PDP - KONDWANI NANKHUMWA WALANDA MASAPOTA A DPP LERO KU LUCHENZA - MVELANI ZOMWE WAKAMBA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 24 січ 2025

КОМЕНТАРІ • 92

  • @rashidadan2533
    @rashidadan2533 15 днів тому +5

    His exllence professor Peter muthalika ,
    The president of the republic of Malawi
    🌹 Congratulations on 2025 election 🌹

  • @POSCMATV
    @POSCMATV 15 днів тому +6

    Kkkkkkkk sizikubebaaa ataaa olo pang'ono APM is my vote
    Koma ndingopitako ndikamudyere ndlamazoooo basiii

  • @Princevenasiyo-b4b
    @Princevenasiyo-b4b 15 днів тому +2

    A DPP mukulira coz nankhumwa wakulandani chi gulu china cha anthu, munya nayo come, 17 September Dr. Chakwera atakugwesaninso.

  • @EliasKhofi
    @EliasKhofi 16 днів тому +7

    Nankhumwa is very young boy.ndipo alibe chikoka anthuwo angofuna amudyere komanso angomva zomwe akufuna kubwebweta 😂😂😂.koma sangadzamuvotele even nthungululuzo zikuchina kuoneselatu nzoofooka akululutila ndi 5 to 6 basi 😊😊.

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 15 днів тому

      😂😂😂Phuma silabwino awa chikangawa anawapusitsa shame...

    • @HestingsChibalo
      @HestingsChibalo 15 днів тому

      ?@@eliffagondewe8214😂😂😂😂

  • @BlessingsHarneck-p3y
    @BlessingsHarneck-p3y 14 днів тому

    Mnsonkhano ndi mnsonkhano wanthungululu m'modzi basi mhuuu

  • @LevisonDaka-f5x
    @LevisonDaka-f5x 14 днів тому

    Am from Zambia but he has got no manifestation this man should just join your other party like dpp

  • @Princevenasiyo-b4b
    @Princevenasiyo-b4b 15 днів тому +1

    Kumtunda chakwera vote ya amalawi tonse ofunira dziko Kathy zabwino, chakwera woyeee!!!!

  • @ChifundoJohn-w3t
    @ChifundoJohn-w3t 14 днів тому

    Za ziiiii basi kwinaku nditukwana ndithu

  • @Auscarmbeye
    @Auscarmbeye 14 днів тому

    Vote yako 40

  • @SamuelKalemba
    @SamuelKalemba 14 днів тому

    Kaligondo wachabe chabe iwe ukuyiwala zomwe akutuma akanadziwa mulimiyo.....

  • @mariawachesterweluzan
    @mariawachesterweluzan 15 днів тому +1

    Opoyira nankhumwa unakango pepesa kwa adad Ako APM My vote

  • @monicatambala5615
    @monicatambala5615 15 днів тому +1

    Kkkk nsanje sizinthu
    Mukuona with your two eyes mmene anthu skumutsatira KN kkk chomwe mukufuna china ndichani kkk
    KN my vote

  • @MavutoFodya-p1u
    @MavutoFodya-p1u 15 днів тому

    Hahaha mpaka wariii hahayeee kma mwana ameneyuuu anthu angokudyela ndithu

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 15 днів тому +2

    My vote is for Apm ....sindingavotele ndi zisilu zomwe

  • @GstarNana
    @GstarNana 15 днів тому

    Apm my vote

  • @IgnatiousFote
    @IgnatiousFote 15 днів тому

    masanje enieni awa

  • @AlumakioChingalu
    @AlumakioChingalu 15 днів тому

    😂 23:27 😢koma kummwera kulidi anthu akhwimthi ndi udindo😮😢 :

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 15 днів тому +2

    Kutha kwa shasha angoku user chikangawa phuma silabwino ayi mwataya omwetamweta 🔥🔥🔥🔥

  • @WaysoLufas
    @WaysoLufas 15 днів тому

    Akulua ndiopoila sakusyana ndichakwera mm!!tasowa ovota

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 16 днів тому +3

    Anthu anali okondwa dzulo kwa Adad not kwa Nankhumwa

  • @DanielChinula
    @DanielChinula 15 днів тому

    Mavote akumeneko mugawane uyitha ase ukatero tidzakulandira😅😅 alande anthu ambiri ana oipa

    • @symoldicky
      @symoldicky 15 днів тому

      balota choncho ,

    • @symoldicky
      @symoldicky 15 днів тому

      history is a best teacher , izizi akanfuse kaliat ndi mboni

  • @DeMu-t2v
    @DeMu-t2v 14 днів тому

    Enatu angokhumata sakuyakha nanga zukhala bwanji?

  • @PhonexDaniel-t5v
    @PhonexDaniel-t5v 14 днів тому

    Wachepa taonani akumuyakha athu awili okha akumuyakha azibale ake okha.

