Limpopo Ntanyiwa kufikano mu studio ndi Nkhanga zaona lero pa 25 JULY 2024

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 жов 2024

КОМЕНТАРІ • 191

  • @RoseChiphiri-ts8jx
    @RoseChiphiri-ts8jx 2 місяці тому +7

    I love ❤ Ntanyiwa 😊 watching from Israel kumunda

  • @originalblack100
    @originalblack100 2 місяці тому

    Comrade Mtanyiwa, pa Limpopo FM KKKK. Kumenya Kugwetsa. Continue sharing the real real chilungamo zowona chiyende ngati madzi. 💌💌💌💌.

  • @MolosonMisitala
    @MolosonMisitala 2 місяці тому +11

    Amalawi gwilanani manja asakukopeni ndi ndalama nthawi yatha kl munthutu umafunika kumpasa zelu osati ndalama nanga zikakutherani mudya chani

  • @MaideLester
    @MaideLester 2 місяці тому

    I support and follow anything Bez it's one of my favourite radio

  • @GwambazohSures-mz4dg
    @GwambazohSures-mz4dg 2 місяці тому

    Good explaination Mr ntanyiwa zooona zokhazokha we are in poor Government states

  • @JonesBenNgaiyaye
    @JonesBenNgaiyaye 2 місяці тому

    May the good lord keep you,bless you,and bless Malawi and Ntanyiwa

  • @philonampha
    @philonampha 2 місяці тому

    😂😂😂😂😂live from capetown, umakwana mtanyiwa❤❤❤❤❤

  • @RhoneckJones
    @RhoneckJones 2 місяці тому

    Limpopo fm With Ntanyiwa is my dosage.

  • @DavidJackson-ox4xm
    @DavidJackson-ox4xm 2 місяці тому +14

    I support Limpopo FM with Comrade Mtanyiwa

  • @AARONCHISUKAMZION-we3vp
    @AARONCHISUKAMZION-we3vp 2 місяці тому +2

    Ife tikuthokoza a Mtanyiwa mukutisegula mmaso,chinthu chowawitsitsa kuti ndalama akumwaza koma anthu mumizimu ovutika ndiambiri development izikhala ya community osati kupereka *5000* Kwa munthu akasova nayo chani pa family .Akuononga ndalama zochepetsera mtengo wazinthu kuti zisikeko kuti anthu akhale ndi kuthekera kokhala pamalawi kuchokera mumamidzi mpakana anzathu kutauni.
    Koma NDIYE ndalama NDIYE zimaphweka.
    Komanso Moyo ukakoma kwambili ziwa kuti imfa nayonso yayandikila.Ukatambatamba uziyang,ananso kumene wachokera😢😢😢

  • @MosesKalenge
    @MosesKalenge 2 місяці тому

    Live from kongo. Mr nthanyiwa. umakwa ❤❤❤🎉🎉🎉🎉

  • @lutankaomba-jr5iz
    @lutankaomba-jr5iz 2 місяці тому +1

    Watching from Ghana

  • @ganizanimanyamba
    @ganizanimanyamba 2 місяці тому +1

    Mr, ntanyiwa ndiwenkatundu more 🔥🔥🔥🔥🔥🔥 tiyenazo

  • @DKMWALE-ew3lp
    @DKMWALE-ew3lp 2 місяці тому

    Ntanyiwa go on!!!!!!!!!!!!!

  • @jfj-bu5wz
    @jfj-bu5wz 2 місяці тому +2

    Limpopo FM emeeeeeeeeee😂😂😂❤

  • @SellinaSanena
    @SellinaSanena 2 місяці тому +1

    Keep the fire burning a mthanyiwa

  • @peterlowole7841
    @peterlowole7841 2 місяці тому

    More fire comrade

  • @Raph-kayRaph-kay-g5v
    @Raph-kayRaph-kay-g5v 2 місяці тому +5

    Comrade mntanyiwa pa rimpopo efyemeeee kkkkkkkk ine kumva kukoma

  • @YasinMusa-ym8lp
    @YasinMusa-ym8lp 2 місяці тому +2

    Ulemu wanu boss❤

  • @MandalaChaona
    @MandalaChaona 2 місяці тому

    Koma Mukutchukatu Anyamata a Chikangawa.. Lero ndinu woyera pakuti Zanu mzobisika . Komabe Malawi wadziwa Kuti inu Munapha ndipo imfa zonse za Amalawi anali mu Ndege ndinu Chikangawa boys.
    Zochita Zanu ndi maumboni okwanira.

