Pakadali pano Anthu aku Votabe ku DPP Convention 2024 Kwinaku Brian Banda Kucheza ndima Delegate

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 11 вер 2024
  • Pakadali pano Anthu aku Votabe ku DPP Convention 2024 Kwinaku Brian Banda Kucheza ndima Delegate

КОМЕНТАРІ • 41

  • @ChawezChinkhuntha
    @ChawezChinkhuntha 23 дні тому +4

    Brian ntchito mukuigwira bwino saname❤

  • @KHWENGWEYAMAPEMBA-l4w
    @KHWENGWEYAMAPEMBA-l4w 23 дні тому +2

    Brian and your team, mumatipatsa zomwe zili pa ground.
    Chakwera ndi onzake ambwititsadi a malawi ambiri koposa.
    Anthu ochuluka ta-da nayo MCP kukhosi.

  • @EmmaEmma-q4u
    @EmmaEmma-q4u 24 дні тому +5

    Tauzani a razalo wo azayamba kunama kuti kudowa ife kulibe ko ma vote athu 😅😅mutu Wa chikangawa sukugwila yakwiya mizimu ya anthu 9 aja

  • @MexcoJepter-p5f
    @MexcoJepter-p5f 23 дні тому +3

    Kkkkkkk koma ndaseka akuti anthu akumudzi safuna chizungu ochewa otero

  • @MemorySambani
    @MemorySambani 24 дні тому +6

    Kunena zowona mcp chawo palibe🤣🤣🤣 i love you dpp

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 23 дні тому +4

    Apm my vote in any way

  • @TemboHaswell
    @TemboHaswell 23 дні тому +3

    Fateleza ❤😂😂

  • @fantesher
    @fantesher 23 дні тому +3

    Galimoto linkanchepa 😅😅😅 fateledza 😂😂 km Brian

  • @EmmaEmma-q4u
    @EmmaEmma-q4u 24 дні тому +5

    Kkk😂😂 Brian ndi can you say that again anakumalizatu ati tabwelezaniso umatha kuipasa moto dpp oyee

  • @user-uk1tt7ho9t
    @user-uk1tt7ho9t 24 дні тому +2

    APM woyeeeeee my vote mavuto mmamidzimu zinthu zakwera koopsya tasiya kukazinga ndiwo kusambaso kwavhepa tiphulensoni pamoto Aproffessor

  • @JamesMwale-o6i
    @JamesMwale-o6i 24 дні тому +3

    Fully support apm and watching from ku

  • @MphatsoMwale-it4xd
    @MphatsoMwale-it4xd 24 дні тому +2

    Tililimozi from jubec ine mphatso mwale dpp my vote

  • @MiziTata
    @MiziTata 23 дні тому +1

    Add more fire

  • @BishopMaxwell
    @BishopMaxwell 23 дні тому +2

    Dpp woyeeee 2025 bomaaaa💙💙💙

  • @aminamussa9835
    @aminamussa9835 24 дні тому +4

    achina Brian apanikizika mesa Kodi Hot current ija ndiyaleloli?

  • @georgekamba6965
    @georgekamba6965 23 дні тому +1

    Peter Mutharika woyee!

  • @AthonyChibwe
    @AthonyChibwe 23 дні тому +1

    Eeeeeesh koma brayan akukweze udindo ntchito ukuyigwila kkkkkk wakumana nonyamata okudowatu

  • @IshmaelWadd
    @IshmaelWadd 24 дні тому +2

    Am from Mozambique zonse tikuonela

  • @ShaficScotch
    @ShaficScotch 23 дні тому +2

    Kkkkkk kmaziliko 🎉🎉🎉🎉moto kutibuuuu

  • @PreciousMakono-f2g
    @PreciousMakono-f2g 23 дні тому +1

    Koma Brian Banda iwe ndi munthu wamkulu muraraaa

  • @MarthaMtonga-qt6tc
    @MarthaMtonga-qt6tc 23 дні тому +1

    Brian iwetu ndi akatundu 🔥🔥🔥APM my vote❤️❤️❤️❤️

  • @AndrewUnbreakable
    @AndrewUnbreakable 24 дні тому +1

    P. Kaliati waonesa ntima ofuna kuthandizila kukonza malawi wathu

  • @YankhoJulyMoses
    @YankhoJulyMoses 24 дні тому +3

    Live from Cape Verde DDP woyeee

  • @ElliotWadi
    @ElliotWadi 23 дні тому +1

    Zoonadi

  • @Jermah51kennias
    @Jermah51kennias 23 дні тому +1

    Brian anabwera😂😂😂

  • @JohnBanda-ux9fy
    @JohnBanda-ux9fy 23 дні тому

    Dzivere mtolo iwe chikangawa.. munthu ululakwa uyu

  • @MaxwellumbiriLumbiri
    @MaxwellumbiriLumbiri 24 дні тому +1

    Tili limodzi Nanu nthawi ino yamavuto kuchokera kn mozambique maxwel

  • @chitanibenito1109
    @chitanibenito1109 24 дні тому +1

    Ya fertilizer yomweyo its too much mpaka k103,000.00 osauka akayipeza kuti??? Koma zonsezi chakwera ndi anthu ake saona achita nkhungu mulungu wampangisa nkungu satana ameneyi.

  • @Lackisonkumwend
    @Lackisonkumwend 23 дні тому +1

    DPP oyeeee,!!!!

  • @kennethmatamanda9057
    @kennethmatamanda9057 23 дні тому

    Kutuwa kumeneko

  • @SkeffaKaifa123
    @SkeffaKaifa123 24 дні тому +2

  • @IshmaelWadd
    @IshmaelWadd 24 дні тому +1

    Chipani choganizila anthu ake dpp bomaaaaaaaaaaa 2025 Peter muthalika 2025 bomaaaaaà

  • @ChikumbutsoButao-h1s
    @ChikumbutsoButao-h1s 24 дні тому +1

    Ochewa amvekaawa

  • @WanangwaMfune
    @WanangwaMfune 24 дні тому +1

    Azasintha chani tiziwe nawo nafe

  • @isaaczuze
    @isaaczuze 23 дні тому

    Mcp ndi chipani cha amthu oyipa
    ..chakwera sakufunikanso ayi achoke basi
    ....chimwendo banda wafika pokunya mwano munthu oti amakonza ma radio koma ndi amene akumakonza ziwembu zambililimbili

  • @patrickmacheso5062
    @patrickmacheso5062 24 дні тому +1

    Ntchito ya manja a APM zikumchitila umboni,, Chikangawa abwelele ku mpingo not ku Capital Hill.

  • @user-ew1uv9vb7p
    @user-ew1uv9vb7p 24 дні тому

    Mwangokhuta inu Ku dowa Mene amakondera mcp guyz zinazi osamanamizna