MUKAMVA KWAYAMBA MAPOKOSO KU UTM MUSADABWE NKHANI YAKE NDI YOMWE WAYANKHULA MATTHEWS MTUMBUKA LERO

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 16 вер 2024

КОМЕНТАРІ • 186

  • @muhamadizaidiphiri4449
    @muhamadizaidiphiri4449 6 днів тому +37

    Koma ine ndikufuna Kuti akabambe ndi mtumbuka modzi mwa inu kuluza modzi akhale Vice President zikhala bwino

  • @clementmahoka6287
    @clementmahoka6287 6 днів тому +22

    My genuine advice to UTM: Don't make alliance with any party unless you are taking the leading role (presidential position) in that alliance. Otherwise, kaloweni nokha kuzisankho, and when you lose accept it and move ahead, you will win in 2030 with landslide because i don't see any leader who can change zinthu apart from leaders in UTM

  • @chifundomatumula1652
    @chifundomatumula1652 6 днів тому +28

    Combination of Mathews mtumbuka and kabambe can take this nation to another level, Akweni pa mpando wa u SG ndiokwanila

  • @SimonJesimani
    @SimonJesimani 6 днів тому +19

    Koma guys achinyamatafe tikanagwirizana kuvotera UTM. Kuli ma candidate abwino kwambiri. Chakwera is a waste of time

  • @AbsalomNkhoma
    @AbsalomNkhoma 5 днів тому +1

    My vote 4 mathews Mtumbuka ,a leader of gud vision ,osati kwinaku

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 6 днів тому +20

    Akulankhula Chichewa koma zamnzeru zokhazokha. You're very wise.

  • @SamukLungu-zg7fl
    @SamukLungu-zg7fl 6 днів тому +7

    Amene azasankhidwe pa udindo wa u president arumbire kuti nkhope ya chirima asazachose paripose pamene yiri osati kungotenga ndikuchosa zose ayi

  • @BostonMalisawo
    @BostonMalisawo 6 днів тому +19

    DR:KABAMBE :AZAWINA KOMANSO DR MTUMBUKA AZAKHALA VICE PRESDENT

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 6 днів тому +14

    God bless you Matthews Mtumbuka. You're the next president.

    • @AngelaMphinji
      @AngelaMphinji 6 днів тому +1

      Mmmm. O mwa. Hundred. Mtumbuka😂

  • @MakhumboMbowe
    @MakhumboMbowe 6 днів тому +1

    a mr.mtumbuka tiri pambuyopanu mulunga akusogorereni ❤

  • @kumbukanikafwafwa
    @kumbukanikafwafwa 6 днів тому +4

    Mtumbuka yu ndendende Peter. ❤❤❤ Chichewa chovuta kma zipatso zautsogoleli zooneka

  • @doreenkaliati3166
    @doreenkaliati3166 6 днів тому +2

    Indeeeeeee awa ndi Nyamata uyu Bola azakhale President or VP oyeeee UTM Moto🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥🔥

  • @BerthaMisanjo
    @BerthaMisanjo 6 днів тому +1

    Mfundo full more 🔥🔥🔥 mtumbuka

  • @JoycieMbaya
    @JoycieMbaya 6 днів тому +6

    Mtumbuka
    president, vice Kabambe. I can't wait to vote!

  • @DeliaKaduya
    @DeliaKaduya 6 днів тому +10

    Komatu anzanuso ankatero asanatenge boma, kungotenga ali buzy kumakakwera njinga ku Germany ife tikufa ndi njala, ntchito 1 million lija lasanduka kosaka chiteze kutchire 😢😢, Ambuye muoneni pomwe wafika Malawi tsopano, tisankhireni tsogoleri yemwe achose misonzi yathu, musalole tizisankhire tokha tsogoleri, Koma inuyo mutisankhire

    • @ussimasi2458
      @ussimasi2458 6 днів тому

      😂😂😂😂kabaza

    • @user-nu3dq5hi7q
      @user-nu3dq5hi7q 4 дні тому

      Pali kusiyana kwambiri pakati pa munthu wa xool ndi un educated. Enawo adanena ndithu kuti,one sindidziwa kanthu. Power mtumbuka akunenetsa Pano kuti Ali ndi upangiri wosiyanasiyana pa nkhani ya chitukuko

