Raped by my Sister's Husband

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 11 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 247

  • @ruthchawinga3969
    @ruthchawinga3969 Місяць тому +10

    Mkhalidwe uwuwu ukuonjeza ofunika chilango abambowa😢maiwa ngati kuli kuteteza banja akulakwitsa akusungitsa chilango choti moyo wawo adzapanga regret mtsogolomu,akanakhala anzeru akanapanga support mwanayu osati kumuyipitsira mbiri😢Zachisoni kwabasi

  • @paulgodfrey3361
    @paulgodfrey3361 Місяць тому +9

    Rodwell, ntchito umaigwira adha, God bless you,
    And this man derseves unyolo

  • @Cee-H-Cee
    @Cee-H-Cee Місяць тому +4

    Mwana wamasiye uyu. Bambo alibe. Mukwizingeni mkulu ameneyu. Sister wake nkhaniyi waikulisa yekha. Akanaitenga bwino sibwezi mtsikanayi atafika potere kulankhura zambiri kwa Rodwell. Nyimbo ikhale yakuwaya nayeni

  • @ELESONKachale
    @ELESONKachale Місяць тому +10

    😢 sambi coz mwanayo anakakhala kut agwilizana sibwezi atawafotokozela chemwali akewo akulakwitsa sister wakeyo kuikila mwamuna wake kumbuyo .

  • @samuzymkwanya8490
    @samuzymkwanya8490 Місяць тому +16

    Ngankhale ataminula sichifuka choti amugwilire alangike amenewo

    • @GiftJulius-gx2kb
      @GiftJulius-gx2kb Місяць тому

      Ndipo anthu amaikila kumbuyo zaboza mwana asaminule uyu wakula poti munthu wamkulu akakhele ndi mkhuli zopusa ma neba opusa malo mothandizana kuteteza mwanayu

    • @tisungebandanyambo1448
      @tisungebandanyambo1448 Місяць тому

      Ndipo inu.... Olo mwana yo atakhala kuti amaminula as a responsible man amayenela kumuuza mwana yo or sister wakeyo kuti mwanayo azivala bwino

    • @patriciazacharia8896
      @patriciazacharia8896 Місяць тому

      Or atavala bum short palibe vuto akanali Mwana abbambo wopusa zedi

    • @eliffagondewe8214
      @eliffagondewe8214 Місяць тому

      To cut the story short bambo uyu ndi chitsiru kwambiri.. Mai naye ndi chitsiru kwambiri 💔💔💔

  • @tiflo2012
    @tiflo2012 Місяць тому +2

    I hope he has been arrested, this is a child..16 year old child!!!!

  • @GraceThawi-rp2vb
    @GraceThawi-rp2vb Місяць тому +3

    Bambo wa 40 years akakopedwe ND mwana wa 15 years🥺mwana wa 15 years anangakhale nchan chokopa mamuna? Bwanj iyeyo sanamuyankhule mwanayo ngat mwana wake kt azivala molongosoka abambo oputsa kmanso ccta wake alibe umunthu ngat kholo

  • @atupelesulaimana5138
    @atupelesulaimana5138 Місяць тому +12

    Achemwali akewo ndi achitsiru instead of helping her she is busy accusing her

  • @Frankkabotolo
    @Frankkabotolo 18 днів тому

    I doesn't matter that this child was dressing well or not him as a parent was supposed to displin her not to rape her..... it was my child or any of my relatives I would have taken matters into my own hands

  • @elizankankha84
    @elizankankha84 Місяць тому

    Doesn't matter whether she did something or not the fact remains that she's a minor and she went through a horrifying incident and she needs help

  • @reginamakowa7675
    @reginamakowa7675 Місяць тому +6

    Azipita kumudzi mwanayi umphawi sumapha

  • @MaryDmadeya
    @MaryDmadeya Місяць тому +4

    Mwanayo amawakonda assister akewo akanakhala Kuti anakakambilana zoti agonane ndi alamwakewo sanakawawuza assister akewo,komaso amayiwo azifuse Kuti Ngati Amuna awo agona ndi mlamwawo agona ndi akazi angati kunjako alandile chilango abambowo aphela Mwana ufulu

