Kodi Achimwene a Charles Sulumba muli bwanji? Ndine kuno chemwali wako Bethsider mkazi was malemu pastor Tavares, Kodi mukudziwa kuti Arch Bishop Zani akudwalatu and akazi awo malemu Agnes Zani anatisiya. Chonde mutenge may details anga ku chokera kwa mwana woopsya the DC you know how he makes jokes with the sense of humour. Where are you now still in Angola, Namibia or South Africa Hilbrow theatre are you still preaching there as a bishop? Please greet mai busa Pink and tell her tamusowa and a a onse. It was nice seeing you here on this plat channel.
Tili mmavuto chifukwa cha inu Akalindo ndi achina Ntambo,ena mwa amalawi osauka ndiokwiya nanu chifukwa munwalozera njiraya ku bagamoyo mmalo mwa ku canane
Mwana Oowooopsaaaa kwambiri

I like this guy, he is a principled man
Bon kalindo, Timothy mtambo,trapence
Anthu omwe munasokoneza dziko pochititsa mademo
So lero don't fool us
I used to underestimate Kalindo's IQ. This interview left my mind blown away.
Big mani katundu amakwana mwana mlomwe nadya nakoka😊
Amangidwe onse. Ku USA anzathu sasekerera zopusa. Trump ataomberedwa khutu, mkulu wa asirikali ake anakakamizidwa kusiya ntchito polephera kuteteza former president. Kwathu kuno VPkufa pangozi yosamveka koma anthu tiri duuuu kupsetsa mtima kwake.
Yamba ndiweyo ma demo-wo
Uzani asilikali anu kuti atulepasi udindo chifukwa apangisa ngozi. Learn to differenciate things. Ngozi ndi chiwembu ndizinthu ziwili zosiyana kumakhala ndi umunthu.
Mr kalindo zimene mukufotokoza ndi zoonadi ndipo ndikugwirizana nanu
Bodza ndavapo ndilakuti anthu amene akupita ku lsrael akukagwira ntchito zaukapolo
Ndimakunyadirani mukutimirira
Mbava za ndale😎😎
Yes, they should revisit their manifesto.
Ndiwe dolo kalindo
Tili mmavuto chifukwa cha inu Akalindo ndi achina Ntambo,ena mwa amalawi osauka ndiokwiya nanu chifukwa munwalozera njiraya ku bagamoyo mmalo mwa ku canane
Ulemu wanu Mr Dc
The Dc mumatiimilila ❤❤
Passionate guy akhalitse bon kalindo
Chakwela akukuenela kumangidwa walephela
Koma Kalindo ali ndi mfundo,,odana ndi uyuyu ndi mfiti Komanso Chitsiru
Koma ichichi anapanga
Power ❤
Massive
Mwini kung'alula
Boooooon kalindo katundu
Mapensioers akuvutika yankulanipo akalindo
Mulungu amuteteze Kalindo
Izo ndiye zoonadi zake
The DC
Umu muli nzelu The Dc
The DC good talking
Kalindo ndi hamala ya 100 pounds
Ndizoona ndege siyingayende opanda black box.akungonamiza amalawi kuwatenga ngat amalawi opusa
Born kalondo uyu samaopa ngona .uyu kumuponya mungono .ngona siyingamudye ayi .mbanga weniweni
Kamuzuso ankamuteroso anthu Pano ali kutiko? Azaziona!
And Chakwera akamakuona iweyo amatsegura nawe mmimba 😂😂😂
The DC bigman wamkulu ❤ ❤ ❤
Dc anavaya
Boni kalindo akantundu kkkkkk wandisekesa penapake, dziko likusowekera anthu onthandizana naye mnyamatayi dziko likupita ili tiyeni tilivere chisoni
DC akunenepatu
Ndipo zoona 🎉
Bon ndiwe president waaamphawi ndizoona😅
Koma Nizoona ayakhe mlandu imeneyi
Fire
The DCcccccccccccc cc 🔥🔥🔥💪
U president ukunika apa basi
The dc
Tisachedwepo chakwera wapanga 0 😂😂😂
Koma ichichi ndi chilombo😂😂😂😂😂😂😂😂😂.
Abwana tipatse u vice wa president wa anthu osauka😂😅😅😅😅😅😅😅😅😅
Kkk DC akuti zero pa 10
🎉🎉🎉
Boza lokhalokha ingopitani ku DPP shut up inu timakuziwani ndinu a DPP
Galu iwe
Ndimakina
the DC dangerous
Kalindo osaopa apha anthu ndi iwowo.mcp chipani chamagazi
Kkkkkk, akanatsala awiri okha basi.
Kucheza kwapamwamba kwambiri
The Dc!!!!!!!! 😂😂😂😂
Ku ukapolo????
Kkkkkk zoona
Kalindo sazatheka😂😂😂😂😂😂
The DC
Atate