  • @samuzymkwanya8490
    @samuzymkwanya8490 6 днів тому +2

    He sounds like VP not President
    But Goodluck Mtumbuka ife a DPP tisankhileni munthu oti tagwile naye ntchito muchaka cha 2025 ADADI akazatenga usogoleri
    Plz ma delegeti a UTM munthu ndiameneyu

  • @GladesMhango
    @GladesMhango 3 дні тому

    UTM oyeeh🥳🥳 waluka Continue waluta🔥🔥🔥

  • @PrescotMkhwema-gl4eq
    @PrescotMkhwema-gl4eq 5 днів тому

    I'm proud to have a youthful democracy in leadership in Malawi

  • @Biath-m4b
    @Biath-m4b 6 днів тому +9

    Zikumveka bwino koma vuto mumalonjeza tikavota simumatikumbukila ai ndye chonde mukunenazo zikhale zoona

  • @JeanfatsanJere
    @JeanfatsanJere 6 днів тому +1

    Mr mtumbuka ur president of Malawi ❤ UTM my vote

  • @MathaNamanja
    @MathaNamanja 6 днів тому +1

    Mmmmm hmmm Ambuye atithandizee

  • @khumbombale496
    @khumbombale496 5 днів тому +1

    Atsogolreli a chipani cha UTM mutachita kuti kutenga A Mtumbuka ndi A Bambe onse kukhala kuyendesa U T M ndipo a Mayi athu okondedwa ndiposo olimba mtima a Kaliyati akhale pompo as SG ndipo musalowe mu alliance.
    Dzikoli lizaphulidwa.

  • @TitusGoba
    @TitusGoba 6 днів тому +1

    Akukhala ngat akuwelenga nkhani pa mbc, ngat Hassan Goba, eg, akumukuntha kwambiri mbomalooooo😂😂😂

  • @DjshukulanGift
    @DjshukulanGift 6 днів тому +1

    Dr kabambe akhare president inu vaic

  • @CelphaStephanSilungwe
    @CelphaStephanSilungwe 5 днів тому +2

    Never make alliance with other parties for utm to be successful

  • @LimbaniZimba
    @LimbaniZimba 6 днів тому +1

    My vote

  • @AndrewjemesJemes
    @AndrewjemesJemes 6 днів тому +3

    Ine sinima vota chifukwa snikhulupilira anthu andale koma uyu afuna aniyambise akanitenga bwino

  • @benitomtegha3788
    @benitomtegha3788 6 днів тому +2

    Welcome Mathews Mtumbuka. This is the rebirth of new Chilimas. Let's fulfill Chilimas ideas and beyond.

  • @MakeSunshine100
    @MakeSunshine100 6 днів тому +1

    Lets go!!!! Lets go!!!!

  • @emmaculatemenzeiwa
    @emmaculatemenzeiwa 6 днів тому +4

    Contesting doesn't mean division. Let the people's choice win.

  • @MpapiParadise
    @MpapiParadise 6 днів тому

    Utm ingotaya nthawi , kulibe wanzelu kumeneku ai . Utm inatha 2021

  • @PatrickFicklem
    @PatrickFicklem 6 днів тому +3

    Maganizo abwino big koma musalonjeze zambiri pakamodzi zingalowe bodza😮

  • @IshmaelAyami-l7s
    @IshmaelAyami-l7s 4 дні тому

    Thandizen Mtumbuka zake Ku Mpotokoo😊

  • @user-iq5xk6ju7y
    @user-iq5xk6ju7y 5 днів тому

    Me waiting the results after the Convention in November. Koma chomwe mudziwe Mtumbuka and Kabambe is more less than WIPON OF MASS DISTRACTION. Fredokiss will be the Minister of youth in the first place, but hope is there to be President in future. UTM ikadzangotenga boma ikubwera kudzakhala 🔥🔥🔥🔥 zinazi tayesa komanso zinazi tazibweleza koma manyaka okhaokha 🤮 a Malawi tikapusa ndithu dzikoli sitidzalinva kukoma mpaka Yesu adzabwera. Unless there is another Malawi after this life kumene mwina SKC anapita kukatikonzera 😭😭😭😭
    REST WELL BIYENI 😭😭

  • @GeoffTchezan
    @GeoffTchezan 6 днів тому +1

    Kodi nd za m'maboma? Kkkkk zikundivuta kunvetsetsa ine😅

  • @WillyNyirenda-l7h
    @WillyNyirenda-l7h 6 днів тому

    Encouraging speech. Let's support him. Let's not look at his age but his ability to deliver. But should be careful not to promise people the moon.