  • @FrankKambwani
    @FrankKambwani Місяць тому +1

    Munthu ukuweta mphaka ndipo mnyumbamo wasiyamo mphika wandiwo limodzi ndi mphaka udzapeza mphika wavubdukulidwa umangodziwiratu kuti ndi mphaka uja,koma chemweri amwanawa ndiwodontha zedi.Solution yake abambowo akasungidwe ku police mpaka mabungwe ndi court achitepo kanthu cfk report lati dzidachitikadi ndipo mwanayu apite kumudz ngakhale ndikovutika koma mtendere wa muntima ukhoza kukhalapo ngati alipo ofuna kwabwino adzimuthandizira alikumudziko.😢😢

  • @MussahDaud-w8o
    @MussahDaud-w8o Місяць тому +1

    My brother your doing great work, that guy must go jail for sure eishhhh

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick Місяць тому +2

    Koma m'bamboyi eeeeeeee ndi mfiti yoopsa ngati Chakwera mmmmmm 😢😢😢😢😢

  • @EdwardGeorgeKasabola
    @EdwardGeorgeKasabola Місяць тому

    Bamboyo akufunika unyolo basi koma tiyikileso Mr Rodwell ntchito mukuyigwila Ambuye azikudalisani

  • @HudBnda
    @HudBnda 7 днів тому

    Kumetsera ma statement wo mwanayonso akuwonetsa kuti mwanayo pa yekha ndi problem. Ndi khalidwe la Ana aja okuti ndi Amano akawadzudzula cholakwa amachita create nkhani yofuna kuthana naye/kumukhaulitsa kuti amvetse kuwawa kholo lake or munthuyo. Zinachitikapo ku mchinji mwana atamukaniza Kopitar ku show usiku , iye kuzemba usiku omwewo napita ku show Kuja. Anakagona komweko koma mmawa kutacha sanabwere panyumba paja.mmalo make anapangana ndi anzake kuti.akanene ku police kuti wathawa kunyumba chifukwa abambo are omupezawo anamugwilira. Ndipo anapita kuchipatala komwe anatsimikiza kuti wagonedwadi.koma chnsecho atagonedwa ku show komwe anagona kuja ndi munthu wina. Abambo anamangidwa.koma mwa chisomo nzake wa tsikanayu anakawulula komwe Ana awiriwa anagona. Ndipo atapanidwa anaululanso munthu weniweni amene adagona naye. Kom chifukwa chokuti abambo a mnyumbamu sankamulora kumapanga khalidwe lonyansa akuti adaaganiza zowakhaulitsa kuti Iye adzimasuka namakhala ndi ufulu oyenda usiku ngati wafuna. Nkhani zoterezi zikachitika pafunika pazikhala kafukufuku okwanira.Lero Ena Ali ku ndende pazifukwa zoti sadalakwe koma chifukwa cha Ana ankhanza ndi olimba mtima ngati awa. Tithokoze nzakeyu amene adabwera poyera ndikuulula komwe adakachita chisembwere chakecho komanso mnyamata amene adagona naye kuti adaavomera kuti adachita naye zosayenerazo usiku onse wa tsiku limenelo. Ndinena pano abambowa adawatulutsa ku sell komwe adawasunga.

  • @florencenyirenda2816
    @florencenyirenda2816 Місяць тому +1

    Azimaitu mitu yathu sigwila ,,moti mpaka mwana ogwilizana nawo angaulure ???

