ASILAMU NAWO ALI PA MBUYO PA BISHOP WA MPINGO WAKATOLIKA

Поділитися
Вставка
  • Опубліковано 27 гру 2024

КОМЕНТАРІ • 321

  • @MartinKapito
    @MartinKapito 19 годин тому +4

    Amen amen ambuye akudaliseni a Muslim komanso ma bishop onse omwe akuima pachilu Gamo Ngati bishop msunsa wamwambayo akusungeni ndi kukutetedzerani poyajhula chilungamo

  • @tinkaphethi1395
    @tinkaphethi1395 22 години тому +7

    Bravo Arch Bishop Thomas Msusa. Your address to your congregants was and is in order. A great sign of experience, maturity and wisdom. Elijah never feared Ahab to convey the message from the Lord about the death of Nabot...

  • @KondwaniChaponga
    @KondwaniChaponga 19 годин тому +6

    Uku nde kuyakhula mwa tchutchutchu bravo💪we need black box

  • @MarriamShakira
    @MarriamShakira День тому +18

    Musilimu oyeee ❤❤❤❤

  • @IbrahimUseni-p8f
    @IbrahimUseni-p8f День тому +17

    Kodi liport lagermany lisanatuluke achakwera kugermany amakatani?komanso blackbox ilikuti?komanso magazi a anthu amene anali mu ndege anapita kuti?abale achakwera kumupha mzanu,,,kuthesa milandu ndicholinga mulungu akudaliseni

  • @LastonMmanga-r2u
    @LastonMmanga-r2u День тому +19

    Wina mphuno biiii!!!! Akuti boma ndilomweri agalu anthu oyipa kupha anzanu kuti muzuze Ena, mulungu sakusiyani choncho ndipo nonse mutha m'modzi m'modzi, xiiiim

    • @kittymalambo1853
      @kittymalambo1853 23 години тому +2

      Anthu ozolowela umphawi mmene Malawi watenthelamu wina nkumati boma ndilomweli

  • @HawaHussein-o5k
    @HawaHussein-o5k 19 годин тому +4

    Ameen mashaallah ambuye alowelele chilungamo chioneke

  • @LawrenceMakina
    @LawrenceMakina 22 години тому +6

    Allah bless you. Mwayankula mwa umunthu ndi mwa uzimi. Mosanyoza koma mopereka uthenga.

  • @FraserNamaona
    @FraserNamaona День тому +15

    It's time to show Chakwela kuti this is 2024 kape ameneyu achoke before voting.

  • @ChancyMakwinja
    @ChancyMakwinja День тому +17

    Ameneo nde asilamu eni eni

  • @mohamedriazshreef8697
    @mohamedriazshreef8697 День тому +13

    We need black box please 😭😭😭😭😭😭😭😭

  • @FracksonKonzani
    @FracksonKonzani День тому +7

    Achakwera mukuva Bwanji komwe muliko dziko likufuna black box mukubisiranji
    Awa ndi asilamu eni eni osati unja amalobwa dzulo unja
    Munya inu a MCP mupumira mphati tulutsani black box ndi akukuyu anuo
    Chilungamo chionetsedwe apa
    A nsusa tili bali yanu pamodzi ndi Aslam onse

  • @RahimYusufu-u2b
    @RahimYusufu-u2b 21 годину тому +3

    Yes yes ife asilam taima pa blakc box zomwe iyakhuile tikhulupirira Paja mudati yasilungidwa pa bwino itulutseni tsopano mkale lija.

  • @IdigoDigoz
    @IdigoDigoz 7 годин тому

    Walayikum salaam landirani ulemu wanu brother msilamu aziyankhula chilungamo

  • @MariaPhiri-s3u
    @MariaPhiri-s3u 22 години тому +1

    Uko ndekulankhula. Excellent talk. Amina!

  • @lungisanishezi1023
    @lungisanishezi1023 День тому +9

    Black box ili ndi ndani please tikufuna chilungamo ife

  • @MarySinjirani
    @MarySinjirani 22 години тому +6

    Chakwela, Moses where is BLACK BOX guys 😩😩😩😩

    • @PreciousSteven-e5s
      @PreciousSteven-e5s 20 годин тому

      Kumkuyu ukumva bwanji waikanda paliwombo malawi kodi mukamapanga zopusa zanuzo mukungoona ngati amalawi ose Ali nawo muzautsiru zanuzo munya simunati agalu inu ndiye uno December nanga tikamafika mu February zikhala bwanji ayi zikgare chakwera uziona ndizikhareyo

  • @HaroonKampepule
    @HaroonKampepule День тому +7

    Maa shaa Allah. Abalalika amenewa basi.

