20 billions. Mmmmmm maganizo anga ngati wachinyamata brother... Ndalama imeneyo atapanga fund . Ma technical college onse omwe Ali Malawi muno .. kungula zipangizo zokwanila . Ngati machine and materials. Ku chito zamanja zonse ... Ma program ngati Plumbing Bricklaying General fitting Welding and fabrication Electrical insulation Motor vehicle mechanic Carpenter Tshirts printing. Ndi ntchito Zina zomwe ndaziiwala . Pakutelo titha kuwatenga ngati . Ma factory kwinaku akusula achinyamata kuwaphuzisa lutso. Chisanzo ... Mij ... Ndisukulu yatola khani . Koma iliso ndi radio station... Two in one .. Ndizelu zanga zochepazi ndimaganiza Chocho broooo
Tell them to first bring the issue to the public for Malawians to say their views and adzitengera kuti amalawi akuti bwanji not to be voted only by the Mps
It’s just a quotation guys. Mike Bango amafunsa progress report nde a vera kamtukule amangopeleka update kuti tinakafunsa mtengo anatiwuza kuti ndi 20billion. Zili ngati inu kundifunsa amwene ndimafuna benz after 1 month mukubwela kundifusa kodi benz ija zili pati ine ndikukuuzani kuti yapezeka ku South Africa koma kuti ibwele clearing zonse pakufunika 15 million.
Koma osakangofusa ku Ruandako kuti anapanga bwanji kuti dzina kawo lipezeke pa jersey ya arsenal paja😅😅😅😅😅.........otherwise ndi zinthu zoti mudyetsa ndalama ulele...kkkkkk...
Kodi Vera yoo mutu wake ndiozungulira siumagwira bwino ntchito eti chitsiru chamunthu akapereke ndalama imeneyo ku anthu wolemera kale sikupusa kumeneko
😮Anthuwa akufunika mapemphero apaderadera ndithu plus kusala kudya
😂😂😂 anthuwa mitu yawo siyikukoka
20 billions. Mmmmmm maganizo anga ngati wachinyamata brother... Ndalama imeneyo atapanga fund . Ma technical college onse omwe Ali Malawi muno .. kungula zipangizo zokwanila . Ngati machine and materials. Ku chito zamanja zonse ...
Ma program ngati
Plumbing
Bricklaying
General fitting
Welding and fabrication
Electrical insulation
Motor vehicle mechanic
Carpenter
Tshirts printing.
Ndi ntchito Zina zomwe ndaziiwala .
Pakutelo titha kuwatenga ngati . Ma factory kwinaku akusula achinyamata kuwaphuzisa lutso.
Chisanzo ... Mij ... Ndisukulu yatola khani . Koma iliso ndi radio station... Two in one ..
Ndizelu zanga zochepazi ndimaganiza Chocho broooo
100% bro
Km zoti kulinjala akuzwa akuti ganizla bwanj ife anthu osauka
Bg mwalomoti mutwuze saku Israel nd Lebanon mwafasa nd zakumalawi singasinde malawi panga vuto pangatani magazi anduna 4 ndi chipembele anaphedwa aja💔😩
Anatiblokera fb page
@@MalawianCamera dzikoli ndi lokondela basi😢
Edzi inawazunguza mutu awa
Mmmhh adha
Koma yeah zovesa chisoni kwambili anthu akuvutika ndeeee muchose ndalama zonse kamba kot mukufuna anzungu akuyendeleni😮😮😮😮😮
mumuze kuti panyapake anthu akufa ninjala chamba asa
Tell them to first bring the issue to the public for Malawians to say their views and adzitengera kuti amalawi akuti bwanji not to be voted only by the Mps
Madness, mtengereni Ku Misala akalandire thandizo Vela yo.
Bwanji zakutherani zoti mube.
Kapena mukufuna kuwapezera anthu zifukwa akakudzudzulani muziwamanga ndi kuwapha.
Malawi Chikangawa Party 👹⚒️🔨⛏️⚒️🔨⛏️👹
That's nonsense, kuzolowera Kuba basi,koma kubako ndi azimayi omwe,shaaa!usamangopanga uhule kumanyengana ndi chitsiru chanucho(chakwera)azikugayirani ndalama akubazo bwanji
20 billion kupereka kwa azungu! Zapanyero eti?
