THE COURT..(Malawi )🤔

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 12 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 461

  • @MwaleYankhoKatanga-k3e
    @MwaleYankhoKatanga-k3e Місяць тому +14

    The second wife is fully genius,

  • @JamesMalemba-tx4uh
    @JamesMalemba-tx4uh Місяць тому +17

    Very beautiful I need kumva chigamulo

  • @ishmaelimani3779
    @ishmaelimani3779 Місяць тому +32

    Apatsidwe gawo lawo mayiwo ,komaso ndasangalala mwayamba kuzenga mulandi mchichewa osati kufuna otathauzila tonse ndachewa 😅😅😅

    • @aminamussa9835
      @aminamussa9835 Місяць тому +3

      Point of correction, tose ndamalawi

    • @marianamwanje8968
      @marianamwanje8968 Місяць тому

      ​@@aminamussa9835ndiposo yonse ndachewa ndiye kuti chani eti

    • @EvelynDamiano-zg9kn
      @EvelynDamiano-zg9kn 29 днів тому

      M'bambo akakhala pa mitala amayenera mkazi aliyense azimupangira zotsogolo payekha ndi ana ake..momwe zilili apapa palibe chifukwa chomwe mkazi wamkulu atengere chuma kugawira mkazi wamng'onoyi..angoyamikanso kut ntsungwana uja wanena kut azimusamala brother wakeyo

  • @ChrispoGawani
    @ChrispoGawani Місяць тому +6

    Mwanayu ndi wa m'ng'ono akuyenera kusamalidwa aphunzire school yabwino azigona pabwino chuma adzapanga yekha msogolo m'mayi wa mkuluyi wavuta sapereka gawo la chuma komanso bamboyu analakwitsa osalemba will iyeyo ndiyemwe anayenera kugawa chuma adakali ndi moyo azibambo anzanga tiphunzirepo apa nkhani izi always zimavuta kwambiri

  • @user-xz3nz7dy1f
    @user-xz3nz7dy1f Місяць тому +20

    Na ngati wakulu adavomera kt ndi mitala ali mwana wa bambo chuma amupase komaso amupase 25% yamwa make 10%nkhani yatha

  • @MwaleYankhoKatanga-k3e
    @MwaleYankhoKatanga-k3e Місяць тому +3

    She knows how to explain,this marriage issue

  • @IsumailaSalanje
    @IsumailaSalanje Місяць тому +4

    Kumupatsa gawo lachuma kukhoza kulimbikitsa antchito kumagwa muchikondi ndimabwana.Mngosokoneza mabanja amenewa

  • @user-vu4cz1mt4f
    @user-vu4cz1mt4f Місяць тому +7

    Apatsidwe chuma chifkwa kuli mwana komanso akaz akuluwo anavomeleza

  • @JeanBanda-zy6wu
    @JeanBanda-zy6wu Місяць тому +7

    Chonde tibweleseleni nkhaniyi timve kuti anagamula bwanji so interesting 😂😂😂
    Komabe mwanayo akuyenela kumugawilako chifukwa amayiwa anavomeleza mitala linali banja ndithu akanafuna akanakana kuti mitala sakuifuna kangachepe ampaseko mwanayo

  • @gremmerchris71
    @gremmerchris71 23 дні тому +1

    Nkazi wachiwiri uziyamika kuti uyu woyambayu anakulola kulowa m'banja lawo komaso pokutenga kuti uzikamugwilila ntchito chokhacho uzimuyamika...usazitenge wapamwamba kwambili kuti wabeleka mwana wamamuna nzakoyo sikufuna koma zidangochitika..
    Komaso iwe nkazi woyamba kuti ufike pomwe ulipo dzidatengela nzakoyo kukhetsa thukuta ndikudzichepetsa kwakwe kuti iweyo ukhale umoyo ofewawo muthokoze pomupatsa shop imodzi over time mudzapeza ina basi simple..mukutelo pokuti iye ndiyemwe wasunga nfunda wanu basi

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w Місяць тому +6

    Amen good wafunsa funso labwino mkazi wa mkulu mahule wa ndi anthu oyipa wake kunalibe

