BON KALINDO LERO PA 5 SEPTEMBER WAYANKHURAPO ZA REPORT LA NDEGE YOMWE INAPHA A SAULOS CHILIMA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 15 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 100

  • @AshrafShadid
    @AshrafShadid 10 днів тому +20

    Speaking on air like this shows that u r a courageous and cool guy, if I have power like u I could have make something strange in this 🇲🇼straight bcz I feel very pain and Huttered

  • @MauriceTayali
    @MauriceTayali 10 днів тому +5

    Always, chulungamo chimapweteka. YUDAS adamupeleka YESU chifukwa cha chulungamo

  • @davidkadyakapita8836
    @davidkadyakapita8836 10 днів тому +2

    Ulemu wanu bwana Kalindo. Zonse mwakamba ndi zoona kuti Chakwera apakile adzipita kwawo pamafunika mai Mary Chilima atengepo mbali pa ndale pokhala President wa UTM 🎉🎉🎉🎉🎉🎉

    • @FidesChandama
      @FidesChandama 8 днів тому

      auze ave ine chakwela akundinyasa akutionjeza kupha anthu ngati akupha nkhuku ngati ana wamake Malawi ngati ya kunyumba yakwawo

  • @andreabanda7838
    @andreabanda7838 10 днів тому +2

    Ife tufuna mai chilima basi. Mai kaliati chonde you are good as the SG or CEO of the party. If you loved Chilima as your boss, please give the G-Z, including all the women, the totality of their moral to vote for change. Dr Mtumbuka, Dr Kabambe, Madam Kaliati and the campaign director including UDF, AFORD, DPP, PP should immediately create an inner circle to help her complain and win the election in 2025. Chonde chonde the G-Z are waiting patiently. We pray for you Bwana THE DC.

  • @chifundomatumula1652
    @chifundomatumula1652 10 днів тому +5

    Zoimila mary chilimazi ndie zopusa, let her mourn it's too early. Utm was not formed as a family party.

    • @JonesChingaya-yf4gg
      @JonesChingaya-yf4gg 10 днів тому

      Thus true, personally I agree with you. Let her mourn her late husband peacefully.

  • @LydiaLuhanga
    @LydiaLuhanga 10 днів тому

    Amen akuti mary asayimire ndi azipani za mcp ,,,mary ayimire abale ateteze chuma cha mwamuna wake alimbe mtima basi mulungu yekha ndiyemwe amupatse mphavu, A mcp inu mukudziwa kuti kungoima mary chanu palibe

  • @MACDONADLITIA
    @MACDONADLITIA 10 днів тому +4

    Mbewu imayambila ku nazale
    Bon Kalindo ndiye mmodzi yemwe anamupusisa Chilima kuchoka ku DPP kupita ku MCP lelo ifa ya Chilima wapezelapo mtaju wopangilapo business ndipo a Malawi timango pusisidwa zili zonse taiwala kuti Kalindo ndiyemwe anayenda maliseche mu nthawi ya DPP.

    • @MzadziWanga
      @MzadziWanga 10 днів тому

      Kalindo analowak liti ku MCP ??? Mesa anali limodzi ndi chilimayo mmene amapanga alliance later on mpomwe amadzalengeza kt watulukak nde iwe ukukamba ziti??? Kmaso ngt anamupusisa chilima bola kusiyana mkumuchotsa moyo ngt mmene achitira a MCP

    • @MACDONADLITIA
      @MACDONADLITIA 10 днів тому

      @@MzadziWanga pamene ankapita ku MCP anali mwana mbiri ya Gadama samaiziwa zoti kunali Solobala samaziwa ndimaesa ndi Chilima yemwe ankatiuza kuti chisakho cha 2014 Iye ndi amene anagwira ntchito kuti MCP iluze anaiwala?

    • @user-ww4ei5fb7d
      @user-ww4ei5fb7d 10 днів тому

      Kulibe olungama akulu, ziri ngati chipulumutso chathu. Odala omwe avomereza machimo awo ndikulapa. Atleast atawona kuipa kwa MCP anamuchenjeza, zinangovuta kuti adamukhulupirira Chakwera mudzina loti ndi m'busa plus new blood in politics. He did not know kusadziwa ndale kwa Chakwera did not mean he is not evil 😢

  • @AnthonyChirwa-t4g
    @AnthonyChirwa-t4g 10 днів тому +1

    the DC makina achilungamo koma chikangawa mapaziake kwambili msiyeni masiku amatha ndikugona chikangawa ine ndikanakhala ndiphavu ine ndikanapita kumeneko kukamupha

