SILIKALI KUWULULA ZA IFA YA ACHILIMA 😭😭🙏

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 30 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 27

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 2 місяці тому

    Chakwera😷🤧🤮

  • @KenChitete-pg3ws
    @KenChitete-pg3ws 2 місяці тому

    Izi ndidzoona,, my question is mr saulo chilima anapedzeka atavulidwa malaya,,kodi zinatheka bwanji kuti atchosedwe malaya???? Funso langa kwa chakwela,,,, kodi chifukwa chiyani mundege munalibe wa MCP????

  • @DevisonHala
    @DevisonHala 2 місяці тому

    Asilikali ine ndifuse inu mudalowa ndale olo ndinu chitetezo chadziko?izi zidachitika mzoipa kwambiri ifa yachilima

  • @AlfredJohn-j5r
    @AlfredJohn-j5r 3 місяці тому +1

    Malume polani moto ndi mabodza anuwo

  • @Martha-m6e
    @Martha-m6e 3 місяці тому +1

    Akuliva kuwawadi

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 3 місяці тому +1

    Koma zovuta kwambili

  • @3FinerDachudua
    @3FinerDachudua 2 місяці тому

    Amwene limbani mtima bs maka poima pachilungamo ngt chimenecho bs

  • @0wenNkhambule
    @0wenNkhambule 3 місяці тому +1

    Chakwela you mast go watinyasa ndi Galu

  • @DanielZitande-y1d
    @DanielZitande-y1d 3 місяці тому

    Mulungu ajutetedzeleni bro ndipo musawope a kupha tuphi koma mdzinu ukadali

  • @CollingsChilongosloben
    @CollingsChilongosloben  3 місяці тому +1

    😢😢😢muwuse mutendele

  • @JorgeSacuate
    @JorgeSacuate 2 місяці тому

    Am writing when misizi ikugwa maso pongomaliza kuvera audio iyi.

  • @JorgeSacuate
    @JorgeSacuate 2 місяці тому

    Bwana inu ngakhale akupheni komamano ngati athu amakumana Chilimayo ndi inawo mukakumana nawo. Malawi kulira sikuzawathera.

  • @MagretMvula
    @MagretMvula 2 місяці тому

    Zikomo bamboo mulungu akhall e nanu uyu chakwela amangike watipweteka

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 3 місяці тому

    Dziko lamalawi panopa likudana ndi anthu achikungamo tinanvesedwa kuti nsilikali ameneyu anamwaliraso ,may his soul rest in peace

  • @innocentchanguya5080
    @innocentchanguya5080 3 місяці тому

    Chakwera watiphela munthu ofunika

  • @languitoneelias9972
    @languitoneelias9972 3 місяці тому

    Inu zoti galimoto,ndege,sitima imakhala ndi gauge konanso ndege ya asitikali angapange clini ndi ndani?

  • @MveraNambala
    @MveraNambala 3 місяці тому

    Mmmm Malawi why Malawi rest in peace avice president nd other people

  • @PatrequeBenjamimMalapo
    @PatrequeBenjamimMalapo 2 місяці тому

    Komaso uyu ndi ndani akutukanaui ?

  • @Fanzo-h2l
    @Fanzo-h2l 3 місяці тому

    Anasemphanitsa mawaya kuti gage izioneka ngativmuli mafuta ana anjoka awa wokhala muudzu ukamadutsa ndi kumakusekelera mfiti idzafanso komatu asaiwale kuti chikumbumtima chinapha njovu itaponda mazira a timba iwonso afenso ndi chikumbumtima

  • @Peter-r9r
    @Peter-r9r 2 місяці тому

    Waing, alura

  • @AufiThera
    @AufiThera 2 місяці тому

    Eheee

  • @AMOSSMBOBO
    @AMOSSMBOBO 2 місяці тому

    Continues ok 🎉🎉

  • @JackMvura-ik2td
    @JackMvura-ik2td 3 місяці тому

    Nyapala opita ku school mpaka kukadziwa za dege iwe pita kabweze phone kobambo wako ulankhulazo zugwirizana ndiumwana wako size yako imva zautsiruzi