    • @MeltonMumba-rn9mf
      @MeltonMumba-rn9mf Місяць тому

      Exactly

    • @patrisiobinalison8476
      @patrisiobinalison8476 Місяць тому

      Uyutu sihule ,mkazi wamkulu pomwe analakwila ndi kuvomeleza mitala

    • @GiftCMlangeni
      @GiftCMlangeni Місяць тому +1

      Mind your tongue remember ngati pali hule ndi abambowo not mkaziyo. Am also aman how can idate wantchito wanga? Mesa amkagwirantchito nde amakapempha banja ngati? Wamkukuyo adavomeleza bwanji mitala nde chitavute nchani kungomugawirako kuti asathe nthawi yaboma?
      Kungoti ndikupatsa business imodzi or minibus imodzi basi nkhani yatha. Komaso akuiwalakuti chuma chimatha, dzina la abambowo lilindi wamwamunayo, enawo mawanja akakavuta adzamufuna nchimwene wawoyo?? Nanga mayiwa akadzakalamba akaziwa adzakwanitsa zonse zomwe zimafunika mamuna akhalepo?? Mmmmh kuipamtima kukuoneka apa

  • @MustafaAmeen-tb6wd
    @MustafaAmeen-tb6wd Місяць тому +15

    Ngat nkazi anavomeleza mitala akuyenela amugawileko nzakeyo chumacho, congratulations ku mboni athandizedi mlongo wakeyo kuti naye azafike ngati pomwe ali iyepo

  • @PeterJafari
    @PeterJafari 2 дні тому

    Kodi anagamula bwanji guys ine ndikusaka koma sikupezeka koma mkadzi wang,onoyi akuyenera amupase ngawo lake ndithu

  • @kesterkaunda
    @kesterkaunda Місяць тому +1

    This is true story or movie?

  • @user-ni2vm8zx9t
    @user-ni2vm8zx9t 26 днів тому +1

    Is this acting classes?

  • @FRANCISLIFFAH
    @FRANCISLIFFAH 3 дні тому

    odandaulidwa munamvomera kunkhala akazi awiri, kwa m'bambo mozi sono musachuluke mzeru cfk mamunayo wamwalila

  • @user-mm2ek3cx8l
    @user-mm2ek3cx8l Місяць тому +4

    PA ana atatuwo dzanja alipo mmozi uyu ndiye mwana wamamuna mpaseni zabamboake

  • @ShadreckKwelani
    @ShadreckKwelani 28 днів тому +1

    Second wife agawilidwe mbali yake.

  • @MarkoMsango
    @MarkoMsango День тому

    Wang'onoyo ndiopusa komaso alive nzeru

  • @NedsonKennedy
    @NedsonKennedy Місяць тому +2

    The best way is, write willo b4 pass away 😂

  • @user-xo6th8bx2p
    @user-xo6th8bx2p 11 днів тому

    I don't think kubeleka mwana wammuna chikhale chitonzo pa anzawo , iwo adakangopempha thandizo la mwana osati mpaka chuma chifukwa mkazi wankulu kuvomeleza mitala sindiye kuti chilichose chomwe ali nacho ndye kuti nkazi wango'ono akhale nazo

  • @user-rj8bv9cw1r
    @user-rj8bv9cw1r Місяць тому +5

    Zaziiii agawe chani,amkaleka kumpasa chumacho mamunayo alipo bwa mg2 anthu oyipa akhoza kukumpha akhaula

    • @MikeMwale-bw1xw
      @MikeMwale-bw1xw Місяць тому +2

      Umfiti suposa pamenepo,kumakhala ndi umunthu palibe amadziwa za imfa kuti ingachitike mwachangu kwa bamboyo,ndili sure naye gawo lake lipezekapo akagamula.

    • @user-cn7uu4mb5n
      @user-cn7uu4mb5n Місяць тому

      Agawe chumacho

    • @PociahMack
      @PociahMack Місяць тому

      ​@@MikeMwale-bw1xw wina wazuzika naye wina kungochoka uko Ali agawe zosathekatu

    • @MikeMwale-bw1xw
      @MikeMwale-bw1xw Місяць тому +1

      @@PociahMack Ayi agawane anapangira limodzi,sikuti wangochoka uko nayeso anali mrs

