Limpopo mmh kwaipa anavula a Chilima lamba ndi ndani poti ndege singapange zimenezo Ntanyiwa uku

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 28 чер 2024

КОМЕНТАРІ • 121

  • @user-hx6ly3cl8m
    @user-hx6ly3cl8m 3 дні тому +11

    Munthu amene amadana ndilimpopo ameneyo ndifiti

  • @clairelewis5309
    @clairelewis5309 2 дні тому

    Comrade Ntanyiwa .God bless you,protect you,guide you and entire family.
    SKC soul im sure ukukuyanganilani Comrade ,and the entire Limpopo DJ's🙏🙏.
    Nkhanga zikungoyenela ziziona👀👀👀👁️.
    Uku tikusala kudya ndi kupemphela ,chilungamo chioneke ndithu.
    Limpopo 🎉🎉🎉🔥🔥🔥🔥🔥 moto kuti buu !!!!, 🔥🔥🔥

  • @ThokozaniSaiti
    @ThokozaniSaiti День тому +1

    Ndege munthu ndiyomwe inachita iziiiii
    Anthuwatu akuona ngati amalawi tikadali ntulo sakudziwa kuti tinachangamukaaa
    Muzionaa ndipo muyankha mafuso onsewa kwa amalawi and to the whole world Mfiti Chakwera

  • @StellaCharles-dq8db
    @StellaCharles-dq8db 2 дні тому +7

    Tikusatira mwachidwi ndinthu ndipo alimpopo mukat musatumize uthenga ndinadandaula kobas andi bon kalindoso ulemu wanu pitizan kuima pachilungamo mulungu alinanu nonse mudzina layesu mulungu wamoyo

  • @RenaChikupila
    @RenaChikupila 2 дні тому

    Dzoooona osamalimbana nawo inu pangani ubwedzi ndmlungu osati munthu odzuza thupi ndyesu yekha oteteza lnuyo antanyiwa❤❤❤❤

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 2 дні тому +3

    The best fm ,,, listening from Botswana I can't wait ❤❤❤❤

  • @user-sh5wq4uf6r
    @user-sh5wq4uf6r 3 дні тому +3

    Ntanyiwa komaso bakili muluzi these guys i salute 💪

    • @FisherAction
      @FisherAction 2 дні тому

      Mulungu akukuteni kut onyansa mtima awa osowa umunthuwa

    • @FisherAction
      @FisherAction 2 дні тому

      Asamakufikireni komano big tawakumbuseni a DPP Asiya uchetewawu adzuke

  • @eunicesaiti
    @eunicesaiti 3 дні тому +3

    Limpopo following 🙏
    SKC and others who died Rest in Eternal Peace 😢😢😢

  • @PatrickMailos
    @PatrickMailos 3 дні тому +6

    My best ❤ Limpopo FM radio

  • @user-tm3zh5zk4t
    @user-tm3zh5zk4t 2 дні тому +1

    Iwe ulingati m,zimayi mabodza umangoduladula nkhani osayimaliza kuchita kudziwika kuti ndiwe wamabodza iwendiwe galu wachabechabe nakutuluka

  • @user-zj1xx1ic2m
    @user-zj1xx1ic2m 3 дні тому

    Listening from cosmo city, just here malibongwe drive south Africa ❤❤❤❤❤🎉🎉🎉🎉🎉 Comrade!!! tili limodzi apa✅✅✅🇲🇼💪💯

  • @HappyAbyssinianCat-xt2bm
    @HappyAbyssinianCat-xt2bm 2 дні тому +1

    Inuyo ndi one ndpo sindmafuna pazidusa one hour tisanakumven mau nice big man

  • @augustMag
    @augustMag 2 дні тому

    The best Limpopo FM radio station is the one 🔥🔥🔥🔥

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 3 дні тому +2

    RIP SKC, kodi nanga anthu 8 enawo imfa zawo zinali zotani? Pamenepa sipakumalongosoredwa
    Mukhale ndi moyo wautali comrade ntanyiwa anthuwo angodana nanu akusowa zochita chifukwa mumanena chilungamo

