MICHAEL USI WAYANKHULA IZI KU CHIRIMBA LERO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 4 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 38

  • @user-zq3uf5bc8v
    @user-zq3uf5bc8v Місяць тому +3

    Kodi akanakhala amakonda skc akanavala jezi ya national team asatipusitse ameneyu

  • @robsontyg3928
    @robsontyg3928 Місяць тому +2

    Bwana wanga Mr Usi ulemu wanu

  • @sangwasa
    @sangwasa Місяць тому +4

    I dont understand why play that boring music, it's difficult to hear the message

    • @bensonmariomario4806
      @bensonmariomario4806 Місяць тому

      That is Y akuti makosana they are not good in news reporting Kom Za music basi

  • @KikaImran
    @KikaImran Місяць тому

    I solute Bwede (the Noma supporter) munapeka nyimbo zomwe anthu akuzigwiritsa ntchito ngakhale ku zipani. Anthu mpangeni support Bwede ndi kenakake

  • @genesismbewe
    @genesismbewe Місяць тому

    I love u our VP... chilima's choice no wonder

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b Місяць тому +2

    Mudziti Mulungu kudzera kwa Chilima anakusankhani inu, odya naye mbale imodzi ndamene amakupachika

  • @PatumaAdam
    @PatumaAdam Місяць тому

    Koma ka audio kwanuko ndiye kakutinyasa bwanji mxeeew

  • @yotamumahomed1313
    @yotamumahomed1313 Місяць тому

    Kodit anthuwo sakufuna zambiri ay akungofuna ndalama zawozo bas

  • @dondamissonchdziwe3958
    @dondamissonchdziwe3958 Місяць тому +1

    Kodi ameneyi mwana wa mphawi yu,utsi Ali pa ngwirizano Ndi MCP? Chifukwa ngati Ali pa ngwirizano Ndi MCP,zimuvuta ndipo ziza muvuta pankhani ya imfa ya Chikangawa forest.ndiponso asapusise a Malawi Kuti azavotere ngwirizano, ngati Ndi madrama zithere pomwepo sitifuna nthira kuwiri nanunso amphawi ndi umphawi wanuwo mukungo imbira m'manja mfiti nchifukwa mwa mphesa Chirima mbuzi za Wanthu kumalawiko.

  • @LimbikanMittawa-d2t
    @LimbikanMittawa-d2t Місяць тому

    Palibe chomwe ndikumva ine nsete zake akuyankhulazi

  • @Littlefair7
    @Littlefair7 Місяць тому +1

    Ngati mtsogoleri USI amayenera kuyitanitsa atsogoleri onse achipani ndi kukambirana zomanga chipani osati wina akulowera uku wina uko ngati za mpikisano, kulibe chipani chimene chinalimba ndi makangano.

  • @GraceThipha-mv7lt
    @GraceThipha-mv7lt Місяць тому

    Sanavale bwanji za utm

  • @angelakondowe
    @angelakondowe Місяць тому

    Tauzeni atsitse zithu zakwela mtengo plz tione za new one osamangoimba nyimbo 😢apa mukachoka pamenepo mukagona ndi njala my country people 😢

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Місяць тому

    Kkkk UTM aigawana basi kkkkkk

  • @YOMALO.
    @YOMALO. Місяць тому

    Now this is great, make Malawi great again

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri Місяць тому

    Things change indeed...chikondi cha mdziko chimatha pomwe okondeka aikidwa mmanda.RIP SKC.

  • @user-fp5qn5ci2v
    @user-fp5qn5ci2v Місяць тому

    Manganya sazatheka anazolowela za chibwana kkkkkkkk

  • @user-um6yo6nc3e
    @user-um6yo6nc3e Місяць тому +1

    Kkkkkkkkk Ndalama adaķonza

  • @user-jb5hr4rz2s
    @user-jb5hr4rz2s Місяць тому

    Kondi kumalawi ko mumango pemerera zilizose

  • @SinsaKachale
    @SinsaKachale Місяць тому

    Mwana oukira uyu ...bwanji sakuvala uniform ya UTM ....osapusisa anthu

  • @MoongaSharph
    @MoongaSharph Місяць тому

    Koma abale mfundo zimenezi za vp kapena khansala ee mavuto amene ali dziko muno zoona kumakamba zokhuza mpila iyayi

  • @TizifaBanda-xn5tm
    @TizifaBanda-xn5tm Місяць тому

    Same ...young boys paid to violence,now they r paid for peace.This is operation stop ku genda but the master is who got cash

  • @MustafaImed-ep3gz
    @MustafaImed-ep3gz Місяць тому +1

    Tiziona chaka chake mnchino

  • @AlickChima
    @AlickChima Місяць тому +3

    Osamapanga ma decision mutakwya mupha chipani..saulos ujayu anali mfana woganiza bho chifukwa chake ankangokhala cheeete amadziwa kuti kutamanga sikufika

  • @bmbboymstyles5894
    @bmbboymstyles5894 Місяць тому

    Koma a Malawi tidzikhalako serious pilizi
    Vice president kumpatsa mic amabatire okutha 😂😂 such a shame

  • @CathrineBizza
    @CathrineBizza Місяць тому +1

    Yudas

  • @EmmanuelMoyo-hy5ni
    @EmmanuelMoyo-hy5ni Місяць тому

    Nfana wa Chikangawa party

  • @SmithChisoni-x4r
    @SmithChisoni-x4r Місяць тому

    Kwinaku nditukwana

  • @GeraldGunde
    @GeraldGunde Місяць тому

    Sidzikundimvera bwino! Kodi a Malawife umphawi kwambiri kapena eti?

  • @user-nj3gn5xq2s
    @user-nj3gn5xq2s Місяць тому

    Ndiye

  • @patrickkusailemp3769
    @patrickkusailemp3769 Місяць тому

    Mwafunsako mtengo wa chimanga ? No mfundo.kampeni ..

  • @julietphiri5510
    @julietphiri5510 Місяць тому

    Drama ya Tiikuferanji?

  • @masterkachingwe7448
    @masterkachingwe7448 Місяць тому

    Boring and loud background music

  • @AlickChima
    @AlickChima Місяць тому

    Manganyayu ku UTM uko mukamapanga zomusala mufa ngati pusi...chagada 😅

  • @IssacMateyo
    @IssacMateyo Місяць тому

    Ulemu wanu Mr ausi 😂😂😂😂

  • @user-wu4tl2yn9e
    @user-wu4tl2yn9e Місяць тому

    Ndizomwe umafuna zimenezo mpaka kuchotsa moyo wanzako galu iwe 😢