Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Koma Amanga liti ngoba akuchoka mboma September Koma Zabvuta basi
Lilime lomweli limatamanda Mulungu lilime lomweli limanena zakupha tizisamala ndi lilime chifukwa ndi kachiwalo kakang'ono kwambili komano kamaontcha dziko lonse
Zisiru zaathu inu a mbc
Amangolonjeza koma sangakwanitse ameneyi amangonena koma zosatheka molomo okudya dzanchere kukomesa lilime ndi ndikanthu kakang'ono komwe kamapanga zambili
Koma Amanga liti ngoba akuchoka mboma September
Koma Zabvuta basi