Chilichose chomwe chimachitika, chimachitika Mulungu akavomeleza,even nthawi itakwana Koma ngat Mulungu sanalole sizingachitike.....sinthawi yonse ili nthawi ya Mulungu,nayeso satana alipa ntchito yake....
Kuba
Kupha
Kuononga
God is so wonderful..zoona mchipululu si mofera zoona...inuyo u have to thank God...umboni mulinawo okwana..kumuyamika mulungu
Amen n amen 🙏
Allah akbar.... I can feel his pain. Komanso mwapadeladela joab mafunso ako umafunsa momveka bwino not like zinazi.... Ineyo i dont mis cruz 5 kamba ka joab.... Mr BYSON K.. ALLAH salakwitsa ali ndicholinga ndimoyo wanu, I'll need to mit in person wen i vist malawi
Joab, ku Zomba Maximum Prison sisewero. Ka 2 weeks kokha kanandikwana ku B Block.
MCP ayı zikomo sitinena zambiri zambiri aziwa ndimulungu watching from Mozambique live in 2024
Joab sopano... mene French yalowela apapa 🔥🔥🔥. I love this show
Joab you are the legend... you know how to handle your job.
Osati kupulumuka ponyongedwapo mwina inali mphamvu ya mitengo.
This is wonderful job Joab
Ndipo sure Mbuyanga anamwalira chabe koma nayeso akuti apumulumuka pa line coz of mitengo
😅😅
Amen amen ambuye ndiwabwino nthawi zonse
Dziko lapansiiii,😭😭😭😭😭😭
😭😭😭 dziko lino ndi loopya tizipenphera kwambiri
@@victoriawilson83 kobasi
This world is corrupt everywhere. It is very difficult to find honest people.
God lives
This guy must be compensated for being in prison and being found innocent after 24 years
The best program in Malawi
eeeish stories we deserve to know. Joab do more digging with such people
Mmmm m'chipululu simofele timangodusa ulendo wa ku kenani🙏🙏🙏
Eeeeh 😢😢😮. Koma ambuye
Eish corrupt judicial system. What was done to this man was evil and he needs to be compensated
😅🤣😆😅🤣😂akuti ndi mzungu simunthuyi....onyonga
KKKK ZONADI ASE ZUNGU SIMUTHU
@@fatsanipharaoh9588 simunthu how?why are they called by their race?
Mzungu si munthu
Chifundo ndi chisomo chaMulungu chilibe malile amakhala nafe munyengo zathu zonse
So why kamuzi day?😢😢😢😢😢
If this man was wrongly imprisoned for 24 years the state need to compensate him
Exactly
Just as Machipisa Munthali
Waiting part 2
Ambuye analowelelapo pamenepa ndithu eshiii long story
Very interesting waiting part 2
He is a good story teller! Blessed Jah rastafari!
When are having the next part bwana joab?
Ndili pao kudikila part 2 nkhani yabwino yopatsa chidwi
Please come with part 2
Wina nkumati boma ndilomweli 😳
Cruise 5 is the best program so far. keep the fire burning
Km Ndaseka ngat zosekesa koma mdalayu mene akuankhulila ashiii😂 aziona ndpo amajuli nda a mcp alibe nao mau🏃😂
When God says yes ,nobody can say no
When are we having part 2 frank?
THIS IS POWERFUL TESTIMONY
Kwambiri. It can only be God.
A life changing program
Mulungu alemekezeke kwambiri pachimenechi
Nkuluyi analowa mndende ndikuyamwa🤔🤔🤔🤔
Ayi tidikile part 2
Ukuyamwa Bola..ife zoti tizabadwa zisakuziwika
Ife kulibe amwene
Ine ndisanabadwe
A kaula mpaka mzungu simunthu😢
Thanks for removing the songs in the vedio
Nde wina aziti mulungu kulibe?
Ati " amene amanyongayo si munthu, anali nzungu " 😂😂😂😂
Very powerful testimony,this is Grace 🙏🙏🙏 and this is the mercy of the Almighty.Glory Glory be to God .😭😭😭 Dear heavenly,may your mercy,grace, favour and your protection be to everyone who shout and wait upon your name.May your healing mercies locate everyone Lord.Above all may love lead in every one's heart,mind and soul 😭😭in the Mighty name of Jesus'Christ
Jah over Everything 🙏
Looking forward to part 2.
Waiting for part 2
I enjoyed the interview the guy so confidence
Very touching
To God be the glory and honr..Amen
im happy that he is free now, but what about the compensation for wrongfully arrested?
Very interesting story
🥺🥺part 2 please Mr Chakhaza
Waiting for next Part
ine mpaka misozi sad story
Kamuzu, John Tembo n kazamira ndi asatana, ndiwo amaphetsa anthu with thy evil mind
Anthu ankaphana okha okha ndipo kamuzu sizikumikhudza apa..ndi chidani chamudzi ichi
Hhhm koma zokhuza 😭😭 sorry sorry madala
The world is very complicated in fact metaphysical that can not be understood fully
Pandisangalasa mpokhapo poti akazi alibe chilungamo ndizoona azimai eeeeeee Anthu okhomelela mwa nyooooo
This guy should write a book atleast please
God is good all the time 🙏
Wat about his Fam,after kumasulidwa
Amen
So sad
😭😭😭😭this is sad story ever.
Ati ndi nzungu si munthu😭😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Wonyonga munthu anali nzungu si munthutuu..
Mulungu ali nanu chochita, amen
ah personally may you live long and happy Mr Kaula
Nkhani yoliritsa
😢nkhani ku polisi imasintha
I wanna make a movie 🎬, true life store 😢😢😢
When God says nobody can say no
Very interesting
Amalawi munkapangana nkhaza nokha nokha apa osati kamuzu...chidani cha mudzi chamukhudza bwanji kamuzu
Cruise 5 💪💪👊👍👍
Kamuzu anali galu munthu osamuziwa mulungu
Mind blowing
Ndi mzungu simunthu
This life no balance, only God knows
God 🙏 is Able
I feel sorry for those who have been executed over false witness 😢🙄😩
it was very sad
Joab umatha hvy!
When is part 2?
😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
I wonder when John Tembo will die because he was the master mind of all those things.
True bro
God is good indeed
Who doesn't knows that Kamuzu was not Malawian? He was a Ghanaian
You sound stupid, Ghanaians don't know anything about kamuzu Banda
Joab you can speak French? Wow!!
sorry madhala, Kamuzu Banda anali galu kwabasi.
So sad ....MCP hmmmmmmmm😭😭😭😭😭😭😭😭
Kamuzu sizikukhudza apa, anthu ankapha okha okha
This story ne
He is wonder working God.
Ndimzungu, simunthu 😂😂
Ati akazi alibe chilungamo kkkk
Koma abale kunja kuno kuli mzunzo
😢
😭
this guy was wrongly convicted abale....i hope atatuluka analisumila boma mkumupange compasate....aaaaaaa😭😭😭
God of time
Eeeeesh 😢
Koma kamudzu Ku masayinila Kuti athu18 aphedwe thawi imodzi.for sure.that guy was not a Malawian.for
Kodi anthu inu mukudana ndi kamuzu Banda chifukwa chiani pomwe anthuwa ankapelekana okha okha