Speech ya abwana inapangila campaign gulu lina and directly DECAMPAIGNED our Engineer Mumba! Bwana Mumba ur ideologies fits into another popular innovational party...PITANI ndithu u running mate ulipo
Aaaa achithyola which God are you mention now 😂😂😂zithu zikavuta Umalakalaka kuchula Mulungu from morning a till evening 😂😂😂😂ur talking very calmly ngati kamuthu kaulemu 😅😅😅😅
Mbuzi ya Msogoleri kugona posaka ndege koma za nyasi tulo nkupirira shame charakwe
Osamatchula dzina la Mulungu pachabe, akukuonanitu Mulunguyo komanso akumva,
Opule kuchisankho ndye kuchezera koma kosaka ndege osapitako
Good question indeed
Eeetu akuti kkkkkkl
I like the point brother
Ndi ma kape ma assassin
Maka maka mmmmh
Kuchezela kumeneko koma kosaka dege ndiye malile 6 koloko
I salute to Chithyola for such speech.. he is composed in his speech
KOMA LERO MULUMGU NDIYE AKUTCHULIDWA BWANJI??😂😂😂
I'm not supporters of MCP but when it comes to Mr Mumba I support him all the way to 2025 all the best for him.❤❤❤
Chithyola nkhopeyo koma ndalama imamuonesa kukongola munthu
Mr chikangawa munamusiya chilima akumwalira uku unsiku onse
Mbuzi iwe
Kuzimva, ati I have never lost , sizingatheke , aaaaaaa ,Mulungu amadana ndi perfectionism kaya
All the best Mumba akubwera boh keep on Pushing Sir.
Apa ndekuyakhula ngati Angelo anthu iyipa inu mukawinamo munyele moto
Speech ya abwana inapangila campaign gulu lina and directly DECAMPAIGNED our Engineer Mumba!
Bwana Mumba ur ideologies fits into another popular innovational party...PITANI ndithu u running mate ulipo
Bakili muluzi tv is loading.......
Happy to see my childhood buddy.vitu u where bon to be a leader.ur leadership skills goes where back
Ulipo nganya?
Osatekeseka MR mumba
Chithyola is cool calm and collected
Mr Chithyola Man of god indeed Madzulo ndi Sabbath osaiwala kukasegulila sabbath
Zovesa chisoni achilima anagona okha muchikangawa inu apule mwagona uko hmmmm mukuyalukatu tionana 2025
VP iyo yilute kumpoto kwithu lero .Mumba is the best future
I wish I could know more about more of Chithyola. So patient in speech. Full of knowledge. Love you bro.
Lelo mukutchula Mulungu ndi anthu akumudzi ovutika😊😊😮
Mumba anayikonda MCP koma MCP sidamukonde abwere ku UTM ndikomwe ndikomwe kufunika anthu atsogolo labwino
Kkkkkkk koma chithola ndewathyokatu
Koma akuvetsatu chisoni maonekedwewo
Zinaziwika kare Kuti mumba akawina nchifukwa amatchingatchinga koma amati chomwe chidzakhala chako nchako basi or mundikhomelere..❤️🔥❤️🔥❤️🔥❤️🔥
Agwesedwamo umu
Mumba so corregous
Mumba well done iwe anthu amakuopa kt ungawine but God is one amamenya nkhondo iwe uli chete
🔥🔥 Mumba
Koma chithyola boza
His grace is indeed sufficient
Mumuyèse chimwendo BP
I wish all the best to Mr Chithyola to won....