Koma zoti anthu akufa ndi njla mukuziwa my poor malawi😢
Maganizo opusa amenewo coz tikuvutika muzambiri mot ndalama imeneyo ipite kwa anthu ovutikitsisawa kut mwina jalayi asayimve kuwawa
Aaaaa...ameneyu ndi galu eeti......zimenezonso ndizochita kuperekera ziphuphu..😅😅😅😅...njala yomwe ya gwira dzikoli koma akuiona???
anthu A mcp ndiaçhamba bwanji awuze chakwela ndi chithyola agule nanga si ndalama akusunga ndiwowo za misonkho
Ndalama imeneyo ikupita komwe kuli lipoti la ndege asatiputsitse agalu amenewa alamulidwa choncho
This point of yours can make sense somehow kuilingalira bho
It’s just a quotation guys. Mike Bango amafunsa progress report nde a vera kamtukule amangopeleka update kuti tinakafunsa mtengo anatiwuza kuti ndi 20billion. Zili ngati inu kundifunsa amwene ndimafuna benz
after 1 month mukubwela kundifusa kodi benz ija zili pati ine ndikukuuzani kuti yapezeka ku South Africa koma kuti ibwele clearing zonse pakufunika 15 million.
Koma osakangofusa ku Ruandako kuti anapanga bwanji kuti dzina kawo lipezeke pa jersey ya arsenal paja😅😅😅😅😅.........otherwise ndi zinthu zoti mudyetsa ndalama ulele...kkkkkk...
20 billion MWK ndi mseu waku mzuzu chikwina. Ganizana za chitukuko mmadera akumudzi.
Kutenga 20blln kuwaptsa. Anthu olemelakale,mmm kuganiza kwa anthu wasukulu yakwachatu uku, oky malawi iweee😭😭😭zantiiii
Zimenezo sizodandaulisa chifukwa amachita ku vote ngati ma mp avotele ndimene zikhalire iye ndi maganizo ake zikakanidwa iyeso avomereza zimachitika
True
Kma nduna za ulendo uno zikubwera fodya kwabas😮😮😮😮
Ma mp omwe avotere zopusazi tumizani maina ku constituency yawo tione ngati aMalawi angavoterenso 2025.
Zopindulira okho kms zopanda mzeru
Maganizo opepera kwabas, aaaaaseeeee
MCP needs God
Kaya chakwera nduna zimenezi amazitola kuti kweni kweni?
Yoonda kale muikamebe otsogoleri opusa ndiolephera
Akufuna kuba awa
Hule wamisala uyu ndalama yoseyo kodi njalayi sakuyiona
Pamtumbo pake zamisala mmalo Moti tigulire cakudya maknhwala Kodi anthu awa ndimisala kapena bwanji?
20bn just for a single season😂😂😂😂😂 eshieeee!!!!!
Kuzungulira mitu
Fodya Malawi alikumawi
Pafunika mapemphelo okwanila nditu Malawi atsogoleli onse mithu yawo siyi kugwira each out Malawi 🙏😭
Plan ndi yabwino. Koma situation ilili ku malawi zizikugwilizana ndalamayo pali bwino ipite ku uduna wazaumoyo agulire😮😮 mankwara mzipatala
Ameneyu akudwala muthu wa ching'alang'ala mpase mankhala amuthu
Mahule awa zaziii
Kodi Vera yoo mutu wake ndiozungulira siumagwira bwino ntchito eti chitsiru chamunthu akapereke ndalama imeneyo ku anthu wolemera kale sikupusa kumeneko
Ife tikusauka kufuna ndalama zomwezo kapena mdziko ma resources mulibe mbali zonse monga kuchipatala, miseu ,ma school kms ma basic needs anthu akusowa bwanji ngat ndalamazo zilipo osathandiza anthu amudziko la malawi
Wachibwana ameneyi
Chitsiru ameneyo hule wacabecabe
Nduna imeneyi yachamba
Zopoyila basi, osangowagulila anthu chakudya bwanji 😊
Ndekupengako 20billion
Zoputsa abwere kuno iwowo ndi Angelo? Anthu amene akumakhala mmaudindo zomvetsa chisoni
Akuona ngat ife ndiopusa eti ndalama akuba kumapangila kampeni . Mtcheww MALAWI we are doomed
Pa nyopawo athu akufa ndi njala akapeleke Kwa azungu MA kholo mwawo
Zimenezo ndie zopusa kod mwatipezelelaeti?? ndramaimeneyo bwanji osatipatsa ngongole ife achinyamata bwanji zoona mmene tikuvutikilamu mungamatiuze zimenezizi mulungu akukhululukileni
Ma ARV akumuzunguza uyu,sure ungatenge madzi amu cup nkukathira mu nyanja kuti uone mmene alekezere,kape uyu
Izi sizoona dziko losauka kale ,lomweso limene lilibe ndalama ,anthu ake Ali ovutika kwambiri kuposa maiko onse ndie zikutanthauza chani ndalama zonseo zipite ku dziko lomwe liri lolemera kale ? Ngati sakudziwa chomwe akupanga pa udindo wake ndibwino angotula udindo wamukulira
Hule uyu, mbava wakuba uyu that is why akukakamira Ku mcp cholinga aziba zaziiiii
Km zoona malawi meneakuvutikirapa 20 billion mukapatse azungu olemeraka km iwe kantukule boma mukulitengangati lakunyumba kwanu bwanji zopusa eti
Mzimu wa chilimatu wawapengesa anthuwa mitu siikugwila ntchito
Atsogoleri awo ndiokomedwa amenewo ndi okomedwa wa bakili muluzi tv sananame kma nthawi ikubwera azisiya poti tsoka mtunda ndinyanja popeza oipayo watsikira ku mcp poona kt katsalira kanthawi kochepa kt azunze malawo
Ameneyu fisi ett koma zachitikuko zilimo mmutumo basi bola iwo ukumwa mkaka kumeneko osaganizila ena
Mmalo potenga 20 billion kugulila mankhwala mzipatalamo ai ndie mwati koma kugulila azungu eni ndalama nso koma kodi maundunawa mukumasankhilana kudziwa kuchindidwa kapena kuchinda bwino bwanji makamaka ku MCP ko?
