Abusa akuti vote yao atengapo anapanga mistake❎ 😂😂😂

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 2 лип 2024

КОМЕНТАРІ • 171

  • @augustMag
    @augustMag 16 днів тому +4

    Powerful words may God continue bless you Fr Mnthalika 🔥

  • @user-sv2vc7ie2m
    @user-sv2vc7ie2m 17 днів тому +6

    Anthu atengapotu phunzilo ndizovuta zomwe tikuziona chifukwa anthu amati akufuna kuona kusintha ndiye aonatu nyekhweeeeee

  • @GiftPhiri-tt7nn
    @GiftPhiri-tt7nn 18 днів тому +4

    Umenewu ndiye utsogoleri munthu wa Mulungu asamaope kuyankhula chilungamo , osati azibusa enawa kungowapatsa ndalama basi kusekelera zopusa , ana anjoka Inu Mulungu akulangani

  • @user-oc8nj3or6y
    @user-oc8nj3or6y 16 днів тому +2

    What a teaching ❤❤❤ impressed me so much waooooo❤❤❤

  • @CathreenKadwala
    @CathreenKadwala 16 днів тому +3

    Father Inu Ambuye azikupasani moyo wautali simuwopa kuyankhula chilungamo

  • @marryphili5419
    @marryphili5419 16 днів тому +2

    Amen abishop ndipo talira mokwana koma mulungu simunthu safulumira ndipo sachedwa one day is one day mulungu ayakha

  • @user-pv9uk6sc3w
    @user-pv9uk6sc3w 21 день тому +12

    A Bishop mwalitha bomali, ndipo kumene ali Chakwera sakugona ndi m'mene mwatulukila ma Bishop. Chakwera ndi boma lake la MCP lalephera tatopanalo.

    • @MeckMdoma
      @MeckMdoma 16 днів тому

      Dpp nayo tinatopa nayo nkuona tinayithamangitsa. Mavuto ali mdziko muno solution si dpp. Awa adzawonjezera kusawuka kwa a Malawi kupsola apa. Malawi is going througheconomic problems because dpp mismanaged this country's economy.

    • @marryphili5419
      @marryphili5419 16 днів тому

      Borani DPP inali bwino fertilize wunali bwino anthu tinali ndi chakudya mapassport amapezeka palipose kuchoka ku mzuzu mupaka kumangochi ndalama sinali yotha mphamvu panopa wesi

  • @user-cf9yz3ei5o
    @user-cf9yz3ei5o 17 днів тому +3

    you have spoken man of. God we. are listing God is God. does not. fail

  • @bysongeorge3243
    @bysongeorge3243 21 день тому +4

    Chilungamo chokhachoka. Zokhumudwitsa wina tinamusankha anali M'busa..koma lero anasanduka ..

  • @patrickndojime1632
    @patrickndojime1632 21 день тому +4

    Father mumakwanisa ulaliki wanu wabwino kwambiri

  • @MorrisMapiri-d6z
    @MorrisMapiri-d6z 15 днів тому +2

    Mlungu anamufunsa KAINI nati: alikuti m'bale wako Abele? Nde anati, taona mwazi wake ukundililira ine kunthaka. Zotsatira anali matembelero pa KAINI. Kukhetsa mwazi kumadzetsa tsoka.

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 7 днів тому

    Amen , tangovomerezani bwana president tulani pansi udindo nokha mukuona kuti zakukanikani .

  • @EvelynLungu-lj8tp
    @EvelynLungu-lj8tp 18 днів тому +3

    Mwaputa nkhondo. Akatorika si anthu wamba. Wina atengapo thembelero

  • @ReginaKasambiza-ie2rp
    @ReginaKasambiza-ie2rp 17 днів тому +2

    Kumwamba kulande vote yanga
    Tsiku lina Mulungu wamva Pemphero lathu

  • @JustinChinombo-dy6tp
    @JustinChinombo-dy6tp 18 днів тому +1

    Amen amen a bishop mulungu wathu salephera, Achilima anati mudima or ukule bwanji koma kuzacha ndithu ❤❤

  • @user-wr1km2gh4g
    @user-wr1km2gh4g 16 днів тому +2

    Kuyankhula kwa mphavu,kopanda mantha,osaopa munthu,tiziopa mulungu

  • @MarkManyowa
    @MarkManyowa 12 днів тому +1

    🤣🤣🤣🤣 Malawi ikakhala Nyekhwe nde taithamatu🤣🤣🤣🤣🇹🇿

  • @user-ir1lj8ir5t
    @user-ir1lj8ir5t 5 днів тому

    Amen and amen inenso ndipemphelo langa ambuye afute ma vote abale anga zoona zomwe timaziyembekezela sizimenezi ayi

  • @user-mj2te7vl6p
    @user-mj2te7vl6p 21 день тому +4

    True talking man of God

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 21 день тому +4

    Azisogoleli ameneqa onse alandile ma thembelelo kuyambila ana awo komanso zizukulu zawo za ana awo onse amene azadye ndalama zomwe akubasi za anath osauka alandile thembelelo ndibkhate mu zina la yesu....