  • @SaudhaKatete
    @SaudhaKatete 2 місяці тому +2

    Limpopo ndi Mr Ntanyiwa keep it up

  • @KennedyPhiri-h9h
    @KennedyPhiri-h9h 2 місяці тому +2

    You are best welcome back

  • @DaveDambo
    @DaveDambo 2 місяці тому

    Limpopo FM ♥️🔥😎

  • @EmmanuelMpalagule
    @EmmanuelMpalagule 2 місяці тому +1

    Eeeeh koma mkhanga ija ndiopsa panopa zafka pot ndkaona mkhanga ndkumasintha njila kkkk kuopa kuyaluka

    • @spargomw
      @spargomw 2 місяці тому

      Kkkkkkkkkkkkkk😂😂

  • @Pangolinimw
    @Pangolinimw 2 місяці тому

    Ntanyiwa❤❤❤🎉🎉🎉

  • @savinapili7185
    @savinapili7185 2 місяці тому

    musamachoke pa Limpopo atanyiwa bandle yanga ndimagulila inu

  • @MaggieKaufa
    @MaggieKaufa 2 місяці тому

    Go ahead Comrade Ntanyiwa with Limpopo fm

  • @jonas-xh4hz
    @jonas-xh4hz 2 місяці тому +1

    i support limpopo fm becoz tells us true issues

  • @kettiemkweu4528
    @kettiemkweu4528 2 місяці тому

    Manganya akufunika dzina Lina ngati a Chikangawa Chifunga

  • @FrancisThindwa
    @FrancisThindwa 2 місяці тому

    Limpopo woyeee

  • @ChisomoBanda-g5s
    @ChisomoBanda-g5s 2 місяці тому +2

    moto kubu 🔥🔥🔥🔥🔥

  • @alickziba6756
    @alickziba6756 2 місяці тому +4

    Eish!!! Ndakapezelera.

  • @John-e2v4l
    @John-e2v4l 2 місяці тому +3

    Musamasowe a comrade mtanyiwa. Bundle yanga ndimagulilla inuo

  • @HalimaDamiano
    @HalimaDamiano 2 місяці тому +2

    More fire ntanyiwa

  • @PETERSINKADZIWA
    @PETERSINKADZIWA 2 місяці тому

    Yudasi sanachite bwino. Pepani Mai Mary Chilima chifukwa chotaya wachikondi wanu. Ambuye Ali Nanu Nthawi zonse

  • @SilungweJoyce
    @SilungweJoyce 2 місяці тому +2

    Comrade Mtanyiwa woyeee,inu mumakwana biggy

  • @EllardHolla
    @EllardHolla 2 місяці тому +2

    Ife timamva kukoma ndi Limpopo FM kuchokela kuno Ku London

  • @HalimaShafie-o7g
    @HalimaShafie-o7g 2 місяці тому +3

    Ntanyiwa ❤❤❤

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 2 місяці тому

    Limpopo fm forever ❤

  • @LamieTiger
    @LamieTiger 2 місяці тому +5

    Balaka athu ake sioputsa siogona putsi chakwera sangawatole

  • @savinapili7185
    @savinapili7185 2 місяці тому

    mumakwana mr comred

  • @SydneyMwale-u9w
    @SydneyMwale-u9w 2 місяці тому

    Wayonda kale chikangawa chakwera kkkk ndiyeno wafa kale

  • @zimmekapachika6784
    @zimmekapachika6784 2 місяці тому +3

    Welcome Welcome 🙏 🤗 ☺️

  • @GiftBanda-fn6si
    @GiftBanda-fn6si 2 місяці тому

    Big man

  • @PetroJack
    @PetroJack 2 місяці тому +4

    Ntanyiwa ndi kawawa❤❤❤

  • @StainMulewa
    @StainMulewa 2 місяці тому

    Mmakwana mtanyiwa tamava zambl

  • @ErnestChansa
    @ErnestChansa 2 місяці тому +1

    Tambala wakuda ndi zima fiti zowopsa manyi mcp

  • @chifundochiphwanya6859
    @chifundochiphwanya6859 2 місяці тому +3

    Chilungamo chiyende ngati madzi

  • @giftmasenti5732
    @giftmasenti5732 2 місяці тому +1

    Ntanyiwa uzithako or 3hours pa Limpopo FM

  • @AubreyChiyaya-ty8ge
    @AubreyChiyaya-ty8ge 2 місяці тому

    Ndikumudziwa ndi wakwathu uyu ndi zoona zomwe mukunenazo

  • @ZionekaMember
    @ZionekaMember 2 місяці тому +3

    Best Radio

  • @FarookHope
    @FarookHope 2 місяці тому

    Zooonadi boss

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому +3

    More fire timakukondan

  • @ChristianMtambalika
    @ChristianMtambalika 2 місяці тому

    Mwaona zomwe timanena zinja manganya ndi sikaliyoti analandira ndalama kupereka chilima ndiye poti yudas anazikhweza yenkhq tiyeni tionere mathero ake 2025