    • @GiftPhiri-tt7nn
      @GiftPhiri-tt7nn 2 дні тому

      Ngati chilima anaphedwa ndiye kut onse anaphedwa , kaya ndingozi ndiye kut onse ngozi eeeeetu

  • @user-ml8lk9dr7t
    @user-ml8lk9dr7t 2 дні тому

    The problem is that ayesetsa kuti akuchiteni chipongwe koma alephera anthuwa Comrade ndiye nzeru zatha

  • @SaulosMbuna
    @SaulosMbuna 3 дні тому +2

    A Ntanyiwa chifuwa SI chipha osatekeseka..imwani madzi ochuluka

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 2 дні тому +1

    Pheee,pano pa limpopo ndi comrade mtanyiwa

  • @davidjames679
    @davidjames679 2 дні тому

    limpopo fm ft bakili muluzi tv 🔥🔥🔥🔥

  • @user-dy5bj9ck5e
    @user-dy5bj9ck5e 2 дні тому +1

    Congratulation Mr mtanyiwa gp🎉❤❤❤

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +2

    Masowela aaah yoooo timbwela from Zambia

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +3

    I can't believe it that our brother is gone just like that No No

  • @stanleychisasa4343
    @stanleychisasa4343 3 дні тому +3

    Chairman ndinga pange bwanji ndizikutumizilani khani

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +3

    Were in Zambia but our hearts our bleeding

  • @user-zj1xx1ic2m
    @user-zj1xx1ic2m 3 дні тому

    Ndiponso chigwada chake chimakhala chosinja kale😂😂😂 Mr ntanyiwa mumayidziwanso Randburg????😂😂 I love u Mr mumakwana Enawa ndi Ana awa❤❤❤🎉🎉🎉

  • @TawongaGSMwale-cc2vm
    @TawongaGSMwale-cc2vm 3 дні тому +1

    Thanks for your update Big Baba

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj 2 дні тому

    Congratulation mr mtanyiwa❤❤❤

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 3 дні тому +2

    Ntanyiwa katundu owopsa zedi ❤❤❤❤❤❤❤❤❤

  • @ClementbWatches
    @ClementbWatches 3 дні тому +8

    Iweyo Ntanyiwa ndi number one ndipo ndimamva nawe kukoma zed. Ndipo timamva zenizeni

  • @tlhalosozindlani4544
    @tlhalosozindlani4544 3 дні тому +2

    Hehehehehe yomweyo galu iwe awuzeneni amvese comred ntanyiwa

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 2 дні тому +1

    Akutimenyera nkhondo anyamata awa amphawife😭😭😭😭😭😭😭

  • @user-qb2lt6qj1p
    @user-qb2lt6qj1p 2 дні тому

    Oyenela kupepesedwa ndi akubanja km chakwela anapepesa ndi 5milioni ndizovesa chison kt chakwela akugawa ndalama kwa anthu omwe malilo sakuwakhuza tichedwepo pamenepa

  • @user-ir2yz5zz5x
    @user-ir2yz5zz5x 2 дні тому

    Chobisika chili chose timavera kuchokera kwa limpopo FM kuchokera kwa khomuredi Ntanyiwa mumati vesa kukoma kwambili ndpo timaku pephelerani kwambili ndpo oyipayo sangaku kwaniseni kt akupangeni chipogwe ndpo mulungu apitilize kukutetezani mix born kalindo mulungu apitilize kukusungani ndimoyo wautari pa libe radio iliyose yomwe ingatiuze zoona zokha zokha ndi limpopo yokha bas mulungu apitilize kukumenyerani khondo nose