    • @mphatsokauta6387
      @mphatsokauta6387 Місяць тому

      @@MikeMwale-bw1xw kungoti kwanthu kuno ma banja samayenda mwadongosolo

  • @vestarmkandawire6138
    @vestarmkandawire6138 Місяць тому +4

    Mkazi wa chigololo ameneyo ndi mbuzi,, banja ndi ndalama ndi zinthu ziwiri zosiyana. Mkazi woyamba ayankha bwino kuti adavomereza mwamunayi akhale awose osati chuma. Ndiye huleyo chuma chake ndimwana wamwamunayo. 1 Akumbukire kuti anali wa ntchito wa mayi wamkuluyo 2 wamulakwira kumulanda mwamuna wamwini. Apapa kunena zoona chuma asamugawire ndi wakuba mayiyu. Zikuonesa kuti wapha mwamuna ndiye kufuna chumacho.

    • @user-rt3nx4dx1t
      @user-rt3nx4dx1t Місяць тому +1

      Wolakwisa ndi mayi oyambayo povomereza mitala,chuma chiyenera kugawidwa basi

    • @FatimaAyami
      @FatimaAyami Місяць тому

      Mwanvetsa koma inu kapena ndinu achibale a MG1

    • @macdonaldkorea2928
      @macdonaldkorea2928 Місяць тому +1

      Inutu ndiodwala, munkhaniyi mwakambidwa zoti wina ndihule? Iwe momwe umkabadwa makolo akowo anakwatirana mwadongosolo? Kumasata nkhani osati mopusa.....

    • @macdonaldkorea2928
      @macdonaldkorea2928 Місяць тому

      @@user-rt3nx4dx1t nkhani koma imeneyi ndithu.....

    • @johnssanamah1408
      @johnssanamah1408 Місяць тому

      Vuto lowakhira nkhani pali za uhule apa mesa akuti unali mgwirizano oti ayese zida abambowo amafuna mwana wa mwamuna ndye atafunsidwa amayi akuluwo anavomera kuti vuto palibe atha kukhala pa mitala mwayi uwo mimba mkubwera akabadwe mwana chimphongo ndye kuti mdala Ku khosi mbeeee kuti mission yatheka mwana wa mwamuna wapezeka.
      Ndye chomuchulira kt ndi hule mumakhala chili chani....?????

  • @HenryLaidon-pl9ly
    @HenryLaidon-pl9ly Місяць тому +5

    1st born wa Dzanja from MG 1 uli ndi umunthu coz pa dziko pano uli ndi brother wako mmodzi from MG 2 komanso ndi mwana musamalire, komano zolinga ZENIZENI za MG 2 PA mlandu wu aaaaaa chabwino tiyeni tione kuti MALAMULO akuti chiyani

  • @samsonmtumbati4855
    @samsonmtumbati4855 Місяць тому +7

    Chuma chigawidwe kwa mkazi wachiwiri chifukwa kumenekonso kuli mwana wabamboyo amayiwo asaphangile chifukwa chakutinso mkazi woyambayo adavomereza kukwatiwa kwamkazi wachiwiri

  • @user-rm4kr8dj1e
    @user-rm4kr8dj1e День тому

    Where is the ruling. I need it pliz. Give me a link 😂

  • @HaroonHaji-rp4if
    @HaroonHaji-rp4if Місяць тому +1

    Malamulo amatiuza momveka bwino zachuma chamasiye mwana wamng'ono komanso ndimwamuna akuyenera kupatsidwa gawo lake koma akharea ndimtsinkhu woyenera ndipo MG 2 sakulakwitsa sichifukwa MG 1 pamene amavomereza mitala anadziwa zoti ali ndi chuma chimene umwini waukulu umakhara kwa ana

  • @LonjezoSingano
    @LonjezoSingano 19 днів тому

    Vuto ndi mayi mkulu kuvomeleza mitala mgayren nzanuyo bs

  • @AshleyMbewe-k5z
    @AshleyMbewe-k5z 24 дні тому

    I second with you bro,the rulling is very important

  • @MwaleYankhoKatanga-k3e
    @MwaleYankhoKatanga-k3e Місяць тому +1

    The first daughter is coming with some juries and want to run away from this as solution

  • @GilbertKuziona
    @GilbertKuziona Місяць тому +2

    Ngati mkazi wankulu akuziwa ndipo anavomeleza zamitala ndipo akudziwadi kut kuli mwana kwa mkazi wachiwiri akuyenera kumupasa gawo lake mwanayo