  • @DenisManjomo
    @DenisManjomo 23 години тому +2

    Much appreciated, good speech 💬

  • @DixonChimanya
    @DixonChimanya День тому +6

    Nanga adauza chakwera kuti ndege idafika ku zuzu ndi ndani
    Nanga adauza nkulu wa asirikali kuti ndege yagwera kowirira ndani
    Nanga adamuza chimwendo kuti ndege yadzaza ndi ndani
    Nanga adavula zovala abale anthu ndi ndani

    • @spargomw
      @spargomw 21 годину тому

      😭😭😭😭😭😭😭😭🙌🙌🙌

  • @JrAlfeoLungu
    @JrAlfeoLungu 6 годин тому

    Kuyankhula kwa anthu a genuine ❤ osat ajiya aja

  • @MaxwellChiwaya-i8q
    @MaxwellChiwaya-i8q День тому +24

    Where is black box

    • @RitaKainga
      @RitaKainga 59 хвилин тому

      Yes,bwanji osaibweretsa poyera, shame on them

  • @AllanMumba-b9q
    @AllanMumba-b9q 20 годин тому +2

    Let Archbishop Msusa state his personal stand and provide a voice space to those who lack platform to be heard

  • @VincentChisale-j6m
    @VincentChisale-j6m День тому +5

    Zoonadi Rev Arc bishop mwanena mau ogwira mtima ndithu mulungu akusongoleteni ndikukutetezani pa chilungamo chomwe mwayakhula ,ndinudi msongoleri wonena chilungamo mulungu akutetezeni kwa anthu akhazawa

  • @GeorgeWahera
    @GeorgeWahera День тому +6

    Black box ,yes . without black box, BIG NO

  • @Nelsonmatenda
    @Nelsonmatenda День тому +6

    Ndine khristu koma ndigwilizane ndi shehe kuti mcp ikutiona ngati Ife zitsilu imagine Nkukuyu ananena kuti black box ili safe, a chakwera akuti ndege inafika ku mzuzu, General wa army akuti ndege inagwela kumitengo yoophya, chimwendo Banda Amati ndege yazaza..nde bwanji a inquiry sanawapeze anthu awa ndikuwazenga? Zopusa basi

  • @ChristopherMangwiya
    @ChristopherMangwiya 16 годин тому +1

    Eya tione ngati muwine sopano,iyi ndiye ndi mipingo yoopsa ikamanga Chao yamanga musawasiye amenewa ,anaphaso sidiki Miya amenewa .

  • @OpexShisha
    @OpexShisha 21 годину тому +2

    Big up Muslim committee
    Chikangawa chisamwe madzi anene zoona zake 😂😂

  • @MayesoGremu
    @MayesoGremu 21 годину тому +2

    Kwachema winachisekodi champana ndithu😂😂😂😂😂😂😂😂

  • @daviemtali3421
    @daviemtali3421 2 години тому

    Bravo Muslim brothers!!

  • @AdamJames-x7x
    @AdamJames-x7x День тому +6

    Ndipo zoonadi ine Ngati m'slam ndili Ku mbali ya bishop msusa 💯 percent, osamabisa chilungamo ayi Muthu anachita kuphedwa osamanamiza anthu ayi .

  • @SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON
    @SYDNEYMUHAMBUWAGIBSON День тому +3

    MCP cant fight God and win...mwina ziyamba ndi iwo let's wait and see...

    • @henryphiri6100
      @henryphiri6100 22 години тому +1

      Adalephera Kamuzu adayesa kulimbana ndi ma Bishop's. Mapeto ake landslide

  • @sparkdymon3429
    @sparkdymon3429 5 годин тому

    Kuyakhula kwamzeru chehee bravo 👏

  • @JohnSailes
    @JohnSailes 7 годин тому

    Kodi akubisa bwanji black box 😂😂😂😂

  • @HusseinAdamLidezo
    @HusseinAdamLidezo 19 годин тому +1

    وعليكم السلام ورحمة الله وبركاته، جزاك الله خيرا

  • @MfuneExwalu
    @MfuneExwalu День тому +2

    We need such kind of readers in Malawi, not onyamula matumbawo kunamiza amalawi , chamba eti

  • @MikeKameta
    @MikeKameta День тому +4

    Nsilamu wanzeru uyu. Kumeneko ndiye kuyankhula. Black box ikufunika apa. A kunkuyu tulusani black box pano anthu adziwe zoona zake