  • @JelemayaMagugu
    @JelemayaMagugu 3 дні тому +2

    Bwana timakukondani ndipo timakunyadirani chifukwa mumatidziwitsa chirichose

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 20 годин тому

    Kkkkkkkkkk koma ntanyiwa kkkkkk usandisekese apa ....redson munlo mutu wake siumagwila olo mpang,ono pomwe ......anamangisa ukwati mamawa pofika madzulo ukwati watha ..naperi seventh day kunaperi ku blantyre ......redson munlo ndi chisilu cha munthu

  • @WitnessMaulidi
    @WitnessMaulidi 2 дні тому

    TAnyiwa we are defending Malawi

  • @alicehananiya
    @alicehananiya 3 дні тому +1

    Listening 🎧 from springs

  • @REXCHARLESKAJAWO
    @REXCHARLESKAJAWO 2 дні тому

    Kkkkkkkkkkkk yochita zonsezi ndege yomweyo? 😂😂😂😂❤❤🇲🇼🇲🇼🇲🇼

  • @Marymahendra
    @Marymahendra 2 дні тому

    That’s true Vs president he was going for funeral with suit and tie now he body is nicked so how take out his clothes is look like something that does happen, am very sorry what happened to him and died like thief and Chikwara he is proud like nothing happened

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda 3 дні тому +1

    Ma demo akanapanga pa 20 coz ana pa 10 akhalabe akulemba mayeso

  • @IssahAluba
    @IssahAluba 3 дні тому +2

    Limpopo FM 💪💪

  • @ChisomoChalera
    @ChisomoChalera 3 дні тому +2

    Timakunyadirani alimpopo fm

  • @josephkuseke4166
    @josephkuseke4166 День тому

    Ku Randburg ndinapezako mbewa ndi ngumbi

  • @user-fh1nc3kf2r
    @user-fh1nc3kf2r 2 дні тому

    Limpopo ndi namber one

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 2 дні тому

    Akufuna ma vote a chakwela kuti mafumuwo akalimbikitse anthu awo akati tiyeni timvotele MCP

  • @MathpeterLemon-ls1ns
    @MathpeterLemon-ls1ns День тому

    Kodi photo ya a chilima yogwira kolona alipo angandionese?

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 3 дні тому

    NTANYIWA MBAMBANDE , KOMA VUTO NDI ROTI MAFUMU NDI ANTHU ADYERA KOMASO MA BISHOP MITUYAO SIGWIRA NTCHITO, NDIPO MAFUMUWA AKUFUNIKA KUWAGWIRA PAKHOSI KOMASO MA BISHOP NDI ANTHU OTI SANGATHANDIZE DZIKO CHIFUKWA MWAIWO U MULUNGU MULIBE MWSIO MEADZAZA NDI DYERA MALO MIYANG'ANA DZIKO MOMWE LIKUYENDERA NAONSO.TIWAPANGIRA MADEMO NGATI SAKUDZIWA ASATIONONGERE DZIKO CHIFUKWA CHADYERS LAO IYAAAAAA

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 19 годин тому

    Koditu pagulupa pali zisilu zina zadya ndalama zokukuba ndiye asowa choyankhula ......mukuteteza anthu oti akukuzunzuni kodi ndalama akukupaanizo akupasani kangati .....chakwera akuchoka pavute pasavute ngati akakamire mmalawi muno mukhala nkhondo ya nyooooo .... Chakwera kumwela sazapita komanso kumpoto

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke 2 дні тому

    Eeeeee imfa iyi ikupweteka ukailingalira, Ambuye kumwambako mumadziwa zonse😢😢

  • @MabvutoMichaelPanagona
    @MabvutoMichaelPanagona 2 дні тому

    Inetu ndi mathokoza kwambiri a Limpopo FM ndipo ndadziwa ndale chifukwa cha Limpopo FM pitirizani kutipatsira nkhani zonse mulungu adzikudalitsani bambo muthwanyiwa

