Bushiri ur a great man that's why ur very blessed I wish if Malawi having too many people like u Bushiri who thinking about there homeland ur great indeed keep it up God bless you more
My Father My Prophet you are doing great job . You are creating work also for Malawians generation . I tap into your Annointing my Prophet . May God bless you all your Enemies will Scarter one by one Molly limpopo
The annointing of Papa Bushiri breaks the yokes of poverty. Try it. You don't know the businesses Bushiri has. Why being so rough without the knowledge of his wealth and Riches. He is the third richest person in Malawi nde mumati ndalama azitani nazo? They devil will never be happy with a progressive person
A Malawi Munatani kodi kumangovuta pa zinthu zopanda pake MAJOR 1 akufuna kutimagira Town mukufuna kumufufuza chiyani at least he's creating jobs zomwe Atsogoleri athu saangakwanitse koma kuba basi ndi ma slangs and fluent English opanda pake hands of BUSHIRI Manga Town SHEPHERD...👏👏💪 Let Them Talk, Idiot's come on Homies If you want someone to investigate I'm gonna show you where to go Pitani ku TONSE ALLIANCE that's where you'll find thieves,mbava,akamatule,matsotsi,wawii,🤞😊
Kkkkkkk OK fine.... Please people stop being jealous,instead of focusing on your demonic poverty , you waste time with whom YAHWE blessed... Learn to love one another.. Learn to thank God......
Enemies of progress.Bushiri is doing this for the betterment of the country. This is malawi property,bushiri is just engineering.its the government which is going to benefit
@@olipamaseko2693and so???? Nde mukufuna kuti munthu atani kodi. Olo Chakwera atasiya kupusa kwakeku this country can’t still go further because of people like you. Bitter and pathetic person
Nchifukwa chake this country can’t go further because of sick and twisted people like you. If you don’t like him very good but don’t shit on whatever good thing he’s doing. And he didn’t ask you to like him or not. Tabakhalabe pa umphawi wakowo mfiti iwe
Wakuba wabela anthu ambiri ku south aafrica, amawanamiza anthu ambiri aike ndalama ku acount yake miez itatu apeza ndalama zambili ku ma count ao, ambiri akulila
Dziko likufunika kukhala ndi munthu ngati uyu,uyutu amadzigwilila ntchito pa yekha wosati zomaba misonkho ya anthu.papa yr great wishing yu best mwatimasula amalawife
Bushiri ur a great man that's why ur very blessed I wish if Malawi having too many people like u Bushiri who thinking about there homeland ur great indeed keep it up God bless you more
I just like the way you express yourself in chichewa its so amazing and keep up the good work
That's a great city for many Malawians let's learn how to appreciate this our man of God 🙏
I salute Bushiri, he is one of a kind
Creating jobs for the young people
He is agood man coz he is dealing with poverty,big up B
Best wishes to man of God. Continue your work. God is with you.
You are doing extremely well Sir I like your tone. U got a very bright future. God will exalt you this year. Stay focused and pray more
Hard workers always think about changing things .All the best man
That guy has got gold mines here in zambia 🇿🇲 and different countries
Where in Zambia?
He is doing great work to develop Malawi
t
He is going great work to develop Malawi
such a very good tone,Bushiri is doing such a good job
My Father My Prophet you are doing great job . You are creating work also for Malawians generation . I tap into your Annointing my Prophet . May God bless you all your Enemies will Scarter one by one Molly limpopo
Love the Bushiris keep it up and God bless.