  • @GodfreyKampezeni
    @GodfreyKampezeni 10 днів тому +5

    We like pple you born kalindo

  • @ChikondiKammaluwa
    @ChikondiKammaluwa 9 днів тому

    Koma dzikolino silolamula azimayi Ayi Moti mgwirizano umenewu atatsogolela ameneyuyu ndiyekuti utha kudzakhala ofoka koma Peter Basi

  • @MkangoBoy-en7ky
    @MkangoBoy-en7ky 10 днів тому +1

    Mnthu wankulu Bon Kalindoo tsopano 🔥🔥

  • @ChristopherNdalama
    @ChristopherNdalama 10 днів тому +2

    NGATI IMAKANIKA GALIMOTO KULIRA MULIBEMO BATTERY KULIBWANJI NDEGE???? NANGA NDEGEYO IMAGWIRA BWANJI NTCHITO ILIBE ZIPANGIZO ZOKWANIRA???? ALL CONCERNED CITIZENS MUST RESIGN😢😢😢😢😢

  • @HendersonDziwa
    @HendersonDziwa 8 днів тому

    Bwana kalindo ipatseni motoo kt buuu

  • @user-ll3qi5im7x
    @user-ll3qi5im7x 9 днів тому

    Mary chilima my vote

  • @MosesChazima
    @MosesChazima 10 днів тому +3

    Mumakwana Mr bon kalindo

  • @GladesMhango
    @GladesMhango 10 днів тому

    Chilungamo chofunika ulemu wanu bwana ✊✊ Bon Kalindo🔥🔥✊

  • @IshmaelMkwanda
    @IshmaelMkwanda 10 днів тому +1

    Bwana DS mulungu azikudalisani mukuyesesa kutimenyela ufulu oziwa zobisika

  • @user-jb5hr4rz2s
    @user-jb5hr4rz2s 10 днів тому +1

    Takondwera kuyikapo mlomo a DC chifukwa sitinakuven

  • @GiftNgwira-e8l
    @GiftNgwira-e8l 10 днів тому +1

    😂😂😂😂😂bon kalindo moto buuuu

  • @billymhoni9527
    @billymhoni9527 10 днів тому +1

    Ndipo mai Chilima alimbe mtima alitenge dzikoli

  • @AdaKalinde-c4j
    @AdaKalinde-c4j 10 днів тому +1

    Ndipo rinari read kukavota Mary akuyenera kuzuka bas

  • @ErnestTewesa
    @ErnestTewesa 10 днів тому

    Mary Chilima oyeeeee!!
    2025 boma
    I'm following you Mr Born
    From RSA enough is enough tell them

  • @replacefruittreenursery
    @replacefruittreenursery 10 днів тому +1

    Koma ineyo ndikhare mburi .paja galimoto ya manual ngati iribe battery timakakha ndiye ndegeyo amaikakha .ndichoseni umburi .

  • @CaptainNyenga
    @CaptainNyenga 7 днів тому

    😂😂😂 koma DC umaimilira open our door to move forward

  • @SirpromiseMatabwa
    @SirpromiseMatabwa 10 днів тому +1

    Zinazo ndizabwino koma osampasaso dzikoli mkazi kulamulira

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon 10 днів тому +2

    BWANA KALINDO ZIMENEZIJA ANACHITA KUKONZA CHAKWERA NDI NDUNA ZAKE.ZOSATHEKA KUTI MUNDEGE MUJA MUNALIBE ZIPANGIZO IYEYO AMAKWERA BWANJI YOPANDA ZIPANGIZO ? INALIBE ZIPANGIZO CHIFUKWA CHOTI ANAKWERA NDI CHIRIMA ? ZOONADI A MALAWI TINANYANYA KUFATSA AKANAKHALA MAIKO ENA UYU CHIKANGAWAYU ATACHOTSEDWA KALE PA MPANDO NDI AFITI ANZAKE A MALAWI KUZOLOWERA KUZUNZIDWA BASI

  • @NorahSomanje
    @NorahSomanje 10 днів тому +3

    Awachotsa bwanji athu ena iyenso Ali momwemo

  • @ManuelAntônioSitiverio
    @ManuelAntônioSitiverio 7 днів тому

    The dc king

  • @DauglasBowa
    @DauglasBowa 10 днів тому +2

    Ambiri tichikhala olimba m'tima ngati Bon kalindo bwezi andalewa titawanyenya koma tili ndi mantha Amalawi