  • @MustapherLino
    @MustapherLino 15 днів тому +1

    😂😂😂Bola kungopita Kwa Peter mutharika mukapepetse 😂😂

  • @QueneteCatundulo
    @QueneteCatundulo 15 днів тому +1

    MCP my vote

  • @FelisterMtoso
    @FelisterMtoso 16 днів тому +2

    Ndiye bwanji mukuti boma ndilomweli? 🤣🤣🤣🤣 mwapengadi ndi zitedze eeti

  • @danielmapulanga1321
    @danielmapulanga1321 15 днів тому +1

    Boma ndilomweli hahaha Ife sitisintha

  • @BerthaChisoni
    @BerthaChisoni 15 днів тому

    Adikile pa 15 pano ...akamufunse kaliat kumaona ngat awina ku conversation...okudya naye anamuliza owooo

  • @SannahAbdulAzizi
    @SannahAbdulAzizi 15 днів тому

    Mkape iweeee

  • @EliasBilliat
    @EliasBilliat 15 днів тому

    Ineyo ndisaikepo mulomo😮

  • @BlessingsMuheliwa
    @BlessingsMuheliwa 14 днів тому

    Mfundo izizi ndizopepela

  • @JimmieKatema
    @JimmieKatema 15 днів тому

    You have been in government for years, you mean you didn't know the problem of the bridge in Luchenza that pple are using boats.

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 15 днів тому

    Kkkkkkkkkk chipani chipanda ndalama ngat ichi sindinachowone mbuzi ngat iyi

  • @JACKSONHULUWA-j2n
    @JACKSONHULUWA-j2n 15 днів тому

    Palibe molalo apa, anthu abwera kuzamudyera

  • @JosephSamuel-f6f
    @JosephSamuel-f6f 16 днів тому +2

    Anankhumwaso ndy ayi osangolowa chipani Cha anzanu bwanji

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 15 днів тому +3

    Mwangokula mimba, koma machende ndi ang'onoang'ono kkkkkkkkkk 😂😂😂😂😂

    • @PatriciaAlomwe-oz8wc
      @PatriciaAlomwe-oz8wc 15 днів тому

      Mwandikomoratu mkuseka kuno kkkkk mwaganizabwanji

    • @JemaxChibwanazulu
      @JemaxChibwanazulu 15 днів тому

      @PatriciaAlomwe-oz8wc Kkkkkkk aaaah enawa asamangotiwawitsa mutu apa ndi bwerera zaozi

    • @HestingsChibalo
      @HestingsChibalo 15 днів тому

      Kuyakhula kwa bwanji uku 😂😂😂😂

  • @Hestingswilson-r5g
    @Hestingswilson-r5g 15 днів тому

    Zachabe chabe wali ndie kuti chani

  • @owenmateketajambo2227
    @owenmateketajambo2227 15 днів тому

    Palibe iliyonse😂😂😂😂

  • @CharlieChirwa
    @CharlieChirwa 15 днів тому +1

    Mwachepa nazo bigy

  • @JoyLuwanika
    @JoyLuwanika 15 днів тому

    Dpp my vote

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 15 днів тому +1

    Anankhumwa. Mwafulumira kuseta musanyere machende ako.

  • @Thanthwe2020
    @Thanthwe2020 15 днів тому

    Ufumu chani 🤣🤣🤣🤣😂😂😂😂 kufuna kuchotsera mavote awina wake? Zaziiiii

  • @MuhammadSamson-yz1kl
    @MuhammadSamson-yz1kl 15 днів тому

    Aaaa koma akulu awa zoti mkadzi wake uja anafusira ekha tikukaikira nanga zikulakhulidwa apazi ndi nfundoizi 😂😂😂😂

  • @ChibisaBanda-w9w
    @ChibisaBanda-w9w 15 днів тому

    Dr Usi akupereka chakudya lero

  • @sanddaniweck2703
    @sanddaniweck2703 15 днів тому

    mayo bundle yanga ine🙃😂

  • @MavutoFodya-p1u
    @MavutoFodya-p1u 15 днів тому

    Awa ndi anadi or kuyenda ndi akazi anu kkk

  • @FebbieNjewa-g3k
    @FebbieNjewa-g3k 15 днів тому

    Kkkkkkkk anthu amangofuna akawone basi,,ziwoneka mu september

  • @ArnoldWachepa
    @ArnoldWachepa 15 днів тому

    Kuvotera uyu mukuvotera MCP. chifukwa zipani zikalephera 50 + 1 zizapita kungwilizano wazipani ndi vote yanu.choncho Nakhumwa azapita ku MCP.