  • @IsmaelBilal-lh1pi
    @IsmaelBilal-lh1pi 22 години тому +3

    Bravo Muslim brothers

  • @ziwani3682
    @ziwani3682 21 годину тому +2

    Mashaallah inenso sindinakhutire

  • @SelinaGamaliyere-q8v
    @SelinaGamaliyere-q8v 21 годину тому +3

    Mizimu ya anthu 9 iwasowetsa mtendere ndipo chikangawa sunati

  • @wisdomchilanga723
    @wisdomchilanga723 19 годин тому +1

    The main thing we need is black box From Mr kunkuyu because at first he said that the black box well kept in a safe place

  • @mutumwathongethonge7892
    @mutumwathongethonge7892 15 годин тому

    I am happy that the things that APM warned Malawians about, are unfolding whilst he is still alive.

  • @WillieLamwa
    @WillieLamwa День тому +2

    MCP party does not practice real democracy

  • @GeoffreyBAyatuKazembe-q7u
    @GeoffreyBAyatuKazembe-q7u День тому +3

    Shek akunena zoona, coz press briefing ya these guys so called concerned faith leaders ikukolezera chikaiko kuti ndichifukwa chani akuyesera kumutseka pakamwa Bishop Msusa??...... Anthu amenewa atha kukhala kuti ali pa contract ndi winawake

  • @Esnart-o6p
    @Esnart-o6p День тому +5

    Nganganga pambuyo pa bishop Msusa

  • @LucyEndmond
    @LucyEndmond День тому +3

    Tsoka mtunda ndi Nyanja, pakuti woipayo watsikila komweko, asegula. M,mimba sanati. Mzimu wamuthu supita padera

  • @RheggieIssah
    @RheggieIssah День тому +6

    This is the beginning of MCP downfall.

  • @LevisonDaka-f5x
    @LevisonDaka-f5x 23 години тому +2

    We need a black box that is when we can know the truth and honest

  • @yasiniKalonga
    @yasiniKalonga 19 годин тому

    mashaaAllah ❤️💕💖💖

  • @manzyjk8453
    @manzyjk8453 День тому +3

    Abwereso ndi. Press briefing yawo adzipembedzo adzulo anja tiwamve ayakhula chani ndi christu koma apa Aslam ndili mbali yanu mwaima pa chilungamo

  • @SamukLungu
    @SamukLungu 23 години тому +1

    Thanks very much keep going

  • @MoosaMwanyali
    @MoosaMwanyali 19 годин тому +2

    Chakwela akathela ku prison basi

    • @SliviaJosephy
      @SliviaJosephy 8 годин тому +1

      Tikamuphera ku chikangawa komweko

  • @ChancyPhiri-i6e
    @ChancyPhiri-i6e День тому +4

    Lululululu apo mwayankhula Black box ndiyomwe yidzanthetsa nkhani

  • @MarkElia-i7q
    @MarkElia-i7q 11 годин тому

    Arch Bishop wathu waima njii pa chilungamo khalidwe loipa ife nziko mwathu sitikufuna

  • @HalisonSolomon
    @HalisonSolomon День тому +2

    NKHANIYI NDI YOONA BLACK BOX ATULUTSE NGATI AKUFUNA AMALAWI AKHALE CHETE, KOMA CHILUNGAMO TICHIDZIWA CHAKA CHA MAWA CHAKWERA AKACHOKA MBOMA . BISHOP MSUSA MUSACHITE MANTHA AMENE AKUSUSAO NDAMENE AKUDZIWA CHIWEMBU CHOMWE CHINACHITIKA PA IMFA YA CHILIMA.

  • @marykadzola835
    @marykadzola835 22 години тому +1

    Amen sheikh,apatu nanu muyembekedzere press briefing Ina ya a mipingo.

  • @alexmulimi8773
    @alexmulimi8773 Годину тому

    Whatever Msusa said is based on his own point of view ,as long as it is not based on facts,peolple can choose to agree or differ with him. In this world there no any report that was established that satisfied all sectors of the society. Some people are born antagonists.

