Adali wachidodonso koma. Mmene ankamuzunzila muja naye osatuluka bwanji kaya 🙌. He unknowingly contributed to his own death but mulungu yekha ndi amene akudziwa zonse
Intelligence is not the same as Wisdom. He was very intelligent, that alone, didn't mean he was a "Leader" in the making. Take this one; some people are born leaders, while others, are made leaders. Being intelligent doesn't mean the particular individual is a leader. What matters most in a leader is "Wisdom". On Earth, there is no School, neither University where one would go to pursue studies in "Wisdom", in other words, it is an "in-born" issue. Thats why, born leaders find it more easy to lead than made leaders.
Statement yanu ya tsankho komanso yogawanitsa as if a kum'mwera kapena a pakati amene akhala akulamulawo atulula dzulo lino chonsecho tikungolirabe.Nde where is your logic in justifying aku m'mwera kapena chigawo cha pakati?
Mr Mtumbuka. You.are very open kkkkk nkhani ya Blantyre.mwatisangalatsa enatu amakwiya nazo koma inu ayi.Good leader May God continue blessing you.
My Vote ❤!!!
Proud of you, Mathews.
Great points Sir...
Zoti ndege yasowa munaziwira munalikuti??
One has to grow in politics.Ndale si sukulu ayi. Osamangoyambira pamwamba.
Uyu munthu ndi katundu 🙌
Zanu uja anali dolo koma anapoila kuyenda ndi MCP phuma la 2025 but RIP skc
VERY TRUE PHUMA SKC ANALI NAWO NKHWILU U-PRESIDENT....HOWEVER ANALIDI DOLO.ANALI KATUNDU
Ma Bishop ndamene anampangitsa munthu uja
Ayi muthu woganiza boooh sangamaveree ma bishops or azibusa
Munana inu@@VinGenerators
Adali wachidodonso koma. Mmene ankamuzunzila muja naye osatuluka bwanji kaya 🙌. He unknowingly contributed to his own death but mulungu yekha ndi amene akudziwa zonse
He's a leader 💪🏻
Vote yanga ndi yanu
Zili bwino kwambiri boss go on tikutsatani mosakaika konse.
Dr.
I can see some fine moments of truth if you won't change after election t the convention
We love utm utm ili ponseponse no regional demarcations
Keep it up, you can lead I believe.
Intelligence is not the same as Wisdom. He was very intelligent, that alone, didn't mean he was a "Leader" in the making. Take this one; some people are born leaders, while others, are made leaders. Being intelligent doesn't mean the particular individual is a leader. What matters most in a leader is "Wisdom". On Earth, there is no School, neither University where one would go to pursue studies in "Wisdom", in other words, it is an "in-born" issue. Thats why, born leaders find it more easy to lead than made leaders.
That's very true
Humble man with beautiful brain
Yah another chilima
Ine pano Ndikugwilizana Nayo statement iyi! Malawi 🇲🇼 learn to do something not Mijedo ndi Kaduka!🗣️🫡
Am impressed in this leader.
Genius
Komatu osamangowanamizira Sir aja
My vote
Me too!!!
I'm so impressed
Anthu ophunzila pa ground pamawavuta amangoyankhula
Katundu muzito
Chophunzira kuposa zakeyu😂😂😂....no chance zakeyu short sellout😂
Kod nchifukwa chan mumaveka pasipasi?
Akhalitsa pa bwino awa sangathandize osauka.
Kumanso munthu wa kumphoto mukudziwa kale
Statement yanu ya tsankho komanso yogawanitsa as if a kum'mwera kapena a pakati amene akhala akulamulawo atulula dzulo lino chonsecho tikungolirabe.Nde where is your logic in justifying aku m'mwera kapena chigawo cha pakati?
Kodi kwanu ndikuti inu mpoto kapena kt
Pour questions
Poor English😅
Poor grammar
Bigy
Not presidential material.
How?Kungodana naye?Presidential candidate mumadziwila chani?
@@GiftKumbweza exactly why our country doesn’t go anywhere. Be smart! You can’t keep making the same mistakes every election cycle.
@@Malani41 And you did answer my question
@@GiftKumbweza read what you just said. You just said that I answered your question. Learn your English.