  • @ReubenMalamulo
    @ReubenMalamulo 16 днів тому +2

    Akudwala chifuwa uyu

  • @IsabelLuka-i8f
    @IsabelLuka-i8f 15 днів тому +1

    Aaaaa ati pdp waliiiiii!!!!!kutengera za adad,za dpp oyeeeeee munakabwera nanunso ndiyanu osati zimenezo mmmmmm sizikubebha😂😂😂😂😂

  • @edsonnyasulu5394
    @edsonnyasulu5394 15 днів тому

    Sanalande anthu akungofuna kudya naye basi anthu ali ndi njala yoopsa mumamizi umu

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 15 днів тому +1

    Nankumwa ndi chitsilu cha MUNTHU chinalephera kutsutsa Ku parliament

  • @CharlesBanda-v8k
    @CharlesBanda-v8k 15 днів тому

    Uyu ndiye utiso mwamkumba kuti 😅😅😅😅 mundibwezere bundle yanga chonde

  • @VaidaSidreck
    @VaidaSidreck 16 днів тому +1

    Uyu akufuna atenge athu apitenawo ku m c p

  • @DalitsoLuka
    @DalitsoLuka 14 днів тому

    Thungululu oliza munthu modzi ayi zikomo

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 16 днів тому +1

    Wachepa uyu

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 15 днів тому

    Za ziii ngakhale zina loti nankhumwa si zina loyenela kukhala zina la president

  • @VeronicaChirwa-ct4os
    @VeronicaChirwa-ct4os 15 днів тому

    Koma iwowa osangozichepetsa bwanji ndi kubwerera ku DPP kapena kukajoina chipani chili chonse chosutsa

  • @peterbyson6269
    @peterbyson6269 15 днів тому

    Nde chambachi amalawi ndi wina aliyense

  • @Paul-q2p
    @Paul-q2p 15 днів тому

    😂😂😂😂😂

  • @fanymatchumbuza6125
    @fanymatchumbuza6125 15 днів тому

    Awa nawo anangozisokoneza and akungofuna kugawa mavoti basi

  • @DominicNantowa-t4d
    @DominicNantowa-t4d 15 днів тому

    Kopusa ndyeleni🤑🤑🤑🤑

  • @JemaxChibwanazulu
    @JemaxChibwanazulu 15 днів тому +1

    Panja penipeni

  • @TinasheKamanga-p9c
    @TinasheKamanga-p9c 15 днів тому

    Anthu paka kupeza malo okhala kumsokhano wadad sitikhala pansi chifukwa chosowa space😂😂😂Apm bomaa kale

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 15 днів тому

    Uyu ayi panja penipeni ,mfundo iyi zero pa ten kagwere ukooo wamva

  • @BlessingsMuheliwa
    @BlessingsMuheliwa 14 днів тому

    Man mulibe mfundo

  • @AlfredKamphonda
    @AlfredKamphonda 15 днів тому

    Hehehehehe ayitu pdp nde kut chan

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 15 днів тому

    Alowe chipani cha Manganya. Zaka 5 zapitazo unali m'boma sunapange nthawi imene yo.

  • @Davis-qo4qp
    @Davis-qo4qp 16 днів тому

    Zakuvuta !!!!

  • @MolesBrown
    @MolesBrown 15 днів тому

    Olo munyoze koma dpp ikudyeka basi dpp ilipamavuto

    • @chifundocharles2348
      @chifundocharles2348 15 днів тому

      😂😂😂😂 ukunama aise, mavuto ake anankhumwa??? Charisma alibe uyu

  • @BakhePaliso-h8h
    @BakhePaliso-h8h 14 днів тому

    Dpp my vote not you

  • @ChisomoLester-h7x
    @ChisomoLester-h7x 16 днів тому

    Ana a DPP, wapakulako zako basi. Kummwera ndikogawana kumeneko kkkkkk adadi akomoka. Apa zikuwawa wa DPP 😂😂😂😂 kt khaaaaa

    • @chifundocharles2348
      @chifundocharles2348 15 днів тому

      Alibe chikoka pa ground 😂😂😂😂

    • @ChisomoLester-h7x
      @ChisomoLester-h7x 15 днів тому

      @chifundocharles2348 chikoka alibe kupatula kwaoko agawanako kumeneko coz ndi kwao thyolo ndi mulanje atengako gawo lake

  • @ShillahLawrence
    @ShillahLawrence 15 днів тому

    Komanotu sananene kuti azapanga chani akadzawina

  • @PaulMhango-x3q
    @PaulMhango-x3q 15 днів тому

    Munthu ukufuna u President ukulankhula mau akuti ukukana kudyetsa wa MCP wa DPP and UTM therefore ukopa bwanji anthu wawinetsakale tsankho and ukuti sungayambe kugulira kabudula mwana womupezaaa aaaa fundo zopoilatu izi and looks you are not matured aaaa nix

  • @StoneckJali-s3n
    @StoneckJali-s3n 15 днів тому

    Mumumva Ife wathu ndi yemweyi basi olo munyoze

  • @YoungMwacho
    @YoungMwacho 15 днів тому

    Useless speech

  • @faithkamlongera5128
    @faithkamlongera5128 15 днів тому

    😂😂😂