  • @lillahnmahuzahshabah5883
    @lillahnmahuzahshabah5883 Місяць тому +1

    Izi ndi nkhaza Mwana amulakwira,mamuna ameneyi she must be arrested

  • @missnevermind640
    @missnevermind640 Місяць тому +7

    Heartbreaking 🥲🥲

  • @janniferkachulu
    @janniferkachulu Місяць тому +1

    Umphawi mmmmmh siwabwino anta. Sorry baby girl. Ambuye alowelelepo ndithu.

  • @NancySayo-o6c
    @NancySayo-o6c Місяць тому

    Ndizowawa iziiii. Sister chonde komwe muli uko pitani kwa sister uyo mkamuteng.ndimwana wakwanu uyo

  • @dorisbwanali150
    @dorisbwanali150 Місяць тому +3

    😢😢 eeeeeeeeh mchemwali opanda mzimu, mphwako ukati anagwirizana,kuteteza banja kumeneko banja lake limenelo

    • @MercywagondweSalijeni
      @MercywagondweSalijeni Місяць тому

      Ndipo ndiopusa bwanji kuphera mwana future uku alaaaaahhhh

    • @dorisbwanali150
      @dorisbwanali150 Місяць тому +1

      @@MercywagondweSalijeni ndipotu amuphera mwana tsogolo fukwa chokonda gadafi mwxiiiiii

    • @MercywagondweSalijeni
      @MercywagondweSalijeni Місяць тому

      @@dorisbwanali150 stupid human being......zachabetu mwali

  • @ShantiMvula
    @ShantiMvula Місяць тому +1

    Amai akuikila kumbuyo amuna awo cholinga asamangidwe 😢akuona kuti avutika amai opusa

    • @ShownyYohane
      @ShownyYohane 21 день тому

      Kuteteza chiwiya akuti 😂😂😂 nakha akawamanga azidya kuti 😮😮

  • @RalphZambezi
    @RalphZambezi Місяць тому

    Zosakhala bho, nangano bambowa akamangidwa mwanawao waulumaliyu anthandize ndani? Mwamva kale kuti kwa mkaziyu mkomvutika mothelatu, mkaziyunso akuoneka kuti zitati zamsomonekela angalowele kuti? Nthandizo lake ndimwamuna emweyu, ngati moyo ukubvuta kwa anthu oti akugwira ntchito kuli bwanji enawa osowa pogwira,

  • @PreciousNanthambwe
    @PreciousNanthambwe 29 днів тому

    Mmakwana Big man ,pitilizani kuyigwira ntchito yabwino ngati imeneyi

  • @EmmaShillin
    @EmmaShillin Місяць тому

    Achemwali akewo ngopepera kwambiriii this is stupidity a munthu mwana akuwathandiza kulera ana aziterosoo zoona😰

  • @MarkMailosi
    @MarkMailosi 25 днів тому

    This is so bad malamuro agwire ntchito and akanakhala kuti anapangana mwanayu sakanawauza achemwali akewo akufuna agwiritse ntchito mzeru

  • @memorymghogho7933
    @memorymghogho7933 Місяць тому +1

    Kuwakopa...like men can't ignore n take another step....kupusatu uku

  • @GraceLobart
    @GraceLobart Місяць тому +2

    😢😢😢😢😢 alandile chilango khalidwe Ili lachulukila kwabwasi😢😢

  • @GoldieArchive
    @GoldieArchive Місяць тому

    Before interview, does the police know?

  • @anittahmazibuko2087
    @anittahmazibuko2087 Місяць тому +1

    Koma sister yo ndchitsru kwabas kufuna kusamala banja? Mot amuteteze mwana akuyankhulaso mopusa

  • @NancySayo-o6c
    @NancySayo-o6c Місяць тому

    Ndimwana uyo inu . Koma ali ndizelu siotse anganene kuti alamu achita izi . Thanks my sister mulungu akupatsa chitsowa chako

  • @tamalangoma2765
    @tamalangoma2765 Місяць тому

    Disgusting 😭😭 this is heartbreaking' why'?