  • @user-xx4jb9se3z
    @user-xx4jb9se3z 20 днів тому +2

    Abusa awawa MULUNGU awapatse moyo wautali.imfa ya chilima akatolika sakugona ndipo akati apemphere amakhala serious mcp bro apule samalani

  • @ThokozaniKaluluma-rj6rp
    @ThokozaniKaluluma-rj6rp 15 днів тому +1

    Koma muli ndi lawyer? Kkkk

  • @marthansaliwa7732
    @marthansaliwa7732 20 днів тому +1

    Amen! Father Ambuye azikutetezani.

  • @user-te3ps3kf2t
    @user-te3ps3kf2t 17 днів тому +1

    Ali ndi khutu amve,powerful Massage.

  • @innocentissah2636
    @innocentissah2636 18 днів тому +1

    Tiwemphelere atisiye anthu oipawa afe ndithu, mkhwiyo wa ambuye uwakwapule anthu akubawa

  • @MosesShaibu-ee8hn
    @MosesShaibu-ee8hn 14 днів тому +1

    Amen jone chilebwe

  • @user-il8cn7ko9m
    @user-il8cn7ko9m 15 днів тому +1

    😂😂 eshi amen

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he 12 днів тому

    Powerful massage
    Pipo shud listen carefully

  • @user-dy4gc2hr5e
    @user-dy4gc2hr5e 10 днів тому

    Powerful message Ambuye akutetezereni ntumiki

  • @AndersonChimwala-hz4so
    @AndersonChimwala-hz4so 21 день тому +2

    Mau ogwila mtima zoona .

  • @user-ek6wf7bt7f
    @user-ek6wf7bt7f 17 днів тому +1

    Father mupitilize kumuthira fire chakwera,watikwana

  • @MestreMaday-fv7qo
    @MestreMaday-fv7qo 13 днів тому +1

    Chipan ali nacho ndi mulungu wathu

  • @lawrencemakina2882
    @lawrencemakina2882 17 днів тому

    Amen. Mulungu ndiye omenyera nkhondo ana ake

  • @MestreMaday-fv7qo
    @MestreMaday-fv7qo 13 днів тому

    IWE loya wachani IWE ndi m.malawi ukunva bwanji siya zimenezo

  • @NatashaBema
    @NatashaBema 21 день тому +1

    Amen abusa inuyo mumatha

  • @user-qg4it7my9n
    @user-qg4it7my9n 17 днів тому

    Amen ambuye akudaliseni coz mwaonse azitumiki asakha kukhara cete ngati dziko likuyenda bwino koma mulungu azapeleka cilango coopsa kwa anthu amenewa

  • @elizasingano
    @elizasingano 20 днів тому

    Amen and amen mulungu atithandiza kumeneya nkhondo imeneyu

  • @WilliamBandaWili
    @WilliamBandaWili 21 день тому +3

    Munthu wamulungu walankhula apa

  • @user-wi8xw9qh7n
    @user-wi8xw9qh7n 8 днів тому

    Yes father God will help us

  • @AndersonChimwala-hz4so
    @AndersonChimwala-hz4so 21 день тому +1

    Anthu amulungu kugwa kwa munthu openphela amalandila nazo Themberelo.

