CRUISE 5 WITH SPY CHESA - THE SNAKE SELLER
Вставка
- Опубліковано 1 жов 2024
- Spy Chesa is a man in a unique trade - he catches and sells live snakes, crocodiles, and other creepy crawlies. He is also a professionally trained traditional doctor. Spy has been making a living out of entering jungles and catching the reptiles, occasionally being called to rescue communities when snakes go on the rampage. It is a lucractive but dangerous enterprise, on his left hand he has lost four fingers but the thumb to a crocodile. On his right only three fingers remain after 2 were amputated after a snake bite.
He is delighted that his business is growing and claims to have chalked a big one by 'helping two MPs win' the previous election through his charms. Watch this program to understand this mysterious man.
joab kod pano anakwatira ndisekuleni makutu abale mwayi ndiwomwewo atengeko mwakhwara koma umakwana aise 😅😅😅
The difference between Green water snake and a green Mamba
Ehe Spy uli apa ? Zabwino zonse m'bale koma zoti uziwanamiza anthu kuti ndiwe sing'anga mmmmmmmm sibwino, koma zoti umaweta njoka ndizoona ndipo ine ndi mboni kwathu kwa Mtuwakale, Lilongwe, Mbabzi TA Njewa. Guys munthu uyu si sing'anga koma njoka amazigulitsadi
Kkkkkkk
hi m'bale
😢😮
Joab ukamapanga zakozo uzilembera wiro usazasiye athu pa umasiye
Good job. This guy is very straight, Mumantha chingelezi akuti ndimayankhula broken english.Nice one!
Joab sunachenjere bho🤣🤣🤣🤣
Please please I just need him number oh wow
Uncle Joab mpaka billy kuyenda ndi Lupanga kkkkkkkkkkkkkkk
Eeeeeh i have been looking for this vedio
Kkkkkk nde nyimbo zonse za Billy basi mwasankhapo imeneyi kuti umakonda zinthu zoononga moyo wako koma siuzindikila.
Kkkk nchito iyi pomazafika pokhala ndi experience Mmm utaona zothimbilira2
Watched it today,Joab munatemaso nanu😂😂😂
4n number
Ndifuna number ya spy chesa
0999885606
Joab, nawenso ndiwe okhwimatu mpaka kugwira 🐍 😂😂😂😂
Kkkkk ayi jowab ukudziwapo zanjokayo kkkk eeeee mpaka mkhosi? Kkkk
Africans should stop looking down on themselves, ma africans zawo ndi zitsamba, no side effects.
Kapena mwina tizipalasa pasi🤣🤣🤣
This is not mamba
Ndiwe wachibwana kwambili
ayi zikomo, business yotha zala.
Ali ndi # yawo 😊😊
Chonde musaike moyo pa chiswe eeeeeee ndaopa bamboyiiii
I surrender man. But thanks ntolankhani. APA speechless
am frowning you here in Lusaka Zambia help me with line of this man plz
Ineso ndikufyna namba yamunthuyo please ndikufuna andithandize pavuto langa
He has a very unique bussines. Dare to be different! Dr Nyangazitheranji😂
joab umatisangalasa heavy ntchito yabhooo
The thing is that you have an experience in handling the snakes just like how our ancestors were able to handle the different animals eg chicken, dogs etc. the rest are the lies.
🤣🤣🤣
@@chifundompokosa1313 qfzzxxxcxxo
Dz7
p
@@chifundompokosa1313
Joab,Longosoka "Lucius Band"nde itiyo?
Nkulu wakumana naxo uyu
Dzala alibe
Komanso njoka inamulavulira mmaso
Eish
Ng'onaso inamuchita zoopsya
hahahah iwe anakonza Joab, malume ingotigailani nambala tione kuti tipanga bwanji tipezane kuseliku ,nafe tipeze yathu mamba
Lol Changu pa malo
Joab 😂😂😂😂😂 you have sufficient heart for us
Koma Joab! I am a snake around your neck are you sure? We will forget you sure! You are too much number 1 my brother kkkkk!
Grt joab
Amazingly frightening!
Ndikufunisisa number ya mkulu ameneyi chonde amene alinayo andigaileko chonde. Kwa amene alinayo number ya mkuluyu andiyimbile pa number iyi +2746090611. U can also watsapp me on the same number stated above.
inuso musamadalile zisamba iii ai ndithu tapepherani kwinako mukangotengako ziwanda bas
Broken English 😂😂😂🤣
Joab kkkkk zibwanatu ai we don't want to loose you bro you stand for us kkkkk nawe uwetatu
Nice one Joab hope nawenso akuchkkkkk mankhwala anjoka kkkkk
Ndufuna mankhwara otindipeze ng'ombezanga zidasowa Mu 2012
Songo is a Mozambican cobra and not the mythical statement the guy is saying.
