Це відео не доступне.
Перепрошуємо.

NDINKAKUUZANI KUTI UYU MUSAMUVOTERE

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 чер 2024
  • NDINKAKUUZANI KUTI UYU MUSAMUVOTERE

КОМЕНТАРІ • 224

  • @user-oc6xd4tv9l
    @user-oc6xd4tv9l Місяць тому +10

    Kkkk koma ndiye wasindikatu 😂😂😂 akuti wakuba uyu chilungamo kuwawa umakwana iweyo 🎉

  • @StevenMjMbama
    @StevenMjMbama Місяць тому +12

    More fire bro iweee Nde wabwela

  • @user-hs2dw7ly2c
    @user-hs2dw7ly2c 3 дні тому +1

    President wa mwazi

  • @PRECIOUSMKUTE
    @PRECIOUSMKUTE 9 днів тому +1

    Koma gayez mwamasuka😂😂😂😂

  • @papelariareis.e.
    @papelariareis.e. 22 години тому

    Ameneyi ndiye mumupha liti bwana??? 😂😂😂🎉🎉🎉 respect

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w Місяць тому +14

    Akuchoka kale uyooo! Sitinaone President wa bodza ngati uyu.

  • @user-kb7gw3tu7r
    @user-kb7gw3tu7r 12 днів тому +1

    Tsono pamenepa NDI pa chisuweni kapena chiyani 😂😂😂😂

  • @user-gs7wc3nx3q
    @user-gs7wc3nx3q 20 днів тому +1

    😂😂😂😂😂 tamumenyeko bakera kumagirasi kwakeukomwina angaveko ndeno mwati kuchipatara kuribe makhwara nanga anthu amene akumwa makhwera deyire akupanga bwanji sakufa

  • @giftmakoyo1441
    @giftmakoyo1441 20 днів тому +2

    😂😂 anthu amafika potopa😂

  • @webstermbewe8395
    @webstermbewe8395 Місяць тому +4

    Adad yes warns us in 2018
    "If not careful will be hold hostage"

  • @SoldierWilison
    @SoldierWilison Місяць тому +2

    Ada inuyo klkkkk chakwela waonjedza ndigaluso wachabechabe😂😂😂😂😂

  • @user-lu8px7td6p
    @user-lu8px7td6p Місяць тому +3

    Chakwera ndi mbuzi ya munthu paribe chamzeru chimene wachita uyu ndi mfiti. Yasatanic God for bit

  • @user-gp2zp2dj1w
    @user-gp2zp2dj1w 21 день тому +1

    Uyuu atimaliza mfit yachabe chabe

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo Місяць тому +4

    Kkkkkkkkkkk ife tili ndi mapwiya basi osati ameneyu mmmmm nyeeee

  • @user-uy8uk7so9d
    @user-uy8uk7so9d 10 днів тому +1

    Kkķkk koma Anthu mwakwiya

  • @MussaJohn-gt8ep
    @MussaJohn-gt8ep Місяць тому +3

    kuyangula vv. big up bredda man

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Місяць тому +7

    Tamumenye bagela yapakamwa achoke mano kkkkkk

    • @SamKaposa-i5c
      @SamKaposa-i5c Місяць тому +1

      😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

    • @ulemujumbe8501
      @ulemujumbe8501 Місяць тому

      😂😂😂 phwasula pakameapo pakhe mwazi

  • @user-pj3qi7gb3s
    @user-pj3qi7gb3s Місяць тому +10

    Kkkk uyu ndiye wang'akula ❤ more fire

  • @jameschibisa1433
    @jameschibisa1433 Місяць тому +2

    😂😂😂😂😂 ng'alulani kuyankhula kuyankhula

  • @chrisschikozera7271
    @chrisschikozera7271 Місяць тому +2

    Muthu oipa uyu ....kwambiri akufuna tonse kutimagilira pachigwe tonsr ndipo mavuto

