Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
No need to blame apa.... 🔥❤😂
Ati a mec aja akubwela kkk
GOGO chalo
Pamalao ngat yaw ot zikulengezedw zinth zofunikir musamakond kuik nkhalamb ngat iz taikan achin navich kape achin ben phir osat ngat midhala ngat imenei taoneran ku mcp momwe anzanu akuchitir
Kodi dpp basi tizingopitiliza kusunga magogo tawonani achapondawo akulephela ndikulankhura ammmm chipani cha dpp ndimavuto akulu apaseni anyamata udindo pls asaaa kkkkkk
Mukuoneka ngti mwalawakotu cheif
Kodi ku dpp kunangonzaza zimbutuma zosaziwa kuyakhula eti
Mandala maso muli nawo Koma gogo zirenje kkk
Chaponda tabwelezani chimanga Mwati 35 pin mukunama chimanga chili 45to 50 pin
Kkkk komatu amalawi mwatitora kwambiri, mbava imeneyi ikuwona ngati tinaiwara zomwe inatipanga zija iri nduna mu boma la Bingu?
Chimene chinatsala kuti mube mbomamo ndi chani?
Akulu inu ndachitsilu kwambiri kukalambako ndkumene kukuyakhulisa zopanda mutu
DPP guys u're supporting stupid nonsense munthu akukanika kulongosola akuchita kumuwuza zochita live