  • @JoshuaNyirongo
    @JoshuaNyirongo 6 днів тому +1

    Dr Mtumbuka ndi mtumbuka. Aphunzira kulankhula pompano asiya kuyowoya

  • @NolityKondowe
    @NolityKondowe 6 днів тому +3

    Vuto ndi wa ku mpoto.Ndale za mmalawi ndi za tsankho ndipo ndi za mzigawo.

  • @CatherineDesire
    @CatherineDesire 4 дні тому

    Kodi usi wadzima 🙄amajijilikila pakatipa 🙌

  • @ishmaelnkosi6228
    @ishmaelnkosi6228 6 днів тому +1

    During Saulos iyeyi anali kuti and why saanamusankhe?

  • @JaporAhmed-e2j
    @JaporAhmed-e2j 6 днів тому

    Pomwe pagona khani ndiposekula makapanipo boma lamalawi tikumvutika kamba kopanda makapan chifukwa tilindizambili zotiyenereza modzikoli dzikomo Dr Matthews

  • @henryphiri6100
    @henryphiri6100 6 днів тому +3

    Tikadzaluza tidzavomereze zotsatirazo chifukwa sitikufuna kuti chipani chife.

  • @jonathanshonga4742
    @jonathanshonga4742 5 днів тому

    mulibe utsogoleri umu, zikatha anona ndi aswiswiri dithu

  • @jimmykanjere5877
    @jimmykanjere5877 5 днів тому

    Akulu awa ndithu zadzawina,mark my words

  • @ChristianMalingamoyo
    @ChristianMalingamoyo 6 днів тому

    Pakati pa iwe ndi kabambe please ,mulungu atipase

  • @MzikaPhiri
    @MzikaPhiri 6 днів тому

    Ine ndamukonda Mtumbuka

  • @lucianogeoffrey4275
    @lucianogeoffrey4275 6 днів тому +1

    Kambalame koulukitsa kamaphonya chisa bwana mukuyenera kukhazika mtima pandi phuma lachuluka. Otherwise you’re a good leader 🎉

  • @AubreyWilson-j8w
    @AubreyWilson-j8w 6 днів тому

    Zikomo bwana Bola nanunso mukazawina musazayambe kunena kuti (wakhwitu wakhwitu)

  • @user-db3mh9wr9v
    @user-db3mh9wr9v 6 днів тому +2

    Mtumbuka ndi Kabambe ndiomwe agathandize dziko lino

  • @user-ro3yw2zv5b
    @user-ro3yw2zv5b 6 днів тому +1

    Where were you Mr mtumbuka?UTM may God see you through

  • @AbelNyirenda-lu1qy
    @AbelNyirenda-lu1qy 6 днів тому +6

    I love you Mr mtumbuka /

  • @TreverDominic
    @TreverDominic 6 днів тому

    Zaziiii bas ina ankatelo

  • @MadalitsoBokosi-j3u
    @MadalitsoBokosi-j3u 6 днів тому +1

    Bola izi sizokhalira kunja nsima misika mumuuze usi apite akajambule tikuferanji komwe akuja chiteze

  • @AustinMhone-r3s
    @AustinMhone-r3s 6 днів тому

    Malawi is lacking good leadership but these two leaders Mtumbuka and kabambe they must lead us ViVa UTM tsogolo lowala.

  • @elsa1973
    @elsa1973 6 днів тому

    Chepesani kusisa voice pa intro makosana

  • @marthamwenelupembe1188
    @marthamwenelupembe1188 6 днів тому

    Mulungu alowelelepo plz🙏 all the best

  • @SaidiMbawa-st6bj
    @SaidiMbawa-st6bj 6 днів тому

    Nthawi yonseyi adali kuti awa ndikudabwa kuti palibe akuluakulu ena palibe apa

  • @giftedmshan6779
    @giftedmshan6779 6 днів тому +1

    Mtumbuka hoyeeee

  • @SlindiryLoveness
    @SlindiryLoveness 4 дні тому

    Zaziii kungofuna kuzaba basi mungakhale prensident waziko inu kungofuna kuzawononga ziko basi bwanji panopa kulinjara osatuluka kuti kamene ulinako wapase anthu ovutika maboza basi

  • @paulbanda9638
    @paulbanda9638 6 днів тому +2

    MCP Kuba kwambiri, tengani dzikoli a mtumbuka

    • @kensonmbewe6692
      @kensonmbewe6692 6 днів тому

      Mudzaziwonanso m'mene adzazibere amenewa ndalama, these are politicians, nanji ma amateur