  • @ChimwemweWanga
    @ChimwemweWanga Місяць тому +2

    Na ngati anavomeleza mitala amugaile gawo lachumacho

  • @McDonaldKanyinji
    @McDonaldKanyinji Місяць тому

    As long as the first wife accepted that they were on polygamy, the worth is suppose to be shared according to how many kids each wife has......... but not equal..... Court should observe this.❤

  • @Standwell78
    @Standwell78 Місяць тому +2

    Abombo tiziyika konse konse chuma tisanamwalile chifukwa izi nde eee

  • @johnssanamah1408
    @johnssanamah1408 Місяць тому +1

    Mboni yafotokoza bwino zedi moti ndikuona akulandira gawo la chuma brother wakeyu

  • @mcsellahntv6896
    @mcsellahntv6896 Місяць тому +2

    MG2 kutha mantha mpaka ku khothi kutengela MG1.

  • @josephgondwe5829
    @josephgondwe5829 Місяць тому

    Nkhanizi ndi za kuMalawi konkuno, I like it kuti you are using Chichewa osati zokhala ndi interpreter.

  • @YohaneJabesea-s8k
    @YohaneJabesea-s8k Місяць тому +2

    Mkazi wang'ono azipepha kuti amupatseko Osat kugawana

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 Місяць тому +3

    Kwakoma ndikuno😅😅😂😂😂😅😅

  • @ChimwemweEddimael
    @ChimwemweEddimael Місяць тому +1

    Aah ine I think this is just acting why do I see the same faces on different cases or maybe it's only me 😂😂😂

    • @corretabanda7685
      @corretabanda7685 Місяць тому

      Eyaka ndi acting. Akufuna kuti anthu adzipita ku khoti zikaavuta, komanso anthu tidzitengerapo phunziro.

  • @EricThanda-qo3jz
    @EricThanda-qo3jz Місяць тому +2

    Koma akhale ndi tv yankhongo yomweyo😂😂

  • @user-lg6ym4hz3w
    @user-lg6ym4hz3w Місяць тому +1

    Kkkkkkkk akazinso alinso ndi ntchito mesa ndi anthu

  • @BrendaSinoya
    @BrendaSinoya 20 днів тому

    Watchitoyo anafoira bamboo alimoyo,akanapempha zake zoti aziyendesa ekha abambowo asanamwalire koma pot mphuno salota

  • @elsontmsukwa4356
    @elsontmsukwa4356 Місяць тому +2

    Ine ndimaganiza kuti chuma chisungike bwino chingokhara ndimunthu yumozi azichiyanganira kenako aziwapasako azake asowekera chinachake chifukwa akapupuluma kugawana mwana tava ndi wamungono nde mwina nikutheka awagawira koma koma mutu wa business alibe apeza chonse chathaso nde mwanayo azapezachani akakula 😢😢😢😢

    • @macdonaldkorea2928
      @macdonaldkorea2928 Місяць тому

      Ayi agawane chifukwa azimai okha okha sangamachitire zinthu limodzi

  • @peterjoshua2595
    @peterjoshua2595 Місяць тому

    I just like the guy who’s sat behind the accused 😅

  • @Memorymillanzi
    @Memorymillanzi 22 дні тому

    Ngati anafika polemba wantchito ndie chuma anali atapanga kale palibeso chifukwa chogawira chuma

  • @MilwardChanza-mr4yr
    @MilwardChanza-mr4yr 27 днів тому

    Mkazi wachiwiri anakakonda anamkagaila ma percentage angat?

  • @graciousbwanali5079
    @graciousbwanali5079 Місяць тому

    Gyz if i can have chance to coach people before the court ambiri sibwenzi akuluza milandu❤

  • @user-pc1rx7uj3s
    @user-pc1rx7uj3s Місяць тому +2

    Odandaula munavomela banja ndinso kuwabelekela mwana ,osati chuma ai ngati bambo sadapange gongosolo chafa kwanu mai

    • @MikeMwale-bw1xw
      @MikeMwale-bw1xw Місяць тому

      Koma banja mukulidziwa inuyo kapena mukungolubwa?