  • @SanudiKAINGA
    @SanudiKAINGA День тому +3

    Nàaam lmeneyo ndiye Muslim association of malawi osati zimenezinja ayi makadeti anja

  • @laurentbutao4084
    @laurentbutao4084 18 годин тому

    Sure Chilima amkakonda kuyendesa yekha .Anali ndi chidziwitso ndithu

  • @PhillipSemu
    @PhillipSemu День тому +1

    Ida katiuza za black box mwina tikadamvako km 😂😂😂 yakwiya ndimizimu kunoooo kuyaluka mcp ija iiiiii mavuto mulinawo ndipo iweyo chikangawa udzafa ngati stephano oipa iwee galu amakuopa ndiomwewo opusa iweee

  • @VioletBanda-lb7sj
    @VioletBanda-lb7sj День тому +2

    hahaha bravo Muslim association of Malawi. muyembekezere brief report yanu. kkk wina athawa dziko lake

  • @EsetaGerate
    @EsetaGerate 10 годин тому

    ❤❤❤❤❤mawu

  • @EthelKubalasa
    @EthelKubalasa День тому +1

    Kodi azibusa abodzawa akuti amalimbikitsa mtendele analikuti mene chakwera amasayinila nkhondo ya ku Israail, bwanji sanamudzudzule chakwela choyamba posafuna mtendele ku Israail. Azibusa wonyenga ndi abodza mulungu adzawakhatha.

  • @ALIEMUHAMMAD-yb4lr
    @ALIEMUHAMMAD-yb4lr 20 годин тому +1

    Nkhan ndiya black box basi.ndipo ngati kunkuyu sapereka tiyen tonse a malawi tipite ku state house tikatenge tokha coz mmene ayankhulira sheikh wo ndi mawu omveka kwa munthu amene ali ndi mzimu koma kwa chakera sangamveke coz ndi chigawenga cha kupha sangamve .nkhani ya bwino ndiyongo pita komwe kuli black box.ndipo akakana kupereka tikango mugwira gira basi then akapereka

  • @StevenAjusugama
    @StevenAjusugama День тому +1

    Weldone well speaking M A M

  • @Mtk-v2-5e
    @Mtk-v2-5e 19 годин тому

    Good message Muslims, you stand for Malawians

  • @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id
    @rachidepitamuhamedmuhame-jg9id День тому +1

    Mulungu ❤❤❤❤❤

  • @JohnPhiri-t2r
    @JohnPhiri-t2r 18 годин тому

    Ulemuwanu shehe❤

  • @robsonmapeto1911
    @robsonmapeto1911 12 годин тому

    Bishop amalankhula ku mtundu kwawo wina kusavuka ndikumakamema agulukunyinde wena kumatsutsa zakukhudzani munjira yanji tikudabwa nanutu

  • @ShamimuBisani
    @ShamimuBisani День тому +2

    Wallaikm salaam warahamatul llahil wabarakatul. Taqilbil ALLAHU AKBRUH til pambuyo pa Bishop MSUSA

    • @YasinterKapinga
      @YasinterKapinga 23 години тому

      Walykm Salaam walahamatulah wabalakatuh allah akhibaru

    • @ShamimuBisani
      @ShamimuBisani 23 години тому

      @YasinterKapinga Shkran cc Allah apitilize kukupasan zabwino banja lanu lonse cc

    • @YasinterKapinga
      @YasinterKapinga 23 години тому

      @@ShamimuBisani mashallah cc inuso chimodzi modzi

  • @FiskaniChidatha
    @FiskaniChidatha 18 годин тому +1

    Am waiting patiently to hear the recorder of a black box

  • @TriciaMalikebu
    @TriciaMalikebu 18 годин тому

    Well done a Muslim council

  • @PatrickMaluwah-bx9or
    @PatrickMaluwah-bx9or 21 годину тому

    Allan bless you and your team.

  • @andiwochishadreck3753
    @andiwochishadreck3753 День тому +1

    Congratulations 🎊

  • @MoyendaChileka
    @MoyendaChileka 17 годин тому

    Walekhumu salamu sheikh

  • @chrismando224
    @chrismando224 21 годину тому +1

    Mbuzi Jimenez zikutitola kwambiri azayankha tym ikubwera

  • @NurjChilawo
    @NurjChilawo 22 години тому +2

    Chaķwera,akukokera burangeti mulifupi😂

    • @HanifaAdam-tm9yv
      @HanifaAdam-tm9yv 21 годину тому

      😂😂😂😂😂

    • @jamessheki4293
      @jamessheki4293 19 годин тому +1

      😂😂😂 akamafunda bhobho 6 am tambala wa number 4

  • @MdokaJames
    @MdokaJames День тому +1

    Masha Allah brother

  • @Eunice-v3m
    @Eunice-v3m День тому +2

    Abwelese poyela black box ameneo nde mau silum wazeru

  • @CeciliaJumpha
    @CeciliaJumpha 12 годин тому

    Mary chilima anayimba nyimbo yoti who allow the plain to fry without black box

  • @LuluKansonde-e6c
    @LuluKansonde-e6c 20 годин тому

    Good speech shelkh

  • @PetrusTlhokwane
    @PetrusTlhokwane 10 годин тому

    Tiyeni tigwilizane tonse ife a Malawi Chakwela tisamulore kupanga misokhano muma lijoni mupaka atuluse black box muona plan iyi ayitulusa