Chicholayo akugona uku akulila garu iwe
Mulungu mukumutchulatchulatu a chithyola
Kkkk
Wishing you all the best Mr Mumba🎉
All the best
Mumba more fire, 🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Kkkkkk mumaopa allah inuyo inuyo,, ndekuti mulungu amakutsogolelqni pakuba mu bomamo
Ziphanapopano zokhazokha
😂😂😂😂😂😂 usachule mulungu iwe wabesa ndalama
Mumba is geneous
Achimwendo kodi mudaziwa kt Mumbayo chimamuna hahahha mamuna zako pa chulu kulinga utakwerapa
😂😂😂😂Chinthyola tsopano kuyankhula mwanzeru komanso modekha 😂😂Mulungu amakumbukiridwa nthawi yamabvuto
Chithyola is not suit for sg .mulembi wachipani amafunika kukhala munthu wa ma vuvu monga chimwendo.
More fire Times ❤❤❤
First comment
Akusidza achithyolawo😂😂😂
Stress ikuwatibula chisankho mchoopsa
Apa awine Richard chimwendo Banda
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Koma guys@@PaulChaleka-lb4vx
😂😂😂😂Uyu bp yakwera
Achithyola 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂Koma ndaseka 😂😂😂😂😂😂😂😂
Mwabesa ndalama inu 😢😢😢😢😢
Kkkkk anyamata
Onse a MCP ndiokuda thupi ngati makala
Kkkkk chithyola mutu sukugwila😂😂😂😂
Achitchora kuyankhula ngati mgelo mbava yachabe chabe
Mbava yotheratu
Ndalama zomwe amabazo lero zabwelera kwa anuwake amene ali anthu akumudzi omwe amati akawavotelewo
Koma chimwendo ndi mbuzi ndamuonadi 😢😢😢😢😢
Chithyola ndodekha chonchi? He has spoken very well
All the best mumba
Mulungu wasankha kale enafe timangokwanilitsa chabe
Positive❤
Mumazitenga ngat mli ndi maudindo Akuma company koma akukusangan ndi anthu omwewa mkuwatenga ngat agalu anu pano munya
Wakupha amafanso end of errs
Chithyola wakumbuka mulungu 😂😂😂😂😂😂😂
koma chitchyola walankhula bwino modzi chepetsa mogwira mtima. akuoneka umunthu ulimo osatikulankhula mwamtudzi , kuzichemerera a yi
Anamuletsa Kani amawopa 😂😂😂😂😂
Positive
Kumbuka mulungu pa mavuto basi 😅😅😅😅😅
Mulungu muzonse kumene.
Kumafunsamutaimapatalitu chifukwa enao akumenyani kkkkk
Mulungu mukumufuna lero😅
Koma chithyolayo sakomoka uyo 😅😅😅😅😅
Ameneyo chityolayo ma 50 kg pa airport zimapita kuti,wayambaliti kuthandidza,thandidzo amapeleka nthawi ya campaign kodi thandidzo mesa amathandidza pofunikira thandidzo 🤔👀🙄
A chityola akuchita kumvetsa chisoni 😅😅
Chipani ichi nchoipa kwambiri. Anthu okupha
😂😂😂chitchola sawina😂😂😂
Kkkkkkk kupemphezela? Anyamata mukuyakhula
Amumba paja mumati simunaluzepo eti
Kkkk khope za mcp szimasowa 😂😂😂
Mumbaaaaa
Mfiti sisambitsa maliro
ZA MUMBA ZATHEKA CHIFUKWA OKUMBA DZENJE AMAHWELAMO EKHA
Ndiye wagwamoditu Mumba mdzenje lake lomwe.
Okay
😂😂😂😂😂💪💪💪💪💪💪🔥🔥🔥🔥🔥🔥
Mcp ndi ndi chipembezo chokuba
Anthu opoila inu zianthu zoipa izi
😂😂😂😂Muphana
Aaaa achithyola which God are you mention now 😂😂😂zithu zikavuta Umalakalaka kuchula Mulungu from morning a till evening 😂😂😂😂ur talking very calmly ngati kamuthu kaulemu 😅😅😅😅
Mbava zina mpaka kutchula dzina la yehova 🤔
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Koma ndie zatenga nthawi kuulusako,kukhalangati zisankho zapatatu bwanji