  • @VioletMaseko-ys4cu
    @VioletMaseko-ys4cu Місяць тому +1

    Zogwilizana sungaululeso Inu aaaa !!!! anthu awa ndioipa

  • @AlinafeNkhoma
    @AlinafeNkhoma Місяць тому +2

    Zopangana angamutseke pakamwa?
    Mtima wanga wasweka😭😭

    • @RiteRoderick
      @RiteRoderick Місяць тому

      @@AlinafeNkhoma Etii etiiiii aaaaaa

  • @MwayiPhiri-f7o
    @MwayiPhiri-f7o Місяць тому

    Ngati nkotheka nkhani zotere maina muzipedza ongoimilira osati Leni Leni la ochitidwa chipongwe ( hide identity) both name and face.

  • @yewomhango-oz8bk
    @yewomhango-oz8bk Місяць тому

    Abambowa ndachitsilu kwabasi,mwanau xaka 16 ndi mwana.kodi mwana kuminula chikhale chifukwa choti amugwilile.😢

  • @EstherNgolleka-zs2fj
    @EstherNgolleka-zs2fj Місяць тому

    16 years???? Amangidweko abambowo coz sanasamale za udindo wawo pomugwililira mwanayo, azimai ambili amaikila azimuna awo kumbuyo khalidwe lopusali.

  • @InnocenceShabane
    @InnocenceShabane Місяць тому

    Anthu ngati ameneyo akufunika 15years in prison ,police ilowelerepo çhonde

  • @Slyvia-uu3wc
    @Slyvia-uu3wc Місяць тому +2

    Apolisi agwire ntchito yawo mamuna amangidwe palibe kutsamala banja pamenepo zimayi oputsa uyu,, kufuna kotani galu malo motsamala bale wako 😮

  • @RittaPhillip
    @RittaPhillip Місяць тому

    Chitidwe uwuwu ukumachulukira makomomu😢 cz mene ndikumuonera mwanayii sangapange zthu zokopa alamu ake angokhara alamuwo amamufuna mwanai

  • @PRISCAMAKHANGA
    @PRISCAMAKHANGA Місяць тому

    Sister wakeyo ndichitsiru sanganene kuti mwanayu amawakopa amunake really? Mwanayu wapanga report zomwe zamuchitikira koma iye akuikira kumbuyo mamuna zoona? Even atakhala kuti mwanayu amavala zazifupi thats not enough reason yomugwililira . Mamunayo amumange ndithu

  • @HappyKulemera
    @HappyKulemera Місяць тому +2

    Akuluake atsikanuyu ndi galu mamuna ukumuikila kumbuyo ngati chiyani zibambo amadzuka bwanji akugona ndikumakalowa nyumbaina umbon wamwanayi ugwilitsen tchito abungwe bamboyo amangwidwe wamuphwanyila ufulu mwanayo

  • @TinenenjiChandamale
    @TinenenjiChandamale 3 дні тому

    Romano achemwali akewo ndiopepera akuyenera kumangidwa limodzi ndi amunawo

  • @JaimenadrenadreJaimenadre
    @JaimenadrenadreJaimenadre 13 днів тому

    Menedzililimo mwanayo anagwilidzana.akuyakhula matso.mulimbe iyeyutu.anamuza.cct wakeyu chifukwa chamatha koma.amafuna iyeyu kuchindidwako.anakaulula mene amafusira chibwedzi.waulula.chifukwa.chamatha

  • @HaliJana
    @HaliJana 27 днів тому

    Vuto ndi Boma la Mr chikangawa chakwera waonongadi dziko kobasi,inu boma la DPP takukumbukani inu lamulo logwililila aaa akuluakulu kodi police ulikuti?