  • @Enock-c9l
    @Enock-c9l 10 днів тому +1

    Koma pa marry chilimapo mmmm no

  • @pysonchisaka3455
    @pysonchisaka3455 10 днів тому

    ngati sunakhwime sungabwele pa air like that 😂😂😂

  • @joycekuyere
    @joycekuyere 10 днів тому

    Koma pa Mary pokhapo ine sindimavomereza, nzeru za chilima sizingakhale za Mary

  • @NEBRA-lm7ji
    @NEBRA-lm7ji 10 днів тому

    Kd za mademo zili pat bwan😢....ifet tikudkil tithese mkwiyo

  • @limbikanimtewa
    @limbikanimtewa 10 днів тому +1

    kalindo amatiyimilira... 🔥

  • @TemwaKabisa
    @TemwaKabisa 8 днів тому

    The DC ❤❤❤❤❤

  • @chibezagoma3892
    @chibezagoma3892 10 днів тому

    Booon Kalindo the DC

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 10 днів тому

    Ine ndagwirizana nazo Mery chilima yemweyo 🥳🥳🥳🥳

  • @HaroonWalusah
    @HaroonWalusah 10 днів тому

    We like you. The DC ❤❤❤❤

  • @collennyadile8179
    @collennyadile8179 10 днів тому +1

    zoona Malawi ndi dziko lomvetsa chisoni kwambiri koma anthu akuvutika

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 10 днів тому

    Long live Mr Bon kalindo, the pangolin❤❤

  • @FaithDonald-ts2pp
    @FaithDonald-ts2pp 10 днів тому

    The DC ❤

  • @JosephGama-v7r
    @JosephGama-v7r 9 днів тому

    Kalindo ndi mpulumutsi ndi tsogolo la Malawi

  • @KinziWindasoni-h4b
    @KinziWindasoni-h4b 10 днів тому +1

    Meryl ekhayo ndi ayi zikhoza kulowa chibwana

  • @MoosaSame
    @MoosaSame 10 днів тому

    Always listening ur truth boss 🙌 ❤🎉

  • @AllanTamula
    @AllanTamula 10 днів тому +1

    Yes, Mary is a joke plus others.

  • @altonchikaoneka-6848
    @altonchikaoneka-6848 10 днів тому

    Takambanikoni za neef abwana anthutu Ayamba kulandidwa Malo komaso Ndi chakudya mmakukamu

  • @user-ps5tv4hq3c
    @user-ps5tv4hq3c 10 днів тому

    Zoonadi chilungamo chimapweteka

  • @vinceynyone6693
    @vinceynyone6693 9 днів тому

    Malawi ndiosamufeladi😢

  • @BlessingsNkhata-q7h
    @BlessingsNkhata-q7h 10 днів тому +1

    ❤❤❤❤🙏👍👍

  • @StanleyLingande
    @StanleyLingande 10 днів тому

    Mr president kalindo

  • @IdrissahChuma
    @IdrissahChuma 10 днів тому +1

    Kkkkkkk mumakwana bon kalindo the DC

  • @UmarMbewe-m9v
    @UmarMbewe-m9v 10 днів тому

    I hope Malawi will not change coz what i know it's dat, the Malawian they just like money.

  • @PrinceThom-pe6ie
    @PrinceThom-pe6ie 10 днів тому +1

    Kunkuyu adauza a malawi anati black box adayisunga Malo a safe.kodi black box yomwe kunkuyu akanena KUTI adayisunga ndiyitiyo?

  • @HaroonWalusah
    @HaroonWalusah 10 днів тому

    We like you The DC ❤❤❤

  • @JimmyMzozoma
    @JimmyMzozoma 10 днів тому

    Till pambuyo panu Adc

  • @alexandermeke6994
    @alexandermeke6994 10 днів тому

    Okay ngati ndi chincho woyamba kumupha ndiwe mwakondwa poti kulibe chilimayo mukhaulabe anthu opusa inu kumukonda munthu atafa koma umamunena ndiwe satana ndi azakowo shame unto you opposition

  • @MangaDamiano
    @MangaDamiano 10 днів тому

    Akakhala pa nkhate sapheka nkhani iyiyi ikukhunza asogoleli athu omwewo and tinawalemba .ntchito ndife kusonyeza Kuti tikuyenelaso kuwachosapo ndife finish Kuti tizingoyankhula sizitithandizayi Koma tikuyenela kupanga action

  • @user-jk8sh7fh2d
    @user-jk8sh7fh2d 10 днів тому

    Iiiii koma azimai akakulaso mphamvu pena ai , even m'mene amapangila gotani hala , kaliati , Jessie kabwila vela kantukule azimai amenewa ine ndimakhulupilira kuti ulemu umene amawapasa amuna awo si wen wen why ndi azimai okula ntima osafuna kuzichepesa ndie pena azimaiwa aaah enawa sandipasa chilimbikiso kuti nkuwaika pamwamba ife nkumaembekeza kusinthadi eeh osatheka amalowa ufiti onyanyila ndipamene uzaziwe kuti akulu akale akamati mfiti yaikazi si-khululuka umaonela pamenepa kuti m'zoona .