  • @Jaydee-mw4
    @Jaydee-mw4 3 дні тому +1

    Yes anawavula ndani?? Poti ndege ilibe manja 😅

  • @boldmovesafrica4551
    @boldmovesafrica4551 День тому

    Hand mistake sorry I want to press like ❤😂

  • @RhaudanRhaviwa-i8b
    @RhaudanRhaviwa-i8b 3 дні тому

    Nthanyiwa umakwana timakunyadila MCP ndiyamagazi mmaja kuyambira kale

  • @JOHNMPEMBA-p3i
    @JOHNMPEMBA-p3i День тому

    I ❤ Limpompo fm

  • @JonathanZiba
    @JonathanZiba 3 дні тому +1

    Ndikangolowa pa UA-cam choyambilila ndi mafuna ndi mvele Limpopo fm koma ka melody mumaikaka kamatalika kwambiri musanayambe kulankhula ofcourse ndika bwino koma kasamatalike kwambiri nthawi Zina timakhala tili pachangu nde kamatipangisa kuti tisamalize kuvela

  • @user-ml8lk9dr7t
    @user-ml8lk9dr7t 2 дні тому

    We are not young GOD is watching

  • @AudettaYohanie-fl3oc
    @AudettaYohanie-fl3oc 2 дні тому

    God pleasease,, protect ntanyiwa Abeg 🙏

  • @user-ui4ux5kc8d
    @user-ui4ux5kc8d 3 дні тому

    Bwana Mtanyiwa gwirani ntchito Basi osalimbana ndizinazi zikuiwalitsani zochita

  • @lawrencemalinda603
    @lawrencemalinda603 15 годин тому

    We salute you

  • @Jasper-xk9iv
    @Jasper-xk9iv 3 дні тому +1

    Limpopo to the world 🌍

  • @user-yi2fg1lh8x
    @user-yi2fg1lh8x 3 дні тому +1

    Listening from randburg..

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 3 дні тому

    Koma nde Apengedi misala mwinanso anachita kuyitanidwa kuti atsekedwe pakamwa nkona adzibusa Mafumu ndi ena azipembezo zosiyana siyana akukhala phe kumangoyang, anila dziko likungowonongeka chifukwa chodya chibanzi Mulungu akulangeni nonse amene mukungolandila ndalama koma chilungamo mukuchidziwa
    Koma nde okapanga kidnap wo adzafera konkotu

  • @EllinaBitto
    @EllinaBitto 2 дні тому

    Mzimu wa Chilima itipatsanso hope ina mayooooooo ine A Chilimaaaaa😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @DoreenEmmanuelj
    @DoreenEmmanuelj 2 дні тому

    Missing dear ❤

  • @Robertmkango
    @Robertmkango 3 дні тому +1

    Limpopo tiziwiseni munthu ama munkhapa chilimayo timuziwe

  • @MuhammadBAKILI-kl2mj
    @MuhammadBAKILI-kl2mj День тому

    Mbambande Limpopo

  • @FocusMind-nj8gy
    @FocusMind-nj8gy День тому

    More fire

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x 3 дні тому +2

    Uyu ndi machine owopsa zedi Ntanyiwa❤❤❤❤❤❤❤

  • @BlessingsKalonga
    @BlessingsKalonga День тому

    Limpopo ndekuti chani

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +1

    Demonstrations a kulu timbwela better there tell us🌟 the 😭 truth why there killed our brother

  • @ZaccheousPetrol
    @ZaccheousPetrol 2 дні тому

    Khumbo la apolisi anthu komanso a army, ma doctors,amphuzitsi....its just better life not to be rich

  • @JhdaLifi-vu9sd
    @JhdaLifi-vu9sd 3 дні тому +2

    A chair man

  • @MwasamboMwasambo
    @MwasamboMwasambo День тому

    Nkhani zodabwitsatuu iziiii

  • @raphaelfanuel4608
    @raphaelfanuel4608 3 дні тому

    Ntanyiwa sing'anga amuka drip yamadzi atapita kukathamangitsa mizimu mwaterooo😂😂😂😂