  • @EliasSupanela
    @EliasSupanela 6 днів тому +1

    True

  • @justinchabwera5380
    @justinchabwera5380 6 днів тому

    Kudzikonda chabe

  • @ishmaelnkosi6228
    @ishmaelnkosi6228 6 днів тому

    Palibe zachilendo zikukambidwa apa

  • @NellieChikuse
    @NellieChikuse 6 днів тому

    There's future

  • @FatimaUmali-pc8sy
    @FatimaUmali-pc8sy 6 днів тому +4

    Atumbuka nawo ndiasakho amangofuna okhaokha maudindo wakhwituwakhwitu zanga eine mtumbbuka Bola kana be 😮😮😮

    • @jonathanmwanja3994
      @jonathanmwanja3994 6 днів тому +2

      Find another reason. That one is outdated.

    • @isaihmagani5697
      @isaihmagani5697 6 днів тому +2

      ​@@jonathanmwanja3994pita nazo kwina zimenezo ku UTM kulibe

    • @ephraimkadamika
      @ephraimkadamika 6 днів тому +1

      Koma nanu pano sitikuyendera za ntundu koma yemwe awombole malawi

  • @MaryChavula-jz3di
    @MaryChavula-jz3di 6 днів тому

    Tadzilankhulani mukamaiza mupumule tilindi ntchito zomwe tinaziwona kale ndi dpp tikufuna zimenezo zongotinamizazi zatikwana

  • @GeoffreyMikondo
    @GeoffreyMikondo 6 днів тому

    Pa mbuyo panu inu ndi kambabe kammbilani mugwile limodzi

  • @Veronica-o2d
    @Veronica-o2d 4 дні тому

    UTM for sale now

  • @OmarManjawira-up3ns
    @OmarManjawira-up3ns 6 днів тому

    A stitch intime indeed serves nine ,Utm as a problem of kuyang'anira zinthu ( kulekelera even the late SKC had a same problem so izizi we re not sure bwana ,,,,,, cos u have never been there before nde this time around Malawians wants anthu odziwa zintchito osati Ya class ,atleast "Kabambe , Atupele, Chihana and APM

  • @KettinesMunthali
    @KettinesMunthali 6 днів тому +1

    Tiyeni tiyese atumbuka mwina angatithandize

    • @patrickmatabwa5828
      @patrickmatabwa5828 6 днів тому +1

      You are right its high time we should try the northerner and its my belief will do better as will be from minority may work for all regions to get the second term.....if we miss this opportunity mmmm kaya
      ..zakwathuzi sizikuthandiza chitukuko chadziko.....

  • @komanicomrademunyenyembe9096
    @komanicomrademunyenyembe9096 6 днів тому

    😢tione zina

  • @RowlandChimzimu
    @RowlandChimzimu 6 днів тому

    Mtumbuka wooooooyeeeeeeee

  • @MarthaGama-q1o
    @MarthaGama-q1o 6 днів тому

    Mfundo ndiye zikuveka koma Poti a Malawi amadziwa kulonjeza koma kukwanilitsa kumavuta, akangowina amalephela kukwanilitsa zomwe amalonje ,chimene chimakula ndi kudzikundikila kusava zofuna zawanthu komanso kulephela Ku tsegula misika ya a dmaric , koma ngati mukunena zowona vote yanga ndiyanu

  • @JuniorSamalia
    @JuniorSamalia 6 днів тому

    Lucky to you!

  • @actuarialscience2283
    @actuarialscience2283 6 днів тому +1

    There is no doubt he is intelligent. Ku MCP kulibe olo wa JCE. Chakwera alibe JC;

  • @user-le9su3mt7r
    @user-le9su3mt7r 6 днів тому

    Good bomaa

  • @jennyx6914
    @jennyx6914 6 днів тому

    amanganya kapena kuti a V P mr usi bwanji sanathamangileko kokadya chitedze abale inu?
    please mr. bon kalindo muuzeni mnzanu kuti akasye chitedze pomwe inu mr bon kalindo mukulankhulira anthu chilungamo our advocate amphawife

  • @mabvutomichaelpanagona1949
    @mabvutomichaelpanagona1949 6 днів тому +3

    Ineyo ndikusapota inuyo nose awiri Dr mtumbuka ,komaso Dr D,kabambe inuyo awirinu amene alephele adzakhale wa chiwiri kapena nditi vice president, mpando wa secretary ndikanakonda wini wa mpando umenewu asachoke akhale pomwepo mayi p, kaliati, mayi kaliati chonde sikukunyozani ayi mpando wanu ndi secretary general ndiye wanu mwachoka nawo kutali ndipo umakhalani,chonde chonde mai kaliati.uyu kazitapeyu mumati ndi Michael usi ameneyu akhale owona za achinyamata kapena nditi wa yufi chigawo cha kumwela adzinamiza anyamata akumeneko kuti adzipeza nthawi yopanga madirama ake akumudikira bon kalindo, nginde,mai asikono komaso achisi ndi enaotelo.