Songo is a black mamba
Kkkkk uzipalasa pansi job usanduka njoka
One big one😅😅
Hahahahahaha Joab I thought you wouldn't carry that green snake. Spy Chesa is an interesting character.
ATR,,,zathu zomwe izi kkkkkkkk
I can love this experience
Koma bambo amenewa shaaaaaaaaaa
Ma MP azimvera okha😂😂😂😂😂
A Malawi anzanga Green Mamba katundu uja ali nkhosi🤣🤣🤣🤣👍
Hahaha koma spy
Mpili 🙈🙈🙈🙈🙈
Mmmmmmm komatu ana asamale pamudzipo.....njoka zimenezi ......
Koma job c aaaa
Joan yekha mafunso ake Amwene, 😂😂😂😂
koma makwelero atuluke mubotolomo kaaaa kkkkkkkkk
😂😂😂 some business has no choice to lost ur life
Umakonda zinthu zowononga moyo koma suzindikila 😂😂😂
Iwe spy chesa unipaseko nambala pa watsap.
Joab iweso ndi katundu kkkkkkk
Cruise 5 💪💪👊
Kkkkk Cruiser 5 ndimaikonda kwambiri, nanga2 zoti pali ulimi wa Njoka sitimaziwa...... koma Joab Ndiwe Opanda mantha
Job ndipatse number yake,,, kkkkllkkk aliposo oposa Joab Ku MMalaw???
email him at mrthaterry@gmail.com
Kkkkkk joab ndikudziwa kuti pochoka pamenepo watengako
Akuzipeleka yekha kwa police
Joan ndiolimba mtima
chibwana ichi iiiiiii kkkk
Joan umatha
Frank, sunachenjere bwino
kkkkkkkkkkkkkl koma ayayaya
Spy Chesa, umakonda zinthu zowononga moyo wako koma suzindikira
Kkkkkkkk
kkkkkk eish Dziko ndi anthu ake kkkkk
MAIWEEEEEEEEEEEEE!!!!!!!
Tathokoza moyowabwino aspay chesa tigawireniko maphon Number yanu
0999885606
@@joabfrankchakhaza thanks
Joab kkkkkkk umatha .
Joab nd dolo
joab ndiwe okhwima nawe usatipusitse
Mmmmmm koma paka kuweta njoka
One of my favorite cruise 5 shows ❤❤❤. Rip Chesa
Wamwalira ndi chani mkuluyu
Anamwalila kodi?
@@SamboRuphan eya anamwalira ,matenda ake sindikudziwa km anaibwereza program Yi on zodiak in remembering his life
Eeeeee matenda ake sindikudziwa km anaibwereza program Yi on zodiak in remembering of his life
Nawe ndiwe wokhwima Joab
Kkkkkk
ulimi wa njoka?
zibwanatu izi iwe Joab
.ukudabwa makwerero mubotoro iwe joab osamasewera ndi achewa
Mmm pa nkhan ya njokayi ndakayika sizitenga mtunda ayi azakumana ndi anzawo azawachesula koma akanati amagwila njokazi kupyolela maphunzilo basi ngat mmene amapangila azungu koma zogwilisa mankhwala achikukuda mmmm ndakayika
Abambowa ndi akatundu.
Kodi tingamupeze bwanji? Tizimuodetsako njoka
And ndikufuna kuima u MP
Tikuwafuna life atithandizeko makhwala
@@fapsonbanda2093 Mankhwala anji ndikipatse number?
Tipaseni # yawo
😲 😲 😲
Nyanga izo
Kkkkk zoopsa
Ndimadabwatu zalazi 🤣🤣🤣
Zintha zala zonse 😂😂
ulimi wanjoka 🤣🤣🤣
😂😂😂
One big one kkkkkk
Amazing job joab. From Zambia, much love for you
4 number tiziwe zambir
Chonde nambala kuyifuninsinsa
Komad
This looks like a boomslang, not poisonous.
This is awesome Joab .. purely Malawian and culturally.....
Kkkkkkkk koma yaaa katundu agawane
Joab. Ndi 1
Big up Joab! koma ndakomoka ndipwete amwene kugawa chumako kkkkkkkkkk! real stories