  • @watsonmhango8794
    @watsonmhango8794 2 місяці тому

    Ndalama za NEEF a amangawana andale wokhawokha,NEEF zikupindulila a Malawi, mukutiwongela misonkho,Thesani NEEF basi

  • @JohnGreen-v8f
    @JohnGreen-v8f 2 місяці тому +1

    Koma ndikupephani kuti mupange njila yoti anthu amene alibe ma 4n yopanda fb kuti nawoso aziva nawo

  • @GrayJumbe-o3l
    @GrayJumbe-o3l 2 місяці тому +3

    Kwachema uku!

  • @MiddayDeleza
    @MiddayDeleza 2 місяці тому +1

    Anthu akumudzi kwathu mwachita bwino osapitako, bola osatengeka ndi ndalama kukubweraku

  • @CostanceLalli
    @CostanceLalli 2 місяці тому

    Hahahaha koma kuli zinthu abale inu mulungu ndi wamphanvu

  • @chirwaellace1093
    @chirwaellace1093 2 місяці тому

    Kamanganya koipa ako ka zakeyu yudas

  • @AiameAdamo-su1nt
    @AiameAdamo-su1nt 2 місяці тому

    Tili nganganga pambuyo panu a Limpopo FM.

  • @Amgwagwa
    @Amgwagwa 2 місяці тому +1

    Ndemwati chinkweza mau kkkkkk

  • @CosimassKalula-x5t
    @CosimassKalula-x5t 2 місяці тому

    Timakunyadilani antanyiwa mulungu azikudalitsani chifukwa mumatiimilila

  • @YellowmanMalawi-qe8zh
    @YellowmanMalawi-qe8zh 2 місяці тому +3

    Manganya sopano

  • @FrancisMazamba
    @FrancisMazamba 2 місяці тому

    Mulungu azikusogolerani amutanyiwa lfe timakunyadilani kwambiri

  • @lyiemanganjira9708
    @lyiemanganjira9708 2 місяці тому +11

    Ndipo timakunyadirani kwambiri,, comrade Ntanyiwa

  • @JemTrucking
    @JemTrucking 2 місяці тому

    Viva tanyiwa ndi nkhanga za bona 😂😂😂

  • @YahayaKondwan-mo8hu
    @YahayaKondwan-mo8hu 2 місяці тому

    Mmm koma manganya iyeyo sadzafa kodi komwe kwatsala tchile mkomwe kumapita moto

  • @FarookHope
    @FarookHope 2 місяці тому

    Umakwana boss

  • @Jonas-v8y
    @Jonas-v8y 2 місяці тому

    9:23 l❤❤❤ ntanyiwa ndagwada pamaso panu B.I.G

  • @MaxWell-d7o
    @MaxWell-d7o 2 місяці тому

    Ntanyiwa woyeeeee

  • @henrykaunda5141
    @henrykaunda5141 2 місяці тому

    Mtanyiwa ndiwaboza,Kodi Kale analikut kut panopa ndipamene aziti amadama ndi zinthu za fake..

  • @SaulosMbuna
    @SaulosMbuna 2 місяці тому

    Kuno ku Peru....Olimpopo

  • @bernardnambwe7753
    @bernardnambwe7753 2 місяці тому +1

    mbambande

  • @JosephAlick-s8e
    @JosephAlick-s8e 2 місяці тому

    Boma lilibe kothawila ili😂😂😂

  • @GospelSoldiers-sr7np
    @GospelSoldiers-sr7np 2 місяці тому +4

    Koma kumangoyankhura pa social media sikusintha zinthu ayi....nkhani ndi pa ground basi kuti zinthu zisinthe

  • @henrykaunda5141
    @henrykaunda5141 2 місяці тому

    Audio singasinthe zinthu komano nwelani ku Malawi kuno tizimvutikira limonzi osat pakamwa pokha ayi

  • @christopherbanda4698
    @christopherbanda4698 2 місяці тому

    Michael usi ndi oipa tikudziwa zonse aululeni musatope

  • @MonyaNtchona
    @MonyaNtchona 2 місяці тому

    Chipani cha utm achisiye ndi agalu anamupereka ausi koma anathawa kale pano akufunaso chaniso