Goshen City is a product of powerful vision
Dziko la malawi silimatukuka ndi nkhani ngati zimenezi. Munthu ngati akumanga town yamakono ngati imeneyi mudziko lathu.ife bwezi tikuonesa chikondi kwaiye ndikumulimbikisa osati kumufookesa pazinkhani zopanda Pache. Anthu akatangale akuwaziwa kale bwanji osamakawafufuza amenewo
Let him to fulfill his duties,. He's so young, hope will do mo than that. All those jealous people must fall. Almighty bless him
Hanifa you are the best ♥️♥️🙏🙏
I will always support bushiri he is a true citizen of Malawi
I salute you Bushiri I will be Uber driver there
Ife anthu akuda ndichoncho sanje kwambiri i respect him a lot
Just wow
Beautiful masophenya
Good work Prophet Bushiri
Vuto ndilokuti ife a malawi makamaka kumipandoko kwachuluka achule kwambili mwachisanzo ine ndili kuno ku south Africa ndapedza ndalama ndithawile dziko lakwathu adzafuna kundifufudza ndiye uchulewo ugalu a aphaka Bushili akufuna kutukula dziko lakumalawi ndiye pakupedzeka agalu ena monga amulaka malilo ndijelasi yao kudzolowela kuvutika ugalu basi Bushiri akufuna kutukula dziko lamalawi
Don't be jealous with someone who is doing great work,because that city will change many Malawians
The annointing of Papa Bushiri breaks the yokes of poverty. Try it. You don't know the businesses Bushiri has. Why being so rough without the knowledge of his wealth and Riches. He is the third richest person in Malawi nde mumati ndalama azitani nazo?
They devil will never be happy with a progressive person
🔥🔥🔥Wabwela ngat coming
💪💪💪
Perfect
this is great💯
We need ro underatand in english too. Inam in South Africa.
Great ideas
Akulephera mapulesident kutukura dziko lanthu ineyo ndingoti Malawi mwana tingathe kumaloza chala kwaathu kuti town yakwathu iyo mulungu pasongolo basi
A Malawi Munatani kodi kumangovuta pa zinthu zopanda pake MAJOR 1 akufuna kutimagira Town mukufuna kumufufuza chiyani at least he's creating jobs zomwe Atsogoleri athu saangakwanitse koma kuba basi ndi ma slangs and fluent English opanda pake hands of BUSHIRI Manga Town SHEPHERD...👏👏💪 Let Them Talk, Idiot's come on Homies If you want someone to investigate I'm gonna show you where to go Pitani ku TONSE ALLIANCE that's where you'll find thieves,mbava,akamatule,matsotsi,wawii,🤞😊
Thanks for budget
That's great
Greatest man
Man of God who only does God mind not him
Boozaa anthu ake ati omwe alembedwa ntchitowo mphekesela ya boza iyii
Major one
Great job
Komatu anthu mupole moto... Mmalo mopanga njira zothana ndi umphawi omwe satana anakutembererani nawowo.. Mukulimbana ndiwo mulungu adawadalitsa, kutaya nthawi ndi za zii limbikirani kupemphera siyani msanje, mulungu adzaona mokudalitsira musiyeni Shepherd Bushiri apange zothandiza human kind
More fire
I like profet he only does God mind not his
Please do the same content in English to enable none Malawians understand
Unless you are from Zambia and some Zimbabwians can understand
It's none of foreigners business
Kkkkkkk OK fine.... Please people stop being jealous,instead of focusing on your demonic poverty , you waste time with whom YAHWE blessed... Learn to love one another.. Learn to thank God......
Ohhh? At least
Nice job
Bushili ndi one akupotsa president ulemu wanu a bushili za ndare simupanga nawo koma kukwedza malawi pa sogolo ..koma muzandilembeko tchito
Aaa pajatu Malawi is full of kaduka,,enawa angofuna amudyere
Zoona zake afufuzidwee munali asadiki miya muzikomo olemera oti amatha kukuthandiza boma lo koma sanafikepo apo fufuzani ndithu
Is right
Akurephera chakwera kutukura ziko.rino angoononga ndarama chakwera chito zamanja ako zikuchitire umboni bushiri
Nsanje aMalawi iiiii munthu akapanga chinthu basi zokamba mbweeee
Bushiri uzangokhara president
Malawi goas on
Vuto la amalawi ndinsanje basi
That is the problem of Malawians
Ndi izi mukuziona ku ma comments kuno, anthu a nsanje akumunyozabe m'malo moyamikila kuti a Malawi ambiri apeza ntchito kumeneko, komanso dziko lathu litchuka ntchito imeneyi ikatha.