  • @user-gv2uu3cs3g
    @user-gv2uu3cs3g 17 днів тому

    Amen a Bishop.Amenewa Ndiye mau

  • @user-dm2fs6hf1b
    @user-dm2fs6hf1b 20 днів тому +1

    Palibe zofuna kutchuka chilungamo chinenedwe achulewa a mcp anapha anthu pangoz ya ndege( chilima) ndi ena onse

  • @WisikiBlack-gj4gu
    @WisikiBlack-gj4gu 21 день тому

    Ameen ameen abusa. Apa boma palibe koma chizuzo basi kuononga dziko uku. Koma apa pakufunika nkhondo ambuye atithandize.chifukwa ngati afika pomupha chilima ife ationa ngati ndani.koma nkhondo ndimeneyatsala basi

  • @CharlesChagudubuka-rm6bh
    @CharlesChagudubuka-rm6bh 18 днів тому +1

    Akuti apule chasanduka choseketsa 😂😂😂for

  • @ThokohPrescotKalonga
    @ThokohPrescotKalonga 21 день тому +1

    Zowona ndithu, malawi akufunika ma demo kuti akozeke

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 21 день тому

    Amen mau awa agwile ntchito kwa woipayo kuti Malawi apulumuke

  • @LingsonMaida
    @LingsonMaida 21 день тому +1

    Ifeso talanda bwana😂😂😂😂😂😂

  • @user-vm7iz6oz6r
    @user-vm7iz6oz6r 17 днів тому +1

    Pano agula mifut malo mogula makhwala zipatalam

  • @BestonMakochera-qk4sz
    @BestonMakochera-qk4sz 16 днів тому

    Sibas katolika waziwa chomwe chinachitik game yathapo yambani kulongeza 😢😢 anthu amene ziululika lero zayambik

  • @JamayakoJamayako-rv2he
    @JamayakoJamayako-rv2he 12 днів тому

    Mateyu 18 vs 18
    Yomweyoo ikhake nyimbo ndi chitsogodzo kwa ife

  • @AdamSteven-ne9hg
    @AdamSteven-ne9hg 9 днів тому

    Ulaliki ugwira mtima ndithu🔥

  • @user-uf4db7im7d
    @user-uf4db7im7d 4 дні тому

    Mwaputa a katolika ndipo simunati muziona, campaign ali mmatchalichi

  • @JosterNgalawa
    @JosterNgalawa 18 днів тому

    Amen bishop, ndipo pitilizani

  • @user-hs4bm2yj8r
    @user-hs4bm2yj8r 14 днів тому

    Amen 🙏 father, Mulungu kutetezeni

  • @deborahngwira724
    @deborahngwira724 14 днів тому

    Mkwiyowutu ukuchedwa. Ine nde ndikuufuna nsanga nsaname

  • @TiyanjaneMkwate-we8gu
    @TiyanjaneMkwate-we8gu 18 днів тому

    Mulungu alemekezeke, amalawi tikuzunzika kwambili, atithandize potiteteza kwa anthu a nkhanza ngati awa.Ft Mulungu akudaliseni pobwera ndi chilungamo.mwina liwu lanu linveka kwa MULUNGU.

  • @1kumilala1
    @1kumilala1 21 день тому

    Mawu amalenga. Amen Father

  • @user-nf3ik3ff6y
    @user-nf3ik3ff6y 16 днів тому

    Amen Chakwela you mast go watikwana

  • @MasausoMsiska-rz3id
    @MasausoMsiska-rz3id 13 днів тому

    Amen man of God

  • @user-do2cs8nf4b
    @user-do2cs8nf4b 20 днів тому

    God is speaking to the government of Malawi anayiwala kuti kunja kuno kuli Mulungu, akupembedza ndalama. Mulungu dzukani pa mpando wanu wachifumu mutimenyere nkhondoyi

  • @thatgirrroskrr3570
    @thatgirrroskrr3570 12 днів тому

    Powerful message

  • @DafterKhungwa
    @DafterKhungwa 15 днів тому

    Amen,nanenso ndayitengako

  • @FazilahKazembe
    @FazilahKazembe 15 днів тому

    Amen wathu sameneyo ..

  • @MacreaChilingulo-ob9gb
    @MacreaChilingulo-ob9gb 17 днів тому

    You are the Greatest , Amen !

  • @allansili-rc9gc
    @allansili-rc9gc 20 днів тому

    Wow this is charming

  • @Allan-bk1
    @Allan-bk1 18 днів тому

    😂😂😂😂eeesh pastor

  • @RachealHarawa-xc9gs
    @RachealHarawa-xc9gs 19 днів тому

    Chilichonse chili ndinthawi koma na apapa zafikapa Ambuye chitaponi kanthu mwasanga

  • @HassanJameskananjie
    @HassanJameskananjie 18 днів тому

    Kod amalaw mupepela mpaka liti lawyer nde kuti chan

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 18 днів тому

    Tathokoza abusa ameneyu musasiye kumudzudzula pali mau amanena kuti :ONDIUZA ANALIPO KOMA KUSAMVELA KWANGA KWANDIPWETEKETSA

  • @MarthaMbewe-uk5nn
    @MarthaMbewe-uk5nn 18 днів тому

    Pharaoh watsala pang'ono kuonetsedwa ukulu wa Mulumgu pompano aziona iyeyo kodi sakuona kuti ulemu wake unachoka Kale kale? President wanji omangotukwanidwa mgati chitsiru?