  • @NdazionaSasu
    @NdazionaSasu 2 дні тому

    Mbambande mtanyiwa❤

  • @user-hg2cw1om1p
    @user-hg2cw1om1p 3 дні тому +1

    Limpopo FM❤❤

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 2 дні тому

    Mmalo mokonza zinthu mudziko muno kuti zikhale bwino, akuganiza zomapanga kidnap ana athu, sizikukumvesani chisoni mukamaganiza zausatana zanuzi👺👹👿 ?, conscious guilty sikumakupezani mukamaganiza zausatana zanuzi asatana inuu👺👹👿?, pam.... panu

  • @Jamesmwale-iz4ri
    @Jamesmwale-iz4ri 2 дні тому

    Tikutsatila mwachidwi

  • @SmileMalanda
    @SmileMalanda 3 дні тому +1

    Ndipo inuyo munasowa😂😂😂😂

  • @chippakaribafox2865
    @chippakaribafox2865 2 дні тому

    Ndege inatengaso ma phone

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +1

    This is sad for sure

  • @AbdulChitundu
    @AbdulChitundu 2 дні тому

    Mumakwana inuyo big

  • @BlessingsKalonga
    @BlessingsKalonga День тому

    Tiuzeni inuyo munali mundegemo mukutifusaso ife

  • @BenardMwale-cp7sy
    @BenardMwale-cp7sy 2 дні тому

    Following ine zanga phee mix lawyer ndilibe kkkkkk

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +1

    We can't 10 July come one come all their see

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo 2 дні тому

    Kkkkkkkk ndiwe galu kwambili eti

  • @MaryChihana-y4b
    @MaryChihana-y4b День тому

    Koma ndiye anthu awa

  • @Mamahashim-xw2bg
    @Mamahashim-xw2bg 3 дні тому +1

    Ndipo mulungu azikudalisani

  • @user-lp7vd6nj9z
    @user-lp7vd6nj9z 3 дні тому +1

    Kkkkkkkkkkk koma zidyamula nandolo

  • @user-no2sn1fo1h
    @user-no2sn1fo1h 2 дні тому +1

    Rip our vp

  • @NizigiyimanaChantal-c2p
    @NizigiyimanaChantal-c2p 3 дні тому

    Apatsa Ambuyache mafiti opephera km mulungu awayendele

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 дні тому

    Chimene akufunira kuti apange kidnap ana athu mchiyani?, ana alakwa chiyani?, even omenyera ufulu athu a genuine mmalawi muno alakwa chiyani?, tiwonensanaa ,

  • @user-mw3kj4qz7b
    @user-mw3kj4qz7b 3 дні тому +2

    Tizapindula

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 2 дні тому

    Limpopo mumakwana from Cape Town

  • @InnocentMasuli
    @InnocentMasuli 3 дні тому +1

    Umatha ase

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 3 дні тому

    Ayelekeze kupanga kidnap anawo awone zomwe zichitike mmanyumba mwawo asatana amenewa 👺👹👿☻

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 2 дні тому

    Koma Limpopo ikubwera boh

  • @PatriciaMbewe-xn7ke
    @PatriciaMbewe-xn7ke 2 дні тому

    Our last hope Limpopo fm

  • @hamiltonsolomon3756
    @hamiltonsolomon3756 3 дні тому +1

    More Fire Limpopo FM.....More Fire ....This is very sad 😢😢😢

  • @user-cq3kb7ii8h
    @user-cq3kb7ii8h 3 дні тому

    Ndipo tisaladi kudyako chilungamo chioneke basi

  • @user-sv2vc7ie2m
    @user-sv2vc7ie2m 2 дні тому

    🙏🙏🙏🙏