  • @user-mf7hf7we2u
    @user-mf7hf7we2u Місяць тому +2

    Ukunama iwe

  • @user-mw8dq4is6k
    @user-mw8dq4is6k Місяць тому +1

    😂😂😂😂😂Mazingazime Chakwera akutionesadi galu ameneyu

  • @Eric-gb9ms
    @Eric-gb9ms Місяць тому +3

    😂😂😂😂😂😂😂 Koma adawa nawonso muli bho big

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 12 днів тому

    Akuchoka galu ameneyu machende ake chakwela mbuzi ya munthu mbava chakwela machende Ake

  • @HassanSinoya-wl3vl
    @HassanSinoya-wl3vl Місяць тому +1

    Ndimomwemo bg man 😂😂😂😂ndichisilu chachabe chabe

  • @user-zt7hy5lh4r
    @user-zt7hy5lh4r Місяць тому +1

    😂😂😂😂 Mazinga zime😅😅😅😅😅😅 ationesadi 😂😂😂😂😂kuchoka kwa Bakili Maluzi😅😅😅😅😅

  • @user-xz3nz7dy1f
    @user-xz3nz7dy1f Місяць тому +1

    Kkkkkkk koma guys mwatha mstha eti😂😂

  • @StevoZimba
    @StevoZimba Місяць тому

    Iwe ndi pangolin wa malawi 🇲🇼

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Місяць тому +2

    😂😂😂😂😂😂😂, muwuze aise ubwino wake ulinaye pafupi pomwepo

  • @ManuelMavuto
    @ManuelMavuto 2 дні тому

    Ndizowonadi kape wakubadi ameneyod

  • @user-sk3ld2ss7s
    @user-sk3ld2ss7s Місяць тому

    Malume, kameteni tsitsilo. Mumafuna prezident otani?

  • @Musa1828-l5d
    @Musa1828-l5d Місяць тому +3

    President wakhaza uyu koma vuto dziko lathu kunachuluka zitsiru

  • @Merinala-t6h
    @Merinala-t6h 19 днів тому

    Ndiwe walesi Kara ndiwe pa muphando

  • @khoviwaedward
    @khoviwaedward Місяць тому +2

    Aaaah tampase pama, ayise

  • @Costance-nf7ue
    @Costance-nf7ue Місяць тому

    President uyuyu ndi galu

  • @user-eh1mg3ww6d
    @user-eh1mg3ww6d Місяць тому

    Ngalu chakwela wachabe chabe wakupha kupha ndi kuononga satana wachabe chabe

  • @officialturfrican_ent
    @officialturfrican_ent Місяць тому +1

    Tizinthu ting'ono ting'ono ndi manganya pliz 😢

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 Місяць тому

    Koma mcp siikwanisa kupha anthu omuukila achuluka kkkkk

  • @JosephyMbizi-k1w
    @JosephyMbizi-k1w 28 днів тому

    mau mau amenewo

  • @esthergweje4038
    @esthergweje4038 Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂 well done bravoooo

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Місяць тому

    Palibe President chisiru ngati ameneyo kwake kuba ndikuononga achoke 😂😂😂

  • @JTUPHIRI
    @JTUPHIRI Місяць тому +1

    Ati Thomasi Chibade anayimba kale ati "chinamuona chakuda.

  • @KingsleyJika
    @KingsleyJika Місяць тому

    Nde mwati myimbo ya chakuda anayimba ndi chibade😂 😂 ndakumvani big

  • @Amina786Wayson
    @Amina786Wayson Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂 koma ndee seka more 🔥

  • @user-ol1hf7ru1v
    @user-ol1hf7ru1v Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂😂 koma timva zinthu chaka chino, auze chitukuko cha chakwera ndikupha ndikumanga

  • @user-uc1pd1tc2x
    @user-uc1pd1tc2x Місяць тому +1

    Waitha big ndipo tachipatsenso chimbama Kumaso kwakeko

  • @PeterMaulana-qk5uq
    @PeterMaulana-qk5uq Місяць тому +1

    Chakwela ndi Satana waononga dziko lathu

  • @user-ri8em6my2e
    @user-ri8em6my2e Місяць тому

    Mbava yoopsa CHAKWERA ndipo sitingachivotere coz adzatilipsira moopsa tikuwona kuchedwa kuvota azipita akalowe kundende basi

