Be strong 💪🏼💪🏼my brother Kamangira inuyo ndi bulinji yathu yoti tiwolokele ife Amalawi tonse kuti tipeze mtendele mu dziko lathu May God help us and brother Kamangira to achieve our struggle 😢😢
In each and every working environment there are two types of people:selfish and selfless,so you are one of the selfless persons in our country.keeep it up.
these stories eishhhhh now ndumvetsetsa mmene zimakhalira ...zimadabwitsatu zinthu zake....olo nkhani ya witika ,kunkuyu why is it taking sooooo long .......nkhani za sata....chunala.....TPIN case......batawalala.....amwenye onse cases dropped zoona?
You are the best of the best Counsel❤❤❤
Big up brother kamangila. We are together
Power keep doing good job bro respect always bro a gift from God
Watching from capetown bro kip doing good work
Long live kamangira God bless, and protect you wherever you shall go our brother your a great man sended by the almighty God
Be strong 💪🏼💪🏼my brother Kamangira inuyo ndi bulinji yathu yoti tiwolokele ife Amalawi tonse kuti tipeze mtendele mu dziko lathu
May God help us and brother Kamangira to achieve our struggle 😢😢
In each and every working environment there are two types of people:selfish and selfless,so you are one of the selfless persons in our country.keeep it up.
U are the best bro , keep up
Bravo brother kamangira🔥🔥🔥🔥🔥
International rescue lawyer ,you are the best brother ❤❤
Bravo man🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥 you are made🎉🎉
Iweyo unangobadwa kuzawombola Malawi munganjo yamoto🔥🔥🔥🔥
With great power, comes great responsibilities, l know you my brother , once a seminerian,always a seminerian .
Jah guide kamangila.
i said it .....mzikamanda,chikopa,kapanda,madise mwandikhumudwitsa koopsa ...i think malawi alibenso chikhulupiliro ndinu oyipa kobasi.....
Tikudalira inu big, langizo bola tisazamve kuti Boma lakupatsani kanthu ndicholinga chokutsekani pakamwa, mudzatikhumudwitsa zedi
❤❤
💪💪💪💪💪💪💪
Mukuyenela mutane nawo and nonsense opondelesa akujayila mmacotimu Komaso inu mumayenela kukala mkulu wa ACB kuti mutane ndi ndi anthu akuba bomawa
We soak him in the blood of Jesus may he not seen when they are trying to find him in Jesus Name
Be strong bigz mumakwana
Live and clear
Loud and clear
We play for u don't be afraid brother
Bwana Lawyer, Kodi nkotheka kuti muitanitse Press Briefing kuti seriousness yazonsezi mukuululazi zinveke mosindika ku Dzikoli
Another Pangolin 🔥🔥🔥
Be strong ❤❤❤❤❤
Kod ndi live eti?? Go on Counsel Kamangira
Traore wa Malawi ❤❤❤🎉🎉🎉🎉
Keep up brother
these stories eishhhhh now ndumvetsetsa mmene zimakhalira ...zimadabwitsatu zinthu zake....olo nkhani ya witika ,kunkuyu why is it taking sooooo long .......nkhani za sata....chunala.....TPIN case......batawalala.....amwenye onse cases dropped zoona?
Thumbs up!!
We can hear you boss
Mumakwana a kamangila kumayakhula mu chizungu choncho
Bravo Bravo
Viva I would like to meet you bro in life
Ka soundiko kumabwenzako next time
Zamveka 🙏
Tikudalira inu big
Hand sam ndi mtima omwe
Inuyo mwatiimilira
i want to meet you my brother i have a case
bwana ndinu munthu olimba ntima kwambili
guys tisamangochemelera koma tiyeni tizuke limodzi pipes mphamvu Zili mu anthu amalamuro tatopa nawo
Back ground music so distracting abale.
❤