  • @AlinafeNkhoma
    @AlinafeNkhoma Місяць тому +2

    Koma ndalira😭😭🙌

  • @EricCanada-ig9xe
    @EricCanada-ig9xe Місяць тому

    Amangidwe Ameneyo bass aaaaaa zosakhara bwino kwa bass aaa zandinyansa bwanji 😢😢😢😢

  • @EdwardWanda-e4c
    @EdwardWanda-e4c Місяць тому

    Sister awawa azikonzekera kukwatiwa kachiwiri chifukwa banja lawolo latha (15y in prison)mwina adikira🤭

  • @MaryhGeorgeh
    @MaryhGeorgeh Місяць тому

    Ndipo a bambo anemenewa amagidwe ndimuthu oyipa kwambiri cc wakeyo ndichisur u kwambiri

  • @Odetta-e5n
    @Odetta-e5n Місяць тому

    Koma abambo amenewa bwanji? Nkhaza zimenezo ! Ufiti basi , alangidwe ameneyo

  • @JosophineSolobala-hp5ds
    @JosophineSolobala-hp5ds Місяць тому

    Some Questions abale aaah, zinamukonela?😮

  • @PatriciaAlomwe-oz8wc
    @PatriciaAlomwe-oz8wc Місяць тому +1

    Enafeso tareredwa ndi ma Ccter anakat azipanga zimenezo alamwathu bwez tisali pano kuvala makabudula timavalaso kuminula kosayamba abambowo ndi anyere za matenda akazi awo ndiopusaso mkaz wa mzulu sangasekerere zemenezo nose ndi amunakowo ndinu zisilu mbuz za anthu

    • @MilliamKatemba4-hn6hy
      @MilliamKatemba4-hn6hy Місяць тому

      Ineyo makhala ndi mlamu wanga ndiposo timanula kumen abambowo ngoipa alangawoso ndye anali okonda akazi kowophya

  • @atupelemposa4786
    @atupelemposa4786 Місяць тому

    Mwamuna wokhala ndi khalidwe logonana ndi ana achichepele atha kugonaso mwana wang'ono wobeleka wokha.
    Akuyenera kumangidwa abambo wopusawo.

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick Місяць тому

    Sister opepera zedi kukana M'bale wako coz chamamuna?? Aaaa banja nkachani mpaka ukadane ndi m'bale wako????😢😢😢😢😢😢😢

  • @ShownyYohane
    @ShownyYohane 21 день тому

    Kuskelela mchitidwe wausiru aa kpena akufuna kunkhwima kapena aaaa,ine litha kuthatu banjalo ansaaa!!!

  • @HarrisonMagwira
    @HarrisonMagwira 6 днів тому

    Kom banja ndichibale ndizosiyana iwowa adamukonda mwanayo mene akondera wawo

  • @JaimenadrenadreJaimenadre
    @JaimenadrenadreJaimenadre 13 днів тому

    Abambowotso.ndiwochititsa manyadzi sangamvulire mulamwawo akaseve.ukayidi

  • @user-wt6xx5jh2x
    @user-wt6xx5jh2x Місяць тому

    Kakhalidwe aka ndimaona ngati kanayamba kale chabe ana apano amaulula but if people could come foward I swear 90% of women have been raped by men who are supposed to protect them

  • @EthelChimaliro
    @EthelChimaliro Місяць тому +2

    Chimukazi chokonda zausiru kusiya mubare wake kumbakera mwamuna pazopusa

  • @BridgetKachepa-lu7gs
    @BridgetKachepa-lu7gs Місяць тому

    Ngati sister wakeyo akuikira kumbuyo amuna ake ndiye Kuti akudziwapo kanthu

  • @MordecaiKaliba
    @MordecaiKaliba Місяць тому

    Sitikudziwa zonse but ndikungokhulupilila kut zinakakhala zofuna mwanayi nkutheka sanakawawuza Chemwali akewa😢

    • @ElizabethMulinde
      @ElizabethMulinde Місяць тому

      Ndipo zoonadi sakanaululu ndipo ndiwachikondo mwana Yu ana ena sangaulule

  • @temwalerato
    @temwalerato Місяць тому

    Next time filter her voice as well... she's a minor hiding her face alone isn't enough!! She needs protection!!