    • @SteveriaNyalugwe
      @SteveriaNyalugwe Місяць тому

      Ndipo mwamunayo akanasiya wilu asanamwalire, ndiye ngati mwamunayo sanamugawire mwana wake alimoyo samamuwelengera. Amafuna mwana osati chuma

  • @AgnessMaumbo
    @AgnessMaumbo 23 дні тому

    Akafukule amunache ankamuuza kuti amupatsa chuma adzamupatse,vuto la tsikana amasiya chomwe apitira maso muchanya kwa zimuna aeni ake kkkkk,akamaona nkazi akuoneka bwino amaona ngati akumusamala ndi mwamuna nde kumakhala kuti ndipite nane ndizikaoneka ngati amene aja,osadziwa kuti munthu wamayi amazilombikira yekha kkkkkkk,kuphunzitsa kwabwino amene akuonera atsikana aphunzirepo sure

  • @marianyirenda
    @marianyirenda 20 днів тому

    Komano walembedwa ntchito mphaka kumasukilana ndi a bwana wosachita mantha mphaka kuvomeleza kuti mukwatilana yikhale mitala ndi mkazi wa bwana mmmmm koma azimayi muzikhala ndi mantha please

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 24 дні тому

    Nkadzi wa chiwiliyo chuma akanapasidwa ndi mamunawakeyo chifukwa chumacho ndi cha kubanja lalikululo mamuna wanzeru satenga wa kwa Nkazi winabkupitisa kwina akanapanga zawo nthawi imene amunawo Ali ndi moyo😢

  • @user-mx5cx3gl4h
    @user-mx5cx3gl4h Місяць тому +2

    Hule ameneyo 😂😂😂eyeyo amachayilila chuma cha bambowo chifukwa chake amakachindana ndi abwana ake 😂😂musamupase kalikonse

    • @user-og1nx7en7j
      @user-og1nx7en7j Місяць тому

      😂😂😂😂😂😂 ooooh?

    • @BrendaMwandumba
      @BrendaMwandumba 26 днів тому

      Ndie malemuwo si hule?

    • @user-mx5cx3gl4h
      @user-mx5cx3gl4h 26 днів тому

      @@BrendaMwandumba onse ndimahule,,,ndiye asavutise kuti amugayileko chuma,, chifukwa iyeso anali ndi nyumba yake,,,,amusiye kazi woyambayo akhazila patendele,,,

  • @HannockMesiwni
    @HannockMesiwni Місяць тому +1

    Apachumacho chinera kugawidwa ndipo nkhani iyi yikuoneratu chilungamo chake ngakhale mwana wamaiwa wakuluyo akuyakhula chilungamo ndinthu apase gawo lawo amai achiwiriwa

  • @FrankNyoni-pm3jz
    @FrankNyoni-pm3jz Місяць тому

    What was the final judgment ?

  • @HildaMachinjiri
    @HildaMachinjiri Місяць тому +3

    😮😮😮 ati ana akazi alibe ntchito nkhani ija waiononga 😂😂

    • @user-xo6th8bx2p
      @user-xo6th8bx2p 11 днів тому

      Ndipo kuyankhula bwinobwino koyambilira kenako nkudzangosokonezanso ekha 😅

  • @user-gu1id5xg6k
    @user-gu1id5xg6k Місяць тому

    Choyankhulila chizungu nd chan pomwe tonse nd a Malawi??

  • @OmexMainala
    @OmexMainala Місяць тому +3

    Maio ndiovuta amafunika nkazinzaoyo amupaseko chuma

    • @MgGondwe
      @MgGondwe Місяць тому

      Ayi asamugawiri arindi mwano 😂😂 Wang, Ono. Uyo

    • @GloryNyirenda-c3i
      @GloryNyirenda-c3i Місяць тому

      Ine sindikuona chifukwa chomugailira chuma , iyenso anali ndi nyumba yake ndiye ngati sanapange naye chitukuko kunyumba kwakeko awo ndi mavuto ake , asayangane za mnyumba mwanzake, and after all enawo komwe achoka ndikutali akufuna akhale ndi katundu ofana ndi iyeyo oti amupeza dzulo! Za mwana Ati asamala mpaka adzaziimire payekha .. nkhani ndiyoti apondeponde apeze zochita.