  • @AlexiousMakondetsa-hl6dy
    @AlexiousMakondetsa-hl6dy 6 днів тому

    Mwauyu ndikuonamo utsogoleri

  • @EliaThomas-vp9jz
    @EliaThomas-vp9jz 6 днів тому

    English v Mathematics Devaluation v Dama

  • @GodfreyWhayo-hh1dm
    @GodfreyWhayo-hh1dm 6 днів тому +4

    Kuyankhula kwa munthu oyembekezera kukhala mtsogoleri wa dziko koma kumeneku .

  • @MavutoLorry
    @MavutoLorry 6 днів тому +1

    Kulibe mapokoso

  • @ExcitedBreakingWaves-oh3zb
    @ExcitedBreakingWaves-oh3zb 6 днів тому

    mtumbuka mukunama.

  • @charleskayerasky1342
    @charleskayerasky1342 6 днів тому +1

    Ali ndi befutu koma azalimba during campaign time😅

  • @andofullkay8404
    @andofullkay8404 6 днів тому

    Fire

  • @user-gd2kl1fx1q
    @user-gd2kl1fx1q 6 днів тому

    Utm forever

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 6 днів тому

    CHITSILU CHSKWRRA ANTHU AKUDYA ZOSADZIWIKA CHITSILU MUTU WAMAKO CHITSILU OSAGANIZA IWE CHAKWERA

  • @TopoTopo-bm4vw
    @TopoTopo-bm4vw 6 днів тому

    Amtumbuka aku achita kuphedwa ndimabugwe ,,,zikakhala bwino chikanakhala chiganizochake ndekuti azakhala ngati achakwela sakuziwa chomwe akuchita asongoleni ngati awa aziza yendela maganizo anthu

    • @henrymwale8994
      @henrymwale8994 6 днів тому

      Wandale aliyese amatero inu Mesa imakhala njira yofuna kupanga anthu kuti adziwe kuti ndiofunikira

  • @user-mv6tn3qv8v
    @user-mv6tn3qv8v 6 днів тому

    Mfundo zabwino kwambiri komaso zogwira mtima koma ofunika anthu kuwachotsa maganizo akuti atumbuka amachita tsankho MMA office kuti azikhala okha okha pachibale Pao

  • @ConlardNkhoma
    @ConlardNkhoma 6 днів тому

    Kkkkkk kusowa msogoleni ndiinu nomwe

  • @rosechapita3434
    @rosechapita3434 6 днів тому

    Inu mukumunyozani pitanitu mukayimile muli phwii

  • @FredKanyerere
    @FredKanyerere 6 днів тому

    Good speach.

  • @OnexAliMwale
    @OnexAliMwale 6 днів тому

    Kulankhula ndikuchita ndi zinthu zosiyana..ndipo palibe chachilendo apa

  • @GraceZumazuma
    @GraceZumazuma 6 днів тому

    Inutu mwinadi kuphula Malawi pa mavuto

  • @JoelCHIHANA-y6p
    @JoelCHIHANA-y6p 6 днів тому

    Wooooooooo

  • @KestonNGUBO
    @KestonNGUBO 6 днів тому

    Kuyakhul bho bho t Mr

  • @omarlux3434
    @omarlux3434 6 днів тому

    Wandale amana muti athu andiphepha mmm izi ine ayi

  • @GeorgeMwale-ce8eb
    @GeorgeMwale-ce8eb 6 днів тому

    Palibe mapokoso apa.
    Manganya ndiamene wazi hitsa yekha

  • @juliussamson6212
    @juliussamson6212 6 днів тому

    CHAKWERA AKUFUNIKA ADXAKHALE LIFE NDENDE MTSOGOLELI OYAMBA KUTI ENA ADZATENGEREPO PHUZILO

  • @AndreaBotoman
    @AndreaBotoman 6 днів тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