  • @EstherKatandika
    @EstherKatandika 27 днів тому

    Ambambowo ndi woyipa mwanayo anamungwililila ndindithu kulakwa achemwali akewonso mzelu sanganene kuti zofuna ayi chikondi alive ndimbale wawo mwanayu adzipita kumudzi uphawi siupha munthu wakula bwanji akufika mmene alilimo zimenezi zikuchulukila kea zibambo ambiri

  • @GloriaKamphulusa
    @GloriaKamphulusa Місяць тому

    Where is this world going to?

  • @CHRISTOPHERMMAKIWA-mu8wn
    @CHRISTOPHERMMAKIWA-mu8wn Місяць тому

    Alamu akewo ndi mulukhu,sanavinidwe apolice amugwire

  • @chifundomitambo6810
    @chifundomitambo6810 Місяць тому +1

    M'chemwali uyuyu eish kubhakila mamuna kumeneko ai zikomo apolisi gwilitsani ntchito

  • @Wyson-bo3sp
    @Wyson-bo3sp Місяць тому

    Mwana mung'ono ngati uyu koma anthu ife nchani?

  • @EstherNgolleka-zs2fj
    @EstherNgolleka-zs2fj Місяць тому +1

    Sister opusa i fill sorry for the child

  • @mackgozambia
    @mackgozambia Місяць тому

    Watching from KATETE ZAMBIA 😢😢😢😢😢

  • @jamesapawo9361
    @jamesapawo9361 Місяць тому

    Ndilibe chonena 😢😢😢

  • @BakhitaKavalo-fc4hx
    @BakhitaKavalo-fc4hx Місяць тому

    Akanati akonza sakadakuuzani chemwali,,, ndinu oipa sister

  • @CHIMWEMWETAMBALA-p4q
    @CHIMWEMWETAMBALA-p4q Місяць тому

    Mayiyo ndi opepela akumuikila kumboyo mwamuna oipayo, mwanayo akanakhala kti amafuna sakanaulula mawu omaliza sister wakeyo ndi mbuzi ya munthu

  • @MariaSinjani
    @MariaSinjani Місяць тому

    Kugwira mbamva sizifunika kupupulumayi mwina akanafotokoza nthawi yomweyo akanathawa komano apa amagwidwe basi

  • @chifunirosaka9077
    @chifunirosaka9077 Місяць тому

    Nkhaza zoyipa kwambili zedi munthu ameneyu akuyenela kulandila chilango

  • @janemvubu7750
    @janemvubu7750 Місяць тому

    Bambo ndiopusa mwana sanapangane naye anachita kumgwira , koma mkulu wakeyo ndi chinsiru ,banjalo lamukomera motani kuyankhula zopusaso, bamboyo mmm akanamangidwa kuti enaso atengelepo phunziro, moti mwanayo anapasa naganozo ochuluka mu mtima mwake ,, 1

  • @shoosterspark.6305
    @shoosterspark.6305 Місяць тому

    Vuto ndi bamboyu alibe umunthu mwana wa masiye mwana oti amamusamaila mwana wake orumala.

  • @JenipharBanda-e4q
    @JenipharBanda-e4q Місяць тому

    Instead of kumuthandiza mwanayu Koma akuyikila kumbuyo abambowo Koma iiiiiii

  •  Місяць тому +2

    sister opusa ndi neba yemweyo.onse apite ku waya

    • @SandraGolowa-ww8mn
      @SandraGolowa-ww8mn Місяць тому

      Ndipo ndi atchitsulu ndili ineyo I can't do this to my blood sister 😊

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Місяць тому

    Kodi kumakhala kuuopa uphawi wakwanu bola kukhala ndi chigawenga😂

  • @ABASHACeeMW
    @ABASHACeeMW Місяць тому

    Koma kumudulir tsogolo mwana uku 😢😢😢

  • @mwaisibuni
    @mwaisibuni Місяць тому

    Mwanayu angopezeledwa lokhala ngati kumudziko sakukufuna

  • @khwesajunior5371
    @khwesajunior5371 Місяць тому

    Athu omwe amakwatilira mavuto eshiii aliso pamavuto kwambir ndipo ana Anu musamaatumize kumeneko