    • @chifundobanda6814
      @chifundobanda6814 Місяць тому

      amugawire Kuti watani
      akulu bwanji sapempha zawakwamkuluyo aaaaa she lost

  • @henrymwale8994
    @henrymwale8994 Місяць тому +1

    Kodi izizi zimakhala zenizeni kapena ndi mwa drama coz anthu ake ndimaona amodzimodzi

    • @SoniahMussah
      @SoniahMussah 29 днів тому

      Drama😅

    • @user-jg2py7jj8c
      @user-jg2py7jj8c 29 днів тому

      Ndi drama yomwe imaphuzitsa anthu zokhudza khothi, malamulo, kuweluza milandu

  • @DeviMono-gv6vz
    @DeviMono-gv6vz Місяць тому

    Aninkhidwe chuma mwanayu nayenso limodzi ndi amayi ake azimwa wamkaka eeee litima bwanji mayi akuluwa?

  • @CathyMasina-q5v
    @CathyMasina-q5v Місяць тому

    Koma nkazi wachiwiliyu ndoipa wadyela😢

  • @user-mi8cx2qz7n
    @user-mi8cx2qz7n Місяць тому +1

    Iwe nkazi wachiwiri ndi wopusa chifukwa court imafuna umboni munasaina pati kuti ndikadzafa nkazi wankulu adzakugaira chuma

    • @MikeMwale-bw1xw
      @MikeMwale-bw1xw Місяць тому

      Mukunama akanadziwa bwanji kuti adzayanbe kufa ndi iyeyo.

  • @ashadokhomzy5781
    @ashadokhomzy5781 Місяць тому +1

    Yalakwatu apa kaya tidikile final episode kuti zitha bwanji

  • @dyba-x9w
    @dyba-x9w Місяць тому +1

    muzimalizitsa mpaka chigamulo osamasiira panjira ai

  • @user-dg9bh2xo8x
    @user-dg9bh2xo8x Місяць тому +1

    Koma akazi olandawa ngokupangitsa munthu kugwila nyasi

  • @user-ym6xu3xt2i
    @user-ym6xu3xt2i Місяць тому +1

    Ama gawa chuma ndi a ku chimuna osati mnkanzi mzako ayi zimatero ndithu

  • @user-sd4jn8ef7e
    @user-sd4jn8ef7e Місяць тому

    ❤ Mai awa sakuyakhura mwanzeru'!!

  • @user-io2uw2me9f
    @user-io2uw2me9f Місяць тому +1

    Amugaileko mwanayo koma osat zimenezozo mesa anakwatila so komaso uyuyu wabereka boy akungoyenela

  • @user-bh7xq3wf1i
    @user-bh7xq3wf1i Місяць тому

    Zogawana palibe aliyense pamalo pake

  • @KondwaniHara
    @KondwaniHara Місяць тому +1

    Chagamulo bwanji?

  • @henrychikuse1543
    @henrychikuse1543 Місяць тому +1

    Uhule ulibe profit chemwali. Komaso kulibeko mau oti amuna athu koma amuna Anga. Mwana wanu ndiwakuchigololo ndiye mwana wakuchigololo sawerengedwa

  • @listonnantapo1670
    @listonnantapo1670 Місяць тому

    Tikudikira chigamulo. Chinapelekedwa, kapena sichinapelekedwe?

  • @neighbourfilms
    @neighbourfilms Місяць тому

    Sound track is too loud please

  • @jameswajumpha6790
    @jameswajumpha6790 Місяць тому

    Waiting for next part

  • @chimuemuechingagwe175
    @chimuemuechingagwe175 Місяць тому

    Milandu imeneyi imakhala yowona kapena amangoyerekeza?

  • @lazaruschitsamba8394
    @lazaruschitsamba8394 Місяць тому +1

    no ngati anafikila zintu atagwila njito alibe chake

  • @RobsaiSaidi
    @RobsaiSaidi Місяць тому

    Bwanji you don't fully finish your court trials... whats the point of not letting us know the judgement. I. USA they finish fully. We love watch such stuff

  • @RemitterFlik1130
    @RemitterFlik1130 Місяць тому +3

    Ndipo anthu musamangoti a agawe agawe muli inu mungapange zimenezo uyotu ndi hule apezaso bambo wina kuti abelekele mwana wa nkazi sinanga ali pa business yopangila ana kwa zibambo omwe akufuna ana osiyana m nyumba ine ndikuti asampase....

