Розмір відео: 1280 X 720853 X 480640 X 360
Показувати елементи керування програвачем
Автоматичне відтворення
Автоповтор
Exactly we need this. More fire guys
Amalawi ambiri tikufuna Lazaro achoke pa Mpando
Uziti Alomwe, kagwere uko Chakwera sakuchoka.
Chakwera tachoka pampandopo
@@tasmania527ganyu mukupanga apayu ndiosenza misomali opanda nkhata, uku maudindo sakhalatu mbali imodzi. Osati maudindo onse ofunikila Central region
@@JustinLipipa You're a big liar. Lomwes were all over in many positions from Bingu to APM. There are several positions now given to northerners and those from the south. DPP likes dominance and arrogance.
Ukunama.
First to comment JJ from SA ndingot mafuno abwino AMEEN
All the people ilike and loves dpp❤
APM our last hope
Ichi ndichipani chime amalawi timakondweramo mwatendere ndithu tili pambuyo pa DP p woyeeeeeeeee
UDF,UTM, AFORD and DPP will make 100% Government, chifukwa muzipanizi muli akatakwe pkha okha pa economy. Key ya development.
UDF, UTM and AFFORD zipani zipani zimenezi zidatha zlibeso mbiri
Mwana Wa njoka iwe kagwere utm my votes SKC forever in our hearts ❤❤❤❤❤
MCP boma
Chikangawa atipha tikuenera kubwelera pa mbuyo chifukwa ndiye Malawi wanukha
Koma ma albino ofunika kuwaganiziratu anayamba ku Asuka koma eee adzalekeso kuyenda mmmm khaza
❤❤😂😂😂
Ulemu wanu atola nkhani mumafunsa mafunso abwino kwambili ndimakunyadilani
Zonse zabwino Dpp yomweyeeeeee waboma basi
Ben Phiri kuchenjera mmalankhulidwe akukwana kukhara spokesman
Chonde chonde A Dpp, utmost, Aford, udf. Pagani zomwezo ine Mcp ayi
Mukhapidwa 70+ % MCP oyeee
Take us out of slavery pliz. Bravo
Ndipo mutapanga alliance zikhala bwino kooooopsaaaaa
Tibwezereni Ku Malawi adad awawa akutitengera kokatiphatonse pliz
Kkkkkkkkkk ok
Boma iloooooooo
Amen❤
Chepadambo sopano.lets walk together
E ufumu umenewu ugawidwepo ndabomera nane iya
Zilbwino
Kkkkkkkk bible kulilowetsa ku chipani anthu a tsoka inu
Ayanga bwino kwambili
Zabwino zonse
Mpanga nokha ife a UTM ayi tinachokako kare ku DPP tipanga zathu apo B mdzavota ndinu mwagwilidzana
Mwinaso Ku UTM uko sakukuziwaniso
Munthu angalankhule chomwe asakuchidziwa?@@ChristopherKawilam
Mau ife team nkhalamba ayi utm my votes SKC forever in our hearts ❤❤❤❤
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂@@ChristopherKawilam
Mmmmmmm koma agogo aloweso gys chenjezo bwanji tidikire migwirizano inayo
Anthu chomwe akufuna okuphawa Achoke bac, chomwe waona wamkulu atakhala pansi mwana olo atakwera mumtengo sangachione.
Tikufuna agogo omwewotu mbali za kunoko
Koma ndiponso inu mpaka nganga kawiri 😂😂😂😂