Ngopenga Mmaiyu
Kodi ndipanjira yoti adzaone umphawi kapena kudzagulitsa dziko? Ngati insurance yolipira ngozi muli nayo pitilizani chifukwa miseu mulibe, ndege mulibe, zakudya mulibe, chitetezo mulibe. Sindikuona phindu ndi mfundo imenei koma kugawa ndaramazo mumaboma onse achinyamata agwiritse ntchito pa zisunzo
Mpaka lero ambiri sakudziwa kuti ife anthu achikuda ndife woposa angelezi asa
Wamisala ameneyo
Nde zachibeanaxo
Malawi we joke too much
Kma 20bilion simacheza gays ndramazo osagula chimanga bwanji ndi kuthandiza anthu amalawi momwemuno zimpindulira chan muthu wankumudzi zimenez aaaaa kma ine palibe chazelu boma ili ndilakuba bas zakukanokan bas 😊
Kodi umakhala ufiti chani ??? Iwe usandilankhulitse pambali wanva vela owoo
ngat ili ya thumba mwake apange kma ngati ili misonkho yathu ife sitikupanga nawo
Atenge yakwawo ngat alinayo or kutundu kwawo anaigwirapo
Akugona ameneyo azigonabe
Apite kumeto ku Zomba salibwino akangaude amenewa
Asongelana simene atibelaso mapasi ake mg 2 chikangawa
Bwanji osatenga ndalamazo kuziyika kapena kugula ma bed muzipatala
Mfundo zamalawi penapakeso aaaaa zogwetsa ulesi bwanji
Madala mwangotinkhazika ku fb simukutiwuza kalikose kayisekenitu akautiyo
alibe nzelu uyu or pangono njala ili ku Malawi ko sakuyiona iyeyo ndalama zichulukilenje
Visit malawi to do what? ngat chilichamba tinange ndalama muchalo masuzgo yaliphaaa koma nduna zinali abale even fertilizer sadagule
Akupenga kwambiri anthuwa
kodi agalu inu makolo athu angadye mpira panopa chilichose ndi chakwera monga mwazina lake
Koma ameneyo akudziwa tanthaudzo la 20billion kapena anangoona atanena mawu amenewo?
Manyaka enieni
Eyoooo!🙌
Koma zoti kuli njala agalu amenewa akuziwa
Dzikoli akuona ngati la agogo ake
Chisilu cha zimayi
Koma awa was ndi athudi?moti muthu angamaganize choncho ndimene akuvutikila athu kumalawi kuno
Maganizowo ndi abwino komo ndalama ya chuluka
Ndipo zapankholo panyini pamako kuzolowera kuba basi
Bwanji osagulira chakudya ndi feteleza awapatse anthu, eeeee
Malawi
Kuti anthu azidzatiseka? Ameneyu pamtumbo pake
Panyapake wandiphwesa mtima pamtumbo pake
Ayi
Mmalo mokuti agulile chakudya koma zinazi
Mayiwa apenga misala ndithu
Kodi mankhwala nchipatala mwagukilamo kale
Zauzilu kwabas,
Ndizopusa zimenezo ndi zachamba
Zoti kuli njala mankhwala nzipatala akusowa simukudziwabe?kod Malawi ndye kt muli ndalama zambiri? ngongole zili thoo koma anthu tamapangani zimene anthu anakusankhilani komatu mawa anthu mukuwazunzawa mudzawafuna mukupangaku ndikupha zoonad 20 billion miseu yoonongeka moti mukamadutsamo simuchta manyaz??hhhh Malawi Mulungu mwamutaya kuti?
Za uhule basss
Visit chikangawa😅
😂😂😂 misala.....
Malo moti agule chimanga apatse anthu ovutika akagule ma jez mbolo ya bamboo ake
Oky visit Rwanda uja akhale visit Malawi ?
Kkkkkkkk...ati visit Ruanda ai koma ..visit Malawi..😅😅😅😅😅