That's why ziko lamalawi lizakalabe losauka mphaka kale kale amufufuza bwanji ngati ziko lamalawi labeledwapo nsaja basi ziko losafuninara anthu zabwino
Ndipo iyi nde ndi mfundo ndithu
A Malawi sanje mlekeni atukule dziko lathu la Malawi
bushiri ndi munthu modzi wachuma yemwe akuyika pa map malawi
Ndimafunisisa utazakhara president malawi ikhoza kukhala yopambana ngat wakwanisa kumanga ndalama zayekha kulibwanji athakhala president buchiri ndimakufila kuzakhala president ndizabwerera kumalawi
The first to comment and hopefully will be the first resident of Goshen 😂
L
But your report doesn't relate with the title of your presentation. Improve pliz
Murekeni munthu atukure marawi
Mzinda umeneu u kubwera ndizolinga chilipo akufuna ku Malawi kuno ndpo zomwe anthu awa zolinga zawo zikwanilitsidwa ndipo akufuna Malawi ankhale mbali imodz yaa tow omwe amachita za satana
Moti musangalale akubwelesa
Chitukuko ku malawi sanjebasi
Nsanje amalawi.. Musiyen bushiri atukule dzulo lathu
A Malawi ambiri amadana ndi chitukuko amafuna kuba chabe, Bushiri asaope munthu.
Nzoona ndithu
Let him to do what he want to do and moreover he is doing that in his country, so let those dogs who has jealous with him to smile urine
Maiko azathu anthu ngati amene ndi amene amatukura dziko,
Kkkk kma guys mawu awa akuyenera munthu wa ndemvu ku face
Ok
Enemies of progress.Bushiri is doing this for the betterment of the country. This is malawi property,bushiri is just engineering.its the government which is going to benefit
Malawi akukanika kutukuka chifukwa chansanje
Ppl are serious wth him ......for show bushiri is doing good jobs for better malawians
Humm
Gays tangoyamikilani muthuyu popangachiganizo chotukula zikolovesa chisonili ngati palizolakwika aakoze ndimulungu
Zokaikitsa ndalama zake aaa
@@olipamaseko2693and so???? Nde mukufuna kuti munthu atani kodi. Olo Chakwera atasiya kupusa kwakeku this country can’t still go further because of people like you. Bitter and pathetic person
Mlandu Ukudikila ku South Africa Aonetse chitsanzo chabwino
Okay?
uyu akhale vice
No need of AcB because he z not apolitician
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
AKADAKHALA KUTI ANTHU ENANSO AMAKHOBILI AKU MALAWI ALI NDI MOYO AKUONETSA A SHEPHERD BUSHIRI PANOPA MALAWI AKADAKHALA ATATUKUKA KOOPSYA
Ndipo nzoona kunoku anthu ake ngansanje yauchitsilu nayo
Wabwera mwa coming
Muuze bushili mon
Aaaa ndalamazi aaaa
Papa help me to change my life
nsanje ndimene yakula nsinkhu
You have to screen this man the so called Prophet, whenever he got his money and how he made it, because this doesn’t look normal at all.
Sanje amalawi musiyeni munthu atukulemalawi
Iwe anthu azakumangisa.
Sanje amalawi
Channel ichi sindichikhulupirila anta
Amaphatikiza choonadi ndi bodza vuto lake ndilimenelo
Apanga bwino nd2
🇲🇿Hi
Zot zikuyenda chifukwa cha a Bushiri nde bodza the guy is bad luck kungobwera zinthu kuzsiiratu kuyenda kumalawi kuno. I dont like this guy
Nchifukwa chake this country can’t go further because of sick and twisted people like you. If you don’t like him very good but don’t shit on whatever good thing he’s doing. And he didn’t ask you to like him or not. Tabakhalabe pa umphawi wakowo mfiti iwe
Bushili is a hill
Wabodza iwe
Amange Malawi basi
Zasatanic basi mboli yako iwe
you need to speak in English
Wakuba wabela anthu ambiri ku south aafrica, amawanamiza anthu ambiri aike ndalama ku acount yake miez itatu apeza ndalama zambili ku ma count ao, ambiri akulila
Dziko likufunika kukhala ndi munthu ngati uyu,uyutu amadzigwilila ntchito pa yekha wosati zomaba misonkho ya anthu.papa yr great wishing yu best mwatimasula amalawife
Do you hv a proof for wat u a sayin
Tazingogwirani ntchito apa... wakuberanipo chan chanu kapena cha makolo anu?
Then akuba bwinotu coz he is stealing to help others