Ngati MCP inalandila Ben longwe uja ankati chakwera ndi osadula komaso Mai yolamu alibe zokoka lero akudya ndi chakwera uku akumupwala opanda zokoka Mai yolamu
Ndamvetsedwa kuti anthu a ku dera kwake amuza kaliyati kuti ngati akufuna kuti amuvotele pa uphungu abwelele ku dpp cifukwa dpp imapanga zimene munthu wakumuzi akufuna nde ngati akweni angabwelele ku dpp musadabwe anena ndi anthu akwawoko. Adad ndiomwe ali mmitu ya anthu
Oooh! Yes, she fits well in DPP. She would be getting back home. I party of angry leadership. Listen to their press conferences,always looking angry. If there is no thaw in the presentation, DPP will prequalify for for the opposition.
Good idea for kaliyati to go back to dpp,
Atha kubwelera ku DPP no problem,, Mu Ndale mulibe udani wokhazikika ndiye tingoti phee tione.
Abwelele mai anthu ku DPP ❤❤❤❤
Akweni ali ndi ufulu wo choka,chipani cha UTM ili ndi anazikambe okhaokha,akweni has stood by UTM as a true hero
Ngati MCP inalandila Ben longwe uja ankati chakwera ndi osadula komaso Mai yolamu alibe zokoka lero akudya ndi chakwera uku akumupwala opanda zokoka Mai yolamu
Apite ku dppko adzatipeza tikalowa m'boma chaka chamawa
Ndipo kupangila zithu mphuma sizingawapindulile Kodi amafuna anthu onse awine Kodi aaaaa asaonetseso umbuli nawo akaliati mwava kabambe anamusakha ndi anthu osati amalowa ekha ayi ngat sakufuna akhale ubwino wake mulungu akaloza waloza utm idzidzimutsa anthu next year take it or leave it
Pitani mai ku dpp
I agree with you atabwerera zicita bwino kwambiri tizinena zoona dpp imatha zipaso zace ziripo mwaaona abusa mayankhidwe ao kunyumba ya parliament kurephereka kuti angoti zoona zinthu sizilibwino komakumangoonjezera kuwawisa amarawi ntima
Kalowe ku dpp ndpo tikakuvotera
Upepera Kweni
Zisiye za UTM
Ineso ndikufuna kuyima as Member of Parliament ku Tchisi ndipiteso ku DPP hahahahahaha koma ndaseka kufuna kukapeza zero
Mlimotsemo kaliati iwe umakwana ku DPP ku UTM you are welcome kupatula ku MCP kokha ayi utsaelekedze,Akweni DPP ,UTM kaya Aford ndi bho bho basi
Ndamvetsedwa kuti anthu a ku dera kwake amuza kaliyati kuti ngati akufuna kuti amuvotele pa uphungu abwelele ku dpp cifukwa dpp imapanga zimene munthu wakumuzi akufuna nde ngati akweni angabwelele ku dpp musadabwe anena ndi anthu akwawoko. Adad ndiomwe ali mmitu ya anthu
Mai kaliati ngati akufuna kuti akhale mp pakufunika kuti alowe Dpp basi
Abwele akweni basi zabobo
Kwao ndi chipani Cha DPP akawinaso uku
Abwerrere akaliyat ku DDP akawina musamvuta u mp
Akabwelera ku Dpp adzawina
kkkkkkk😂😂😂😂
Sumadziwa kukamba nkhan iwe
Akweni kumbuyo sitibwelerako pitani chisogoro timakukondani musatigwetse mphway ife
Akufuna kuthetsa UTM Awa mbuzi za anthu ndi galu kwabsi kaliati
Khalani mu UTM mamie
An opportunist polician.
Abwelere akweni Ku DPP Ife tisangalara kwambili ❤❤
Oooh! Yes, she fits well in DPP. She would be getting back home. I party of angry leadership. Listen to their press conferences,always looking angry. If there is no thaw in the presentation, DPP will prequalify for for the opposition.
go back ku DDP mamie
Olo atabwelela tkhoza kumulandila ki dpp
Ndife amodzi ubwino wake..Dpp+Utm umodzi mulimphanvu
Aka Akalowe ku dpp ndi akakhala mp kwawo akawina mosavuta
Taikonda imeneyo❤❤❤❤😂
Appange momwemo abwere ku dpp
Zamuvuta kweni😂😂😂
Inetu ndikugwiri zana nazo zoti apite ku D p p
Waganizabwino
Good
Good decision go back to dpo
❤🎉
😂😂😂 sitimavotera munthu ife koma timavotera chipani
Zikawoneka ndinthu
Tiyen ku DPP mayi anga
Abwelele ku mudzi
Abwerere ku DPP ndipo adzapambana u MP..?UTM manyaka sangawine ali mu UTM
Abwelele ku dpp
Bwelani akweni takulandilani kale tilibe nanu vuto
AKWENI AKWENI bwelani malo alipo
Okay
😂😂😂❤❤
Kkk😂😂
Good
❤❤❤
Lowani dpp mupambana kwinaku mmm
Zakhala bwino
Eya abwerere ku DPP ndi kwao balibe chovuta tiwalandira ndi manja awiri 🎉🎉🎉🎉🎉🎉🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳🥳
Koma adzapezeka wa mtima ofuna kutumikira a Malawi posayang'ana udindo? Mayiwa akundikumbutsa royalty yomwe anali nayo pa a chilima
Vuto sanapange chiganizo choyenera Kt aime u pre, u SG akanawina mosavutikira chipani akanachigwira bwino kma apapa eeee sizinayende mayiwa skc anaima nae munyengo zambiri 😢
Sono za manganya zili pati???
Azipitaso ku tikuferanji kkkkkkk
Zionek
Tikufelanji ija adakonzaa😂😂😂
Samachedwa kukwiya musiyeni abwelere ku dpp ko vuto palibe