  • @gracekamzati
    @gracekamzati 17 днів тому

    Ameni abusa ine nde sinavotereko ndipoyamba pomwe ili siboma ayi koma kupha anthu

  • @PeterChuma-yf1ps
    @PeterChuma-yf1ps 12 днів тому

    Vote yanga naneso itengedwe

  • @KennethMchenga-j9c
    @KennethMchenga-j9c 15 днів тому

    Uthenga uwo siwamasewela mulungu akutetezelen ameni

  • @sthoramexjrsa902
    @sthoramexjrsa902 20 днів тому

    Amen father 🙌🙌🙌

  • @user-vz6jp6pb5j
    @user-vz6jp6pb5j 19 днів тому +1

    Amen father

  • @user-ve4zn2ne1k
    @user-ve4zn2ne1k 21 день тому +2

    Alleluia Abosa naneso ndi banja Langa ndaitengako mulungu afufute ndithu!!!!

  • @WilliamNhlane-fd9hi
    @WilliamNhlane-fd9hi 17 днів тому

    Amen God hear our prayers , rescue Malawi

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 19 днів тому

    Ulemu wanu Abusa ❤❤❤❤❤❤

  • @user-wd5tw1mz8h
    @user-wd5tw1mz8h 18 днів тому

    Wakutumani ndimulungu lankhulan mosaopa chifukwa malawi waonongeka ndi chakwela

  • @tresawillicky
    @tresawillicky 21 день тому +1

    Mau amphamvu zedi

  • @PaxKinley
    @PaxKinley 15 днів тому

    Ndatenganso nane VOTE yanga

  • @ChilangoNdalama
    @ChilangoNdalama 20 днів тому

    Amen abshop

  • @user-uy8uk7so9d
    @user-uy8uk7so9d 2 дні тому

    God be with you

  • @munashemoyo4190
    @munashemoyo4190 21 день тому

    Amen father Amen mau mau

  • @harrisbanda5891
    @harrisbanda5891 20 днів тому

    Tikufuna anthu olimba mtima kumalawi kuno ngati fazzala awaa

  • @user-oc9vl9xz8e
    @user-oc9vl9xz8e 21 день тому

    Uthenga uwuwu ukamufika woipa chikumbu mtima chimugwile

  • @AchinaKellz
    @AchinaKellz 20 днів тому

    Ine aroma ndimayiziwa ndiyimeneyi kafuseni malemu kamuzu aroma sia mcp

  • @GeorgeKambwiri-xr9ri
    @GeorgeKambwiri-xr9ri 12 днів тому

    Koma yaa🤝 9:58

  • @user-uy8uk7so9d
    @user-uy8uk7so9d 2 дні тому

    Munavotela zisilu kodi nanu

  • @alexmkolongo3089
    @alexmkolongo3089 19 днів тому

    Chakwela azindikile kuti akadzangotuluka boma akutengedwa komaso manganya ndi wa MCP asamatinamizepo apa

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 14 днів тому

    Yangaso ndatenga

  • @AlexKaunda-ny2eg
    @AlexKaunda-ny2eg 21 день тому

    Mukatenge chinzukwa uko Kuti chilamulire Amalawi mwandilidza😢

  • @zondanitzulumusicfly.5202
    @zondanitzulumusicfly.5202 21 день тому

    Mulungu wanthu ndi lawyer basi

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 14 днів тому

    Bishop Amen

  • @isabelmartin7567
    @isabelmartin7567 14 днів тому +2

    Analowa mu Zina la ubusa 😢😢😢osaziwa satana watola joker eeeeee ai chakwela wapweteka Malawian 😭😭

  • @EnockMuyaya
    @EnockMuyaya 5 днів тому

    Mumatha kurarika bwino bwana

  • @gladysbonongwe1038
    @gladysbonongwe1038 21 день тому

    Amen

  • @BlessingsMakalani
    @BlessingsMakalani 21 день тому

    Amen Amen

  • @user-gg9hw4oj2v
    @user-gg9hw4oj2v 20 днів тому

    Amen 🙏

  • @KingsleyTenthani-kf9px
    @KingsleyTenthani-kf9px 19 днів тому

    Momwemo abishop