Kodi ndi MBC vs DPP? Mukamanena zokut CDF yakwera kufika pa 200mita, muzinenanso kut: Mafuta a galimoto anali pa bwanji Mafuta ophikira anali pa bwanji Chimanga chinali pa bwanji Fetereza anali pa bwanji U fresh anali pa bwanji You need to be non partisan otherwise, simumatha ntchito.
Very informative, gentlemen you're doing your country a real service. Keep it up
Live from south Africa ❤❤❤❤❤
Well analysis...keep it up...guys
Keep it up guys we love you 💓💓💓💓💓❤❤❤❤
Very true, APM is not giving a message of how he will implement his lies. He says Mangochi will become like Singapore within 6 months - mabodza
Powerful I love timvetse program
Anthu olikonda dziko lawo awa despite ndalezo koma akukamba zoona zokha zokha anthuwa
Mmakwana guyz pitilizani osaopa komaso alibe gawo kwainu akunama ameneo
Awawa 100%, support
Ulemu wanu akuluakulu mumatha Malawi muno pakufunika Muthu ngati kasakula
Awuzeni amvetse a Kasakula ndi amzanu onsewo mumakwana
Manember plet Anna Adad sitikuwafuna boma ndilomweli
Watching from a distance
Chilungamo chimawawa azibambo inu mkuyankhula zoona zokha zokha
Osabesa vot povotela Amp mutaya vot
Ajijo mwasinthatu ngat zocheza
Emusipi kodi sikubwereka ndalama ?
Kelvin mpekasambo zomwe mukunenazo ndi zero pa 10
Anthu alibe fundo awa, composition mulibemo 😂
Makape okhaokha...km nde muli pachi ntchtotu
Chisankho cha 2014 wina anazipha PP italuza analinso oyankhulitsa ngati awa ndikuonanso masophenya kuti modzi mwa anthu awa akuzazipha pa 16th semptember pompa
Katsakula Chitsiru Cha Munthu
Mboli zanu
at this point its mbc against dpp.
Iyi niwayilesi ya boma kapena ni ya mcp awa wonse mu September wa choke ntchito kampeni pa ladio yathu nili ku zambia
Pitilizani kuwadziwitsa zowona zokhazokha aMalawi makampani aboma la MCP adagulitsidwa ndi Bakili Muluzi ndipo ndiye adawononga dziko
Koma inu ndinu zimbuzi
Chilima alikuti ?
Nthawi zina muzitiponyerako ma video wama cadet akumenya anthu osalakwa kuti anthu ena omwe anayiwala azikumbukira
Nyau ya kukasungu ikukamba za ufulu chosechi azanu akumangidwa nsi ufulu wanu ngat wanu omwewo
Mcp ponena mabodza kut azasintha dzikoli samanena ma specific details kut azapanga chiyani kut anthu azizadya katatu, kugula fertilizer otchipa ndye musamulese munthu akuziwa chomwe akuchta through experience
Inuyo gyz mumakwana and boma ndiromweri
Ndiye apekasambo mfundo mwanenazo achakwera akuzikwanitsa?
Kagwiridwe ka ntchito ku MBS akuyenela kukhala silent pa nkhani za ndale
Nyau ya kukasungu ikukamba za ufulu chosechi azanu akumangidwa ndi ufulu wanu ngat wanu omwewo
Mbuzi inu
Awine apm awagulile alobino Mabelo aja
Koma butò la a Dpp kutukwana kokhako amadziwa amaonongadindziko ali nďi mtima woiipa ndipo ndi zigawenga tiyeni tiyetse UTM chonde.
kasakula ndiwe chisilu cha munthu
Amalawi. Zikoli ndilanthu sikuti ndlachekwela kapana LA apm tivetsese,akhala wasoka ongova chinthu chinthu chimozi achimene Iye chamuny'asa
Mbudxi inu akupasani chani chakwela
Iyidi ndi wailesi ya boma……🤦♂️
koma anthuwatu ali ndi mitu ikuluikulu...
Wadzaka zochepayo akukanika kupanga deliver 4 years down the line
Mitu youmayo munayamba mwakhala president or nduna agalu nonsenu mukuyankhulanu ? Inu opusa mbuzi za anthu
Ndekuti iwenso ngati sunakhale President kapena nduna ndiwenso mbuzi
Kodi ndi MBC vs DPP?
Mukamanena zokut CDF yakwera kufika pa 200mita, muzinenanso kut:
Mafuta a galimoto anali pa bwanji
Mafuta ophikira anali pa bwanji
Chimanga chinali pa bwanji
Fetereza anali pa bwanji
U fresh anali pa bwanji
You need to be non partisan otherwise, simumatha ntchito.
Kasakulayo ndi zoba ndithu
Kasakula ndiwe ovetsa chisoni ukuona ngat ku MBC ko mukhalako kwa nthawi
Akasakula ku ma interview munakhala nambala 4 takanani? Waganyu wa MCP galu iwe mutu ngat Fuwa
Machende anu
Zikwanje zija mayazi eti
You're saying no sense I think you're mad
Akalowa apitawo muzati chani… this tv.just finishes our taxmoney.
Anthu awa akufotokoza zoona zenizeni. Keep it up.
Apa ndiye 0% zafodya zenizeni mukuyankhula apazi zikuoneka kuti munthalika wakuzunguzani mitu, tangoikani nyimbo ya Peter tivine apa😂.