  • @ellafalinya4918
    @ellafalinya4918 Місяць тому

    Sister wake wamwanayu ndi mbuzi to be honest

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate Місяць тому

    Pita ukakhare kwamayi ako mwana lwe alamwakowo akupatsa matenda

  • @chinsinsimakhuwa1575
    @chinsinsimakhuwa1575 Місяць тому

    Tasugwidwako ndi azilamu anthu timavala chilichose abambo awawa angokhala chiwanda

  • @AlasonPaulo-ht7zb
    @AlasonPaulo-ht7zb Місяць тому

    Zandikhuza kwambili😢

  • @muzipasimphande8501
    @muzipasimphande8501 Місяць тому +3

    This is a child please 🥺,it's like you are blaming her and emphasizing on amaminula and it's her fault that's bad atsogoleri..The child was/is traumatized you can't expect her to be okay after everything or atakhala kuti anamva kukoma,she is underaged simple.

    • @MilliamKatemba4-hn6hy
      @MilliamKatemba4-hn6hy Місяць тому

      Kuyakhula kopusa uku mwana wanzanu ameneyo

    • @HenrySam-sq2yb
      @HenrySam-sq2yb Місяць тому

      Of course, this is a way to keep the conversation flow. It's not necessarily blaming her but this also helps the girl to disclose more on the bad behavior of her in law.

  • @JohnMilo
    @JohnMilo Місяць тому

    Nde nkuluyo wamangidwa?

  • @YasinMmadi
    @YasinMmadi Місяць тому

    Iyi ndi ntchito ya ma NGO kuti ayere mmaso mmamidzi ndi mma nyumbamu Ana ambili akudzunzika koma sama ulula chifukwa Cha mantha kotero mwanayo aloledwe adzipita ku mudzi komanso akakhale mmanja mwa ma bungwe adzikamuthandiza mwanayo kuti akapitilize maphunziro

  • @MalitaKapesi
    @MalitaKapesi Місяць тому

    Apite kumudzi kwao mwanayu umphawi sumapha akakhala abambowo alandile chilango bs

  • @atupelemposa4786
    @atupelemposa4786 Місяць тому

    Mwanayu apite ku safe home

  • @johnssanamah1408
    @johnssanamah1408 Місяць тому

    Ngakhale mwamuuza kt ayang'ane kumbali koma nkhopeyo ndi dzina tikulidziwa komanso ana ama 2000 pena amatha kuchimwitsa munthu.....mwina potsuka mbale,kukolopa amatunura heavy ndye ndi mphamvu ya chakumwa eeee anangoona kt eeeeee

  • @eliffagondewe8214
    @eliffagondewe8214 Місяць тому

    Bambo yi amangidwendinthu this is abuse..

  • @RiteRoderick
    @RiteRoderick Місяць тому

    Kuphaa mwana wamng'ono 😢😢😢

  • @BrendaDimba
    @BrendaDimba Місяць тому

    A chimange chibambocho mwanayo wachepa 16yrs

  • @GiftJulius-gx2kb
    @GiftJulius-gx2kb Місяць тому

    Ndimwana uyu sikuti amabisa mzelu zachibwana

  • @liliansembereka
    @liliansembereka Місяць тому +1

    Amangidwe mzimbamboyonso

  • @LuciaJames-xh3ms
    @LuciaJames-xh3ms Місяць тому

    Zimai opanda zimu or banja litakoma bwanji mpaka kumusi kulila barewako zikhare zogwilizana anganene aaaah Mai oipa kwabasii