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 10 днів тому

    Mumpangitsa Mary kuyamba zokhima sanga khale pa mpando asana tsazike Mpando umeneu Athu Amalodzana

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 10 днів тому

    Iyeyu chotchinga chake chinali Chilima yemweyu ndipo anamupha basi.

  • @frezarphiri3480
    @frezarphiri3480 10 днів тому +1

    Pa Mary apo ayi mumuphesa mwana wa Eni ake

  • @SamboRuphan
    @SamboRuphan 10 днів тому

    Anthaso kumupha merry chilima,,angozisiya

  • @LameckDanken-tm4rt
    @LameckDanken-tm4rt 10 днів тому

    Fire 🔥 🔥🔥 man kkkkkkk

  • @GrantsWilliam
    @GrantsWilliam 8 днів тому

    Iwe ndi galu kwambr mesa ndinu nomwe mumati ndege idachita kukoledwa ndi ndege inzake mmwambamo ma battery ako ase

  • @user-wl7xn3or6d
    @user-wl7xn3or6d 10 днів тому

    Nbusa ujatu lelo ndi kambuku pano akungo endaenda ngati Wamisala

  • @user-gi1gh9ry6h
    @user-gi1gh9ry6h 10 днів тому

    Kkkkkkkkkk😂😂 mbava chakwera

  • @Andrew-mr5kp
    @Andrew-mr5kp 10 днів тому +2

    The nyonyolido mumakwana mumatiimirira

  • @JanaJovian
    @JanaJovian 10 днів тому

    The Mr DC❤❤❤

  • @jixonromeo4111
    @jixonromeo4111 10 днів тому +1

    That’s true their just making business

  • @Iponga
    @Iponga 10 днів тому +1

    Awuzen agaluwa azinva

  • @ClementMinyanga
    @ClementMinyanga 10 днів тому +1

    Aboma akuziwa chilichotse

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi 10 днів тому +1

    😢

  • @Trishamanda-b5z
    @Trishamanda-b5z 10 днів тому

    Thanks bro ❤

  • @AHMEDMOHAMED-i2h7c
    @AHMEDMOHAMED-i2h7c 10 днів тому +1

    The bc

  • @ZaccheusDyson
    @ZaccheusDyson 10 днів тому

    Nkhaniyo ndioona coz awa amkat tinawauza asatere apa asinthaso kt samalumikizana chinyengo

  • @YasenYasen-q9g
    @YasenYasen-q9g 10 днів тому +1

    Dc❤❤❤😂

  • @ephraimkamwana2609
    @ephraimkamwana2609 10 днів тому +1

    May God bless u l thinks its G0d who sent you to fight for the malawians continue

  • @user-oq8js5fd6u
    @user-oq8js5fd6u 10 днів тому +1

    The DC

  • @andrewchikafa7322
    @andrewchikafa7322 10 днів тому

    Zophatikizana tinaesa kale 😅

  • @FunnyKalimwayi
    @FunnyKalimwayi 10 днів тому +1

    aboma pantumbo pawo ose

  • @RobertNyaude
    @RobertNyaude 10 днів тому

    🤣🤣 ana akuzuka.

  • @EmmanuelMalongo-b3y
    @EmmanuelMalongo-b3y 10 днів тому +1

    Misheck

  • @MorganMwikhala
    @MorganMwikhala 10 днів тому

    Ndipo ife ndiogona ndithu

  • @kennedybanda
    @kennedybanda 10 днів тому

    Chifyenthe kodi

  • @LushaWalance
    @LushaWalance 10 днів тому

    Koka2 uyu ndiopweteketsa mtima

  • @AHMEDMOHAMED-i2h7c
    @AHMEDMOHAMED-i2h7c 10 днів тому

    The b c

  • @peterthawi
    @peterthawi 7 днів тому

    😂

  • @PotipharEphraim
    @PotipharEphraim 10 днів тому

    😂😂😂

  • @Benjamin-v9z
    @Benjamin-v9z 10 днів тому

    Ulichitesi iwe zindele zimakuvela

  • @PreciouBanda
    @PreciouBanda 10 днів тому

    Iwe ka sound kali pasipo osamayika ayi zapamtumbo zimenezo ife zopusa ayi tikuyenda okwiya kwiya

  • @BessieMhango
    @BessieMhango 10 днів тому

    Ppppppp

  • @user-ll3qi5im7x
    @user-ll3qi5im7x 9 днів тому

    Mary chilima my vote

  • @HaroonWalusah
    @HaroonWalusah 10 днів тому

    We like you. The DC ❤❤❤❤

  • @EmmanuelMalongo-b3y
    @EmmanuelMalongo-b3y 10 днів тому

    Misheck