  • @AdamMbwana-pj6jw
    @AdamMbwana-pj6jw 2 місяці тому

    Keep it up mtanyiwa

  • @ElizabethKazambwe
    @ElizabethKazambwe 2 місяці тому +9

    Ife makutu amangokhala kunjira kutchereza za ntanyiwa ngati inu kulibeko ine sinitaegula limpopo

  • @JimmyMhone-b5p
    @JimmyMhone-b5p 2 місяці тому +2

    Dziko la lazarus ndi anthu ake akusangalala koma a Malawi akuvutika

  • @MusaMajudu
    @MusaMajudu 2 місяці тому +7

    Musamasowe choncho antanyiwa❤❤

  • @chrisgremu740
    @chrisgremu740 2 місяці тому

    Ngati ndalamazo ndi za boma ndiyekuti ndizawoso anawo

  • @dumisanimoyo3152
    @dumisanimoyo3152 2 місяці тому

    Ntanyiwa plz ungoyika kanyimbo kaja ka paul subili (ndilekeni ndinene chondifikila chindifikile

  • @Mervic-vm8eo
    @Mervic-vm8eo 2 місяці тому +1

    Mwabwera inuyo BIGY🔥🔥🤣🤣

  • @KendalBonongwe
    @KendalBonongwe 2 місяці тому

    Yose 🎉🎉🎉

  • @JaneNgwira-d7t
    @JaneNgwira-d7t 2 місяці тому

    Rimpopo femeee ni Rimpopoo

  • @BlessingsTembenu
    @BlessingsTembenu 2 місяці тому +1

    Ayerekeze manganya kupanga zakumatako zakezo tiwone kuti afika nazo pati,kachitsilu kamunthu kameneka

  • @FloridaMakwinja-eq2ek
    @FloridaMakwinja-eq2ek 2 місяці тому +1

    Malangizo anga ndi oyi
    Musamasowe PA radio
    Enafe mumatipatsa phuma
    Timaganiza ngati anthu Oyipawa akumangani😂😂😂😂😂

    • @AnnieBanda-rb2dk
      @AnnieBanda-rb2dk 2 місяці тому

      Agalu awa opusa amangomanga aliyese agalu amenewo

  • @GeorgePhiri-ub2of
    @GeorgePhiri-ub2of 2 місяці тому +2

    Dpp pitani pagalaund kapangeni kampheni akitivisi awa angokudyela ndalama umboni mwauona kale masakho akukaronga analakhula zambili omwewa kubwela chisakho mcp kuwina kumangochi bt chimodzimodzi basi muli mtanyiwa wasowa zoona ?

  • @JumanKanjala
    @JumanKanjala 2 місяці тому

    Bwana mumatiyimilila koma bwan musamachuluse nyimbo pls

  • @BraghtYohane
    @BraghtYohane 2 місяці тому

    Ndioipadi usi ukalowa maso umawawa ameneyo achoke azipanga masewelo Ake omweyo ndiwamphasulo ameneyo mpando umenew utha azipezera sugar masewelo omweo muthu wakeyo opanda fundo ngati uyuyu mmmmm waboza iweyo usi iweyo

  • @RossPanganani-l9s
    @RossPanganani-l9s 2 місяці тому

    MCP ichoke pamodzi ndi chakwela alibe usogoleli

  • @tauhidtimba
    @tauhidtimba 2 місяці тому

    Athu amene avotera mcp kuno kumangochi analonjesedwa kuti akangovotela mcp ndikuwina asapazidwa wina aliyese tumba la ufa lolemela 50kgs munthu aliyese ndipo antu oposa 872 analandililatu matikiti aufa anawawusa anthuwa kuti kungowina mcp ntawi yomweyo anyamuke tikiti mmnja kukatenka ufa kunyumba ya kasala wa mcp 50kgs

  • @christopherbanda4698
    @christopherbanda4698 2 місяці тому

    Galu ameneyo

  • @PatrickSomanje
    @PatrickSomanje 2 місяці тому +2

    Manganya ali ngulu la chikangawa oyipa kwambili

  • @ElizaGedion
    @ElizaGedion 2 місяці тому

    We loves u

  • @MerryWayson
    @MerryWayson 2 місяці тому

    Welcome welcome Mr Mtanyiwa timakunyadilani tili Pano chifukwa cha inu

  • @ChimwemweSuluma
    @ChimwemweSuluma 2 місяці тому

    Amaoneka kuchenjeretsa a Michael usi