  • @judithchaima
    @judithchaima 27 днів тому

    Mwana wamkazi alibe phindu Mai uyu akuyankhula bwanji? Uyu uhule wake zimuonekera ndithu

  • @MCLoudZeka
    @MCLoudZeka Місяць тому +1

    chigamulo chikut bwanji tinveka

  • @AfonsoBenjamim-k6k
    @AfonsoBenjamim-k6k Місяць тому

    Munthu walembedwa ntchito chofunilanso abwana ndichani ? Musampase hule ameneyo

  • @TumpaleMsukwa-l4i
    @TumpaleMsukwa-l4i 29 днів тому

    Kma poti ana akazi alibe ntchitopo akurakwisa ana ndi ana zilibe ntchito kt ndiakazi or aamuna

  • @ConfusedAstronaut-qv6wq
    @ConfusedAstronaut-qv6wq Місяць тому +1

    You are excellent girl.

  • @user-jm7tv7rm7e
    @user-jm7tv7rm7e Місяць тому

    Azibambo muziwapatsiratu ma mg 2 gawo lawo musanafe

  • @KamongoNowa
    @KamongoNowa 19 днів тому

    Chuma chigawidwe basi

  • @mphatsokauta6387
    @mphatsokauta6387 Місяць тому

    palibe kumugawila koma kugawana...100% ya assets yo then awona anthu oyenela kugawana ndangati then aliyense atenge percentage yake. community of property ijayo

  • @bonfacekantwanje6223
    @bonfacekantwanje6223 Місяць тому

    Akuti akufuna chuma Cha chani? Koma guys😊

  • @KondwaniGumba
    @KondwaniGumba Місяць тому

    Ngati adali mkazi wa malemu ndikumuberekera mwana , akufunika kukhara ndi gawo la chuma Cha mamuna wawe. Ndikukhulupirira kuti pakutha pa khaniyi ikomera odandaula.

  • @IdrissahJames-gu2yo
    @IdrissahJames-gu2yo 25 днів тому

    Zinko nd Anthu ake....koma apopo plz plz 😢 Awapatseko Gawoo la Chumachoo plz plz

  • @SteveSangwa-tb7lk
    @SteveSangwa-tb7lk Місяць тому

    Wakuba ameneyo ku banjako anapitilako chumacho

  • @MagangaLeman
    @MagangaLeman Місяць тому +1

    Muzitipasilanso nthawi ya chigamulo kuti tizitengelapo phunzilo

  • @MonicaThocco
    @MonicaThocco Місяць тому

    Mwamuna wa mwini ndi wa mwini basi ,ndipo mwana ndi mwana posayang'ana kuti mwanayo ndi wa mkazi or wa mwamuna ,anali pa business acc wa ,aluza basi

  • @miryamkatundulu
    @miryamkatundulu Місяць тому

    Please men before you die, write your last testament and will so that life is not complicated.

  • @gracejere452
    @gracejere452 Місяць тому +1

    Mboni yufanana ndi step mom😂😂😂

  • @alnordtembo8930
    @alnordtembo8930 Місяць тому

    Yuleyo anamumangira kare nyumba yake naye nde chuma chakaicho

  • @ShamirahMakungwa
    @ShamirahMakungwa Місяць тому

    Munthu utha kuvomera mitala malingana ndinyengo mmene iliri...vuto ndimalemuo coz sitikuziwa kuti ankagwirizana chani ndiwantchito wawo akakhala awiri.kmanso ngati inali mitala mamuna amapanga equal popanga zithu.iwowo kod sanasiye will...

  • @rachelbanda-xh7iv
    @rachelbanda-xh7iv Місяць тому

    Agawireni chabe zapadziko izi ndizotsala

  • @user-zz4uj4yt7p
    @user-zz4uj4yt7p Місяць тому

    Balibe zogawana aliyense amagawa kantudu uyo ndi hule

  • @user-vu4cz1mt4f
    @user-vu4cz1mt4f Місяць тому +8

    Komatsu inu omwe mumapanga post muzimalizitsa mpaka kuchigamulo coz timaphunzilira momwemu

  • @AminaPhiri-pp9tw
    @AminaPhiri-pp9tw Місяць тому +1

    Kkkkkkkkkk koma apa zivuta