DR JOYCE BANDA’S SPEECH AT PEOPLES PARTY 2024 CONVENTION

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 вер 2024
  • DR JOYCE BANDA’S SPEECH AT PEOPLES PARTY 2024 CONVENTION
    "PP ndi Mafunde atha kupalana ubwenzi"
    Mtsogoleri wa chipani cha PP a Joyce Banda walengeza kuti chipani chawo chikuchita zokambirana ndi chipani cha Mafunde kuti apalane ubwenzi.
    A Banda ati iwo ndi mtsogoleri wa chipani cha Mafunde a George Mnesa akhala akuchita zokambirana ndipo afika pogwirizana kuti ayende limodzi.
    Iwo ati alengeza kutsogoloku kuti ayenda motani komanso kuti agwirizana.

КОМЕНТАРІ • 8

  • @HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE
    @HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE 9 днів тому

    Amene amakana kugwesa kwacha amaganiza bwino ndithu inu munasocheresa dziko ,remember currency work like acids and bases the smaller the figure the bigger the value,the bigger the figure the smaller the value 😂😂😂wake up Malawian osamachemere ndi umbuli akuonesa apa

  • @user-pf5er7gc9s
    @user-pf5er7gc9s 10 днів тому +1

    Munayesesa inde koma chimanga chinali Cha malemu bingu inu munagulisa ndege chimanga chomwe anasiya bingu mpaka chinaola mumangoyemda yenda kumangoononga chuma chaboma cash get nkati. Tikakusankhaninso musinthe simumva kopereka mbuzi mpaka magalimoto 20 kuwononga chuma chaboma.

    • @JustinKamanga
      @JustinKamanga 10 днів тому

      @@user-pf5er7gc9s za cashgate bwanji sumnanene

  • @RICHMANCHIMWAZA
    @RICHMANCHIMWAZA 10 днів тому +1

    But Amayi khani yogwesa kwacha eeee siyabwino think twice

  • @HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE
    @HEROTHATNOBODYCANCELEBRATE 10 днів тому

    You made a big mistake by devaluation of the Malawian kwacha,the problem you tell anthu osaxiwa ndalama

  • @DawoodAlli-i9u
    @DawoodAlli-i9u 10 днів тому

    Nde zibwezi zakozi zikugwesa kwacha koma sizikuthekatu

  • @gracem-y8p
    @gracem-y8p 10 днів тому

    Mwadula pempero