  • @VictorNyasulu
    @VictorNyasulu Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂😂 zisilu ziliko koma zimanena chilungamo chisiru choyimira amalawi umakwsna kkkkkkk

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy 24 дні тому

    Kkkkl 😂😂😂😂Ineyo ❤❤

  • @OmegaMussa
    @OmegaMussa Місяць тому +2

    Shakwela phatumopake

  • @blessbless6929
    @blessbless6929 Місяць тому

    Ndiye mwati sanamumangebe mkuluyu? 😂😂😂😂😂😂😂 ukaponyedwa kung'onatu

  • @GeorgeKACHULU
    @GeorgeKACHULU 3 дні тому

    Mumatha man kkkkkkkk

  • @NumbDee
    @NumbDee Місяць тому

    Useless president ever

  • @MaggieMuhone-r7m
    @MaggieMuhone-r7m 28 днів тому

    Kkkkkkk Kkkkkkk Kkkkkkk ndakomoka

  • @user-uk3bz1hr5t
    @user-uk3bz1hr5t Місяць тому

    Ing'alure.iweyo 😅😂😂

  • @shepherdkingston
    @shepherdkingston Місяць тому

    Umakwana galu chakwela

  • @user-hh4wn4vf9e
    @user-hh4wn4vf9e Місяць тому

    😂😂😂 koma ndaseka lne 😅😅

  • @user-gk6bf7xe9g
    @user-gk6bf7xe9g Місяць тому

    TV yanj imeneyi amwen km mwabwera ndi Moto ndithu 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @HarrisonMwanga-xy4sc
    @HarrisonMwanga-xy4sc Місяць тому

    Akudalila daudi suleman,kuti azamubela ma vote.popombonyetsa, network.ndi,zomwe akudalila

  • @user-be5fc3ed1i
    @user-be5fc3ed1i Місяць тому

    Apo ndiye chakwera wakumana nazo😂😂 kodi iwe ndindani kwenikweni katundu mzito womangira wire 😂😂😂😂😂

  • @DaveSitolo
    @DaveSitolo Місяць тому

    Kkkk mbavaaaaa 😂

  • @user-un6qv6sj3h
    @user-un6qv6sj3h Місяць тому

    Kkkkkk yomweyo galu iweeee mbava yachibusa

  • @EyobeAyala
    @EyobeAyala Місяць тому +3

    Ndipo Galu ameneyu wagwetsa ndege ndikuzagwetsaso kwacha😢 ,achoke😢😢

    • @user-uu9pv6jd4v
      @user-uu9pv6jd4v Місяць тому

      Chakwera our pride

    • @user-uu9pv6jd4v
      @user-uu9pv6jd4v Місяць тому

      cadet manyazi Ulibe iwe ungandiuze zochita ineyo opepera zaumbuli izii

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl 12 днів тому

    😅😅😅😅😅😅 zoonadiitu

  • @user-gd6zb2bv8f
    @user-gd6zb2bv8f 21 день тому

    Muuzeni man kkkkkkk

  • @stevezulu2108
    @stevezulu2108 Місяць тому

    😂😂😂 I like your hair Cut

  • @jollyfriday1892
    @jollyfriday1892 Місяць тому

    Chakwera ndi wasatanic oopsa kwambiri

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl Місяць тому

    🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣komaditu guys iyiyi ndi mbamva kobas

  • @CaciousChiwengo
    @CaciousChiwengo 25 днів тому

    Iwe choka apa

  • @danielsaidi7230
    @danielsaidi7230 Місяць тому

    Mukungotayanthawi yanu pachabe, ifekuno kumalawi tikudalila ulamulilo wachakwera chifukwa akukomza msewu was M 1 road, from nsanje to chitipa . Ufune usafune chakwera 2025 to 2060 wooooye!

    • @abasikazembe892
      @abasikazembe892 Місяць тому

      Iwe galu ungadye msewu mbuzi yamuntu iwe

    • @user-db3pq4nt9z
      @user-db3pq4nt9z Місяць тому

      Ulifwiti iwe ungadye nsewu ? Mbuzi yamunthu iwe

    • @HalisonSolomon
      @HalisonSolomon Місяць тому

      Ndiwe mbuzi yamunthu ndi chakwera wakoyo wakutumaeti ? Iweyo ndikupanda nzerukwakoko ungadye nseu kupanda manyazi kwakoko

    • @jennyx6914
      @jennyx6914 26 днів тому

      futsek
      fokkof

  • @danielsaidi7230
    @danielsaidi7230 Місяць тому

    Pamene mukupanga ma editing anuwo achabechabewo ife tili bize kupusha zathu panyumbapathu.