  • @AmbonisheJohnKayinga
    @AmbonisheJohnKayinga 21 годину тому +1

    Apanso inunso muyembekezere press briefing kkkk nde chikagawayo

  • @hastingskayange
    @hastingskayange День тому +1

    Ndipo a Moslem association ndikutaileni katengo chifukwa report lopanda uboni ochokela m black box uli chabe ndipo bolaso adangokhala osapanga inquiry zatitaitsa ndalama ndi nthawi yathu...mcp mpata mulibe inutu munene chilungamo basi ife amalawi tidzakunkhulupilirani ngati mutatulutsa black box basi😂

  • @osmanmdala-uh7xw
    @osmanmdala-uh7xw 22 години тому +1

    Lazarus Chakwera, the way how handle this matter "anthu takugwirani ufiti" but if your hands are clean, why don't you just come out call mr Kunkuyu to come with black box. He's a minister of information and he informed the nation that the black is kept safely...

    • @RodgersMwanakhu
      @RodgersMwanakhu 22 години тому +1

      Nkhani yonse yagona pa black box ,,,black box ndi mwini nkhqni

  • @GoodsonGeleta
    @GoodsonGeleta 55 хвилин тому

    Ndi report losakwanira koma popedza anthuwa uzimu alibe akuzimva udolo, koma Chilungamo ndizinthu zopweteka zinachitika zija 😊

  • @lawrencemsonthi6146
    @lawrencemsonthi6146 2 години тому

    Uku ndiye kulankhula anzathu a Moslem limbikilani cholinga dzikoli lidziwe kulemekedza munthu osankhidwa ndi ziko kuti sakuyenela kuphedwa wamba tithokozenso a Thomas Msusa momwe alankhulila tiyeni mukhale pa chilungamo ife timalimba mtima chifukwa cha inu atumiki a Mulungu wina aliyense onyodza atumiki a Mulungu afe ndithu idzi zikuyenela kutetedza aliyense mziko muno kuti munthu sakuyenela kuphedwa mwachisawawa

  • @FlynessWinga
    @FlynessWinga 22 години тому

    🔥🔥🔥🔥🔥🔥God fearing muslim

  • @JericoNkhoma
    @JericoNkhoma 22 години тому

    Muislam wanzeru siwaja wokonda ndalama, a dzakulangani Yehova.

  • @SolomonNjolomole
    @SolomonNjolomole 23 години тому +1

    Zina umangoona utaziyamba sure madzi achita katondo mcp.

  • @BreezeBarry
    @BreezeBarry День тому +8

    MCP have no chance

    • @TherryApasta
      @TherryApasta День тому +2

      Ndipo MCP iziona ankayenda mbali,a Christ ndi Islamic yawataya asala ndi nyau za zikwanje kkkkk😂 osawasiya akodwa okha pansampha

  • @MaryPhoya
    @MaryPhoya 20 годин тому

    Well speaking, sir

  • @WilfredKazembe-i6q
    @WilfredKazembe-i6q 23 години тому +1

    Enough is Enough Mr chakwera tell us where black box?

  • @FrancisNyayi
    @FrancisNyayi День тому +2

    Komadi no black box ahhh anthu sankhulupukiradi

  • @ProspaDMitummba
    @ProspaDMitummba День тому +2

    Ambuye akudaliseni pakuima pacilungamo

  • @user-tg7ls4vw9p
    @user-tg7ls4vw9p 2 години тому

    Where is the black box?😢

  • @Randy-er2xo
    @Randy-er2xo День тому +1

    Akapolo a mulungu azitere kuopa moto osati asatana agalu enawa mukalape anthu adyera inu

  • @ChrisLoyd-y5m
    @ChrisLoyd-y5m 21 годину тому

    Koma kwachema😂😂😂😂😂😂

  • @EmmanuelSimthole
    @EmmanuelSimthole День тому +2

    Nganiyitu ili very simpuloo tuluzani black box ngani itaa that's aoooo ine simsilamu koma sheikh uyu wayankhula moopa mulungu

  • @daviemungadetse1222
    @daviemungadetse1222 18 годин тому +1

    All we need now is the black box case crossed.simple