  • @GraceLimani-zw7dx
    @GraceLimani-zw7dx Місяць тому +1

    auzeni zoona amalawi

  • @russellsombwa1609
    @russellsombwa1609 Місяць тому

    More fire

  • @CHOTSANCHOIPA
    @CHOTSANCHOIPA Місяць тому

    Chitsiru iwe takasambani

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r Місяць тому

    Chakwela mbuzii

  • @HusseinMoffatt-mi1fl
    @HusseinMoffatt-mi1fl Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂😂zoonadi guys uyuyekha nde ayi ndi mwikho

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 Місяць тому

    Mr chifunga park and goo please 😥😥

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 Місяць тому

    Tamupatse mbamayo aisee, siwawandikana naye pompo!, tamupase kiki,

  • @user-vl8uw8mc3u
    @user-vl8uw8mc3u Місяць тому +1

    Zoona

  • @greymitomoni4047
    @greymitomoni4047 Місяць тому

    🤣🤣🤣🤣mazingazime

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg Місяць тому

    Poyamba chinali chimbava Koma pano ndi chifiti😢😢😢 nyini yake 😂😂😂

    • @harrisbanda5891
      @harrisbanda5891 Місяць тому

      😂😂😂😂😂😂, komaa guyz kkkkkkkkkkk, chaani chake?

  • @HanifuKalino
    @HanifuKalino Місяць тому

    Kkkkkk km iwe ndiye wamaliza😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @LucksonJamaliWilliam
    @LucksonJamaliWilliam Місяць тому

    a malawi nkhani ndiyomweyoooo bomalibwelele komwe linalo

  • @BlessingsmadalitsoShumba
    @BlessingsmadalitsoShumba Місяць тому

    😅😅😅😂 umakwana iweyo

  • @paulmakaula4937
    @paulmakaula4937 Місяць тому

    Timpatse nthawi apapa wakonza kaye foundation

  • @Abdulhakeem-jf1qd
    @Abdulhakeem-jf1qd Місяць тому

    Ayinvere chakwerayo mamphumi lake chakwera ndi osatira onse

  • @jamesgama5489
    @jamesgama5489 Місяць тому

    Iwe nde sunabwere kuzakhala pa social media pa mcp akupha mamawa

  • @LastonBamusi
    @LastonBamusi Місяць тому

    Bkkkkkkk😂 abale inu kumalawi

  • @DadiraiMundandishe
    @DadiraiMundandishe 18 днів тому

    😂😂😂

  • @GeorgeChakuamba
    @GeorgeChakuamba 29 днів тому

    Guys mmmmmmm

  • @TraverMbewe
    @TraverMbewe Місяць тому

    Maziga zime😂😂😂😂😂😂

  • @BlessingsWakhutamoyo
    @BlessingsWakhutamoyo Місяць тому

    Awa akuti

  • @ChawasoMlotha-ys6bf
    @ChawasoMlotha-ys6bf Місяць тому

    😂😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @HopesonBuledi
    @HopesonBuledi Місяць тому

    Watenga kut ma lawyer brother man?

  • @user-qu9iu7hs8k
    @user-qu9iu7hs8k Місяць тому +2

    Mukhaula chakwera mpaka 2030 wooo😊

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 Місяць тому

    Zoonadi

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z Місяць тому

    Boo Wang'alula tu brother nthawi yake yatha kuba kubakuba ine ndili ku USA komasindingavoteleu yu

  • @STARLIGHTGSM-cd8uv
    @STARLIGHTGSM-cd8uv Місяць тому

    Kkkkkkkkkkkl koma iwe ndiye unabwera

  • @OwamiSimeon
    @OwamiSimeon Місяць тому

    😂😂😂😂😂umakwana